uncle k apapa mwatichita nkhaza , mukanamaliza part iyiyi 🤣🤣🤣 ,anyway pamenepo mwayitha coz ma guyz awaw amakhulana kwambili chifukwa cha Lucy ndiye zilibwino akumana onse inuyo mulipompo as a street lecture
Kantande wamela mizu Hahaha mpaka zafika pamenepa ayi ndithu zikomo koma Uncle K drama mukupanga pamenepa mukufuna kuti Lucy apange bwanji hahaha Come on street lecture is that a joke 😅😅😅