Тёмный

KALATA YA PROPHET HABAKUKU YOPITA KWA MARY CHILIMA KUTI AIMILE U PRESIDENT ASALORE ENA ATENGE CHIPAN 

Makosana
Подписаться 92 тыс.
Просмотров 15 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

16 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 115   
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 6 дней назад
Ambewe ai ma prophet wa ndakuba amafuna kuba azibusa wa tisawakhulupirire watililisa chikangawa 😭😭😭😭😭
@SuzenBokola
@SuzenBokola 2 дня назад
Habakuku moto 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥fire yomweyo beauty
@Rometcma
@Rometcma 6 дней назад
Zanu za ufitizi musiye mukumupempherela ngati anakuuzani musiyeni Mary Chilima azipanga zake chonde, Mary Chilima don't allow that akupwetekani these people seems like anthu abwino then disaster chonde were ever you are musalole A Malawi kumbukilani za Chilima ananamizidwa lero Ali kuti nde these are false prophet please pass this to Mary I love her❤❤❤❤
@jennyx6914
@jennyx6914 5 дней назад
habakuku akufuna njira yoti apemphe ndalama kwa Favid mbewe ndi khruku habakuku akweni ali bwino pa SG to be honest she is fit and full loaded
@kondwamlungu8384
@kondwamlungu8384 5 дней назад
Yes nadinadi viewe thenathena 🔥
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 6 дней назад
koma zimakhara ngati ndi munthu wopepera koma ambuye atimenyera nkhondo mary chirima ayima apitirize masomphenya asck amen
@lyiemax
@lyiemax 6 дней назад
Amen Man Of God 🙏🙏🙏
@JamesKalasa-s6s
@JamesKalasa-s6s 6 дней назад
Mfundo wakambayi ndi yofunika kuti asalore kuti yemwe wabwela kumene adzatenge mpando ayi. Eni utm tikuwaziwa patricia can be good president koma ndi obalalika okha amazizi sangalore
@LinessLewis
@LinessLewis 5 дней назад
Habakuku woyeeee future minister of finance
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 6 дней назад
Uyu nde walankhura za nzeru,koposa onse
@JamesSaiti-h1l
@JamesSaiti-h1l 5 дней назад
Azibusa ife ayi takana mery chilima tsiyeni
@kondwamlungu8384
@kondwamlungu8384 5 дней назад
Yes nadinadi vinkhale nthethena ku UTM 🔥 kangivilimakola chomene
@Paenda-pt6gb
@Paenda-pt6gb 5 дней назад
Owo ok, kodi UTM ndi ya kubanja kwa Chilima eti? Ayi uthenha wamveka.
@LindaChiwanda
@LindaChiwanda 6 дней назад
Maliam wamaliza ndalama za Bushir ndiye wamutuma kut alowe ndiimeneyi Komatu za Mary ndizoona zinazo zitayeni
@WatsonMsukwa-y5i
@WatsonMsukwa-y5i 5 дней назад
OK
@AubreyWilson-j8w
@AubreyWilson-j8w 6 дней назад
Wamisala anaiona nkhondotu kkkkk
@ChifundoChiwanda-ru3pg
@ChifundoChiwanda-ru3pg 5 дней назад
Aaaaa!, isiyeni UTM yikuziwa zomwe ikuchita,
@OsbertMwanyali
@OsbertMwanyali 6 дней назад
Ife aku mzuzu mental hospital tikupepesa pakuthawa kwa patient wathu uyu😂😂😂😂
@JamesKalasa-s6s
@JamesKalasa-s6s 6 дней назад
Wamisala anaona zithu anthu wawachulawa komaso mfundo yosawalora anthu amene wabwela kumene ayi
@tamalangoma2765
@tamalangoma2765 5 дней назад
@@OsbertMwanyali 🤣🤣🤣🤣
@chisomotaika4479
@chisomotaika4479 5 дней назад
Kkkk ife timadabwatu😂😂😂😂🤣🤣😅😅
@IreenMayepe
@IreenMayepe 5 дней назад
😂😂
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 5 дней назад
Prophet wathu❤
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 6 дней назад
Amen
@user-rd2td7bg4c
@user-rd2td7bg4c 5 дней назад
Kd uyu ndimaona gt wamisalatu😢😮
@SildaKatundu
@SildaKatundu 5 дней назад
Prophet Mbewe ayi
@rabeccamasebo6261
@rabeccamasebo6261 4 дня назад
Wamisala anaona nkhondo ,ine ndagwirizana nayetu 😂😂😂😂😂😂
@CadTafa2
@CadTafa2 6 дней назад
Prophet mbewe ayi Bora DPP
@Littlefair7
@Littlefair7 5 дней назад
Zopusa basi, prophet amakhala busy ndi zandale?
@mphatsomonjeza4371
@mphatsomonjeza4371 5 дней назад
Kkkkkkkk. Koma abale Zoona izii???
@mzeewandembonyirongo2972
@mzeewandembonyirongo2972 6 дней назад
Misala yikukolera but pipo dont know...he needs to be taken for treatment 😢
@Lizzie-h1k
@Lizzie-h1k 5 дней назад
Kkkkkk...mmmmm apa wapengeratu...kkkkk ilitu ndi dziko...likufuna serious😅😅😅😅
@Jessymsowoya
@Jessymsowoya 6 дней назад
Ambewe nde ai ife tifuna mary yo ayime basi
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 6 дней назад
Wa misala adaona nkhondo
@prettytambala5687
@prettytambala5687 5 дней назад
Shalom malawi Shalom
@SydneyNyasuli
@SydneyNyasuli 5 дней назад
Kkkkkk coma abusa asakhilanthu kkkk Malawi ya
@HarryKandani
@HarryKandani 5 дней назад
Fredo 😂😂 mbambande Habakuku
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 5 дней назад
😂😂😂😂 abakuku ndi one walakhula zazelu
@SueWahna
@SueWahna 5 дней назад
Fredo tavala lamba iwe ndi jeans 😂😂😂😂😂
@kondwanimunthali7401
@kondwanimunthali7401 5 дней назад
Psychiatric
@Jessymsowoya
@Jessymsowoya 6 дней назад
Ambewe nde ai nar
@MalizeniOliviaBridan
@MalizeniOliviaBridan 5 дней назад
Ndakunva prophet
@JoyceLiwonde
@JoyceLiwonde 5 дней назад
😅😅😅😅😅Koma Kuli zithu kumalawiko
@kelvinfaki7837
@kelvinfaki7837 5 дней назад
Telesha akhala ndani
@JalanAmmo
@JalanAmmo 4 дня назад
It means we don't allow.
@Sofi-p1v
@Sofi-p1v 6 дней назад
Prophet Mbewe ndiye ayi
@ArthurSuya
@ArthurSuya 6 дней назад
Ndiopenga mdala iwe getout
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 5 дней назад
Zoika zibusa mundale zakanika kale chakwela anali busa
@tamalangoma2765
@tamalangoma2765 6 дней назад
🤣🤣🤣🤣 Habakuk for UTM President
@EmmyYafete
@EmmyYafete 5 дней назад
Ahabakuku sitikufunaso abusa ayi,bola asatanaomwe
@GriffinAziziSokoh
@GriffinAziziSokoh 5 дней назад
Komaso azibusa ayi mavuto awoneka kalewa
@FracksonMadani
@FracksonMadani 5 дней назад
Maganizo oti UTM ipange alliance ndi chipani chomwe sichinalamulireko dziko lino ndiabwino not kupanga alliance ndiomwe analamulapo mudzawonanso izii mwazionazi
@NoahPhiri-f7m
@NoahPhiri-f7m 6 дней назад
Mary Chilima akukwana ndi Bomba kuchita m'gwilizano ndi DPP Afford UDF ndi UTM satana Chikangawa akugwa basi
@jennyx6914
@jennyx6914 5 дней назад
iremember this guy loves too much chakwera ndiye pano wasinthanso ngati Joseph phungu nkasa anthuwa they are hungry for money basi amene angawonere ma interview ake muona kuti amanena kuti chakwera ilove you my president
@hesbaluku7281
@hesbaluku7281 5 дней назад
😂😂😂 shalom Malawi shalom
@GriffinAziziSokoh
@GriffinAziziSokoh 5 дней назад
Amwene mayi si chilima amwene akathana ku zisankha
@Lizzie-h1k
@Lizzie-h1k 5 дней назад
A mad man so de battle!😅😅😅😅
@GiftKgomongwe
@GiftKgomongwe 6 дней назад
Ayi maprophet wa musawakhulupilile kukakhala kupephera tizipepera tokha ambewe musayikemo
@osaukaonjoya
@osaukaonjoya 6 дней назад
Marry chilima musiyeni naye ananale mukufuna mupangeso chipongwe
@BenardChilemba
@BenardChilemba 6 дней назад
Si prophecy iyi iyaaaaa
@AbdurRashidKachala
@AbdurRashidKachala 6 дней назад
Aaaa khani ija yasithaso
@ClaudiaarmandoMafunga
@ClaudiaarmandoMafunga 5 дней назад
Koma yah tinva zinthu
@YonaPearson
@YonaPearson 5 дней назад
😂😂😂 koma prophet
@papelariareis.e.
@papelariareis.e. 5 дней назад
Vice habakuku woyeee 😂😂😂
@MasterChilangiza
@MasterChilangiza 3 дня назад
Nanga bushili akhale ndani munawadyera ndalama aja tisiyeni ma pulani athu ndiomwewo kkkkkk inuyo timafuna kusankha inuyo abusa kuti mutiimile pau president kkkkkk mukuti bwanji inuyo
@FatsanTobiyas
@FatsanTobiyas 5 дней назад
Fhitsililu mbuli mbava owe oba ndimavesi kagone galuuuuu
@Charity-z6q
@Charity-z6q 6 дней назад
Kkkkk eish koma zinazi
@TywellShumba
@TywellShumba 5 дней назад
Aka kakufuna ndalama ku UTM osalola mubusa kuti azikhalaso msogoleli
@RoseRose-w8r
@RoseRose-w8r 5 дней назад
Abale azibusaso lero zoona Kodi amalawi TIMAKHALA bwanji
@SydneyNyasuli
@SydneyNyasuli 5 дней назад
Nyimbo yokoma kkkkkkk
@AgnessMaumbo
@AgnessMaumbo 5 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂😂aProphet aja kuno,kkkkkkk🙌
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 5 дней назад
Munayambatu kunena bwino nde zapitaso kwa maliam😅😅😅
@VioletMbale
@VioletMbale 5 дней назад
Who does that! Kutsokoneza kokha batsi don't mix nkhani nde yalowa kuchikondiso😅
@WinnerMtumbuka
@WinnerMtumbuka 6 дней назад
Kalata ya ndale mapemphero kufusilaso azimai koma misala sizinthu 😂😂😂😂😂😂😂
@LuciusMaison
@LuciusMaison 6 дней назад
Kkkkkk
@josephmlikiliki6278
@josephmlikiliki6278 4 дня назад
kkkkkkkkkkk koma
@VioletBwinja
@VioletBwinja 4 дня назад
Kkkkkkkkkkkk
@AubreyChiyaya-ty8ge
@AubreyChiyaya-ty8ge 5 дней назад
Wamisala uyu
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 6 дней назад
chiri chose chiri manja mwambuye akuziwa
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 6 дней назад
Week ya mmawayi apempha thandizo believe me
@ShaffieKaisi-r5v
@ShaffieKaisi-r5v 6 дней назад
Prophet sitidzamukhulupiliraso bola enawo😅
@BrendaDimba
@BrendaDimba 6 дней назад
Prophecy prophecy😅😅😅😅
@FletcherGuzani
@FletcherGuzani 6 дней назад
Zoona prophet habakuku
@jeansikwese4720
@jeansikwese4720 6 дней назад
Koma Mulungu akuwona izi
@alexgweje8610
@alexgweje8610 5 дней назад
😂 Koma ziliko
@KentWilliam-r2v
@KentWilliam-r2v 6 дней назад
Abusa ayi or aprophet
@EphraimMaluwa
@EphraimMaluwa 5 дней назад
Kkkkkkk kkkkkk adaah awaa
@VioletMbale
@VioletMbale 5 дней назад
Koma uyu anachenjeletsa akatelo akufuna ndalama 😂😂
@user-qn3be8ry4r
@user-qn3be8ry4r 6 дней назад
Asankhale watumidwa ndiasatana kuti ulowetse ziwanda
@NancyLennoh
@NancyLennoh 6 дней назад
Wakhuta Kodi uyu eti😂😂😂😂
@piliranifosternguluwe7737
@piliranifosternguluwe7737 6 дней назад
Ndizomwezo tikukana anthu opanga za uzimu kuti asamatisokoneze.....wina walephera kale
@NoahKalima
@NoahKalima 6 дней назад
Ukufuna upemphe iwe,,sakuziwa iwe ndina kut ukafuna kupempha ,umabwera ndyoyamikila
@RobertChikawonda
@RobertChikawonda 6 дней назад
Za ambewezo ayi
@marymcheka612
@marymcheka612 5 дней назад
😂😂😂km
@angelmwethewa8010
@angelmwethewa8010 6 дней назад
Kkkkkkkkk koma guys ndiye UTM kuiphatikiza ndi Mbewe ingawine???????kkkkkkkkkkkk
@jeremiahmalikebu2393
@jeremiahmalikebu2393 6 дней назад
6 mita ya Bushir adamaliza, akatero akufuna amukaweso prophet Mbewe😂😂😂
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 6 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 6 дней назад
Ameen ameen olo nane ndili chocho mvelani mawuwo ine ndili dziko la Botswana koma chilungamo chimenecho, woyeee woyeee malawi 🇲🇼 watsopano ndamene tikufuna mbewe, atupele , utm moto moto 🔥
@JamesPhilimon-h2w
@JamesPhilimon-h2w 6 дней назад
😂😂😂 politics, Gospel as prophet & musician zonse nokha kkkk
@henryhenry6632
@henryhenry6632 6 дней назад
Waledzela kachaso 😂😂😂😂
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q 6 дней назад
Wamisala uyu kkkk
@DoroBrighton
@DoroBrighton 6 дней назад
Akunana zazibusazi ayi atisokoneza asatipangire zochita
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 6 дней назад
Wamisala amaona nkhondo
@MCAnthonyNdau
@MCAnthonyNdau 6 дней назад
Kodi utm ndi chipani chaku banja
@CharlesNdalama-v5b
@CharlesNdalama-v5b 6 дней назад
Uyu ndiopenga
@SymonMbuto
@SymonMbuto 6 дней назад
wamisala anaona nkhondo🤣🤣🤣
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 6 дней назад
Akufuna 6mita uyu galu
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 6 дней назад
Hahahaha
@jackmambo2638
@jackmambo2638 6 дней назад
Zikatelo za bushiri zatha et
@user-hh4wn4vf9e
@user-hh4wn4vf9e 6 дней назад
❤❤😂
Далее
Как мы играем в игры 😂
00:20
Просмотров 169 тыс.
Oyenda ndi Lupanga adzaphedwa ndi Lupanga
7:53
Просмотров 57 тыс.