Тёмный
No video :(

Ine ndi wa MCP koma zomwe andipanga a Mcp zandililitsa (Isiah Sungamoyo) 

Malawian Cameras
Подписаться 28 тыс.
Просмотров 48 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

19 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 565   
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i Месяц назад
If you were a wise person, you would cry out to God and not to a sinner like Lazarus chakwera
@inutuinutu5573
@inutuinutu5573 Месяц назад
❤❤❤
@giftmwale8475
@giftmwale8475 Месяц назад
Who the hell are you to judge chakwera
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i Месяц назад
@@giftmwale8475 is chakwera an angel? I know you are one of his praise team members, as long as he is not an angel,he remains a sinner,You cannot understand the pain of justice.
@ChimzOliver
@ChimzOliver 21 день назад
@@inutuinutu5573 aaàaaaaààà
@NyarineJames
@NyarineJames Месяц назад
Mr Isaiah Sunganimoyo, palibepo chipongwe pamenepa. Yemwe wapangidwa chipongwe choipa ndi Dr Saulos Chilima.
@NoluvuyoMatutu
@NoluvuyoMatutu Месяц назад
serious aaah km ndaseka 😂😂😂
@ChristianMtambalika
@ChristianMtambalika Месяц назад
Kuti ifeyo tikhululuke tiuze amene anapha chilima
@MisheckAselo
@MisheckAselo Месяц назад
For sho 😂
@AlexGomani-ss5nj
@AlexGomani-ss5nj Месяц назад
Kkkkk for real bro
@vicshyma5644
@vicshyma5644 Месяц назад
Ndipo live
@user-yi2fg1lh8x
@user-yi2fg1lh8x Месяц назад
Anenedi timukhululukila
@EvanceSungani-cv9jk
@EvanceSungani-cv9jk Месяц назад
😂,
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d Месяц назад
Zakuchipani kwanu zimenezo Ife zisatikhuze iyaaaa
@mavmsusa1310
@mavmsusa1310 Месяц назад
Ndiye Ife titani tsaano, Ochewa? Potidziwitsa dzani apa?
@Yusufu-Daudi
@Yusufu-Daudi Месяц назад
🤫🤫🤫 ife phee Kuma stand kuyang'anira bs kuti zitha bwanj
@JasonMailos
@JasonMailos Месяц назад
Kkkkkk
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp Месяц назад
😂😂😂😂😂 waidziwa congress
@NoluvuyoMatutu
@NoluvuyoMatutu Месяц назад
😅😅😅😅😅
@AchinaKellz
@AchinaKellz Месяц назад
kkkkk Malawi chikangawa party 😂😂😂😂😂mbuzi ikathawa nsipu ndie kuti pali linthumbu, vuuuuuuu😂
@nellybruhan5834
@nellybruhan5834 Месяц назад
Awa asakhale kuti atumidwa ku chipani chaocho kuti azikapanga snitch ku opposition, plz otsutsa musamulandile uyu akuonongelani zinthu
@user-hw5xx9kb2s
@user-hw5xx9kb2s Месяц назад
100 % ndikazitape ameneyu
@PeterChilombo-ou2cd
@PeterChilombo-ou2cd Месяц назад
@@user-hw5xx9kb2s wabodza uyu akayambitse cake cipani akuphetsani cokaa tiyeuko
@ChikondiKwengwere
@ChikondiKwengwere Месяц назад
Munthu angatumidwe izi kkkkkk
@nellybruhan5834
@nellybruhan5834 Месяц назад
@@ChikondiKwengwere musapusisike inu, this is the time that people do unimaginable things to get what they want... Walandila ndalama uyu ku chipani chaocho... The cry is very fake just to buy Malawians sympathy
@EthelKspito
@EthelKspito Месяц назад
Osamulandiladi watumidwa uyu kulila kwa boza kazitape
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Месяц назад
Takhala tikumvani thawi yonseyi, yimeneyo ndiyo MCP. Tathokoza kupepesa kwanu ku zipani zomwe mumanyoza. Pangani chisankho chabwino
@user-px9gd6fc6w
@user-px9gd6fc6w Месяц назад
😂😂😂😂😂😂😂😂 best comedian of the year mulowa malo wa abambo asikono
@blessingsmimu5236
@blessingsmimu5236 Месяц назад
😂😂😂
@sufiammadi
@sufiammadi Месяц назад
Mupwetekana ndithu ife ku ma stand basi 🙌🙌🙌😂😂
@aminkums515
@aminkums515 Месяц назад
You are still young mr. MCP sukuidziwa . U can feed a dog in 1 day and the dog Will not forget you in whole life. Dog is better than mcp
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b Месяц назад
Mawu akulu akoma akagonela kma timayakhula ife kuti fisi ndi fisi ngakhale atasintha phiri akakhalabe fisi njoka ndi njoka singasinthe mamba 😂😂😂😂
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 Месяц назад
Ungapereke moyo ku MCP 😅😅😅😅 ndiwe galu kwabasi,komaso umanyoza asilamu usiye udzawona zoposa zimenezo
@MicaelGraciano
@MicaelGraciano Месяц назад
😂
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona Месяц назад
Iwe ndiwe chitsiru tsopano uti titani iwenso ndi chako pitiriza MCP.
@user-sb2mw3xz4j
@user-sb2mw3xz4j Месяц назад
Okay takumvani nde tiuzeni now za kuchingangawa forest
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 Месяц назад
Iwe ndi amene unkaletsa achina bon kalindo kupanga mademo mu lilongwe ndie lelo ukulila chiyani
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Месяц назад
😂😂😂Ndankumbukila galu uyu
@frankmamu413
@frankmamu413 Месяц назад
😂😂😂😂
@clojistix_g
@clojistix_g Месяц назад
Mu ndale mulibe ubale kapena udani wa muyaya, you've learnt your lesson hence make the right decision, the parties you both criticised and castigated are more than ready to welcome you. However, from today onwards be patriotic to your country, the people that voted for you and a party that [at least] has the welfare of people at heart. Blind patriotism is what you've been practising and now have learnt a bitter lesson. As my President's norm in all his rallies, let me equally follow his steps..... (1) UKAKHALA PANSANA WA NJOVU USATI KULIBE MAME (2) MUKADZONA NKANGO UKUTHAWA TCHILE NDIYE KUTI WAKUMANA NDI KANUNGU. Miyambi yalero ndi imeneyi, zikomo.
@jeanbotomani9081
@jeanbotomani9081 Месяц назад
Chikangawa party mumphana muona
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn Месяц назад
Tachokakoni inu kodi bwanji mukhala ngati za MCP sim'mazidziwa pitani ku zipani zinazo
@juliusnjerengo2610
@juliusnjerengo2610 Месяц назад
Iweyo wekha akanakupha zikanakhala bwino kwambiri.
@fae6833
@fae6833 Месяц назад
akuchitabwino kwabasi. mudyana nonse nding'ona zokhazokha
@user-cw6jg6xg7h
@user-cw6jg6xg7h Месяц назад
😂😂😂😂
@user-gd6zb2bv8f
@user-gd6zb2bv8f Месяц назад
Kuli bwino kumenyedwa ndi dzina la Yesu osati za Chipani
@raytavares2256
@raytavares2256 Месяц назад
You gave your life to me mortals instead of serving and surrendering your life to YESHUA HAMASHIACH and preaching the gospel of salvation, I hope you learn from this and SERVE GOD ALMIGHTY ONLY. ❤❤❤That's a sign because you left the place alive and had it been not for the mercy of the ALMIGHTY GOD. Now you want empathy from the oppressed people you have been ignoring.
@PharrohmagawaZimba230
@PharrohmagawaZimba230 Месяц назад
Mutayambana ndi asilamu mumayankhula ngati ndinu mzeru
@HamzahJohnathan
@HamzahJohnathan Месяц назад
Anthu akupha inu a MCP zigawenga ndi garu chakwela
@user-sl2dz8dv8m
@user-sl2dz8dv8m Месяц назад
Mr Sungani Moyo,dziwani kuti moyo wanu ulimmanja mwa Yehova,Zindikilani kulemekeza anthu onse,okusamalirani mmawa simumuziwa.Ambuye alemekedzeke kuti mwaphunzira
@user-cy5ko2qw5d
@user-cy5ko2qw5d Месяц назад
Chikangawa party kapena kuti ng'ona party ndiyoopsa 😂😂😂
@annamazingashaibuh6276
@annamazingashaibuh6276 Месяц назад
😂😂😂😂😂
@user-zf7xk8fk5s
@user-zf7xk8fk5s Месяц назад
Uyuu ndi mbuzi yosasamba chifukwa zomwe amayakhura zaunsiru kwambr end akufun kumatitorab kupusa amalaw ndip adzikambiran komweko ku mcp
@JacobKasalika
@JacobKasalika Месяц назад
Aaaa iwetu zinakuvuta kale, so ukupempha support Poukila chipanichaki.
@temwarachaelkhonje3733
@temwarachaelkhonje3733 Месяц назад
Its the "ndalakwa shaaaani....ndalakwa shaaaan...." for me😂😂😂😂😂
@ChisomoKapanda-jg2uf
@ChisomoKapanda-jg2uf Месяц назад
Mene ndasekera ine😂😂
@KwestalanjesAjangale
@KwestalanjesAjangale Месяц назад
Tangotiwuza chimene chinapha chilima apa osati mbwelerazi
@Yusufu-Daudi
@Yusufu-Daudi Месяц назад
Nde ukutiuza ife kuti titani, vuto ndi dyera likupweteketsa sunati zimene wakumana nazo ndipang'ono chabe zeni zeni zikubwera
@happychimwemwe-1805
@happychimwemwe-1805 Месяц назад
Zako zimenezo pa chichewa amati odayanjana oleke
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw Месяц назад
Amakupha ndinasi kumene ngati mmene chakwera anamuphera chilima
@user-mr3vw1ym3r
@user-mr3vw1ym3r Месяц назад
Vuto lake anyani Akongeresinu kusamva, mumayikonda MCP kuposa moyo wanu komanso kuposa Mulungu, akangokunyengelera tikuona utabweleranso, ndiye ngati uli wa nzeru ukungoyenera kuchitaya chipani chimenechi koma ngati suchitaya ukadzaphedwa adzakhala mavuto ako amenewo.
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 Месяц назад
Ife sizinatikhuze nao zanuzo amwene lero zakhala bwino kuti waidziwa mcp kuti ndiyakupha
@user-un7rc7qg4w
@user-un7rc7qg4w Месяц назад
Dyela silabwino uziona wakula watha big man
@VictoriaWilly
@VictoriaWilly Месяц назад
Mufunse akulu akale akuuzeni za MCP. Vuto Ana a masiku ano makani kwambiri simuziwa kuipa kwa mcp. Ndiye phunziro ndi limenelo.
@JoelMwenegamba
@JoelMwenegamba Месяц назад
Just pray to God u r still arrive mcp imapha samala.
@user-xe5lb4uf3n
@user-xe5lb4uf3n Месяц назад
Vuto munasankha molakwika. Munthu wabwino ngati iwe mbale wanga kutsatira MCP. Anthu akupha awa . Mukafuna kukhalabe ndi moyo sankhani Chipani china. MCP IMENEYO CHIPANI CHAKUPHA ICHI.
@CatherineDesire
@CatherineDesire Месяц назад
Chakwera kukamwa chimlomo chapasichi ngati chule kulowa mkati 🙄🤣🤣🤣🤣 ka Chilima kanali handsome akulu
@giftedmshan6779
@giftedmshan6779 Месяц назад
Osat game wayionela patali kut 2025 kuvuta
@HenryChapananga
@HenryChapananga Месяц назад
Ndiwee galu kwabasii usazabwerenso kuno,,, koma lzeck rip
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i Месяц назад
Zakudya zikasowa ng'ona imadya olo mwana wake kumene...mudyana simunati.....
@MicaelGraciano
@MicaelGraciano Месяц назад
😂😂😂
@user-ey6in8is5h
@user-ey6in8is5h Месяц назад
Wazidziwa liti "Lucious Banda "song!!
@Environmental_scientistmsc
@Environmental_scientistmsc Месяц назад
Amutuma uyu ndigalu cholinga akufuna azifuna kulowa UTM kuti azikatola mabodza musachilore chimenechi
@mtenderemitembe3433
@mtenderemitembe3433 Месяц назад
Zandale zopanda phindu. You're still young you can be concentrating on entrepreneurship and build Malawi you have the ability. Use your money wisely. Energetic as you are you can do something contributing to the country.
@Hassanhasssen
@Hassanhasssen 26 дней назад
Nkodo mesa umati ndiwe owopya kwambiri wakhala ukunyoza asilamu bola pamenepo akuchita bwino mulungu ndi wankulu AIHAMUDUIIH mulungu alipo
@nyuchikphiri4221
@nyuchikphiri4221 Месяц назад
Kupereka moyo wanu kwa munthu osati mulungu?muli ndi tsoka.ngati ukuzembera UTM ife ayi.khanali ku mcp konko mudziyedzekana
@morrismjere3927
@morrismjere3927 Месяц назад
That's what happens if the party is full of cowards. Phanani nokhanokha
@MikeMwale-bw1xw
@MikeMwale-bw1xw Месяц назад
Adamera mapiko anzanuwo adayiwala komwe achoka😂😂😂 Auzeni azikumbukila mtsogoro moyo, mmbuyo moyo.
@RamseyWasi
@RamseyWasi Месяц назад
What if mkanalandila kenakake lero, Mkadaliuza DZIKO kuti mwalandila ntereshede???? Ndaale ndi CHILOMBO CHOOPSYA KWAMBILI BLASA. SIYANI NDAALE.
@daviemalikhwa8679
@daviemalikhwa8679 Месяц назад
Iwe sukudziwa kuti wokuononga ndi yemwe amakudziwa? Lero izo mzako yemwe unkamuthandiza ndamene wakuonetsatu. Politics is a dirty game indeed
@user-ck7eb7tb7v
@user-ck7eb7tb7v Месяц назад
Zakuchipani kwanu ife sitingaikirepo mulomo yathu imakhala vote ku chipani chathu. Rest in peace SKC
@kubengovender6996
@kubengovender6996 Месяц назад
Madala musatiuze zamanyizi , this is not apolitical party people we can call!!
@user-mi3fw1zg8b
@user-mi3fw1zg8b Месяц назад
Uyu watumidwa ndi Chakwera musamale naye ma opposition Leaders ngati akufuna ayambitse Chipani chake
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn Месяц назад
Zanu izo ndi RUTO wanuyo i ife tiili NYACHIIII Kuma stand ndipo musaganize zobwera ku UTM TADZADZA
@lyiemax
@lyiemax Месяц назад
MCP is not a party to support, choose another party to support
@PeterMajamanda
@PeterMajamanda Месяц назад
😂😂😂 kumangonamiza anthu bas,mwatumidwa bodza et
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Месяц назад
Iwe tangopita ku dpp uzikapanga zimene azako akupanga ngati boni kalindo amtanyiwa achikuni chautsa azako akupanga ndalama ku dpp iwe bze ku mcp sigawa masiwiti ayi ndipo sipanga zachibwana uyende bwino
@OjessAndisoni
@OjessAndisoni Месяц назад
Isaiah wabwelela zenje lokumbakumba mkamwa mwa MCP😂😂😂😂😂sorry imeneyo ndiye chikangawa lmapha m.maso mulingwaMCP eeeeee
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo Месяц назад
Km zachaka chino eeeee🙌🙌🙌timangomva za congeresi Km pano tadziona ndithu
@ForestElf-z1h
@ForestElf-z1h 19 дней назад
Sorry my brother,,,,,,,mcp ,,,is working like for long time ,,,I wondering ,why, why why????? I'm asking myself about mcp ,,,,,😭😭
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v Месяц назад
Chokakoni bwana MCP nkhaza zao zinayamba kale fisi ndi fisi sangasinthe
@user-qp6qh2dj6l
@user-qp6qh2dj6l Месяц назад
Ngati chakwera anapha vice president wake ndiye ndiye inu munganunkhe kanthu?
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w Месяц назад
Usabwere ku UTM mwazola magazi abambo anu konko ku MCP
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 Месяц назад
Mbusi ya munthu ndalama ikumpani kodi pomwe simukumva ndipati asijupondani kumene akumenyeni zezeni chizilu iwe cha munthu Galu Wachabechabe
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj Месяц назад
Amuchita bwino wankhala akunyoza DPP komanso UTM munthu ameneyu
@JannahMajola
@JannahMajola Месяц назад
Musamaoneke ngat ndinu ofoila kwambili kamba kot akuthamangitsan ay achina abdullu lapken .chilima mwawayiwala kod ndinu ophusa kwabass simunatuso Mayesa mumaziwa kunyoza zipembezo inu
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Месяц назад
Khalqn komko bambo musachokeko mcp ndiyabwinotu paja ,momwe watulusa vn iyiyi uphedwad bola ukanangokhala chete
@user-jj3oo6jh1l
@user-jj3oo6jh1l Месяц назад
Makola anu adakuunzaniko kt chiyani pankhani ya MCP cos ifetu makolo adatiunza kt ngati mafuna kuzunzika mutalima mudzalowe MCP adatiphera anthu oti adatikonzera tsongolo lanthu km zachisoni anthu mulibe pambuyo pa ng,ona
@AdrianKambanizithe
@AdrianKambanizithe Месяц назад
Mwachixziwa Leroy chipani cha kongiresika?
@chikuchapotera9878
@chikuchapotera9878 Месяц назад
Ndiye kuti zachilima zija zinali zokonzadi eti? Ngati ukuti MCP itha kukupha it means it's a party that kills wavomelaza 😢
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i Месяц назад
MCP ilibethawi yokumbukilla athuomwe anawathandiza bf kulamula ziko akanakhalakuti amawelenga zaathu omwe awapingila ubwino sakanampha amiya sakanampha chilima ndimwayi achimwe mwapezeka ndimoyo muzipemphela kwambili zatelomo awonangati mwawayalusa ndipo akusakani moyipa be careful
@user-ei5fc4bl1d
@user-ei5fc4bl1d Месяц назад
Samalani achimwene! Mwadzina lanu sungani moyo wanu. Mkango sitiusisita ku ndebvu.
@user-qn2nu4xs9i
@user-qn2nu4xs9i Месяц назад
Akuku.....sungani moyo wanu mwadzina lanu...ndiye tikuthandizeni bwanji?? Chifukwa mukutiuza ife si a MCP, ......😅😅😅😅😅😅
@kennedybanda
@kennedybanda Месяц назад
Mulamba ukapita m'matope ndekuti madzi aphwera.
@BrightonKennedy-jd6fl
@BrightonKennedy-jd6fl Месяц назад
Tauluraso yemwe anapa DRsaulosi chilima,kuti mulungu akukhululukire, ndi kukupasa moyo wautari.
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi Месяц назад
Tinamuuza uyu kuti ndi bombo clat😂😂😂 koma iye sazindikira. Mcp mwachita bwino
@dinganinedsontchongwe610
@dinganinedsontchongwe610 Месяц назад
Umakonda zinthu zoola ngati khwangwala ndiwe galu uzipanga manyazi kulankhula zinthu ngati izi munthu wachinyamata ngati iwe koma kuganiza ngati nkhalamba????umabakila za ziiii muntamata ofoira
@user-qv4ko6ps4j
@user-qv4ko6ps4j Месяц назад
Iweyo ndi chitsilu kwambiri chifukwa siudziwa tanthauzo la dzina loti ndale,,,,,,,usova. ,ndale ndi nkhondo za mumtima ndipo zikatulukila kunja zimapweteka ndipo uli ndi mwai sadakuphe komano zafikapo samala because chikangawa party ndi mchotsa moyo mafiaz
@LinessdorisScot
@LinessdorisScot Месяц назад
Tiyeni muphana simunati, mizimu ya anthu ajja ikukutsafirani
@charlesjimu6054
@charlesjimu6054 Месяц назад
That is what you wanted because you knew that mcp is not a good party ever since
@user-os4iz4tn9z
@user-os4iz4tn9z Месяц назад
Ndiye ngati mukudyana nokhanokha ndiye ine munganditani??
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад
Boni Kalindo akamayankhura inu munkati ndiwafodya lero ndi izi 😂😂😂😂😂
@user-ui4ux5kc8d
@user-ui4ux5kc8d Месяц назад
Tsoka sasimba zomwe ukukambazo ndi mwai ndiye ndi nthawii yopanga chisankho chyenera Zama number ziribe ntchito bola ulimoyo basi
@MphatsoIshmaeladam
@MphatsoIshmaeladam Месяц назад
Mwadzi wa chilima umenewo ndipo nonse a MCP simunati mugogodana
@brownpetroscoplandmalemia1551
@brownpetroscoplandmalemia1551 Месяц назад
What goes around comes around
@victorauwana7258
@victorauwana7258 Месяц назад
Ukuona ngati tiwala kufa kwa Chilima?
@user-ys9hr2yj2f
@user-ys9hr2yj2f Месяц назад
Awa ndimaphwala awa sunati iwe umanyoxa size paka asilam ngat zikugwirizana nd zachipan akutuma
@GetrudeBanda-sd1yf
@GetrudeBanda-sd1yf Месяц назад
Ameneyu musamulole kulowa ku zipani zanu ndipo musayerekeze kulibwino akhaleopanda chipani alindicholinga ameneyo akupwetekesani
@user-pf3in2fw5y
@user-pf3in2fw5y Месяц назад
That is MCP brother,party full of blood.
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w Месяц назад
Komanso undipatse Phone No ya Chakwera 😂😂😂,ndifunse ndekha kuti ndege yinagwa bwanji??
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko Месяц назад
Ndiye ukumuuza ndani nkhani zanyumba mwakozi?
@user-wx1ri9xv3f
@user-wx1ri9xv3f Месяц назад
Ndipang"Ono pamenepo uyembekeze zina😢😢😢😢
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v Месяц назад
Chikangawa Congress party akuphani kumeneko
@user-tb6yh1kx3o
@user-tb6yh1kx3o Месяц назад
Pamenepo mpang'ono chakwela alingati nkhumba yomwe imatha kudya mwana okhala wake ukhale komweko
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Месяц назад
Zili koko iwe suziwa kt ameneyo ndi kango?
@katalamajames4947
@katalamajames4947 Месяц назад
Agift banda musamusiye ameneyo mumuphyotole mbolo yake yusadura mwana wangono ali nkukamwa kwakuthwa ananyoza mpingo wachisiramu ameneyo or mutamupha galu alibe phindu lililose
@RoseChiphiri-ts8jx
@RoseChiphiri-ts8jx Месяц назад
Ok basi takumvani komano khalani konko ndi chipani chanu chomwe anakusila agogo ako 😂😂😂
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z Месяц назад
Anthu oyipa inu
Далее
MOMWE ZAYENDERA KU CONVENTION YA DPP
42:41
Просмотров 33 тыс.
BON KALINDO  PA 20 AUGUST 2024 |
16:39
Просмотров 18 тыс.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Просмотров 231 тыс.
Mangochi ikuti Chakwera ndi Chikangawa.
5:04
Просмотров 38 тыс.