Тёмный

KAMLEPO KALUA WAULURA ZINSISI ZA BOMA PA VOICE YOMWE WATULUSA LERO EEH ZIKUCHITIKADI IZIZI KOMA? 

Makosana
Подписаться 111 тыс.
Просмотров 38 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 105   
@ChazamaManda
@ChazamaManda 2 месяца назад
KK I salute you for speaking for northerners ✊
@happynyirenda8790
@happynyirenda8790 2 месяца назад
Thank you Mr Kalua,msewu imeneyo ilimidwe,kawakumbutsa pafupipafupi
@princealick6901
@princealick6901 2 месяца назад
Be strong Mr kamlepo . God is with you
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 2 месяца назад
Akupatsani foni yanu bwana zopusa zimenezi
@PreciousChlima
@PreciousChlima 2 месяца назад
Comrade kalua let God be god
@WhiteDaudi
@WhiteDaudi 2 месяца назад
Kodi sikali Ngw,oma munango nenepa mulibe mzelu galu iwe amalawi asikudandawula iweyo kuti mwatani ndiwe mbusi zikali Ngw,oma👂👂👂👂
@MarthaPhiri-q8m
@MarthaPhiri-q8m 2 месяца назад
Ambuye ave kulira kwanu MADALA kmaso muzipephera molimba mulungu yekha ndamene Ali ndi mphamvu zamoyo wanu osat muthu ayi mulungu akuchitireni chifundo, mutuluka kudzera mu phamvu ya mulungu kma maso anu akhare kwa mulungu 😢
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 месяца назад
Bwana musadandaule mr chikangawa tiponda munsiye
@ronaldordinga6537
@ronaldordinga6537 2 месяца назад
Inu ndi amene munasala pa anthu omwe munakakamiza multiparty system zomwe mnalakwa MCP singakunereni kukondwa chifukwa inu nde multiparty system ku mlw kuno
@KikaGray
@KikaGray 2 месяца назад
Koma chakwera uli nditsoka ndipo masku ako achepa ndi team yak
@AgogoBaussmaney
@AgogoBaussmaney 2 месяца назад
A kamulepo mugosiya za ndalezo muzipanga zanu Mesa ena aja anakakusiyani pa roundabout your still energetic you can do something to boost your business and life. Moto sagula Osakakamira mphika omwe ukupita pa Moto. Mwina mukuziwapo kanthu😮😮😮
@MaryNyalapa-u2t
@MaryNyalapa-u2t 2 месяца назад
Nkhani ndi nsanje mr Kaluwa.anthu Awawa samapumq Nanu bwino.umphwawi ukuwapweteka ndinkona akumaba maphone. Amati anthu Opita kosiyana sapikisana.komanso mtengo opanda chipatso sugendedwa.Muli mphatso mwainuyo imene mulunguanaika ndinkona akudana Nanu.let God be God.Ambuye akupaseni double ngati yobu.
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 месяца назад
Afiti awa, may God punish them. Be protected Mr kamlepo
@DilaGerald
@DilaGerald 2 месяца назад
Bambo kamlepo kaluwa akaphedwa, dziko lino liyaka moto, Kamlepo is our Hero, No way.
@Maxwell-e2d
@Maxwell-e2d 2 месяца назад
Kod nkulu uyuyu koma mwati sakupenga???😢😢 Kapena kapena osati akufuna ndalama zachipepeso 😂😂😂😂😂 Apapatu ndiye bola kumangomvela haye haye haye haye haye haye haye haye haye haye haye haye haye shoooooooo 😂😂😂😂😂😂
@JusticeNyirenda
@JusticeNyirenda 2 месяца назад
​Ali kale ndi ndalama awa iwe usavutike,,,
@chiefmitengo
@chiefmitengo 2 месяца назад
Kkkkk Fodya anakonza
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 2 месяца назад
osadandula boss anthu opusa amenewa sangawine ngakhale akuwonetsana machine obera mavoti
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 месяца назад
Peter wa nthalika samalakhula chisawawa ai inu akamulepo bvuto ndi chani munthu 😅
@ChristianMalingamoyo
@ChristianMalingamoyo 2 месяца назад
Malawi we're blessed with strong freedom fighters but we citizens,we don't help them to fight this evil government
@madalitsochiumia755
@madalitsochiumia755 2 месяца назад
KEN zankhale ng'oma&ngwape LAZ chakwela ndinu mbudzi .mmusiye kamlepo khaluwa . & Phone mpeleke that's all
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 месяца назад
Akamulepo khalani chete basi simuziwa chikangawa ndichitsiru? Ngati ku africa kuno parliament sinaotchedwe kukala koyamba ayese kupha inu,i was thinking that bakili adali woyipa koma tikuona lero ndimanyi awa tikuwona awa
@MussahWilliam-py1ff
@MussahWilliam-py1ff 2 месяца назад
Be strong
@FebbyPhiri-n7j
@FebbyPhiri-n7j 2 месяца назад
Munthu yu anakulakwirani chiyani abale 😭😭😭😭
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 2 месяца назад
Brother Kamlepu the only solution contact H E directly as you had been doing in the past
@LydiaMakonde
@LydiaMakonde 2 месяца назад
Agayankhe galu ameneyo
@JECKYGREY
@JECKYGREY 2 месяца назад
Kom chakwera eeee mulungu
@blackwellblackwell6337
@blackwellblackwell6337 2 месяца назад
big speach
@KingfrahMachado
@KingfrahMachado 2 месяца назад
Mmmm kod Malawi akupita kut kod zona kweni kweni Mcp ikufuna itatha anthu onse zoona ayi zikom mulungu ndiamen aweluze Zikhale ng'oma ndiwe galu kwabas 🐕🐕ndi Chakwela wakoyo
@wonganimazunda4703
@wonganimazunda4703 2 месяца назад
Kodi mapangila recode ndichan siziveka bwino saname
@sydneychimbewaphiri1117
@sydneychimbewaphiri1117 2 месяца назад
Ndiye osapita kukhoti bwanji kuti akubwezereni 4n. Nanga amamanga 4n kusiya munthu?
@isaaczuze
@isaaczuze 2 месяца назад
Bwana kamlepo simuphedwa ayi ....mulungu sangalole kuti anthu tonse tizivutike mmalawi muno .....iphani kamlepoyo koma malawi anunkha
@SamboRuphan
@SamboRuphan 2 месяца назад
People are weeked 😢😢😢 kukufunika kuwapengesa misala achakwela
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 2 месяца назад
Akamulepo Mulungu alinanu cholinga ndipo Mulungu ndizatheka bji zidutsa nyengo izi
@sethmoyo9978
@sethmoyo9978 2 месяца назад
Chakwela ndi mfiti kwambili.
@TemwaniJuma
@TemwaniJuma 2 месяца назад
😢
@EdwinHambisa
@EdwinHambisa 2 месяца назад
Kuli mulungu akupulumutsani a Kalua
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 2 месяца назад
Akamulepo kaluwa musaope imfa siithawika kuteloku zimene akupanga chakwera zo kwa inu nawonso ndi imfa ikwasaka asiyeni aliyese azamfa
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma 2 месяца назад
Dada kamlepo kudandaula yy chiuta wali mbaliyinu wakudankha kufwa akumanyikwa charaaa
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 месяца назад
Akamulepo bambo anga chonde chonde tasiyani zandale izi mwakula baba chonde 4n ndikachiyanisonkuposa moyo omwe mulinawo bwana kaluwa chonde kulani Please
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 2 месяца назад
Man kawasumileni anthu amenewa and the must pay you big
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 2 месяца назад
Paja amasowa awa mwina afuna adzisowetsoso
@marryphili5419
@marryphili5419 2 месяца назад
Anthu awawa ndi akuba sure zoona munthu kumubera foni akuwona ndinu apolisi amutundu wanji kuvutika chani Koma abale apolisi Akumalawi ndiwovesa chisoni shame
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 месяца назад
Ineyo sindisapota dpp ayi koma moyo omwe amapnga peter wa nthalika pakhani yandale ndimasangalala nawo inuyo akamulepo ndinu munthu wankulu bvuto ndichani abale bze ndi ndale mpakana liti pa msikhu wanuwu abale ai mukutipangisa manyazi please bwana kaluwa mwakula
@HildaSingin-vm2tr
@HildaSingin-vm2tr 2 месяца назад
Mmmm ambuye alowelelepo tiyeni tiwayikidze mapephelo anthu awa ndi mikango chaka cha mawa tizawakholopa
@chrisboyce2
@chrisboyce2 2 месяца назад
President wa ku Bangladesh wanthawa dziko lalero anthu atafika potopa ndikupita kunyumba kwake komweko kunoso ku Malawi 2025 Chakwera akangoberaso zisankho azawona zakuda!
@JoshuaNyirongo
@JoshuaNyirongo 2 месяца назад
Mabungwe muli pheee anthu akuzunzika..
@GiftFrancesco
@GiftFrancesco 2 месяца назад
Nkhan ndyomweyo ya Mademo pa 8 BT & LCity And another city in 15 this month
@isaaczuze
@isaaczuze 2 месяца назад
Boma la anthu okuba ndi umbava koma akuti ndi mmbusa
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 2 месяца назад
Kodi akulu inuyo nthawi ija mu ulamuliro wa A Muluzi mumati mulowa nthengo Tsono awawa muku waopa? Tati uzeni Ifeyo tiripo MCP pa ground singa phule kanthu,bola tiziwe, Kuti tikumenyana Ndi MCP kapena A sirikari Amalawi, Chakwera pamene wangopha Chilima pamodzi ndi Wanthu wena aja, OLO nkhondo itayamba sanga wine, Asirikari akumwera Ndi mpoto,sanga thandize MCP, uyu fisi wachabe chabe Chakwera afuna kuphesa mtundu wa achewa ifensotu Ndi Achewa koma zopusa zongawa mtundu wa A Malawi sitikufuna makolo athu ada ngopita kumwera Ku ntchito And ndife Asirikari okwana kunja Kuno
@JeniferethelKalinde
@JeniferethelKalinde 2 месяца назад
Anthu okuba apeleke fon ya bwanayo
@paulcedrick7212
@paulcedrick7212 2 месяца назад
Kuwopa chala chwee mwana chweee 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥
@JOSEPHDYMONCHIRWA
@JOSEPHDYMONCHIRWA 2 месяца назад
Mesa iwo akuti ndi olemera nanga ndichifukwa chiyani akulephera kugula cellphone? Kkkkk zamanyazi
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 2 месяца назад
Koma aken zikhale perekani phone ya eni ake kuba kumeneko
@KikaGray
@KikaGray 2 месяца назад
Boma lagwa ili
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 месяца назад
Amalawi kusamva mumati mukufuna kusitha zithu pano ndiizi mamvuto tikumana nawo ananena Pete kuti fisi ndi fisi sangapite tchile Lina kukasitha Zina
@FelixLusaka
@FelixLusaka 2 месяца назад
Why don't you go to court? You are just complaining here May be you want to buy semperthe ? Go to court please
@zawadimwagomba317
@zawadimwagomba317 2 месяца назад
Nsewu wa nthalire zinayamba liti Mr kaluwa
@RaphaelKweve-u5s
@RaphaelKweve-u5s 2 месяца назад
Bwana Kaluwa kodi mukuganiza kuti imeneyo ndi njira yabwino yopangira claim phone yanu komaso zinthu zomwe anakuwonongerani ndi kukutengerani?,,,,,palibe formal way of claiming your Items?
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 2 месяца назад
Musaope Bamboo anga sizingatheke zimenezo ife tonse tili maso pa nkhani imeneyi sangakupheni Malawi Ili tcheru
@RaphaelKweve-u5s
@RaphaelKweve-u5s 2 месяца назад
Zikundivetsa chisoni mmene mukuyankhulira
@sanlakedickson6780
@sanlakedickson6780 2 месяца назад
ovotela MCP anthu ake anagwa nkunyu
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
koma musiyen mwanawa wakwathu muramu wathu mutiphere chirima reroso mkurimbanaso ndi kamrepo asiyen ana akwathu
@RachealLongwe-c2p
@RachealLongwe-c2p 2 месяца назад
Zinthu sizkuyenda pa Malawi
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 2 месяца назад
Munthu wakulu kilira koma kumati chakwera sava kulira kwa kamlepo mmene anayambira muja my malawi why you do this 😢😢😢
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 месяца назад
Kwatumbuka kuli zitsiru zamafumu ndithu kodi agaru in a livingstonia asatana mbuzi zaziwanda kumwamba kukuoneni,
@DerickZiba
@DerickZiba 2 месяца назад
Give back the K phone
@MorganMwikhala
@MorganMwikhala 2 месяца назад
4:13 zomwe anawononga abweze
@Margaret-t7m
@Margaret-t7m 2 месяца назад
Mulungu amve kulila kwanu dada mmmmm
@sethmoyo9978
@sethmoyo9978 2 месяца назад
Kamlepo kalua u deserve to be our president
@MasaMasina
@MasaMasina 2 месяца назад
Jokes
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 месяца назад
Mwamuputa kamulepo modandaula momwemo ma vote atengedwa mwava agaru 😂ndinu opusa mumanganiza ngati mbuzi achure
@JOHNOlesmasCosmas
@JOHNOlesmasCosmas 2 месяца назад
Kod lawyer wa Kamlepo kalua alikut nayeso wangokhara chete osapita ku court bwanji kut munthu akhale mfulu uyu
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 месяца назад
I said the same thing kuti the best thing ndi kungowasumila chifukwa izi zomangong'alulazi sizithandiza.
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 2 месяца назад
Kodi lawyer wanu Ali kuti ndipo akutipo chaniiiii????
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 2 месяца назад
You dont know how it works with this politicians... The judicial system is captured no matter how he trys he wont win
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 2 месяца назад
Aphedwe Zikhale ng'oma asanaphe inu chimunthu choipa ngati imfa.to hell with him.
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 месяца назад
Chakwela ndi Galu ndi mfiti
@daviechannel8603
@daviechannel8603 2 месяца назад
Mmmmmmmm
@swinibanda5412
@swinibanda5412 2 месяца назад
Nkhwidzi nsanje ufiti zikupwetekani mwachita kuonetseratu
@Thewarrior7093
@Thewarrior7093 2 месяца назад
Koma za phone zo zandikwana , why can't u just buy another phone and move on?? Komanso it's better to act than to be sending ma voice note akwanira
@edsongeorge8032
@edsongeorge8032 2 месяца назад
Ndiyandalama zambiri aise
@mbonilekisebe2286
@mbonilekisebe2286 2 месяца назад
It's his phone nde asapange claim??
@vincentmpighu1080
@vincentmpighu1080 2 месяца назад
Hater
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
ndipo zikhare sitikufuna ife ukunamiza anthu kunkhata bay chimunthu chakuba ndi mganda wakoyo
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 2 месяца назад
Kodi osampasa bwanji telephone yake mbuzi inu
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi 2 месяца назад
Muli ndisoka a mcp
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
ndiposo ife anthu ndife zisiru mafumu nanuso kumpotokoo ndinu zisiru koposa kufera ndarama ana anjoka inu
@AbduKalhackimKadzuwa
@AbduKalhackimKadzuwa 2 месяца назад
Kodi usilu bwanji
@MynessChirwa
@MynessChirwa 2 месяца назад
Kulakwa
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 2 месяца назад
AKAMPLEPO KAKUWA ,MUSADANDAULE MULUNGU ALINANU , NDIPO ACHAKWERA MATSIKU AWOT OKUFA AYANDIKIRA , AZIKHARE NG,OMA NAYE ALI PANGOZ YOOPSA ONSE AMCP SAMALANI KWAMBILI ,ANTHU MUDAPHA KUCHIKANGAWA AJA ABALE AWO AMADALIRAT NDIPO SANGANGOKHALA CHETE KUKUSIYANI MUZISANGALALA MUYENDA MARISECHE MISALA DZIKO MUNO NDIPO MUKULIMBANA NDI ANTHU OSALAKWA ,OLAKWA MULI INU ,AGALU INU MACHENDE AMANU KUYAMBIRA PRESDENT WANUYOSO MUZUZIRANJI ANTHU MUDZIKO LA DEMOCRACY? KODI PM AKADAT AZICHITA MUCHITAZI MUKADALOWA BOMA? CHILIMA MWANGOKONG,OTHA AGALU AMFITI INU ,MUTHU ADAKULOWESANI BOMA MUDALI KUNJA 31 YRS KOMA KUMUPHA AMFITI ZIKHALEYO MUTU NGAT WAMVARA CHIGOBA CHASITIKALI .MASOWO OFINYIKAWO MWAZAZA UMFITI MENEMO ,MALO MOMUUDZA CHAKWERA ZAZERU MUMAYAKHULA ZOPUSA ZONAMA AGALU INU MWANDIKWIISA KWAMBILI CHOMWE INEYO KUPEPHERERA DAILY BOLA CHAKWERA AFEEEE NDIPO AFEEE NDITHU WAPHA CHILIMA NDI ZING,OMAYO MIMBA NGAT MWAKHUTA NSIMAYA YANANTIBURE CHONCHO UMFITI BAS
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
mkuyankhura hee msewu wakusisya munadya kare ndarama iweyo ndi mganda anthu wopusa inu wosamakonda kumuzi kwari
@JervisDicksonMzinda-vu9vr
@JervisDicksonMzinda-vu9vr 2 месяца назад
How much money did Kamlepo and Mganda eat? How much money was initially allocated to the MZUZU Usisya Road project? Give your answer in Billions because I want to relate the billions embezzled to the billions initially given for the project. I want to estimate the number of billions which they eat..
@custommantchombe-rn1oo
@custommantchombe-rn1oo 2 месяца назад
Kumulakwila munthu
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 месяца назад
Akuifuna 4n osagula yawo bwanji
@desmondshugar4585
@desmondshugar4585 2 месяца назад
BOMA iyi itipweteka ndithu
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 2 месяца назад
Sakuphani iyayi akunama amenewo mimba ngat ameza azimai oyembekezera atatu choncho paimidwapo zikhareyo shape ngat chigayo chopera soda.
@swinibanda5412
@swinibanda5412 2 месяца назад
Kodi inu bwanji zipani zose mumangoti akufuna akupheni siinu amisala koma? Chimtima chanutu inu ndichoipa mulikutali ndi mulungu
@Kasiya-gp7fm
@Kasiya-gp7fm 2 месяца назад
Iwe mtima wako ndiwoyera ?
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 месяца назад
Ndikapolo wachabe uyu tasiye
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 месяца назад
atiziwa kumandemo uyu
@vincentmpighu1080
@vincentmpighu1080 2 месяца назад
Team chikangawa
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 2 месяца назад
Akamulepo Mulungu alinanu cholinga ndipo Mulungu ndizatheka bji zidutsa nyengo izi
@rodglae6657
@rodglae6657 2 месяца назад
😢
Далее
#kikakim
00:17
Просмотров 8 млн
These Are Too Smooth 😮‍💨
00:57
Просмотров 6 млн
Afrikaans Nuus l 22 Oktober 2024
23:51
Просмотров 10 тыс.
#kikakim
00:17
Просмотров 8 млн