Тёмный

Limpopo FM Ntanyiwa wayiphedula nzammene black box inachotsedwela mu ndege madzulo zonse zili umu 

Malawi Trends TV
Подписаться 38 тыс.
Просмотров 41 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

26 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 84   
@ShakilahMbwanaa
@ShakilahMbwanaa 2 месяца назад
The best redio Limpopo fm ndakukondani anthu okonda Malawi tisankhale mu ubuli much love the fm Limpopo
@JamesKhudze
@JamesKhudze 2 месяца назад
Best radio station
@user-oh9bh1cl3b
@user-oh9bh1cl3b 2 месяца назад
We love you guys keep on letting us know what is happening in our funken country
@CarenNamwera
@CarenNamwera Месяц назад
💪💪💪mmakwana comrade ntanyiwa
@JaiMkupa
@JaiMkupa 2 месяца назад
Tili pambuyo pano the Best channels of Malawi
@JowasiMasina-fy8ji
@JowasiMasina-fy8ji Месяц назад
The best Radio Limphopo
@DavieMathyola
@DavieMathyola 2 месяца назад
Tili pa mbuyo mpanu bro mtanyiwa comrade excellent
@SalaJawali
@SalaJawali Месяц назад
Ambuye amava a tiyakha ndinthu amen
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 2 месяца назад
Chakwera amusankhe mkazi wa Sidik Mia kuti akhale VP apo biiii sapezeka wina aliyense.
@lyiemax
@lyiemax 2 месяца назад
Powerful speech ever
@user-mk9ro8fd4u
@user-mk9ro8fd4u 2 месяца назад
Keep it up limpopo fm,tell the nation the truth without fear
@HiryChimalizeni
@HiryChimalizeni 2 месяца назад
Keep it up comrade mtanyiwa cralify everything we are tired with mcp
@CharleGollie
@CharleGollie Месяц назад
❤❤❤❤ mumakwan guys Limpopo FM ntanyiwa
@InnocentNgeya
@InnocentNgeya 2 месяца назад
Pangatalike bwanji,, mulungu apereka mayankho ake,,,, panopa ambuye aulura zonse mwez uwuwu usanathe. Limpompo fm wailes koma iyiii. Pitilizani osaopa kupereka chilungamo
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 2 месяца назад
Our only best radio
@StewartGoma
@StewartGoma Месяц назад
This is very painful too sad politics killed 9 people 😭😭😭💔
@fidelixdezembro4599
@fidelixdezembro4599 2 месяца назад
Man zaululika kale,pali audio inayake yomwe ili ndi maumboni onse.
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 2 месяца назад
We will find and give you a good position in our new Government ❤❤❤
@TapiwaMwanjah
@TapiwaMwanjah 2 месяца назад
Great job comrade,❤️
@ChettoSongeah
@ChettoSongeah 2 месяца назад
Mr Ntanyuwa you're eyes of malawian haaa tawaululani a fiti amenewa McP ndi anthu inuyo muzafa imfa yanu yosakhulukilidwa
@FREEJOEKASONGO
@FREEJOEKASONGO 2 месяца назад
Even here your neighbor countries we are not happy
@NEBERTMVULA
@NEBERTMVULA 2 месяца назад
CHAKWERA, KUNKUYU, KEN ZIKHALE NG'OMA, MKAKA, CHIMWENDO BANDA, CATHERINE HARA be careful Malawians are watching your footsteps. MCP IS ENDED!!! IT WILL NEVER EVER BE AGAIN!!!
@SteveChirwa-ne9nt
@SteveChirwa-ne9nt 2 месяца назад
Best channel!!!!!!
@KasimIbbu
@KasimIbbu 2 месяца назад
Km achakwela km ndiwesilu kwabas
@WillyAndaki
@WillyAndaki 2 месяца назад
Ikhalitse limpopo fm with Comrade ntanyiwa
@user-oe6hy4fy5v
@user-oe6hy4fy5v 2 месяца назад
Ma radio akanakhala ngati awa bwenzi kulibe chinyengo
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 2 месяца назад
Best Limpopo fmmm
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 2 месяца назад
This is our 👀 radio ❤❤❤❤
@user-cl5qw1kp1h
@user-cl5qw1kp1h 2 месяца назад
Brother timakunyadira timamva zambiri, kodi iwowa akungosakha akazi kukhala VP chifukwa chani akufuna azigona nawo chifukwa alibe mamuna
@ChristopherUmari
@ChristopherUmari 2 месяца назад
Takuyamikani mayi chilima pokana zachibwana zimenezi
@TatendaMakuyana-su7fe
@TatendaMakuyana-su7fe 2 месяца назад
Best fm radio
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 2 месяца назад
Nyumba ya magazi Galimoto ya magazi a chilima
@MirriamRaja
@MirriamRaja 2 месяца назад
Mulungu wamwamba mwambayo azikutetezelan nthawi zonse pamene mukuuza choonad a Malawi ndipo tili pambuyo panu Imani pa chilungamo ndipo chidzakumasulan
@MoseChikopa-qy3og
@MoseChikopa-qy3og 2 месяца назад
U r the best
@user-ug6ox9rf7c
@user-ug6ox9rf7c Месяц назад
Koma chonde muzika ma date kuti tiziziwa kuti ndiya lero kapena ya kale
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 месяца назад
Kusaganiza akufuna nayeso asowe
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 месяца назад
Achakwera Munthu wakhaza kwambri
@corretabanda7685
@corretabanda7685 2 месяца назад
Ngati kuli munthu amene anakonda kuyankhula chilungamo anali a Chilima ndipo Mzimu wawo ufukulambe chilichonse chomwe a Malawi akuyenela kudziwa.
@JuliusLuwanda
@JuliusLuwanda 2 месяца назад
Iwe mtanyiwa ndi 1 palibeso
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no 2 месяца назад
Tiyakhadi tokha amalawi vot yanga nde phavu yanga😢😢😢😢
@user-mi3ot6ms8x
@user-mi3ot6ms8x 2 месяца назад
Koma Limpopo ndi number one
@AroushMussah
@AroushMussah Месяц назад
Very painful 😢😢
@fidelixdezembro4599
@fidelixdezembro4599 2 месяца назад
Don't worry, pompanonso chakwera anfanso!!! Sipapita nthawi
@alicembetewa5151
@alicembetewa5151 2 месяца назад
kkkkk
@DoreenKaunda
@DoreenKaunda 2 месяца назад
Kkkkkkkk koma guys eish,eee chilima watiphweteka mmmm
@user-et1tl1qs2j
@user-et1tl1qs2j Месяц назад
Kutsatila mwachidwi
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 2 месяца назад
Big proud💪
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 месяца назад
Comredy mtanyiwa agogo Anga akufuna akupaseni zukulu wawo akuti muzikhala naye
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 месяца назад
Mai Zamba chinyemba Ngati kalongonda😢😢😢😢
@KingsiryMchona
@KingsiryMchona 2 месяца назад
Antanyiwa koma mulipo mwangoti ziiii
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 месяца назад
Vuto la chakwera ndi hule ndinanena ine amaona ngati kuti mai chilima ndi ophweka ngati hule la sadik mia tamangomu kwela mkazi wa sadik mia mbuzi iwe
@DavidMtambo-zm8ne
@DavidMtambo-zm8ne Месяц назад
Paja or fiti yimapemphera yapempheradi
@JacquelineNgondoma
@JacquelineNgondoma 2 месяца назад
He suppose to resign,ndpo thus the bst angachte asatikwiyisebe
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 2 месяца назад
Uyu payekha sangapange resign PAKUFUNIKA kuyenda pa mseu kuti adziwezoti amalawi sitikumufuna
@ChristopherUmari
@ChristopherUmari 2 месяца назад
Nanga ndale zomapanga anthu atagona ndiye ndale zanji zimenezo
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 2 месяца назад
Dzikomo mayi chilima chifukwa chakuyankha kwanu uvice umenewo akapase akadxi achakwera chifukwa sitikufuna kuliranso
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 2 месяца назад
💪💪💪💪
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 2 месяца назад
Iweyo jemus chakwera apa ndipo ungadziwe kuti kudziko lapansi kulibe chobisika koma ndiye mwayaluka amphawi kufuna kukakamira kudya ndalama zaamphawi
@maskinmsungeni8763
@maskinmsungeni8763 2 месяца назад
Aiwale ndipo amwene azavotere MCP Mwadzi wa chilima ndi anthu onse uzakukanthani
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 2 месяца назад
Palibenso kutiudza lipoti labodza Limpopo ilipo tiziwa zonse mulungu wasikira mwa Limpopo manyadzi bwanji ku state ?
@user-zp3fb7el4z
@user-zp3fb7el4z 2 месяца назад
Apenga misala anthu oipawa
@user-es4jt6ds8m
@user-es4jt6ds8m 2 месяца назад
Koma a Malawi ndife anthu okanika ma umboni wose akutchura anthu angapo ndipo anthuwo alipo kunkuno Ku Malawi bwanji osawagwira eeee ayi
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 2 месяца назад
Israel kapena America Awapatsa ndege achakwera posachedwapa ponamizira kuti ndi ya chipepeso Koma pali pa chifriend chawo
@DoreenKaunda
@DoreenKaunda 2 месяца назад
Ndichoseni umbuli guys,kodi radio imeneyi ndi ya mmalawi muno?koz ena akuti ai ndi ya ku Joni?
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 2 месяца назад
APAPA COMLED FALITSANI UTHENGA OTI 21 DAYS IKANGOTHA MADEMO AYAMBE CHAKWERA NDI NDUNA ZAKE ZONSE ACHOKE
@Telezatembo-de4ng
@Telezatembo-de4ng Месяц назад
@moyo77777
@moyo77777 2 месяца назад
Kom ndiye mcp alibe zelu why
@GilbertKuchipinda
@GilbertKuchipinda 2 месяца назад
Limpoo limpo limpopo
@martinBPhiri
@martinBPhiri 2 месяца назад
Odziwa chilungamo satsogoza kugwira ufiti ena
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki 2 месяца назад
Ndili okonzeka kulimbana ndi MCP ndife ndife
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 2 месяца назад
Chakwera kumuseweresa mulungu koma chikhalirenicho anthu unawawerusa anthu amundege asanapedzeke unkaganiza chani ?
@user-zi2mj1bn5v
@user-zi2mj1bn5v 2 месяца назад
😢😢😢 achakwera ayalukatu apa
@user-nx6dk4bj8v
@user-nx6dk4bj8v 2 месяца назад
Bola musamatinamize
@DoreenKaunda
@DoreenKaunda 2 месяца назад
Ndiposooo iiii,
@PeterSadulo
@PeterSadulo 2 месяца назад
Osafooka
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no 2 месяца назад
💪💪💪
@chaleraeaster-ce2kc
@chaleraeaster-ce2kc 2 месяца назад
Go dipa
@El_lam825
@El_lam825 2 месяца назад
😢😢😢
@TryceMagombo-sh7kb
@TryceMagombo-sh7kb Месяц назад
Very bad
@gearardphiri6904
@gearardphiri6904 2 месяца назад
Tikuvera
@user-nx6dk4bj8v
@user-nx6dk4bj8v 2 месяца назад
Owo
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 месяца назад
Kod8
@DavieMathyola
@DavieMathyola 2 месяца назад
Tili pa mbuyo mpanu bro mtanyiwa comrade excellent
@JacquelineNgondoma
@JacquelineNgondoma 2 месяца назад
He suppose to resign,ndpo thus the bst angachte asatikwiyisebe
Далее
Report La Chilima Labwela - Ntanyiwa Kufotokoza
31:53
CHIBANGILI CHIKUPANGA ZODABWITSA KU BLANTYRE PART 1
13:53
12 August 2024
2:38
Просмотров 103
BRIAN NDI A SHADRICK NAMALOMBA KUPANIKIZANA MAFUSO
32:31
BON KALINDO LERO PA 27 AUGUST 2024 |
17:02
Просмотров 11 тыс.