Тёмный

ZOOPSA ZAULURIKA MZIMU WA SKC UKUMUBWELERA PRESIDENT ANATHAWILA KU ITALY KUTI AKALAPE MACHIMO 

Malawi Trends TV
Подписаться 42 тыс.
Просмотров 86 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 258   
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 23 дня назад
Ndipo kudziwike kuti kuli mulungu ku dziko la Malawi 😢😢
@domminicchikalenda
@domminicchikalenda 14 дней назад
He is more knowledgeable in spiritual matters more than many of us writing the nonsense here. An iron sharpenes an iron, he wanted to learn from someone who has the same Moto of servant leadership at heart
@misoMoyo
@misoMoyo 23 дня назад
Tsono mukamati bodza bodza anthu sindikumakumvetsani ena kuti munaganiza chani likhala bodza bwanji munthudi wapita Ku Italy kma zinthu zinazi ai ndithu ngati mulibe zoikira comment kungoona za nzanuzo anatiphera anthu ambiri osalakwai mizimu Yao iwasowetse ndithu mtendere Ambuye mutimenyere nkhondo ndinu
@MustafaIbraimo
@MustafaIbraimo 19 дней назад
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 23 дня назад
Comrade za report zo musazengelezetu mutiponyele timadalila pompa apapa
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i 23 дня назад
SKC ndiathu ose omwe anamphadwa mopanda chifukwa ambuye chitaninawo athu oyipawo misozi sikutha pakhope zaathu olila tikulemphela kuvomeleza zakuti chilima ndimalemu ndichithu chosayuwalika Bola inu achikangawa munakangomuchosa nkono kapena kumusowesa kwamasiku chabe kuti mukawina muzamutuluse koma kufika size yakupha 😭😭😭😭😭 ambuye achitenanu ndithu inu Mr chikangawa
@UngweruGausi
@UngweruGausi 19 дней назад
Okumba zenje agwelemo yekha misozi yosatha mumaso
@jicakadewere40
@jicakadewere40 17 дней назад
Momwe amapanga zimenezoo samadziwa kt akuchimwaa? Eeeish.
@yamikanitagoneke9215
@yamikanitagoneke9215 15 дней назад
Mmmhhh muzonse tiyamike mulungu iye salakwitsa
@BarwickSalanje
@BarwickSalanje 23 дня назад
Akalapa bwanji pamaso pamunthu kusiya mulungu...akuluwa zinthu zawavuta basi
@user-go2ge4sp9m
@user-go2ge4sp9m 23 дня назад
😂😂😂😂😂 kayaa
@ubs7030
@ubs7030 22 дня назад
Iwe ndiwe Satanist ndi DPP yakoyo, mukunama boma simungatenge.
@ubs7030
@ubs7030 22 дня назад
Sanje yakuvutani
@user-tk6qh9zs7h
@user-tk6qh9zs7h 18 дней назад
Nsanje yawakuta mpaka ku Matako a dpp ndiye palibe Cha nzeru chomwe angalankhule. Agalu a dpp kusankha Munthu okodzedwa kukhala Mtsogoleri wawo. Pano dpp tasintha dzina tsopano ndi Mikodzo Party
@AndrewZimba-m3j
@AndrewZimba-m3j 17 дней назад
Ndiye kolapako mpaka anthu 385 bodza ilo❤❤
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s 23 дня назад
Mukundipheranji😢kolona ali pakhosi
@user-ld8gb9xm7v
@user-ld8gb9xm7v 23 дня назад
Kkkk ndiye kuononga ndalama kukalapa ku Italy kuno church kulibe 😂😂
@user-no2mx4go8p
@user-no2mx4go8p 23 дня назад
Kaya kkkkkkkkkk
@AlcidiaMacario
@AlcidiaMacario 18 дней назад
Kkkkkkkk
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 23 дня назад
Blood of innocent pple
@RebeccaWalusa-lb5yi
@RebeccaWalusa-lb5yi 23 дня назад
Choipa chimasata mwini oyenda ndilupanga
@CHAKAKACHAKA-MANMW
@CHAKAKACHAKA-MANMW 13 дней назад
MULUNGU ALANGA YEKHA AMENEWA
@SilajuJenala
@SilajuJenala 22 дня назад
Allah knows the truth
@LisaKamanga-l3z
@LisaKamanga-l3z 23 дня назад
Kkkkkkkkk akuti Lapken anafika ndi mfuti
@AnthonyChirwa-t4g
@AnthonyChirwa-t4g 21 день назад
cha nambar one anyamata akhanga zaon ulemu wanu mmatisangalasa komaso kutionesa zithu zoti enefe sitikuziziwa mwaichi ulemu wanu
@NoorRasheed-re5vh
@NoorRasheed-re5vh 23 дня назад
Komabe zonse mukupekazo pofuna ulamulilo wa Dpp odzavota ndife ulapa
@AckimKasiya-u7q
@AckimKasiya-u7q 23 дня назад
Awawa too much mabodza
@patrickscott9086
@patrickscott9086 7 дней назад
I remember imfa ya Chilima Chakwela anabisa km uyu ananena kut amalawi Chilima kulibe wafa ndi2 Km boma limabisa
@FeliaNgunga
@FeliaNgunga 3 дня назад
So we have no God in malawi😂? God is alive 💪
@AnnahMpamati
@AnnahMpamati 18 дней назад
Ndipo mulungu amukathe motheratu chakwerayu popeza iiiii ndi muthu woipa kwambiri kumupha mnzake zaziii , chikungoyenda yenda ngati chigalu tsono mumayiko amnzake ,chikapange ngozi kumeneko bac asaaa
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga 23 дня назад
Muonda nawo mabodza anuwotu
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 23 дня назад
Waonda kale Gogo wakoyo can't you feel the heat already 😂😂😂😂 blood ya munthu njoopsa munya
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 23 дня назад
Umakondanso kumvera LIMPOPO eti? Carry on Ccta.
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 23 дня назад
@@EmmanuelGasiten-fo5dr imatitsegula mmaso , 😂
@IshmaelChimtanga
@IshmaelChimtanga 23 дня назад
Utaonde ndi iweyo uziona ndi bale wakoyo chakwerayo
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 23 дня назад
Kape muziona nonse
@ColiousLevinson
@ColiousLevinson 22 дня назад
Mwachebwetsa anthu sangadye kunyumba kwako komaso sangadye kwachakwela awuzeni anthu adzingwila nchito ife SITI ngasinthe
@EuritaDeric-fz3ds
@EuritaDeric-fz3ds 19 дней назад
Mulungu wathu ndi wamoyo
@Martha-m6e
@Martha-m6e 23 дня назад
Ambuye ntchito ndi yanu.asowe mtendele onse amene anaikapo mau.
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 23 дня назад
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa
@ubs7030
@ubs7030 22 дня назад
Nonse mukunyoza president ndinu alomwe nokhanokha.
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 22 дня назад
Ochewa tili nkatimo aise
@CatherineMbela
@CatherineMbela 21 день назад
Muuze avesese aise
@HawardStainly
@HawardStainly 19 дней назад
Iwe monga mchewa?mbava ya mcp iwe
@JamiluSunday
@JamiluSunday 11 дней назад
Muli ndivuto ndi alomwe eti?
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 23 дня назад
achimwene munthu alibe mphabvu zokhululukila machimo amunthu mzake ai nanu please nthawi zina dzilakhulako zoona abale mabodza daily kodi mmaona ngati mene munayambila kuwanamiza mukuona ngati sadziwabkuti ndimabodza?
@OwenNthala
@OwenNthala 18 дней назад
Munthu oyipa uyu kwambili 🤔 But anyway 🙄 mzumu wa a Chilima & other 8 innocent people 😭😭 May their souls continue rest in peace in the name of Jesus 🙏🏼
@FeliaNgunga
@FeliaNgunga 3 дня назад
So we have no God in malawi😂?
@JimmyMkandawire-f8g
@JimmyMkandawire-f8g 19 дней назад
Alangidwe ameneyi palibe kumubakira and tikusintha boma afune asafune
@augustMag
@augustMag 20 дней назад
Mulungu wamphamvuzonse wa dziko la Malawi tithandizeni misozi ya Amalawi sikuyima sikusiya kusika mmasaya anthu 🙏🏼🙏🏼
@PERRINGSKACHOKOCHA
@PERRINGSKACHOKOCHA 14 дней назад
Akulu bodza musiyw kma ndinu mbuli yakulu radio yabodza iyo
@ChippieNkhwali
@ChippieNkhwali 15 дней назад
Winawu ndi umbuli,,kuli mulungu ku italy?
@bamusilabana6423
@bamusilabana6423 7 часов назад
Mulungu sanyengeka, mawu amatelo
@FaithDonald-ts2pp
@FaithDonald-ts2pp 18 дней назад
Kodi munthu amalapa machimo ake kwa papa?🤣🤣🙌🙌
@FazirahCoster-o4c
@FazirahCoster-o4c 9 дней назад
Chakwera and his priest, am talking about papa both of them they have most sins, repentance can't work if you are asking a person, no!!! , but in only one God can work, otherwise they will just worst their time
@PeterChiko
@PeterChiko 17 дней назад
Znamizanani bible limati wakufa sadzoiwa kanthu biii
@user-tk6qh9zs7h
@user-tk6qh9zs7h 18 дней назад
Agalu inu siyani Bodza. Ndipotu ukamamupekera bodza m'dani wako zimakhala ngati kuti iweyo opeka bodzawe ndiwe CHITSILU komanso wa Nsanje ndi osowa zochita. Kukhala wa dpp ndi Njira imodzi yokalowera ku Gahena. Ndipotu mubangula simunati komanso Chakwera akulamulirani mpaka 2030 wooooooo
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 23 дня назад
Komabodza kamabodza kamabodza kamabodza kambodza kamabodza kamabodza palibe chimene amalakhula choona mabodza 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@AnnieKwisanja
@AnnieKwisanja 23 дня назад
Nawenso ulibe matsiku osatila munthu wakupha iweee
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 23 дня назад
Ndiwe oipa iweyo ulibe mzelu poti sadaphe m,bale wako
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 20 дней назад
Nankhumwa ndi mbudzi ya munthu koposa mbudzi zonse, chimunthu chopanda mzeru.
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 23 дня назад
Makendulo aja osazawaphwekesa
@NancyNyelenda
@NancyNyelenda 22 дня назад
Tanyiwa usazafe uzangosowa 😂😂😂😂😂 umandivetsa😂😂😂😂😂😂
@joaquegerman2250
@joaquegerman2250 23 дня назад
Koma ntanyiwa umayitha chakwelayo angofabasi
@FazirahCoster-o4c
@FazirahCoster-o4c 9 дней назад
Kulapa sitimalapa kwa munthu ot nayeso akuyenera Kulapa, at, km kwa mulungu mmoz yekha bas
@VeraVermaak
@VeraVermaak 22 дня назад
Iwe mbunzi yamuthu timalapa kwa Yehova osati kwa muthu papa ndi muthu ngati iweyo amapita ku toilet
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 23 дня назад
Apite Ku assembly chakwela akupita vacatin chifukwa chani kkkkkkkk
@CharityMhone-uk9ym
@CharityMhone-uk9ym 22 дня назад
Ku Vatican ndkumene kuli satana wamkulu Tate wake,sanapitilre mapemphero koma kukapereka magazi anthu kwa papa
@michaelmvula134
@michaelmvula134 20 дней назад
We are tired of talking about maliro amodzimodzi as if onse akumwalirawa sianthu. We get no food from your cheap lies on media.
@ubs7030
@ubs7030 22 дня назад
Iwe ndi Limpopo wakoyo ndiwe opusa, wava, ukulankhula zopusa.
@RhodaBandah-sh1ir
@RhodaBandah-sh1ir 21 день назад
Wina uyo ambuye chitaninayeni
@decemberjonathan3001
@decemberjonathan3001 18 дней назад
Umagona naye limodzi uzinamiza azibare ako
@migneslutepo221
@migneslutepo221 20 дней назад
,,😂😂😂😂 Koma abare boza mumaliziwa mulungu adakhara pasi pano bwezi tose anati ononga 🤣🤣🤣
@fannyzimba149
@fannyzimba149 23 дня назад
Ndiye pope ndi mulungu ?Azionatu awa asowe ndithu mtendere mulungu awakanthe chilungamo chioneke may the souls of those who died in Chikangawa Continue to be Resting in peace 😭 😭 😭 😭 💔 💔 💔
@JamiluSunday
@JamiluSunday 11 дней назад
😢😢 rip chilima
@chiletsokazembe-ri4ic
@chiletsokazembe-ri4ic 23 дня назад
mmm; udziyankhula moopa mulungu, inuyo wakuuzani ndindani? mmalo mopemphelela dziko lathu kut chikondi chipite patsogoro kom muli busy kufalitsa uthenga olakwika omwe satana akusangalala nawo, kod ndinu anthu otani iwe ndiwe wasataniki munthu oipa mulungu wa malawi salora kut zomwe mukufuna zichitike.
@AshimayeGama
@AshimayeGama 22 дня назад
Chakwela ndi chilima dzawo dzinali dzimodzi chilima oyipa kwambili ndamene wawonongetsa dziko lamalawi mbudzi ikasangalala amalonda alipafu
@JimmyMkandawire-f8g
@JimmyMkandawire-f8g 19 дней назад
Kkkkkk koma wabisala m'mbatata nsana ukuoneka. Kkkkkk ndaseka kwambiri
@InnocentPemba
@InnocentPemba 15 дней назад
Kwasala ndi kupenga basi
@timothymhone2340
@timothymhone2340 23 дня назад
Koma mtanyiwa uyenera kulapa bodza
@KampidoStevenSymon
@KampidoStevenSymon 14 дней назад
😂😂😂😂😂 km yeah
@ShearstonNyirenda
@ShearstonNyirenda 20 дней назад
Vitsilu ntanyiwa umboni wonama
@SarahNyama-i3v
@SarahNyama-i3v 17 дней назад
Ayi amalapa kwa jar
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v 22 дня назад
Ku italy kukapempheleredwa,ku germany kukaphiphilisa umboni wa ndege koma abale,chakwera alangidwe anakali moyo
@juliochiwalo
@juliochiwalo 20 дней назад
Anthu onse atengedwawo kuononga ndalama zaboma basi akulephera kuwapasa ndalama zao amalawi omwe anapuma ntchito zaka zitatu zapitazo what a shame to chakwera and his mcp govt
@NaomieBanda-t6g
@NaomieBanda-t6g 15 дней назад
Ndipo pemphelo la papa wawoyo siligwila ntchito mpaka iwoso apume kuti chilima naye apume
@JaydragaFelisiya-hz2km
@JaydragaFelisiya-hz2km 11 дней назад
Munthu woi uyu😢😢😢😢
@FumbwaLyson-3710
@FumbwaLyson-3710 17 дней назад
Kukamba chilungamo imfa ya chilima ikupweteka mmalawi aliyese koma akulu awa asamatinamizepo coz itangochitika ngozi adati ali ndi umboni onse pa imfa ya chilima maso athu anali kwa iwo koma mpaka pano kuli ziiii apa akutiuza zina haaaaa uyuu asamatipepeletse😂😂😂😂😂
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 23 дня назад
Apule awona nyekwe pankhani ya ndege. Mizimu ya anthu 9 iwonesa Malawi nyekwe. Akumana ndi papa koma papa si Mulungu koma ndimutumiki chabe. Ndipo wasiya mupingo wake wa assembly of God chimwalilire anthu 9 aja ali busy kupita ku Roma ccap seventh day. Cholinga amupemphere kwa Mulungu koma Mulungu akukantha
@samuelsaizi2463
@samuelsaizi2463 22 дня назад
I don't believe that 384 apple are among the president of Malawi trip.
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya 20 дней назад
Kd MOTi ngozi yadzuloyi aphas ndi a mcp machende Ako iwe chilimayis mulungu anapangila dala kt zichitike izi dziko la Malawi likanakhala pamavuto ndiye iwe pathako Pako limpompo ndipo mulungu akukanthe iweyo shupt yese amavomeleza izi ndiwopepela
@christophergibson72
@christophergibson72 19 дней назад
Ndipo zoona ase
@YankhoRumwila
@YankhoRumwila 16 дней назад
Ndipo ka radio station ka mbuli ngati aka sindinakaone
@BenardChitera
@BenardChitera 13 дней назад
Rip Biyeni
@AlbertKonde-ug4qy
@AlbertKonde-ug4qy 17 дней назад
Tmakunyadilan koma mumachedwakuyankha
@violetpotani
@violetpotani 23 дня назад
Uyuyu afera kutulo palibe chumuyendera
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 21 день назад
Oyenda ndi lupanga lupanga lomwelo lidzamupha yekha Mulungu kanthani wonse womwe anatenga po mbali pa za imfa ya Chilima ndi anthu wonse mizimu yosalakwa zombvetsa chisoni ndithu SKC ngati anangochoka kuti abweranso
@LiamTennessee
@LiamTennessee 22 дня назад
Kaya wasolola report ndani Limpopo fm ilinaayo
@chiletsokazembe-ri4ic
@chiletsokazembe-ri4ic 22 дня назад
Mmmm kukhulupilira zabodzazi
@HilaryGomonda
@HilaryGomonda 20 дней назад
MCP kuzangoluza koma muzakhalamo mmalawi muno ?
@GonjetsoBonface
@GonjetsoBonface 11 дней назад
😭😭😭😭😭 rest well
@LexaKamanga-y6d
@LexaKamanga-y6d 17 дней назад
Muyamba kulangidwa musanamwalire
@YankhoRumwila
@YankhoRumwila 16 дней назад
Iwe galu wa Limpopo pita ukabibe ndi bodza lakolo and ulibe nzeru .pathako pakoso ndipo.
@HarveynsonthiNsonthi-u4n
@HarveynsonthiNsonthi-u4n 18 дней назад
M'mesa iwowo ndi abusa akupita Kwa papa bwanji ... abvomereze pamaso pa a Malawi ambuye achitira chifundo palibenso njira ina
@PiusChawinga
@PiusChawinga 23 дня назад
Ntanyiwa bodza
@AckimKasiya-u7q
@AckimKasiya-u7q 23 дня назад
Wamabodza uyu
@ubs7030
@ubs7030 22 дня назад
Iwe mtanyiwa, ndiwe chitsilu, ukumanyoza president osalakwa, macadet sangaloweso mboma.
@christopherMacheso
@christopherMacheso 19 дней назад
Choipa chisata mwini
@alicklabu2494
@alicklabu2494 19 дней назад
aaa Ntanyiwa ndi wabodza uyuuu.... umapusitsa osalowa mkalasi iwe...
@joebrown1158
@joebrown1158 23 дня назад
Was Chakwera really Was a pastor of what ? Which Bible Chakwera was reading?
@GrecianHaward
@GrecianHaward 18 дней назад
Olny God can judge
@frankdomingo1109
@frankdomingo1109 18 дней назад
Madness has begun!
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya 20 дней назад
Ndipo chakwela wachita kuyitanidwa osati mabodza anuwa ai kmso chakwela sakufa ai chifukwa ndiwosalakwa atafe ndi petulo wanuyo nkhalamba vimilomo ngati zokuna za alonwe kuyankhula ngati wagona kubumbu kwa get shupt alonwe mademo mungapange ndife achewa inu ? Mwachepa muzingolila choncho munya mesa mtanyiwa wanu yemweyi anakuuzani kt mangochi DPP yawina ndiye sinunaona inawinila kumapwala akew😊
@user-hy9ge8tw3r
@user-hy9ge8tw3r 18 дней назад
Big up urself ❤
@user-sm8gx4vf1v
@user-sm8gx4vf1v 19 дней назад
Kuti tidziwe chilima wamwalila tinadziwila radio imeneyi koma anthu inu kutukwana makudziwadi koma mulungu akukhulukileni
@michaelmvula134
@michaelmvula134 20 дней назад
Unfortunately, you don't know how God operates. God will never accept any prayer that is evil in nature. Just wait for your day of the Lord. Accusations will not qualify you for righteousness.
@ubs7030
@ubs7030 22 дня назад
Kodi a DPP mwaiwala kale zomwe anthu amakumachilani komaso anthu anakuchotsan mmboma, I hope you are worse now than before.
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 22 дня назад
Chakwerayo mpaka azipha yekha muthu wqkhaza ngati ameneyo sinamuone ine ayi mizimu ya athu onse imuzuza kwambili mpaka azipha yekha
@christophergibson72
@christophergibson72 19 дней назад
Iwe nde msaname umandinyasa wava umsowa zochita eti
@YankhoRumwila
@YankhoRumwila 16 дней назад
Ada uli ngati ine, ada amenewa ineso amandinyasa
@user-co6sc8om5n
@user-co6sc8om5n 19 дней назад
Inu osati apita kukalapa anthuwa onse ndi asatanic including papayo
@SellinaManda-z8h
@SellinaManda-z8h 9 дней назад
Mulungu alipo
@JamesMadina-uv6xe
@JamesMadina-uv6xe 23 дня назад
Koma abale mulungu chitani kathu plx ngat ali olakwa😢😢😢😢😢
@jixonromeo4111
@jixonromeo4111 23 дня назад
Kuchokela ku Blantyre 😂
@user-sz6bi3tw5y
@user-sz6bi3tw5y 20 дней назад
Ntchimo limadzudza
@HENRYCHAONA
@HENRYCHAONA 20 дней назад
Anthu osewo akukatani
@RahimLuemba
@RahimLuemba 20 дней назад
Chmfit chosekerera icho
@AlexLekani
@AlexLekani 22 дня назад
Why killing innocent souls,God will punish him
@KingsleyKabichi
@KingsleyKabichi 22 дня назад
Amkalimbana ndi akatolika apengatu ameneyu sanati.
@GregoryMatambo-m6y
@GregoryMatambo-m6y 16 дней назад
Kkkkkk koma muli ndi bodza lamkukhuniza kkkkkk
Далее
Cleaning🤣 #shorts #トイキッズ
00:18
Просмотров 10 млн
Cute
00:16
Просмотров 5 млн
BOOON KALINDO WAULULA ZISISI LELO🙆‍♂️
15:23
Просмотров 11 тыс.
Cleaning🤣 #shorts #トイキッズ
00:18
Просмотров 10 млн