My Best actor CHICCO koma samatenga mbali kwambili mfanayu amandiwa Maka akamanvana ndi Jah Man 👞 zimandinvekela kuti film yapsa bwino any way zili bwino kwambili
Alliance ya Lucy ndi Linda eeeee Noxy alipavuto kkkkkkkkk........Kantande wayaka moto pamene amupezere Noxy kaya zikutha bwanji kaya 😊😊😊😊.............Uncle K inuyo mumatha , mwamudekhetsa Ivy 😅😅😅😅😅😅..........aProfet apapa inuyo mwadya 1 , mtumiki wamulungu aziyanjanitsa anthu keep it up Mr Prophet...............
Kamtande wangomenya flash kkkkkk Koma akazakumana ndi Noxy ndiye zizitha bwanj. 😅😅😅😅😅Inuso a busa kungoyenda chamnyang'a bas muli pameettting ndi a Food organiser kkk. K50 pin yachepa, abusa ,musazunguze a food organiser mutu😂😂