Тёмный

Limpopo FM khetchemu Ntanyiwa kutulukila tsopano ndipo amva kuning'ina ku bomako lero 

Malawi Trends TV
Подписаться 22 тыс.
Просмотров 25 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

25 июн 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 88   
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 дня назад
Mr Ntanyiwa tiudzeni anapha chilima asanathawe tidulanepo dziwalo please fast
@user-ks3uw8gj8h
@user-ks3uw8gj8h 2 дня назад
Komatu a Chimwendo Bandawo Mulungu akuwawona , ndipo akapitiliza adzamfa imfa yowawa
@leoleonard2103
@leoleonard2103 День назад
I love Limpopo fm because imakamba zowona, pls Malawi samala ukuyitana nkhondo mudziko Lako samala 👌🏽☝🏽🙌🏾
@MerryWayson
@MerryWayson 2 дня назад
Mr Mtanyiwa mulungu akutetezeleni muzonse tili Pano chifukwa cha inu❤❤❤❤❤❤
@FisherAction
@FisherAction 2 дня назад
More fire big thus true
@donexmakande5979
@donexmakande5979 2 дня назад
Ntanyiwa ndikatundu umatiyimilila go forward big Ulemu wanu
@MozzyBSaimon
@MozzyBSaimon 3 дня назад
Inenso ndilj ku Capetown ma polo ake ndimupitila komko adxiwe kuti ndithana naye asanabwele.kwa Comrade mtanyiwa
@user-zr7wk4oq2x
@user-zr7wk4oq2x 2 дня назад
Buddy Ntanyiwa‼️ Proud of you brother 🖤🔥🔥
@user-oy6dl1pv9e
@user-oy6dl1pv9e 2 дня назад
Ine phee mwachidwi ndi Limpopo ❤
@HalimaDamiano
@HalimaDamiano 2 дня назад
God bless you ntanyiwa
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 3 дня назад
Tili Tchelu kunvelela from Mozambique. Umayita big Ntanyiwa.
@DavieMasowo
@DavieMasowo 2 дня назад
Mulungu azikutetezani amtanyiwa
@YasinMmadi
@YasinMmadi 3 дня назад
Ng'alulani a limpopo
@user-artharkkadango
@user-artharkkadango 2 дня назад
Alibe manyaz mkomwe zoona kuba ndalama za nzika zoona km ku Malawi kuno aaah😅
@JOHNOlesmasCosmas
@JOHNOlesmasCosmas 23 часа назад
ndidasiya kumvera ma radio Aku Malawi coz alowetsa ndale koma inu a Comrade Ntanyiwa mmakwana simunyengelera pa Limpopo FM mmaitha man
@MphatsoIshmaeladam
@MphatsoIshmaeladam 2 дня назад
Truth always painful more 🔥 ntanyiwa chilungamo tikuchifuna infa ya chilima
@IshuKatanga
@IshuKatanga 2 дня назад
he is staying at Sea point Cape town don't worry is just a small boy
@jesusminded3033
@jesusminded3033 2 дня назад
No,he is not.He is a patriot.Belueve that and it is the people who love justice who can agree with him.Don't insult people simply because they don't think the way you think.If you have a different view criticize constructively my friend Good day.
@JusticeNyirenda
@JusticeNyirenda 2 дня назад
We don't need this 🥱🥱
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 2 дня назад
Chakwera akutsegula mmimba ndi nduna zake komwe aliko mpdze pedze man😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 2 дня назад
Tiuzeni ndithu comrade Ntanyiwa,, ayaluke amenewa 😂😂😂
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 дня назад
Mtanyiwa agogo Anga akufuna akupaseni khunda mukaotche
@TamalaMwamlima-gk5im
@TamalaMwamlima-gk5im 2 дня назад
Ingalule mr ntanyiwa nazoni
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 дня назад
Mtanyiwa mulungu azikudalisani kwambili ndipo azikutetezani kulikose komwe mukuyenda
@EllenNamulu
@EllenNamulu 2 дня назад
Mulungu akhale nanu boss
@user-cy4pg1bo5o
@user-cy4pg1bo5o 2 дня назад
Ng'alura big umakwana kk
@benjaminjobo3525
@benjaminjobo3525 2 дня назад
Munthuyu ndikumudziwa
@JumaAlli-vf6jp
@JumaAlli-vf6jp 3 дня назад
Mumakwana abwana
@janemanyamba7201
@janemanyamba7201 2 дня назад
Ulemu wanu bigger mumatiuza zoona zokhazokha palibe chinsisi padziko lapansi palibe wa muyaya
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 дня назад
Iwe kalasonga ndi kudula machende pa two days wait and see
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 дня назад
Chimwendo Banda mphono Ngati nkhumba😂😂
@johnmpatama1461
@johnmpatama1461 2 дня назад
Tipatseni house number komanso street name. Tikamuchedzere galu ameneyi
@kasupeowenpaul
@kasupeowenpaul 2 дня назад
Sea point Baba
@user-artharkkadango
@user-artharkkadango 2 дня назад
Be safe my bro.... God will save and can't found u
@MayamikoSambo
@MayamikoSambo 2 дня назад
God is in control
@SostenKuyeli
@SostenKuyeli 2 дня назад
You will be protected by the almighty God
@amosnyongo6565
@amosnyongo6565 День назад
Sea point
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 День назад
Sizachilendo kubedwa ndalama mu fon popanda pin abale tidzinena zoona ,palibe akudziwa zoti ena akumachotseledwa ndalama? Osamangotsutsa zilizonse
@tlhalosozindlani4544
@tlhalosozindlani4544 2 дня назад
Yes yes yes heeeeee we respect you ntanyiwa yomweyo galu iwe usampase ndimpasa kkkkkkkkkk
@MalinoChidzulo
@MalinoChidzulo День назад
Kaya amati social media kaya tizinva basi
@davidwakhokamoto1124
@davidwakhokamoto1124 2 дня назад
Number yagalu ameneyo pls aziwe kut tilipo ochuluka ambiri
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 2 дня назад
Mbava
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz 2 дня назад
Limpopo ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@EliasJimmy-fv1wk
@EliasJimmy-fv1wk 2 дня назад
Ntanyiwa tikufuna nyimboyo chilima MMM
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 2 дня назад
Aaaaaa koma macadeti mulibe manyazi akutumani kuti muzitsutsana ndi COMLED ntanyiwa , inu mukuona ngati zibisika zimenezi ,moti chilima anachita kuphedwa SIMUKUDZIWA ,munya muona mwachita zaumbuli , Malawi wa pano si wakale mukhaula ndi mcp yanuyo
@clementchatepa
@clementchatepa 2 дня назад
Amalawi tinasukusula pano tiye nazo fada
@marygoza1205
@marygoza1205 2 дня назад
Alandila zingati abale ake akuvutika ku Malawi uko shame
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 2 дня назад
WINAWE UCHITA MANYAZI CHIFUKWA CJIFUKWA ANTHU ANAFA AJA ASANAPHEDWE AMAYANKHULA NDI ACHIBALE AWO MCP INAPHA ANTHU OSALAKWA
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz 2 дня назад
Timpeza ndipo asowa
@user-hh4wn4vf9e
@user-hh4wn4vf9e 2 дня назад
Ntanyiwa ndiwe 1
@user-zx3pz2wy1j
@user-zx3pz2wy1j 2 дня назад
Koma nambala ya chisisi ayidziwa bwanji pochotsa ndalamazo?
@wilsonali7890
@wilsonali7890 2 дня назад
Guys Ku Cape town ko yekhayo just set out
@EllinaBitto
@EllinaBitto 2 дня назад
Mnthanyiwa❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 A Chilimaaaaaaaa mayo ineeeeee
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi 2 дня назад
What is rong is rong...amalawi atopha ndi ulamuliro wangaza ndi kupha
@ChikumbutsoTsalangu
@ChikumbutsoTsalangu 2 дня назад
Respect
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 2 дня назад
Mbabane za boma
@MphatsoIshmaeladam
@MphatsoIshmaeladam 2 дня назад
Ndipo please akatinamiza ndi report lawo inuyo bwelani ndizonse mwatisungira kut choona chioneke
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j День назад
Ndipo kwambiri tu mmm
@user-er7ub4ug7y
@user-er7ub4ug7y 2 дня назад
Comled mtanyiwa l proud of you 💪💪💪
@user-dt8nr1zx6e
@user-dt8nr1zx6e 2 дня назад
❤❤❤❤
@user-ym8rn5kd1s
@user-ym8rn5kd1s 2 дня назад
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 2 дня назад
Za ziii
@ThomasPeter-zt2ju
@ThomasPeter-zt2ju 2 дня назад
Mbolo yako
@dennisrobert4617
@dennisrobert4617 2 дня назад
Kanyimbo munayambira kaja kamandikhudza ndingakapezs bwanji
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 2 дня назад
God will punish them
@shephardlonex3371
@shephardlonex3371 2 дня назад
Iwe usanamize anthu pano 25million ayitenga bwanji without pin.?
@JusticeNyirenda
@JusticeNyirenda 2 дня назад
You don't understand technology
@SandrahEsther
@SandrahEsther День назад
Okuba amaba bwanji mma foni aanthu pin amaitenga kuti?
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o 2 дня назад
Boza ilo ndipo ndikuona kut pano wasanduka slave chifukwa ntendere ulibe ukungoyenda tchelutchelu paliponse ,zoona abale ako osawawona chifukwa chomenyera ufulu wa chipan cha dpp nkukhala wopanda ntendere koma kumalawi uzafika
@user-hx6jl2jq9j
@user-hx6jl2jq9j 2 дня назад
Panyo pako ukuti boza
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 2 дня назад
Ma cadet ena a MCP ndameneyu mutha nonse,am watching you where you're
@ThomasPeter-zt2ju
@ThomasPeter-zt2ju 2 дня назад
Machendeko
@user-zv3cy2xj5p
@user-zv3cy2xj5p 3 дня назад
Bodza ili anakhapa bwanji anthu awo anali mu ndenge, ndiponso bwanji inuyo osangobwera ndikupangitsa msonkhano poyera kut tikudziwen mwina mungadzakhale vice wa dziko
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r 3 дня назад
Ndipo bwanji osangobwela poyela ali busy kulimbana ndi boma zimenezi zimafunika akubanja komaso kubisalako zikuwonekelatu kuti boza pali anthu amamugwirisa ntchito
@CatherineMbela
@CatherineMbela 2 дня назад
Inu inu anthu onsewa akuyakhula kumapeleka ma umboni nanga akhale Kuti sanaphe anthu akuwamangilanji anthu ose azingopeka achewa Pena pake kumavomeleza zinthu
@LucianoKapepuza-sy9wx
@LucianoKapepuza-sy9wx 2 дня назад
Wa MCP iwe kape chisilu chakumuzi
@GodfryMalishe
@GodfryMalishe 2 дня назад
Ndinu achisiru kwambili ndipo palibe chanzeru chomwe mwakambapo apa
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r 2 дня назад
@@CatherineMbela eya asisi anthu akuyankhula zinthu zambiri nanuso mumaziwa kuti chinthu chikachitika pamachuluka zoyankhula zoona komaso za boza koma limachuluka kwambiri ndiboza amati chilungamo chimamasula ngati iwowo akuziwapo kanthu kungopita live kukawawuza chilungamo koma za mu social media sizingatithandize anthu akuyenela kumangidwa chifukwa alibe umbo ena imakhala sanje koma zikuvesa chisoni dziko lathu mumalo mogwirana manja ndipomwe akapasula akuchulukila bible limati muzako akakuchitila choipa iweyo muchitile zabwino ndipo umupemphelele ndiye woyankhulafe ndifeso timawoneka ochimwa pamaso pamulungu mwawona
@OssmanAbubaker-st7pu
@OssmanAbubaker-st7pu 2 дня назад
Bwana please tatitumizileni phone number ya mnyamatayo inendikufuna ndimugwire chifukwa inendili ku Cape Town comwekuno Sakundiziwa bwino bwino mnyamata ameneyo
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 2 дня назад
tbwela komko cpt
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 дня назад
Mr Ntanyiwa tiudzeni anapha chilima asanathawe tidulanepo dziwalo please fast
@user-ct7jo8df6m
@user-ct7jo8df6m 2 дня назад
Sea point
Далее
LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA
41:25
Просмотров 1,3 тыс.
skibidi toilet zombie universe 33 ( New Virus)
02:59
Просмотров 1,4 млн
BON KALINDO LERO PA 28 JUNE NDETU KULI NKHANI |
17:01
Nkhanga zaona Chakwera. Mzimu wa Chilima ukwazuza
31:56
Chimtengera - Iwe Malawi (Stool Session)
8:42
Просмотров 3,8 тыс.
Asilikali akuulula momwe anamuphera Chilima
3:23
Просмотров 74 тыс.