Тёмный

KU GWEDEGWEDE KWAYAKA MOTO UKU ZAUZIMITSENI NDI INU OVERANU | 

DZIWE TV
Подписаться 33 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

13 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 32   
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 3 дня назад
😅😅😅😅😅😂😂bwanji kumasula kuti chikangawa akudwala kaya kaya😅
@ernesthkaunda7902
@ernesthkaunda7902 3 дня назад
Nice program.....keep it up
@RABSONSIKELO
@RABSONSIKELO 2 дня назад
Ku opposition kuja mkowawa osazakuphwekesa aii
@paulbanda3028
@paulbanda3028 3 дня назад
Mmakwana
@MabvutoMwakalinga-yl3ft
@MabvutoMwakalinga-yl3ft 3 дня назад
Ife tikuonera ndipo tikumvera mwatcheru....tiuzeni zikuti bwanji
@RodrickLucious
@RodrickLucious 2 дня назад
Aaaaaaa A Dpp ndizitsilu kwambiri akusowa zochita ndimakadet awa iyaaa
@TroubleKatsala-jp2li
@TroubleKatsala-jp2li 3 дня назад
Kodi achilima Aja munawalandantchito poeaganizilakuti Anaba ndrama lelo anthu ena m'bimamo akuba koma simukuwaimitsabwanji?
@MadalitsoChipangula-i3z
@MadalitsoChipangula-i3z 3 дня назад
Potsendera mfundoyi mpakana kuwalanda ziphaso zoyendera m'mayiko ena.
@robsonmapeto1911
@robsonmapeto1911 11 часов назад
Munthu uja anamuzunza zedi
@GraceMwase
@GraceMwase 30 минут назад
Ndipo ndimamva chisoni kwambiri Chilima anazunzidwa mpaka kuphedwa chonsecho ena akuba sakuimitsidwa ntchito mmmmh God will surely avenge his death
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 дня назад
Ndlama.tadyera nsalu tilandra koma voti kuipasa MCP or m'busa atameza baibulo or sheikh atamedza Quran
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 3 дня назад
Malangizotu aulele awa a pule mutamawagwilisa ntchito a Malawi azakukondani!!!
@UsiAnussa-n9h
@UsiAnussa-n9h 3 дня назад
Ameen
@RaphaelKatimba
@RaphaelKatimba 3 дня назад
Ngati simuyankhula za Chakwela ndiye mwalephera ma guy
@PaulChaposa
@PaulChaposa 3 дня назад
Palibe asakuziwa😂😂😂😂
@kadijachilwan967
@kadijachilwan967 3 дня назад
Ine sindikuona omuvotera zonse ndimbava zokhazokha
@HendrickBanda
@HendrickBanda 3 дня назад
🔥🔥🔥
@MuhammadjacksonMmad
@MuhammadjacksonMmad 3 дня назад
Okay nice
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 3 дня назад
😂😂😂😂😂Olo musanene ife tikudziwa kale
@RaphaelKatimba
@RaphaelKatimba 3 дня назад
Koma iweyo Selina ndi shasha kwambili. Koma a Malawi 🇲🇼 amakukonda kwambili
@jozyomar5361
@jozyomar5361 3 дня назад
Komabe wayidziwa 😂
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 3 дня назад
Kkk mukuziwapo kathu mesa amwalila mbali imozi😂😂
@JohnJumah-yf7qt
@JohnJumah-yf7qt 3 дня назад
Olo musatiuse tivela mu program ya nkhanga saona ndi antanyiwa
@TobbiePahuwa
@TobbiePahuwa 3 дня назад
Adya limodzi onse ndi okuba 8:18
@IbrahimJackson-i8h
@IbrahimJackson-i8h 3 дня назад
Abasi ife tanva
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 3 дня назад
Ayi zilibho kkkk
@ChicoBanda-kq7py
@ChicoBanda-kq7py 3 дня назад
Nditchoto yabwino
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 3 дня назад
Zoonadi zimenezo akugawa ma 2pin ndi salu lero angowanamiza anthu kuti alowa chipani cha mcp iwowo kuyakhula km anakawaziwa anthu achiyawo sanabise ayakhula kuti tizingo wadyela amenewo nawo amtenje angakope anthu kape ngat amenewo musawapange trust anthu amenewo ayakhula kuti sali ku mcp iwowo amapitila ndalamazo km samgayelekeze ku votera mcp mwanya amtenje 😂😂😂😂😂😂😂
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 3 дня назад
😂😂😂😂😂😂😂
@KazembeSemion
@KazembeSemion 3 дня назад
😂😂😂😂
@BiliatMzungudala
@BiliatMzungudala 3 дня назад
😂😂 tayankhulani inu
@UsiAnussa-n9h
@UsiAnussa-n9h 3 дня назад
😂😂😂😂😂😂😂
Далее
THE JAAKEV SHOW with KELL KAY
1:45:31
Просмотров 44 тыс.
WHICH SODA CAN FLY THE HIGHEST?
00:48
Просмотров 6 млн
Мои нет в ЛАПКЕРАХ
00:11
Просмотров 319 тыс.
LIVE: BBC Question Time US Special | BBC News
58:33
Просмотров 52 тыс.