Тёмный
No video :(

Limpopo FM Nkhanga zaona pa 14 June 2024 Comrade Ntanyiwa akuti zinayambila ku police zonse 

Malawi Trends TV
Подписаться 36 тыс.
Просмотров 24 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

20 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 38   
@patrickndojime1632
@patrickndojime1632 2 месяца назад
Nkhanga zawona ndi kawawa most ❤❤❤❤❤❤❤❤❤ My big brother
@francisvisage2705
@francisvisage2705 2 месяца назад
Mr Mtanyiwa ulibe nzako, inu ndi man.. 🎉.. A man with a Lion heart... You have unveiled deep things before our eyes and heart. Keep doing the good work... God keep you.
@earthware2311
@earthware2311 2 месяца назад
Mtanyiwa ndikupasani ulemu wanu ..mumatha kufuvuza eeeee ❤
@user-dy5bj9ck5e
@user-dy5bj9ck5e 2 месяца назад
MR mtanyiwa iweyo ndi akatundu ndimakudalilani💪💪💪
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q 2 месяца назад
Nthanyiwa ndi 1 moooor 🔥🔥🔥🔥🔥 fire
@ElvisSpesho
@ElvisSpesho 2 месяца назад
Iweyo ndi dada, FM imeneyi awo akudana nayo a MCP Ife ndiongo tsatira ndkudziwitsidwa, GOD bless you jahovah
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 месяца назад
Kapena mwina FM yanuyo kulibe amene amapangako zamalonda mwina
@jackiendlovu9564
@jackiendlovu9564 2 месяца назад
Koma afiti amenewa ndiopanda nzeru eti Achakwela ndi gulu lanu mintel zanu siyani otchipa agalu apanga nzeru mbuzi zodana ndi anthu omwe angapitetse Komwe Malawi analili
@user-yu9dm4ch1b
@user-yu9dm4ch1b 2 месяца назад
Patakhala Pali m'bale wako iwe issah ungat za ziii kulitu mulungu ine wa Mcp koma sanachite bwino
@MemoryKaunda-js9qv
@MemoryKaunda-js9qv 2 месяца назад
Wonder shall never end in malawi
@XtinaBrown-tx8bb
@XtinaBrown-tx8bb 2 месяца назад
Zilikotu ziliko ,,,chophelana chani ngati iwoso sazafa😢😢
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 2 месяца назад
Powerful 👊
@nessiemfunie
@nessiemfunie 2 месяца назад
Chakwera waopya Ku ntundu wa a Malawi 😭😭
@XtinaBrown-tx8bb
@XtinaBrown-tx8bb 2 месяца назад
Mizimu 😢😢 anthu 9 osalakwa mhuuu
@CatherineKamsare-cy3yo
@CatherineKamsare-cy3yo 2 месяца назад
Chilima wafa imfa yowawa ndithu mpake anagwira Colona😢
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg 2 месяца назад
Mwazi wa Munthu osarakwa ndiwowophyaaaaa simunati zonse mwapanga kumbalizo mulungu anaona ziululika and mubweza 1 by 1 You çan not kill innocent people for position Mene mwawaphera anthuwa nzovesa chisoni and mudziwedi kuti the whole Malawian is angry with you killers inuso muyembekezere mutsatira
@user-hg2cw1om1p
@user-hg2cw1om1p 2 месяца назад
Mvuto a malawi tilibe chimvano ndizopweteka kwambiri zachitikazi ndiye even a police akumalawi akumapha a malawi azawo chifukwa cha mwenye koma ine ndikanakhala ku malawi pakanachematu 😢😢asatipangise kukhala gangster aMCP
@xadrequexadreque-og6zc
@xadrequexadreque-og6zc 2 месяца назад
Koma ndiye kuti a chakwera sazafa? Afuna akhale okha olamula pa malawi? Komatu aziwe kuti ku malawi kuli anthu ophunzira kwambiri musaone ngati chilima mwamphayo ndiye kuti zathela pompo ai.
@blacksonpeshes5057
@blacksonpeshes5057 Месяц назад
mulungu azikudaritsani antanyiwa ndi sitafu yanu
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 месяца назад
Unonyepa
@ChiefJustin-cl8jl
@ChiefJustin-cl8jl 2 месяца назад
Yam'baya tulo tamthawa
@BridgetChumachiyenda
@BridgetChumachiyenda 2 месяца назад
Eeeeeh km dziko ili mulungu achite nafe ndinthu
@user-yk5xv4dt7v
@user-yk5xv4dt7v 2 месяца назад
Kd bwana ntanyiwa inu ndinu okwatira?ndimati ngati simunakwati mukwatile mulongo wanga mukhale mulamu wanga ndinu katundu Palibeso lipopo fm ndikawawa
@JabiruWitness-s3c
@JabiruWitness-s3c Месяц назад
I%.
@louismagongwa
@louismagongwa 2 месяца назад
chomcho eeee mcp
@rosechapita3434
@rosechapita3434 2 месяца назад
Koma zimenezi akuluakulu amazinvera
@HanifuMbwana
@HanifuMbwana 2 месяца назад
Ngati Limpopo fm iliyabodza tionela ku maliro anthu onse akazavala nsalu za utm
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli 2 месяца назад
Inenso ndikudikira pa point imeneyi Ngati dzirichomwecho tingoti Limpopo FM 💯
@user-lx8ow6ek6k
@user-lx8ow6ek6k 2 месяца назад
Sizingatheke kukavala za utm nkhalamba zija zingavale za utm
@thomsonmbewe260
@thomsonmbewe260 2 месяца назад
Zovuta 😭😭😭
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 месяца назад
Kkkkkk ndiye achakwelawo athu akutchewu samudziwa chakwelayo kkkkkk koma iweyo ndigalu kwambili
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 2 месяца назад
Ziliko auze
@BrajamesJames-fi8ll
@BrajamesJames-fi8ll 2 месяца назад
Kma chakwela
@HallimaMakwinja
@HallimaMakwinja 2 месяца назад
Chilungamo chiponse pamenepo MCP chipani chamagazi
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 месяца назад
Big Mani muchedwa nazo zochita tamapangani zina zamalilozo zachitoka basi
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 месяца назад
Zazi zimenezo
@peterkakhome6976
@peterkakhome6976 2 месяца назад
Issac kapena kuti isaki ulibe nzeru iwe chitsilu zedi
@IssacMateyo
@IssacMateyo 2 месяца назад
Kkkkkk ndiye achakwelawo athu akutchewu samudziwa chakwelayo kkkkkk koma iweyo ndigalu kwambili
Далее
Construction site video BEST.99
01:00
Просмотров 304 тыс.
ОБЗОР ПОДАРКОВ 🎁 | WICSUR #shorts
00:55
BRIAN BANDA KUWELENGA NKHANI
21:59
Просмотров 32 тыс.
NKHANGA ZAONA
21:49
Просмотров 72 тыс.