Тёмный
No video :(

GWEDEGWEDE LERO NDE KUNALI KUGUDULA NDIWO ZAGULU | ZITHUNZI ZA ANDUNA KUNO | 

DZIWE TV
Подписаться 28 тыс.
Просмотров 23 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 35   
@kadijachilwan967
@kadijachilwan967 Месяц назад
Apolice amaonjeza nkhanza pansewu😢
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Месяц назад
Zikhale ng'oma ma bombasa wagulakoso 😂😂😂 wausilu iwe
@giftmasenti5732
@giftmasenti5732 Месяц назад
A Traffic police ambiri za miyoyo ya anthu alibe nazo ntchito nde ndizimenezo
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 Месяц назад
Powerful GwedeGwede,,bambo banda
@CatherineDesire
@CatherineDesire Месяц назад
Chipewa cha khwangwala kuteloko amafuna anyemere kaye kuti adutse ndi mwana wodwala ,utsilu dyera
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk Месяц назад
Kkkk chipanda kuyankhula bwezi ali mumaguza omwewo kkkk
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 Месяц назад
Live from south Africa cape town
@B1Chitatata
@B1Chitatata Месяц назад
Salute
@SurprisedDrumKit-ql7rj
@SurprisedDrumKit-ql7rj Месяц назад
Za police mbuzi zaanthu izi kma kuba ndikupempha
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Месяц назад
Munadza makosana ❤❤
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Месяц назад
😢😢😢😢 apolice apamalawi vuto ndi umphawi anthuni
@MerryWayson
@MerryWayson Месяц назад
Sitidya ndale kkkk ndimakunyadilani kwambiri Mibawa TV
@ishmaelchirwa9303
@ishmaelchirwa9303 Месяц назад
Anduna akutsotsola ulusi pano akuti kuionesa 😂
@mathewsmdzanja3276
@mathewsmdzanja3276 Месяц назад
I salute mibawa
@user-gw2zb8pf7n
@user-gw2zb8pf7n Месяц назад
Mwanayo anali ndi 1 month and 3 weeks mgalimoto ndinali MO ine😢
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Месяц назад
Chakwera mumuudzeso kuti opha nzake afeso chifukwa chakwera anapha chilima my boss he call chakwera bull dog😂😂
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg Месяц назад
Mumakwana guys 💥
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z Месяц назад
Zoonadi apolice amaonjeza
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 Месяц назад
Nkaka akulembaso MSCE
@HarryMasamba
@HarryMasamba Месяц назад
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkk Komatsu dzina izi
@LucianoKapepuza-sy9wx
@LucianoKapepuza-sy9wx Месяц назад
Nawo a MCP asatile malamulo a gwirizano wawo kuti apite s Utm asogoleke nawo
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Месяц назад
Ndipo apolice akumalawi ndinu otembelekdwa ndipo mukulephela kugwila mbava koma kulimbana ndi athu osalakwa
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 Месяц назад
Steve ndi Selina mativesa kukoma
@StevieChikaonda
@StevieChikaonda Месяц назад
Muli ndi mtopola guyz😊
@dumisanimoyo3152
@dumisanimoyo3152 Месяц назад
Tisakubisileni apolice alowa chiwewe kusaka ndalama
@user-lc3sw8iz2g
@user-lc3sw8iz2g Месяц назад
Ku malawi zimathera tikufufuza.
@user-jn7bt1uy5s
@user-jn7bt1uy5s Месяц назад
Mbambande mibawa
@user-bc2mu2ns5n
@user-bc2mu2ns5n Месяц назад
Futso nkhumati kodi sopano kubako mwathana Nako?
@gwatandingo9502
@gwatandingo9502 Месяц назад
Wanga kufa mwana chifukwa cha wa police wandigwira nayeso adzafera pompo ineyoso natopa nawo mbuzi zimenezo pofunika osamawanyengelera😢😢
@CatherineDesire
@CatherineDesire Месяц назад
Va police palibe vomwe vikuchita vimangodziwa kupempha ndrama pamseu ndikumanga mbava yoti anthu aigwira kare anthu eniake,ndipo vitengelepo phunziro mwina vingayambe kugwira ntchito bwino vipewa va mbalevo
@AlasonPaulo-ht7zb
@AlasonPaulo-ht7zb Месяц назад
Zoonadi Inu muli bwino kwambili
@MosesShaibu-ee8hn
@MosesShaibu-ee8hn Месяц назад
Madokotalanso ali ndivutolawo munthu akumuwona ali pamzele komakungobwelawinawake wawudindo amakudusila chifukwachani winayusi munthu kodi?
@NaduMbewe-zz6iw
@NaduMbewe-zz6iw Месяц назад
Kkkkkk
@WysonYohan
@WysonYohan Месяц назад
Malawi tingogulisa tigawane ndlama bc
@OfwaMwambila
@OfwaMwambila Месяц назад
If u stopped by the police officers on the road in ur 🚗 .who is supposed to follow the other? 4me i don't go out to a police office who stopped me coz i had no intention of stopping.u stop me,u come to me &tell me why you stopped me not me coming to ask u
Далее
WANG'ALURA UKU AKUPHUNZITSA SAKUOPA ALIYENSE  |
29:10
Просмотров 4,6 тыс.
GWEDEGWEDE  20 AUGUST 2024 |
24:13
Просмотров 14 тыс.
ANG'ALULA MOSAIPA LERO PA 10 July 2024
27:53
Просмотров 20 тыс.
CRUISE 5 WITH ISAAC JOMO OSMAN
1:11:28
Просмотров 60 тыс.