Тёмный

KONDWANI NANKHUMWA WAUZA ANTHU OMWE ANABWERA KU CONVENTION YAKE KUTI AWAPATSA NDALAMA YA GO AND BACK 

Makosana
Подписаться 92 тыс.
Просмотров 6 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

17 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 22   
@PetroKachingwe-jf7dh
@PetroKachingwe-jf7dh 3 дня назад
Ulemu wanu Abwana Mwayesetsa kwambiri kumbali yanu apa zatheka basi Onyoza anyoze Gwilani ntchito ndi MCP
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 3 дня назад
But Nankhumwa is a good person very humble very kind so charismatic, My worry is asangokhara ndi mtima ofuna kuchosera ma vote akumwela nkupampatsa mwayi zipani zina
@ansteadmponela8578
@ansteadmponela8578 3 дня назад
Y .o
@wisdomchilanga723
@wisdomchilanga723 3 дня назад
Mugundwani wa chikangawa Malawi party
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 3 дня назад
This is another branch for mcp
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 3 дня назад
Ngati anthu sakuziwa zayiwe satana iwe umawoneka ngati munthu wabwino
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 3 дня назад
Osangoti ndalama zochekera ku mcp bwanji, mufuna muwapusise ndani inu
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 3 дня назад
Anankhumwa mukusewela ndi njoka Inu mulibe utsogoleli mungolankhula zoloweza
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 3 дня назад
Ndalama watenga kwa chakwera zo becareful
@MaggieBanda-ft5tu
@MaggieBanda-ft5tu 3 дня назад
Blanch of chikangawa party
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 3 дня назад
Mbambande awawa anakoza
@PaxKinley
@PaxKinley 3 дня назад
I know Kondwani Nankhumwa koma ndi Mbuzi ya munthu ndi ndi munthu oipa akufuna kugulitsa dziko, Chikangawa Party
@MayesoKalupha
@MayesoKalupha 2 дня назад
Kodi inu tatiyeni timuyeseko nankhumwa tisamangosankha azidalawa,nchifukwa mzeru zao akumangoganiza za kupha.
@ruthmpunga6331
@ruthmpunga6331 3 дня назад
Apule sakukhulupila anthu awo mpaka kupeleka okha uniform Ndalama imeneyi sangalozedwe kumpasa munthu ndiye ine ndiakhulupilile kaya
@isaaczuze
@isaaczuze 15 часов назад
Za zii zosakoma olo ....nankhumwa chanu palibe
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 3 дня назад
Mwa nankhumwa ndimaonamo chitsulo cha njanji
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 3 дня назад
Vuto la ku Malawi azitsogoleri ali ndi flowering politics, kungofuna kutchuka basi, koma kuti a Malawi mudzawPangila chiani ayi, ndipo mudziwe izi: mkango woopsya ndi wosabangula kulira ayi, chitsanzo ndi Chakwera, adanamiza a Malawi zinthu zambiri, nothing happened.
@GenialaChalera
@GenialaChalera 3 дня назад
Umakwana
@SmdiziOfficial-xg1tt
@SmdiziOfficial-xg1tt 3 дня назад
Koma mwayesetsa bwana kumbali yanu
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 3 дня назад
Olo kutani chipani iche palibe yemwe angavotere uyu ndiwokuba ngati chakwera
@GodfreyChauluka
@GodfreyChauluka 3 дня назад
😂😂
@MayesoKalupha
@MayesoKalupha 2 дня назад
Kodi inu tatiyeni timuyeseko nankhumwa tisamangosankha azidalawa,nchifukwa mzeru zao akumangoganiza za kupha.
Далее
Семья с двойным дном. Рассказ
2:45:06
Семья с двойным дном. Рассказ
2:45:06