Тёмный

Israel Malawi Farming, Listen to Prophet David Mbewe 

Malawi Page
Подписаться 78 тыс.
Просмотров 16 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 32   
@joycegondwe9560
@joycegondwe9560 10 месяцев назад
Ambewe inu mukudya Asiyeni ana bwanji simunaalembe ntchito chete. God is watching you.
@KangombeMpha
@KangombeMpha 8 месяцев назад
Za ziiiiii prophet sinanga iweyo uli ndi chakudy
@alicehananiya
@alicehananiya 10 месяцев назад
Powerful message
@OsamaMakalaso
@OsamaMakalaso 10 месяцев назад
maitha prophet dvd mbewe
@JamesPhiri-rz7lk
@JamesPhiri-rz7lk 10 месяцев назад
Akunama ameneyo! Kapolo samalipilidwa,zasiyana ndi amene akupita ku israel chifukwa adzikapatsidwa malipilo
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 10 месяцев назад
Very powerful massage ❤❤
@redetembo3249
@redetembo3249 10 месяцев назад
Abusa kodi mukifuna anthu azipempha kwa inu?
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 10 месяцев назад
zimenezo kod zipulumutsa athu ulibe zelu iwe sukudziwa cholinga cha boma unqli mbuli ku xool ndiye kt kapolo amalandila ndalama ufunq unamize ndani
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 10 месяцев назад
Makhozawo 😢😅man of god okkk
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 10 месяцев назад
That's true the Man of God, but let's pray hard for our country Malawi otherwise Chakwera will exchange us with money 😊
@lewisbonongwe8518
@lewisbonongwe8518 10 месяцев назад
True
@StanfordMNthali
@StanfordMNthali 10 месяцев назад
Iwe Mbewe ukunenepa ndi chambale
@joycegondwe9560
@joycegondwe9560 10 месяцев назад
Eti. You have built houses using zopereka . Anthu nkumasekelera ngati akulalika uhtenga wachipulumutso.
@StephanoMussa-q6d
@StephanoMussa-q6d 10 месяцев назад
Ukapolo sulipidwa man
@nditumenichagunda4192
@nditumenichagunda4192 10 месяцев назад
Tatilembenitu ntchito Kodi kapolo amapanga yekha chisankho chopita, church chanji chovala mpaka chipewa
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 10 месяцев назад
Masiku omaliza kodi boma la Malawi silingathe kupanga ma farm paokha kuti achinyamata azigwila ntchito nyanja tilinazo misinje tilinayo koma kuba basis
@ChristopherKabanga
@ChristopherKabanga 9 месяцев назад
arembe ntchito uziwapasa 500,000 pamwezitu
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 10 месяцев назад
Zoonadi 😢😢 Amalawi apita kuukapolo
@MoosaSame
@MoosaSame 10 месяцев назад
This different story what are you telling us nw?
@SamuelAmos-s6t
@SamuelAmos-s6t 10 месяцев назад
Komano minthu wa Mulungu anthu wa a pita kolipidwa, koma isreal ku iguputo samalipidwatu nde tiyeni tiwaleke apte mwna mkukasnthako miyoyo.
@gomezthera535
@gomezthera535 10 месяцев назад
Atumiki akumalawi sazatheka gwirani chimozi utumiki kapena Andale kusiyana kuti uku walowa uku walowa 😂😂😂
@williamsalexmbonga
@williamsalexmbonga 10 месяцев назад
Mukuyankhula motumbwa chifukwa mulimpogwila anzanu akusowatu zochita ku Malawi ko thats why akukayesa mwayi .Imeneyo campaign or you are preaching mawu a Mulungu
@DamisonZuze
@DamisonZuze 10 месяцев назад
Asiyeni awa anagwa kale kale . Anaphonya nseu.Izi zisa Mulungunso.
@PatricaTchuwa
@PatricaTchuwa 10 месяцев назад
Ndipo asatibowe chimunthu chonama ichi, prophet wa fake xa ziii zoyakhulaso ximenezi tikupitabe ku Israeliko oana kt utani
@joycegondwe9560
@joycegondwe9560 10 месяцев назад
​@@PatricaTchuwakhuluku wamunamiza Walter kuti utenga mpando look at the outcome. False prophet
@CleverlyKanthyos-ds5sg
@CleverlyKanthyos-ds5sg 10 месяцев назад
Malawi ali ndi vuto amafuna Kuti azawo asakhale pa bwino ayi,maboza okhaokha,thawi zogwadira Muthu kapena mupingo zinatha,tiyeni tiwafunele zabwino,go to South Africa ask Malawian people there, about work u can understand
@KhristJah
@KhristJah 10 месяцев назад
Tikupita tikakwanilitse ulosi kusiya ndiukapola wa Jesus😂😂
@BesterJekapu
@BesterJekapu 10 месяцев назад
Kathandizani anthu kut akawone ufumu wkumwamba asati kulimbana ndi boma nthawi zonse
@DamisonZuze
@DamisonZuze 10 месяцев назад
Nanga zikugwirizana ndi chipulumutso . Lalikirani Za Ufumu wakumwamba . This is religion not Christianity. A Christian is led by the holy spirit . You preach by His will . Not by your sense of knowledge.
@walekengwira3468
@walekengwira3468 10 месяцев назад
Anthu anga akuonongeka Chifukwa chakusadziwa…May God help us
@BrendaKamtsina
@BrendaKamtsina 9 месяцев назад
This man is not man of God amawelenga Bible kuti azilitsutsa otembeleredwa uyu ndakaikila kwakukulu zokalowa ufumu wakumwamba .
Далее
THOUSANDS GATHER IN MALAWI FOR A HISTORICAL CROSS OVER
35:47
TIKUFERANJI? 27 FEB 2016
28:05
Просмотров 104 тыс.
Prophet S Msimanga 23 Jan 2024
55:03
Просмотров 85 тыс.
ZION  BY PROPHET DAVID F. MBEWE # FROM LIWEC
6:52
Просмотров 38 тыс.
TIKUFERANJI 09 FEBRUARY 2019
27:16
Просмотров 169 тыс.