Тёмный

Ku DPP Kuli Ma Gawo Awili Ena Ozindikila Zakufunika Kwa ID Ena Ongofuna Kusokoneza - Agape Khombe 

Nyasa VoiceBox
Подписаться 27 тыс.
Просмотров 3 тыс.
50% 1

On Nyasa VoiceBox, Agape questions the DPP's decision to go to court over using ID as voter identification, while the same DPP is requiring delegates to have a National ID to participate in the convention.
Pa Nyasa VoiceBox, Agape ikukayikira chigamulo cha DPP chopita kukhoti kamba kogwiritsa ntchito ID ngati chizindikiritso cha ovota, pomwe DPP yomweyi ikufuna kuti nthumwi zikhale ndi chitupa cha National ID kuti zichite nawo msonkhano.
#malawi

Опубликовано:

 

10 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 64   
@CassimoMangochi
@CassimoMangochi 26 дней назад
Machende ako iwe khombe ma ID ali ku central osati malawi yonse
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 26 дней назад
ID ndiyofunika and dpp siyikukana kuti ID ndiyofunika. Koma anthu mumalawi tilimo over 20 million koma anthu ama ID 4 million ndiye mukuganiza kuti anthu 16 million anachoka ku Rwanda kuti asavote mec or nrb school yimene anaphuzira ndi iti.
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 26 дней назад
ID ndiyofuni bvuto DPP imakhulupilila ma activist ndamene amasokoneza kwa mbili andi ngati DPP ikumaluza zisakho akumaluzisa ndi ma activist amene daily amakhala ngati olakhulila chipani very shem
@EdwardSamsonMillimbo
@EdwardSamsonMillimbo 26 дней назад
Osamaphatikiza chipani ndi bungwe kumakhala kusokoneza
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 20 дней назад
Ndiye anthu 20million-wo onsewo ndiakuluakulu palibe ana a les than 16 yrs? Masamu ako ukuwapanga bwanji galu iwe
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 20 дней назад
@@isaacchiwaula731 galu sinalengedwe ndi chifaniziro cha Mulungu uziwe chimenecho. Koma poti anthu opusa amadana ndichoona chilungamo chimapweteka ndichifukwa wakwiya ndipo ukwiya ndichilungamo cho muoaka utavesesa
@user-nq2ih6xl5z
@user-nq2ih6xl5z 26 дней назад
Iwe uli ndi zaka zingati, khala chete palibe chanzeru chomwe ukukamba mbolo yakonso
@user-qi8xe7qh1e
@user-qi8xe7qh1e 26 дней назад
Iweyo or mayi ako kapena bambo ako kaya mayiko mayiao anayamba liti kungwirtsa ntchito id mayiko agogo akowo ukafunse kuti agogo anthu kunjaku akunena za ma id kodi id chiyani ukaone Ngati angakuyankhe usaowaletu uli m'gulu lakupha chilima kuchikangawa masiku abwela khalano pheeee mudzaone
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 26 дней назад
Well spoken
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 26 дней назад
Ndiwe galu kwabasi 😂😂
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 26 дней назад
Mukhaula Chaka Cha mawa a MCP mufuna kubera using IDs 😂
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 26 дней назад
Mcp yikabera bwanji pamene inuyo adpp ndinu mukufuna kuba kuti mukatenge anthu mu Mozambique umo wopanda chiphaso kuti azavote mu malawi musawope inuyo ndinu munayambisa ziphaso mumalawi muno sopano bwanji mukuti sizabwino vote ndichinsisi chamunthu mwina dpp yikhoza kuzawina ndi ma ID omwewo ndiye mukuganiza chani makamaka
@marryphili5419
@marryphili5419 26 дней назад
Chisiru iwe ife ma lD tilibe chifukwa cha boma la MCP likufuna kubera zisakho bwanji amanamizira netiweki
@user-mj2te7vl6p
@user-mj2te7vl6p 26 дней назад
Aliyese akavota opanda ID propaganda iweyo
@LamseyLazarous-dl5qd
@LamseyLazarous-dl5qd 26 дней назад
Mbalame iyi
@ChimwemweBotha-k2z
@ChimwemweBotha-k2z 25 дней назад
Wayamba liti iwe kusapota MCP, paja waiwala uli ku Salima Technical umapanga support DPP. Ukufuna uoneke wa nzeru lero. Iya
@AbdalaZiyada
@AbdalaZiyada 26 дней назад
Iweyo ndi mbuz Yaa Munthu
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 18 дней назад
Chinyau cha Khongelesi chisatisokosere apa. Shatapu🙄🙄🙄🙄
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 26 дней назад
Nkhopeyonso ungooneka ngati kuti ku chikangawa Kuja unalikotu.
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 26 дней назад
Akufuna azizanyamula anthu kuchokera ku Mozambique cholinga azivota muno even Kuvota katatu
@Kiyamachilipa
@Kiyamachilipa 26 дней назад
Inuyo muli mbali itinerary, mbuli kapena ozindikira
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 26 дней назад
Inunso ndiye ndinu a chitsirutu, nkhani ya ma ID on election we know The motives of MCP nkubela zisankho. DPP siinanene kuti ma Deligates akavota ndi ID ayi . Ife tikudziwa kuti zigawenga za ku Zimbabwe ndi Ruanda zinalowa kumalawi kuti azachite chipongwe anthu and one of them ndi a APM,. Zigawengazi zauzidwa kuti munjira ina iliyonse akuyenela kumupha APM. Ndiye if u talk of ma ID ku convention, it's part of security purpose kuti akaone kuti amene akulowa ndi ndani. Aise iwe ndiamene uli mbuli mapeto.
@petertaulo8014
@petertaulo8014 25 дней назад
Utha kuyankhula koma uziwe kuti za imfa ya Chilima uzayankyha iweyo ndi anzako
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 26 дней назад
Kupanda id tizizatenga anthu maborder kuzavota kuno ku malawi
@user-hw5xx9kb2s
@user-hw5xx9kb2s 25 дней назад
Komaso ID simakhala ndi expiry date mwini alimoyo
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 26 дней назад
Palibe akukana kuti kukhala ndi ID koma kuti azifulumilitsa pomwe program ya ma ID yayamba posachedwapa zimafunika adakaunikira bwino chifukwa anthu ambitious alibe ma ID ndiye zovuta kuti anthu akagwiritse ntchito ma ID pozavota chifukwa anthu ambiri sadzavota chifukwa Ena alibe ma ID
@joebrown1158
@joebrown1158 26 дней назад
Iweyo ndiweso galu wa munthu kodi ndi angati amene ali ndi national identity?
@felixjoseph8161
@felixjoseph8161 26 дней назад
Kodi si uja anamukhapa chilima ku chikangawa ndiye lero angatiuze chiyani mapwala ake
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 26 дней назад
Bon kalindo ndi mbuli ndi amene akuwawuza a dpp za id saziwa chinachilichonse
@user-lp2sd7lt8b
@user-lp2sd7lt8b 26 дней назад
Kodi aDPP ali m'boma bwanji tinavota ndi maID
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 26 дней назад
Ndizofunika koma nanga bwanji madera ena dza nzikazo zikuvuta kutuluka ?
@MadalitsoChinkhonyo
@MadalitsoChinkhonyo 26 дней назад
Ndiwe ngali kobasi bwela tikakumana konko
@tasmania527
@tasmania527 26 дней назад
DPP ndi chipani cha anthu a mwano, a makani, ozikonda, ndi osankha mtundu. Amafuna zinthu zizikomera iwowo. Lamulo la ID linapangidwa pass kale kale ku parliament a DPP ali momo, koma lero chifukwa cha hunger for power akubweretsa zitsokonezo. Tikudziwa kuti anazolowera kubera zisankho ndipo ali ndi mantha ndi zisankho zikubwerazi.
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 26 дней назад
Kodi ngati panopa adpp akuchiwona kuti chiphaso chauzika sichabwino kodi boma limene linabwelesa chiphaso chazika ndindani amenewo nzeru alibe akufuna iwowo kuzabera zisankho akufuna kuzatenga amu Mozambique mo asatipusise opanda chiphaso asavote
@user-nq2ih6xl5z
@user-nq2ih6xl5z 26 дней назад
Iwe wabadwa liti kodi, mu nthawi ya kamuzu, muluzi, bingu timavota motani
@johnsoldier
@johnsoldier 26 дней назад
Iwe agape ndiwe kape kwambiri ndichifukwa ma demo anu munapangitsa ndi munuro adakuvutani iwe umakonda ndalama kwambiri ndiwe galu
@TonykalicheloKalichelo
@TonykalicheloKalichelo 26 дней назад
Kkkkk mumafuna mukalowe mukapange chisokonezo km mwagundikatu
@johnchicoti
@johnchicoti 26 дней назад
Cholinga chakuti adzabele zisankho a Dpp
@petertaulo8014
@petertaulo8014 25 дней назад
Iwe agape manyi ako
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 26 дней назад
Amalawi musaganize kuti anthu wose amene anaphuzira school kuti ali ndi zeru zina ndizipukupuku zeni zeni tonse mumalawi tikufuna kuvota mumalawi si muli anthu 3 million okha mec misala yokha yokha
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r 26 дней назад
ID ndiyofunik koman N l B ili ndichinyengo coz akuchita kusakhila owapasa lD ,koman ndiwe chisilu ndithu komaso ndiwe chikangawa
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI 26 дней назад
Chakwelawamupha chilima zasala zosatila Zach
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 26 дней назад
Kod iweyo ndiwosindikila kwambili kapena ndiwophusa bwanji Id amek mbali zina zisigwera ntchito machini palibe amene akuless kut ma Id akukanisa ayi akuyenera aliyese apese Id avote
@EmilyBanjachikwatula
@EmilyBanjachikwatula 26 дней назад
Tangopangani zoti anthu akhale ndi ID basi osati network idzivuta ku mmwela konkha ndiye kuti chani?? zikavuta basi tidzakatenga makalata kwa amfumu chifukwa chomwe akutathauza a dpp inu simukuchidziwa iwo akufuna kuti aliyense akhale ndi cha nzika koma mukufuna ku central konkha ndiye mumafuna adpp atani?
@Kiyamachilipa
@Kiyamachilipa 22 дня назад
Pepani bwana muli ku thiko kapena chikangawa?
@JohnTimbenao
@JohnTimbenao 26 дней назад
Iwe ndiwabodza bwanji. Iwe mabvuto omwe akuchita a nrb ndi mec sukudziwa. Ndiwe chitsiru. Ufuna kundiuza kuti munthu amakhala nzika pokhapokha akakhala ndi chiphaso cha unzika kokha. Galu
@PollyLysonLutepo
@PollyLysonLutepo 26 дней назад
Choyamba m'dzifunse kuti, Kodi chomwe chapangitsa kuti ID aikane ndi Chiani? Ine ndaona kuti zida zolembetsera ma ID zili pa chigawo Cha pakati pokha. Koma anthu ozavota Ali zigawo zonse ku M'poto ndi kumwera komwe. Ngati ndi njira yomwe m'napeza yozabera mwalephera. Chonde amabungwe ndi Dzipani zotsutsa kanani zovotera ID. Nafetso tikufuna kuzavota Kodi zogwilitsa nchito ID zinayamba chaka chiti? Kodi kumbuyo kunalibe zitsankho? Ndikubwelezatso ID, Tikane. Iwe walankhula wamva kuti takana za ID? Wukawawuze omwe akutuma kuti Takana.
@ConlardNkhoma
@ConlardNkhoma 26 дней назад
DPP yasowekela utsogoleli
@isaaczuze
@isaaczuze 26 дней назад
Awanso ndiachisilu ....mukufuna kusangalasa apongozi.......mugwela limozi ndi apongozi anu
@isaaczuze
@isaaczuze 26 дней назад
Amalawi ambili chakwera sakufunika chifukwa zimene akupanga sizikugwilizana ndi zomwe analonjeza .....ulamulilo wachakwera anthu ali pa umphawi wa zaonene ngakhale Pali zisilu zina zikuti chakwera wakweza ziko koma anthu ndi amphawi .....palibe cha nzeru chimene chakwera wapanga ndipo chakwera sindizamukhululukila ....munthu woyipa kwambili
@isaaczuze
@isaaczuze 26 дней назад
Ine chakwera Toto ...mbuli zokha zili pambuyo pake chifukwa mukupasidwa ndalama zomwe wabela amalawi
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d 26 дней назад
Machendeako iwe khombe
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 26 дней назад
Iwe galu kwabasi
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 26 дней назад
Dpp singapange zimenezo uyu akunama mbunzi yachabe iyi
@user-iw6cz5ft2l
@user-iw6cz5ft2l 26 дней назад
dpp sinakwitse kupita ayi
@MsondaBanda
@MsondaBanda 26 дней назад
Dpp expired no mutu
@HarryKandani
@HarryKandani 26 дней назад
Iwe khombe zidya ndalama za abusa ako a devaluation kwamtele wo and shut up
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa 26 дней назад
Agape khombe chitsiru cha munthu iwe puppet wa mcp u don't know what ur saying palibe akudana za id koma ma id ku southern region, eastern region and northern region sakulephesa anthu chitsiru iwe
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc 26 дней назад
Useless man mbolo yako nonsense
@NosiphoMazibuko-e9z
@NosiphoMazibuko-e9z 26 дней назад
Mbuzi iwe mukufuna kubela mavoti tikifuna 2025 owina adzawine zenini zimokondela vuto ma Id akutuluka kulilongwe konka inu mukwanitsa bwanji onse apedze ma id poti network ikumakuvutani ma passport ndi awa akukanika kutuluka
@ConlardNkhoma
@ConlardNkhoma 26 дней назад
DPP yasowekela utsogoleli
@Kiyamachilipa
@Kiyamachilipa 26 дней назад
Titenga iweyo kuti utsogolere
@yobesaikonde6166
@yobesaikonde6166 22 дня назад
Kkkkkkkkkkk Atsogoleri ine wa DPP Ndikuti eeeee utsogoleri tilibe , the interigent old man should rest. Enawa ndi nthata za njala akufuna mdala am,bele.
Далее
A DPP Kwawo Ndikufuna Kudzaba Mu Boma - Ben Longwe
35:40
The AI Cybersecurity future is here
26:42
Просмотров 157 тыс.
A Chakwera Opanda Anthu Mukhala Mfumu? - Pastor G Tembo
15:01
TIMES TV KUING'ALULA MBC TV - APWETEKANA AWA🙌🙌
30:44