May GOD bless you all the time Father Nthalika, anatenga Boma kuti atizunze anthu awa, Mulungu awasegure mason awone momwe amalawi akuzunzikira, Nonse omwe mumalankhulira Boma muopen Mulungu musanalankhu zanuzo.
Lazalo munthu oyipa mtima kwambiri ndipo umunthu unachoka kale kale mwa iye,zoti ankatumikira nkachisi wamulungu ndakayika ndithu. Ambuye atichitire chifundo atichotsere chipsyinjo chimenechi,Lazalo ndi chiwanda. Tiimba bwanji nyimbo ya Chauta ku Bagamoyo.