Тёмный

KODI A VAISI PULESIDENTI AYAMBA KUTUMIDWA NDI A PULESIDENTI CHAKWERA PANO? 

MALAWI WATHU
Подписаться 10 тыс.
Просмотров 11 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 50   
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 5 месяцев назад
Ine peter munthalika sindimanva zonena zake
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 6 месяцев назад
Awa eish
@raytavares2256
@raytavares2256 5 месяцев назад
If Uladi has been forgiven then Norman Chisale and Brown Mpinganjira must also be forgiven like the way Suttar here in uk has been forgiven.
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 6 месяцев назад
Kumkuyu uziyankha ngati ndiwe munthu woti uli ku State house and ndiwe munthu mukulu wazeru zake komaso poyankha musatengere ndale muziziwa kuti kumwamba kuli Yehova. Chilima anamuyimika ntchito chifukwa chamilando. Pamafunika mulando uthe ndipamene ayambe kumutuma akapezeka osalakwa. Musatenge ngati amalawi wose ndiopusa . Amalawi ake ati amene amgasanhalale ndizopusa zimene zikuchitikazi. Tili ndi ana amene tikufuna kuwaphuzitsa chilungamo poyankha osati zopanda pake
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 6 месяцев назад
Bwanji iye chakwera amati Aku amereca amati akulowerera zakukhoti iye sanalowerere apa?
@MaxweJohn
@MaxweJohn 6 месяцев назад
Apule akanabwela atiuzekuti ndiyambaso kumutuma
@Yusufu-Daudi
@Yusufu-Daudi 6 месяцев назад
Kunkuyu palibe zimene ukuyakhula apa
@KumbukaniChimbalanga
@KumbukaniChimbalanga 6 месяцев назад
Kuyankha kwakeko! Ungolimbana naye uyo ndiopanda mzeru
@FrenceTsitsani
@FrenceTsitsani 5 месяцев назад
Zomwe akuyankha kumkuyu akusephana ndi mfunso chifukwa munthu amene ayankha milandu amalandidwa ziphatso zoendera zantheka bwanji kt atumidwe kunja
@KimChisola-gm7yw
@KimChisola-gm7yw 6 месяцев назад
Apulezidenti akuopa kuyaluka
@ChancyMinofu
@ChancyMinofu 6 месяцев назад
Mmmm koma anthu andalewa koma amaopa Mulungu? Koma eeeee ayi ndithu Mulungu alowe m'mitima mwa anthu andarewa makamaka akumalawi kuno eeeee oho
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj 6 месяцев назад
Akukuyu ndi mbussi yophanda bussa capital city of Port Elizabeth sauth Africa live now
@HanishaissahKagansa
@HanishaissahKagansa 6 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂 president uyu akumatitenga ngati ife anthu opanda nzeru komano chimene timalondoloza chilichonse chimene amanena 😂😂😂😂
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 5 месяцев назад
Kunkuyu ni masimba
@gabrielmaluwa1038
@gabrielmaluwa1038 6 месяцев назад
Aaaaa awa ndachitsiru a kunkuyu
@raytavares2256
@raytavares2256 5 месяцев назад
After all he has been getting free salary for all these months which he has been suspended.
@wisdomchilanga723
@wisdomchilanga723 6 месяцев назад
Nkunkuyu Mutu umamupweteka kwambiri palibe chanzeru chimene angayankhe apo
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 5 месяцев назад
Tamuonereni chikhophe chake ngati munthu wakufa chalazalo
@raytavares2256
@raytavares2256 5 месяцев назад
Sometimes stupid questions don't benefit anything from us, can you imagine wasting time to discuss about who introduces the president of Malawi to stand up within the presence of the deputy president, why not ask questions which benefits citizens to have updates concerning all the crimes of ministers or civil servants who broke the law or were suspects regarding financial embezzlement or fraud and money laundering from the government of Malawi. The deputy presidents are meant to be immuned or have the right to pardon themselves in the events where his job discription would be having difficulties to be replaced in accordance with his portfolio, again the president has the right to offer clemency or pardon anyone who has committed crimes or serving jail sentence like MP Uladi. But why not discuss more important things than the questions which are of no kupindula 😢???
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 6 месяцев назад
Mtsogoleri akapena and kupereka dedline kufika siku ili zizaduse zikadusa president amabwera ndikuchosa ntchito anthu aja alephera ndiye president amaziwika kuti safuna zachibwana. Mwachisazo nduna yazaulome mbwezi pano ntchito inatha and ku immigration bwezi pano ntchito inatha tili ndi musogoleri sakuziwa kanthu
@StevenGJohn
@StevenGJohn 6 месяцев назад
Kunkuyu ndichitsiru kwambiri machende ako
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 6 месяцев назад
Kumkuyu chilima chakwera mpakana ndi ma judge omwe macende anu mukufuna muzitipusisa ifeo inu agalunu muuzane kuti ma chende anu nonse mpakana ndi ma judge achilaziwoso malisece awo nawoso onse 😂
@LuteSynos
@LuteSynos 6 месяцев назад
Tizaona thawi. Ya vote😢😢 for😅
@BrightZionga
@BrightZionga 6 месяцев назад
Kunkuyu adzapsya ndi mano omwe
@MphonoMatube
@MphonoMatube 6 месяцев назад
anthuwa onse ndi atambwali okhaokha
@AbuOsman-ts6ef
@AbuOsman-ts6ef 5 месяцев назад
Dzatopesa izi
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 6 месяцев назад
Poti chilimaso naye mutu ukuwoneka kuti siwugwira ntchito akanakhala wazeru akanakana kuti abwana mulando wanga uthe kaye. Kuti ndine sindingalole zopusa
@princedavidmapiri2876
@princedavidmapiri2876 6 месяцев назад
Kumalawi kuli zibwana zeedi komano anthu awawa asawayese Kuti amalawi ndi anthu opusa matsiku amatha ndikugona 2025 ndipompano chenjerani ndimayankhowo
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 6 месяцев назад
Akoma lero chilimayo mwakwera pansana kuti akuoloseni mwauponda
@dorcasmwale6328
@dorcasmwale6328 6 месяцев назад
moti nthawi yonseyi chakwela samadziwa kuti anali asanapezeke ali olakwa? kapena chilima anawawopyeza a president ?
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 6 месяцев назад
Nsanje kwambili adpp
@clemencechilindira2318
@clemencechilindira2318 6 месяцев назад
Ufumu umodzi sumaukilana
@PatrickGonagona
@PatrickGonagona 6 месяцев назад
I think kunkuyu ndi mbuli
@HaroonMaundala-lg5lg
@HaroonMaundala-lg5lg 6 месяцев назад
Kukuyu mboliyako wava. Iwe ndiwe chisilu cha muthu. Ifetu tikumafuna kuti uziyankha zeni zeni osati zotitayisa thawi. Galu wakoyu amakupasa ndalamayu azakupwetekesa wava.
@spargomw
@spargomw 5 месяцев назад
Kunkuyu wamwa mankhwala nthaw yaitali nde mutu wake sugwira. Mutu ofanana nd wa Mbalame'wo
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 6 месяцев назад
Kodi apule alakwa kuwtuma achilima amalawi ndinu wotani
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 6 месяцев назад
Kumkuyu ndimbuzi
@dontreybanda278
@dontreybanda278 5 месяцев назад
Kunkuyu mapwala ake
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 6 месяцев назад
Mxm this government is useless nyani eeich 😂😂😂😂 manyaka
@billymhoni9527
@billymhoni9527 5 месяцев назад
Chilima alibe mulandu
@JaffaliWasili
@JaffaliWasili 6 месяцев назад
Inu kodi kunkuyu ndimunthu wa dziko la pansi galu ngat uyu mbolo yake
@LajabuYassin
@LajabuYassin 6 месяцев назад
Boma ili lizipita latitopetsa lamaboza likapume
@PaulMvuma
@PaulMvuma 6 месяцев назад
Kodi bwanji amalawi muli ndisanje
@HanishaissahKagansa
@HanishaissahKagansa 6 месяцев назад
Zanje yanji inu mbuyo mosemu unayamba wamva kuti chilima wapita kwakuti ?
@IshakaLifa
@IshakaLifa 5 месяцев назад
😂
@AishaChipande
@AishaChipande 6 месяцев назад
Pachipysisi pako kukuyu
@KindwamiZhuwaki
@KindwamiZhuwaki 6 месяцев назад
Kunkuyu udali munthu wabwino koma pano chidazi chako
Далее
CHILIMA FORETELLS
3:42
Просмотров 21 тыс.
Masintha Yalira Imfa ya Chilima!!
15:38
Просмотров 10 тыс.
Osayiwara Kuti Zinayamba Bwanji?
8:51
Просмотров 3,5 тыс.
AKWENI ALAVULA PANO...?
56:50
Просмотров 262