Kunte inu mukulimba ndi iwe iwe wie akubawo adikire zimenezo 😅😅😅😅😅😅 ulemu wanu..... Boss yooo next azakhare serious coz he cud be furious when he saw zithu zabedwa nde akusekasooo Koma zimayamba 1212 next time i hope he gonna show us good things Thanks guys
Commedy sili mwala kweni kweni, content sikusangalatsa, kunte wapeza ntchito yaulonda after orientation akuba abwera amumenya aba katundu, abwana amupeza kunte atakomoka. Not that good as we expected