Тёмный

LIMPOPO FM KUBWELETSA ZOGWILIKAKO PA NKHANI ILI MDZIKO MUNO IJA AKAMUNA PA RADIO AWA 

Malawi Trends TV
Подписаться 48 тыс.
Просмотров 27 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

13 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 232   
@HamdanAmaziNdala
@HamdanAmaziNdala 3 дня назад
INSHA'ALLAH INSHA'ALLAH brother ameneyo tikupepha kti amwlire nde iweso ufuna amuonjezere masiku achyani
@christinachikadza3760
@christinachikadza3760 3 дня назад
Ha ha ha ha let God be the judge apapa wayamba kale kumenya nkhondo
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l 2 дня назад
Ambuye,choñde,,musamupitilire chikangawayu,ntengeni uyu,watikwanakwanasi..chonde,,tantengani uyu.Ameni🙏
@fannyzimba149
@fannyzimba149 3 дня назад
Osapita ku Bottom bwanji ku Lilongwe mmesa akuti boma ndilomwelo mmesa amati chilichonse chili bwino ndiye athawilakonji ku malawiko
@EnerstManess
@EnerstManess 3 дня назад
Ambuye musamusiye chakwera tengen chonde watikwana
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 3 дня назад
Kkkkkkkkkk 😂😂😂😂😂😂😂
@patriciacraiton-sf5vu
@patriciacraiton-sf5vu 3 дня назад
😂😂😂😂😂😂
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 3 дня назад
Ayambile makolo akowo
@EnerstManess
@EnerstManess 3 дня назад
@@NancyNyirenda-v9o iweyo bwanji
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 3 дня назад
@@EnerstManess woyamba iweyo kenako makola ako wofunila zoyipa amako ugweremo wekha chidzenje ukufunila azakocho
@PatrickChagaka
@PatrickChagaka 3 дня назад
Ambuye ndagwada pamaso anu modzichepets ndimopempha ambuye chakwera ntengeni padzikopano watikwana kwabasi
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu 3 дня назад
😂😂😂😂😂 koma yah, anthu tatopadi
@PhelokaziRadebe-es4gz
@PhelokaziRadebe-es4gz 3 дня назад
Ha ha ha ha nyc jock
@jay_sido
@jay_sido 3 дня назад
Pemphero lako laveka mwana wanga
@JohnGreen-v8f
@JohnGreen-v8f 3 дня назад
Kkkkkkkk usasekese
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 3 дня назад
Ndpo zoona galu ameneyu tatopa naye amalawi
@MosesTangwe
@MosesTangwe 3 дня назад
Mulungu wathu ndiwamoyo ndipo sangalore anthu ake kuti azifutika chifukwa chamunthu mmodzi
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 3 дня назад
Amen and Amen
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 3 дня назад
Ok chabwino takumvani a limpopo , mulungu achite kufuna kwake
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 3 дня назад
Umakwana mr Don't trust ulemu waanu big.
@EsetaGerate
@EsetaGerate 3 дня назад
Anapha uja ndimkatolika anyera awona 😂😂
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 дня назад
Wailes ya maboza Limpopo fm
@RajaAlicky
@RajaAlicky 3 дня назад
Allah subuhannah wataAllah tikupempha mtengeni chakwera insha'Allah onesani ukulu wanu nd mphavu zanu KT osatila ake atengerepo phunziro insha'Allah
@DamianoYohane
@DamianoYohane 3 дня назад
Kodi ku Malawi anthu adzayamba kubwerako liti ochokera ku mayiko ena kudzalandila mankhwala
@frazereline
@frazereline 3 дня назад
Amabwera koma kukalandira mankhwala kwa sing'anga
@DuncanRashid
@DuncanRashid 3 дня назад
basi tikhalabe okozekela kukakumba basi iya.......ndipo Richard chimwendo banda asamale next person akhala ameneyo ndithu
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 3 дня назад
Mutiuza zoona ndiinu a Limpopo Fm❤❤❤❤
@EooJacko-l4o
@EooJacko-l4o 2 дня назад
ndinu onama kwambili alimpopo FM
@serakillo8668
@serakillo8668 3 дня назад
Oooh yes pamenepo ndy akuona mizimu ya athu 9 ija yabwera pamutu pake bas zabwino palimbe ...any am stell wait nice ans not her that no l want nice one ❤❤
@BlessingsPhoso
@BlessingsPhoso 2 дня назад
Tamuona lazalo Relo maboza
@leahkasiwa5033
@leahkasiwa5033 2 дня назад
Basi ndiyendela ku Gardencity konko nkawone zeni zeni 😂😂😂
@HawardKalipande
@HawardKalipande 3 дня назад
Apa Tikufelanji ikutenga boma!! Nthawi mkachitsilu. Ntcheu ija osazaiphweketsa
@rexnyalugwe4910
@rexnyalugwe4910 3 дня назад
Nde achila msangatu, lero Ali ku Blantyre kuchita majowajowa
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 дня назад
Komatu wailes iyi anakhonza ndi maboza ayi ndithu
@MosesLackson-l4f
@MosesLackson-l4f 3 дня назад
Momwe mukuonela amwalira liti?
@CharlesjeremiahNyirenda
@CharlesjeremiahNyirenda 3 дня назад
😂😂😂😂😂 koma awa
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 3 дня назад
😂😂😂😂😂😂ayi zikomo
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 3 дня назад
Kkkkkkkkkkkk Koma iwe
@AuphieBannet
@AuphieBannet 3 дня назад
😂
@Yoxym
@Yoxym 3 дня назад
Lero
@FungulanReuben
@FungulanReuben 3 дня назад
Ngt wafa nkono ndiye ntima ungakhale bwino, ndiye kufako
@VinciusmajiduMchepaanaffi
@VinciusmajiduMchepaanaffi 3 дня назад
Ambuye landiran mzimu wake munthu yu akafumule waononga zi2 pa malawi😢😢
@MulangoGrading
@MulangoGrading 3 дня назад
Mumakwana Boss
@MsaiwaleBamus
@MsaiwaleBamus 3 дня назад
Dziko abale mmmmm ndipo ndale🙌🙌🙌
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 3 дня назад
Tiuzen zenizenizo please Mutu ukuphweteka 😢
@Linda-r6w
@Linda-r6w 3 дня назад
Zabodza ,Chakwera Ali ku Bt lero
@HezekiahMachekaphiri
@HezekiahMachekaphiri 3 дня назад
Iwe Garu cadet chitsiru
@Yusuf-j6c
@Yusuf-j6c 3 дня назад
Muchedwesatu kulenheza a Limpopo FM tangonenan coz tuzwa kut inu chilungamo muchiziwa kut wafa tangonenan bas aaaaa
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 3 дня назад
😂😂😂 ndiwomwalira kale uyu iyah
@Kalumbijoyce-hb8gr
@Kalumbijoyce-hb8gr 2 дня назад
😂😂😂 koma akupangila mafizo ku BT apa mmm
@SbaniCaros
@SbaniCaros 2 дня назад
Chikangawa saakufa cz akuyenela kutiuza what happened by chikangawa forest.
@KennethBilali
@KennethBilali 3 дня назад
ambuye chonde malidzan 100%
@charlessulumba2521
@charlessulumba2521 3 дня назад
😂😂😂😂 koma anthu mwatopa eti
@JamesEuginio
@JamesEuginio 3 дня назад
Akuti akukasewera gofu Ku bangwe
@EooJacko-l4o
@EooJacko-l4o 2 дня назад
mwauponda muyamba ndinuyo kumwalila chakwera ali bwino bwino
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 дня назад
Chikuvuta ndi chani kuti chakwera angofa machende ake
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 дня назад
Mbolo siyinafeso chifukwa monica amakonda mbolo😂😂
@MosesKamtndo
@MosesKamtndo 3 дня назад
Wishing him well, God is to judge
@ClintonHarold-g9h
@ClintonHarold-g9h 2 дня назад
Iwe ndiwe wamisala peza zochita
@finchiadriano
@finchiadriano 3 дня назад
Akulu inu ndabodza kwambili 😂😂😂😂
@JulietKapata
@JulietKapata 3 дня назад
Chonde ambuye mutengeni munthuyi😢😢😢
@JamesEuginio
@JamesEuginio 3 дня назад
Dan lufan tikudikira utuluse nyimbo yakuti apully zikuwayendera motani paja iwe ndi ozisata
@chifundobuledi
@chifundobuledi 3 дня назад
Stroke yongofikira kutchaya kugwetsa mmmm ena ake anadwala choncho sanathe week anamwalira kuteroko akumupumisawo ndi ma chine amumangilirawo, za moyo palibe amtaaaaaa
@MikeEvason-rx4qf
@MikeEvason-rx4qf 3 дня назад
Ambuye tichoseleni oipayu
@StewartGoma
@StewartGoma 3 дня назад
Ndibwino kuti amwalire zinthu zikhoza kuhlala bwino
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 3 дня назад
Ubwino wake mulungu akayamba ntchito samailekeza panjla
@MadehNYC
@MadehNYC 3 дня назад
Osakabaya Jackson bwanj wa poison asowe timadalilatu ife kuti wavaya
@VincentKalata
@VincentKalata 3 дня назад
Bas wavaya ameneyo 😂😂😂
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k День назад
Kkkkkkkkkk aripa matenda akaya kaya nzanu akuziwongoratu uku nde zatheka bwanji tinene kt wabwezedwa pa dipot kt azarape kaye
@georgeaiwa8661
@georgeaiwa8661 3 дня назад
Ku Garden City nkofera, palibe amabwerako 😂 Bola akanapita Kwa Sing'anga
@FlorenceMainga
@FlorenceMainga 3 дня назад
Apite ameneyo amulondola chilima amaona ngati iyeyo wamuyaya mulungu afuna ndithu
@AlexanderMateketa-i8l
@AlexanderMateketa-i8l 3 дня назад
Ndipo ingakhale new year ku malawi
@josephalfred5138
@josephalfred5138 3 дня назад
Amuuze alape akhululukidwa asiye kuweluza ekha oweluza ndi mwini mulungu
@TimeAbilu
@TimeAbilu 3 дня назад
Tiye timpasile mwini moyo Allah it's our answer
@AsimaBayisoni-l8n
@AsimaBayisoni-l8n 3 дня назад
Mulungu tengeni mwachangu
@getrudeminikwa9636
@getrudeminikwa9636 3 дня назад
Following
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 3 дня назад
Izi mulungu amachitira dala
@AbudulJohn
@AbudulJohn 3 дня назад
Ameyo apite bs ife sitikufuna
@IsaiahElesoni
@IsaiahElesoni 2 дня назад
Tiyankhureni zooona
@RhodaAjussa
@RhodaAjussa 3 дня назад
Get well soon apule
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 3 дня назад
Chiipira achaje , make ati mwana . Chitsilu chiri ndi mwini wake .
@BensonChilundu
@BensonChilundu 3 дня назад
Mmmmmm,Mulungu ndi oophya ndipo salola munthu yemwe wakhetsa mwazi wa munthu mzake dziwani Kuti Mulungu amakantha chifukwa cha mkwiyo
@nonontsane2521
@nonontsane2521 3 дня назад
Mulungu ndie mwini kuweluza bc
@PhelokaziRadebe-es4gz
@PhelokaziRadebe-es4gz 3 дня назад
Ha ha ha ha 😂😂😂 nyc jock 😂😂 Achakwera komatu kumakalimbikila kulima mizimbeyo kumeneko ndi chinangwa kuti enafe tisaza vutike njala tikafika 😂😂 Komaso nayiwala jecket ya black ija mundisiyile yimandisangalasa
@isaaczuze
@isaaczuze 3 дня назад
Chimwendo mimba yaiyikuluyo ....uziona bwana wako akufactikuonele ndi matama ako aja ...
@EllenGomani-i4f
@EllenGomani-i4f 3 дня назад
Afe basi akamupeze chilima
@robenallie6985
@robenallie6985 3 дня назад
Ndipita mawa ndikaone ngati angandilore
@PreciousMangulama-l4i
@PreciousMangulama-l4i 3 дня назад
Tilakhuleni akamati manga ati magezoona
@JananaKing
@JananaKing 2 дня назад
Kkkkkk ok
@RaphaelKatimba
@RaphaelKatimba 3 дня назад
anthu musadabwe Chakwela wamwalira kale .komano akuoneka ngati ali chifukwa cha machine amene amumangilira ku ICU. machine amenewa sizimatheka kuti azimiletu ai. ma Doctor amaonetsetsa kuti munthu adzioneka ngati ali moyo cholinga chipatalacho chipezepo ndalama zokwanila. chifukwa munthu amaoneka ngati akupuma koma atafa kale. zimenezi zimachitika chifukwa cha machine ameneo. enafe zimenezi timazidziwa bwino kwambili. munthu atha kumaoneka ngati akupuma izi zimachitika chifukwa cha machine amenewa.
@johnkambala692
@johnkambala692 3 дня назад
Za ziiii. Chilungamo chake chiti. Mawa akasewela golf ku Limbe Country Club
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 3 дня назад
Apita chinunu osayankhula😅😅😅😅
@LOKAMJ
@LOKAMJ 3 дня назад
Kkkk ife chete kudikilira,, tione ngat apiteko
@MiracleDamiano
@MiracleDamiano 3 дня назад
Zazii tiyeni tione ngat ati apite kapolo iwe
@SoundmasterElectronics
@SoundmasterElectronics 3 дня назад
Kutchaya kugwetsa
@LuskaMoses
@LuskaMoses 3 дня назад
Kodi mfiti imadwaraso asafe asathawe milandu ya anthu 8+1😢ijaayakhe ameneyo watsara chimwendo banda uzimbere komwe uliko ukachita chimutu ndati chimbiniradenicho😢
@SamNkhomo
@SamNkhomo 3 дня назад
Tili pa mbuyo panu bwana
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 3 дня назад
Elections 2025 tikufuna azakhale mbone
@chifundochasweka-kv8fw
@chifundochasweka-kv8fw 3 дня назад
Ambuye onetsani mphamvu zanu kufuna kwanu kuchitidwe😮😮😮
@HondaFredzoG
@HondaFredzoG 3 дня назад
Ambuye chonde ntengen chakwera
@agrochemicalsSeed
@agrochemicalsSeed 3 дня назад
Ambuye awakumbukile,amen.
@AlbertBandah
@AlbertBandah 3 дня назад
Akuchedwa kufa
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 3 дня назад
Kodi Nanga aboma akutinji osatiwuza mene alili sogoleri wathu tiziwe mene alili
@TakondwaSaidi
@TakondwaSaidi 3 дня назад
😅😅😅koma iwe ndiye ukuipasa mototu
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 3 дня назад
Wagwa ameneyi ndidikira loweluka ku golf club ngat sazabwera huh
@MandalaChaona
@MandalaChaona 3 дня назад
Chikumbumtima pa Chiwembu anachita kuchikangawa chikumubandula kupha anthu 9 eeeeee tsiku limodzi. Mtendere uzavuta kuupeza. Mabanja ali pa umasiye Chifukwa cha Chiwembu chomwe anachita. Sadamwalire but he will never have peace omudandaula achuluka
@PaulMaliseni
@PaulMaliseni 3 дня назад
Sangafe achira ndip numufunila uchira kwa msanga
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 3 дня назад
The accents propagating the death of Chakwera are from one particular region of the country . My only hope is that Malawi shouldn't fragment into triblistic conflicts .
@MaxwellSamson-t5q
@MaxwellSamson-t5q 3 дня назад
Uyuu azipita bas
@EsetaGerate
@EsetaGerate 3 дня назад
😂😂😂😂😂😂😂 koma chikangawa watha basi
@MosesDicostar
@MosesDicostar 3 дня назад
Nthenda imeneyi aujeni anamwalira nayo moti aujeni ajaso simachizika kumangokumbilatu manda
@MussaRonald-h6o
@MussaRonald-h6o 3 дня назад
Kkkkkkk😂😂😂😂😂
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 3 дня назад
Achile kuti ziisakho zikubwelazi tizazionele limodz
@LucianoMangawu
@LucianoMangawu 3 дня назад
Let us wait and see
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 3 дня назад
Ambuye mtengeni chakwera yu waonjeza ndi anthu ake kuba kupha osawelenga za mavuto a wanthu corrupt president in africa
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 дня назад
Tauzeni amcp ngati sakudwala mmawa apangise nsonkhano siwojinjilika ndi minsonkhano apange mmawa pa 11😂😂😂😂😂😂
@Jaydee-mw4
@Jaydee-mw4 3 дня назад
Angofa basi alibe ntchito ai mbuzi yamunthu imeneyo😂🎉
@JoeNsongo
@JoeNsongo 3 дня назад
Tiuzeni zoona Zake mr limpompo
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 3 дня назад
Mukutizuza time inayake aaaaa
@JerieWytonTengani
@JerieWytonTengani 3 дня назад
Bwanji athawira ku dziko Lina kuzafuna mankhwala, zoputsa ndithu.
@AsimaBayisoni-l8n
@AsimaBayisoni-l8n 3 дня назад
Mulungu tengeni mwachangu chakwela
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 3 дня назад
Koma ngati wafa chakwela wafa infa yabwino yosabvulidwa shati sapato ngat chilima😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 yashuti ,,,BT yashuta
@MalidadJaffalie
@MalidadJaffalie 3 дня назад
Mwachidule wamwalila mbali imodziyokha nankha stock mpaka muntima sibasi wapitililatu😂
@umalikawiya9995
@umalikawiya9995 3 дня назад
Aaaaaaaaaa Akanali moyo kani 🙄🙄🙄🙄🙄 Eshii Oky 😂😂😂
Далее
BON KALINDO - 14/10/24 KWACHANO TIONE NYEKHWE
17:04
Просмотров 5 тыс.
NKHANI YADZIDZIDZI - COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM
19:11
Nancy vs Che Nkope - Apatseni moyo wautali
11:05
Просмотров 3,5 тыс.