Тёмный

KANDIMVERERE!! KUSANTHURA BWINO ZAKUTHETSEDWA MULANDU WA CHILIMA by (DPP) 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 54 тыс.
Просмотров 12 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

12 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 70   
@AdmoreSingini
@AdmoreSingini 4 месяца назад
Mwalandira ma envelope this is un professional to journalist like you guys ndimakupasani ulemu koma apapa mwapala guys.
@EvansNaphazi
@EvansNaphazi 4 месяца назад
Ma tv omwe akudya ndalama za boma sasowa
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 4 месяца назад
Program yoonetsa mbali iyi,ndipo Chawezi aononga Mibawa ndi Program aaah
@Mikelemiphert
@Mikelemiphert 4 месяца назад
This guy ndi wa MCP no doubt about it, muononga nazo mbiri ya Mibawa Tv
@user-ms8tm3yf7d
@user-ms8tm3yf7d 4 месяца назад
Chawezi,,,,,ngati magwiridwe ako a ntchito ali choncho basi ntchito yanu simuiziwa,,,,ndiwe chisiru kwabasi
@user-le3lr6jn7g
@user-le3lr6jn7g 4 месяца назад
Ngati kuli munthu amene akupangitsa kuti MI awa ibowa ndi Chawezi MI awa muzimvere chisoni ndi chifukwa chake times imakuwinani
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 4 месяца назад
Chawezi mbuzi yosaganiza yeniyeni anganene kuti katangale akuyenda bwino kumalawi ndiwe manyakanyaka wezi mumutu muli mphusi ndiwe mumthu mumozi sukufuna Malawi akhale wabwino anthu opanda zeru wanditolamo kwabasi
@uchizJoelMumba
@uchizJoelMumba 4 месяца назад
Chawezi banda kulakhula mmene khani ilili koma cadet sangakondwe ndichilungamo cadet uli madzii!!!!
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 4 месяца назад
Chawezi banda manyazi mulibe munthu womvetsa chisoni chawezi
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 4 месяца назад
Koma uyuyu asadzabwelenso apa Malawi akadasuntha America ija ikudzudzula chani iwe ndi mbuzi ndithu......mulomo wabodza umanyansa Yehova
@jamesgama5489
@jamesgama5489 4 месяца назад
Chakwera ankati nyasi saphimba zimawulura ndi ntchentche apa tichedwepo paphimbidwa nyasi apa.
@RaymondProsperDouglas
@RaymondProsperDouglas 4 месяца назад
Kuyankhula kuti akutameni ndani a chawezi
@AndersonInnocent
@AndersonInnocent 4 месяца назад
Sindidzamvelanso mibawa ai chifukwa chokonda mbava Chakwela ndi Chilima ndi mbava zachabechabe komanso Nankhumwa mungamuike mugulu loti angathe kutsogolela dziko
@DavieWemusi
@DavieWemusi 4 месяца назад
When nonsense is well dressed 😂 a Chawezi Banda nzeru zake ziti zoti mukapikitsane ndi Professor Arthur Peter Mutharika.. ma dunderhead journalist 😂😂
@FelixBMbewe
@FelixBMbewe 4 месяца назад
😂😂😂 am ashamed of myself this guy ndimaona ngati ndi ozisata koma aaaa he's corrupt
@PiterDeleza
@PiterDeleza 4 месяца назад
Achawezi mukusocheresa anthu inu muzinena zothandiza dziko lanu osati zopusazo.
@muhammadshaibu5809
@muhammadshaibu5809 4 месяца назад
Wakwiya ndi program iyi ndikhadeti, koma zoona zake ndizoti muli chilungamo chokhachokha
@yamikanifischer
@yamikanifischer 4 месяца назад
Chawedzi chibandzi chikusamwa ndithu
@simonpaul6567
@simonpaul6567 4 месяца назад
Ndinu a mcp inu asakudziwa bdani nonsens
@petermukhori1796
@petermukhori1796 4 месяца назад
Kodi Chawezi anachokako ku MBC? Kapena ukuku wapita ngati guest?
@FrancesMitengo-p2d
@FrancesMitengo-p2d 4 месяца назад
CHAKWERA AKUOPA CHILIMA KUTI AMUULULA CHIFUKWA MULANDUWU UKUMUKHUZA CHAKWERA CHILIMA SANABE YEKHA AI
@Amgwagwa
@Amgwagwa 4 месяца назад
Obwande. Mulibwanji
@TyconSululuwa
@TyconSululuwa 4 месяца назад
Aaa koma inuyo mukuyankhula bodza ngt ana eni eni Amalawi anachenjera and moreover anthu tikukuziwani kuti ndinu ma cadet a MCP
@honestmlengah30
@honestmlengah30 4 месяца назад
Chawezi Banda! Chawezi Banda! Chawezi Banda! How many times have I called you? Ask yourself where is Steven Maseya, where is Hope Chisanu. Nawonso ankatero kazikangogwirani ntchito yanu osamalowerela nkhani za ndale muzanong'oneza bondo. I didn't expect this from you Deus big time!
@user-mj3ms4jt3b
@user-mj3ms4jt3b 4 месяца назад
Nthawi ya DPP kunali katangare wa nyoooooooo ndipo samaika zinthu poyera. Pano boma ili tiyeni tilithoko chifukwa likumaika zinthu poyera. Chinaso chilungamo tiyeni tiziyankhula, amalawi tikanakhala kuti tikulamulidwabe ndi DPP motsogozedwa ndi amaliseche akumwera bwezi tili pamavuto akulu kuposa amene tili nawo panowa
@DavieMisomali
@DavieMisomali 2 месяца назад
Chawezi kunali azako ankachemelera nchochi, uziwekuti tonse alliance ikamachoka Chaka 6:09 chamawa iweso upezeletukoka Malo oti uzikagwila
@marypatriciamakuru226
@marypatriciamakuru226 4 месяца назад
Aaaaaa cha we, I ndiwe mbuzi ya munthu ulibe umunthu ndi Amalawi anzako Chasunthamo ndi chani mbuzi ya Mano kunsi iwe watikwwana
@JTUPHIRI
@JTUPHIRI 4 месяца назад
Chawezi sangandize kanthu tsogolo la dziko lino, akuoneselatu kuti ndi ojiya wa MCP zomwe sizoyenera ndi program yanuyi.
@user-pw2dq1yw4b
@user-pw2dq1yw4b 4 месяца назад
Uyuu WA tonse alliance
@louisgolden
@louisgolden 4 месяца назад
Iwe cheweza mapazi ambuyako MCP ndi manyi achipani anthu woyipa opita pasogolo ndichitsiru osangoyamika kandalama akupasako bwanji iwe galu eti
@LukaAron-el5qh
@LukaAron-el5qh 4 месяца назад
Aaaaaaaa chawezi nde makhwara alipo kuchipatalalo
@duncainjimmy
@duncainjimmy 4 месяца назад
Ngati katengale akutha bwanji dziko likusauka kuposa ma boma Ena aja bwanji ?
@Littlefair7
@Littlefair7 4 месяца назад
Kodi mkulu Chawezi wabwereranso ku Mibawa? Nkhani yabwino ndimadabwa uli kuti? Bwande kuyipatsa moto mibawa😂😂😂
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 4 месяца назад
Aaaa iwe ndi galu kwabasi chisilu ndi MCP yakoyo pali chadzelu ndikoyamba kukumvelani tv yanuyi ndimangomva kuti mwadya ndalama zaboma apa ndadzimvela ndekha inu afiti amene mukuthandidzila kuti malawi tikhale mamvuto tikomane 2025 kodzekani ndi MCP yanuyo
@zayedmitawa8345
@zayedmitawa8345 4 месяца назад
Chawezi anayamba bwino koma waonetsa kuti akudya za MCP. Kunena zoona Boma komanso ACB lilibe umboni okwanira kuti Chilima ndi wa corruption kapena Chakwera akuopa kuti apangidwa involved no matter kuti constitution ikuwateteza. Pa za Nankhumwa,DPP siinampilingitse koma amaoneka kuti anali ndi dyera lolamulira DPP nthawi isanakwane. Nankhumwa anabweretsa mgawikano mu DPP ndipo at the end anaonetsa kuti MCP bought him to bring confusion in DPP. Chawezi nawenso ndiozitsata koma uli mbali ya Chakwera.Supposed to be Neutral ndie poti mwati the program is sponsored exactly we know the Sponsor.
@ScrarNation
@ScrarNation 4 месяца назад
Chawezie ndiwe zoba what you should know is dpp government siinamangeko vice president chifukwa nthawi ya dpp kunalibe katangale ngati pano and you should refrain from attacking APM and dpp in almost all your every program
@henryhenry6632
@henryhenry6632 4 месяца назад
Guys ndakunyadilan kufotokoza monveka bwino
@user-le3lr6jn7g
@user-le3lr6jn7g 4 месяца назад
Mau oti Chawezi, ndichitonga tanthauzo lake ndi Chaulele nde Chaulele sichingakhale chikuyankhula chanzeru
@duncainjimmy
@duncainjimmy 4 месяца назад
Mwauluratu a Chawezi kuti mukusapota MCP ndipo mwamema apa kuti kusavotera MCP ndi mistake yaikulu maka pa nkhani zakatangale
@veronicatembo382
@veronicatembo382 4 месяца назад
Chawezi Banda uyu akufuna ku state house, muzivera mene amaikilira boma kumbuyo,
@YoungMwacho
@YoungMwacho 4 месяца назад
Chawezi ukuoneka ngati ndiwe pro MCP. When analysing try to use logic, do not comment ngati ndiwe party loyalist. Nankhumwa sadekha koma is dull. Chawezi your profession is compromised.
@juliusnjerengo2610
@juliusnjerengo2610 4 месяца назад
Ndachitsiru awa.
@giftmwale8475
@giftmwale8475 4 месяца назад
Chawezi the great❤
@mavmsusa1310
@mavmsusa1310 4 месяца назад
Chawezi ndi wa Congress, period!!!!
@mavmsusa1310
@mavmsusa1310 4 месяца назад
Chawezi, bodza!! Mlandu sunayende bwino. Ukunamiza ndani kodi?
@user-je7qi9cr6e
@user-je7qi9cr6e 4 месяца назад
Chawezi siulisharp
@FelixLastoJafali-we7yb
@FelixLastoJafali-we7yb 4 месяца назад
Chawez musachuluse ndale plz amalawi zatichulukira
@innocentmanyera1861
@innocentmanyera1861 4 месяца назад
ipondeni fadaaaaa kkkkk koma chawezi hahahahah
@duncainjimmy
@duncainjimmy 4 месяца назад
Ngati chili chitsanzo chabwino bwanji Chakwera akubisidwa kwambiri koma only attacking Chilima why
@user-pw2dq1yw4b
@user-pw2dq1yw4b 4 месяца назад
Chawezi iweyo usayikile kumbuyo mcp mwanva malawians there suffering bro don't say boma lako LA mcp lasintha zinthu
@JamesChingombe
@JamesChingombe 4 месяца назад
Nichifukwa chake timamvela times coz inu amibawa mumawonetsa mbali kwambiri
@user-rl5zq1qr4d
@user-rl5zq1qr4d 4 месяца назад
iwe chawezi pannyero pako onse amene wachula aja kuti anawachosa chifukwa Cha katangale panopa ndi afulu sanamangidwe katangaleyo ndiye atha bwanji chilima anaba lero ndi mgulu ndiye katangaleyo akachepa bwanji pantumbo pako Nankhumwa ukununenayo sanatsutse mothandiza anthu anai kumbali ya boma ndichifukwa chale boma limangopanga ziri zonse once again pantumbo pako
@daviechirwa5596
@daviechirwa5596 4 месяца назад
Akufuna promotion awa
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 4 месяца назад
So mankhwala aliko kuchipatala pamene nankhumwa anavomereza budget no mutu chawezi
@jamesLimited-gu9nd
@jamesLimited-gu9nd 4 месяца назад
Achiweza ndi wa mcp
@user-uf4db7im7d
@user-uf4db7im7d 4 месяца назад
Galu ameneyu kwambiri chawezi mbuzi ya munthu. Udzachita manyazi iwe
@Johnybegood260
@Johnybegood260 4 месяца назад
Mwaonesa mbali
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 4 месяца назад
Chawezi ndiwe galu iwe nyasi iwe
@yamikanifischer
@yamikanifischer 4 месяца назад
Chawedzi uziyenda cha mpen wamva
@gabrielmaluwa1038
@gabrielmaluwa1038 4 месяца назад
Chawezi ukuyankhula bwanji
@JamesChingombe
@JamesChingombe 4 месяца назад
Palibe zothana ndikatangale kuno kumalawi
@JustinPhiri-kq2bb
@JustinPhiri-kq2bb 4 месяца назад
Mlandu umenewu bigfish ili involved
@NoelKhwimba-bh3ts
@NoelKhwimba-bh3ts 4 месяца назад
Chilima waiphula
@spargomw
@spargomw 4 месяца назад
Chaweziyo asatipweteketse mtima ndipo asatiyankhulitse pambali. After all dressing yao ili poor heavy. Munthu wakuda mkuvalaso malaya akuda, mavalidwe abwanji awa? Faken bastat
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 4 месяца назад
Agalu
@FelixBMbewe
@FelixBMbewe 4 месяца назад
You must be jocking?? Koma mwazidyatu za MCP moti really Chawezi you can go so low and say live on tv that we are on the right path when it comes to corruption? Like seriously?? what a shame. Am so disappointed in you personally.
@jamesLimited-gu9nd
@jamesLimited-gu9nd 4 месяца назад
Achawezi ndintola nkhani wa mcp
@user-uf4db7im7d
@user-uf4db7im7d 4 месяца назад
Mtolankhani uyu anthu amulemba chalk kumbuyo mbuzi yopysa
Далее
Вопрос Ребром - Булкин
59:32
Просмотров 1,1 млн
Customer Care Sn2 Ep 48B
24:59
Просмотров 28 тыс.
CRUISE 5 WITH ISAAC JOMO OSMAN
1:11:28
Просмотров 61 тыс.