Тёмный
No video :(

Limpopo Ntanyiwa watulukila lero ndipo boma ligwa ndi BP ndithu chifukwa eeeh sakupeleka mpata 

Malawi Trends TV
Подписаться 38 тыс.
Просмотров 28 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

28 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 103   
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp Месяц назад
Tufuna group Yanu amtanyiwa tikulira mpaka pano
@SymonYohane-i5q
@SymonYohane-i5q Месяц назад
Mbambande iweyo ukundimvesa kukoma kwambiri timafuna anthu ngati antanyiwa ky dziko lanthu likhale lamphavu 🎉🎉🎉🎉🎉
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Месяц назад
More 🔥 comrade mtanyiwa ❤❤😂
@yusufbakali
@yusufbakali Месяц назад
We will waiting for nkhanga zawona
@StiveKantiki
@StiveKantiki Месяц назад
Big up mtanyiwa❤ km ine ndikuifuna nyimboyi mwaika kumapetoyi guys
@FrankHaruni
@FrankHaruni Месяц назад
Ofunika kuwayakhula amalawi mr usi atiwayamba kunamidza athu khati wa utm aliwa mcp amalawi akuiwala kutindi thawi yakapeni akutengeka audzeni bwino amalawi mr tanyiwa
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma Месяц назад
Tidya ife ndalama zo Koma vote yathu ndiye ng'ooo aiwale tiyeni tidye
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p Месяц назад
May God bless you ❤❤❤❤❤ god loves you more
@FatimanickisJaffer
@FatimanickisJaffer Месяц назад
Akagawa kwandan pot kumangochi nd kwa ayao ndy akut akufun achewa km kul zinthu 🤞🤞🙌🙌🙌🙌🙌😎😎😎😎😎
@DavieKidison
@DavieKidison Месяц назад
Limpompo FM 🔥🔥🔥 bro umakwana akhale poyela agalu amenewa
@bensonnamizinga9750
@bensonnamizinga9750 Месяц назад
Keep it up brother ntanyiwa
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka Месяц назад
Ife mai dzimbiri amatithandiza tili mudzi umodzi anali be sankho zimai ozichepetsa 2014 anali MP wadera lathu tisalile
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 Месяц назад
We love ❤you too ntanyiwa ❤❤❤🎉
@user-ik5sz8hc6f
@user-ik5sz8hc6f Месяц назад
Pambuyo pa Limpompo yomweyo
@user-ny3it3jp9l
@user-ny3it3jp9l Месяц назад
Lipopo fire 🔥
@ChrisEnos-to5uv
@ChrisEnos-to5uv Месяц назад
Yomweyo Galu iweeeee😂
@user-oj2jr6kf9c
@user-oj2jr6kf9c Месяц назад
Yooooo!!!!!!! Iweyo mmmm umakwana njala simafika ndikamamvera limpopo
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Месяц назад
Ndipo zoona njala sumaimva
@RoseChiphiri-ts8jx
@RoseChiphiri-ts8jx Месяц назад
Ntanyiwa zulo ndinakusowa 😊
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y Месяц назад
Ulemu wanu ali Limpopo fm❤
@FatimaBakali-v7q
@FatimaBakali-v7q Месяц назад
Timakukondani Kobasi a Mtanyiwa
@RhodaBandah-sh1ir
@RhodaBandah-sh1ir Месяц назад
Koma Bt isakhe mbali ku ndix nde anthu anakwiya kalekale
@HaliJana
@HaliJana Месяц назад
KOMA CHAKWERA UMAGANIZA CHANI PAKUMUPHA CHILIMA,ULI NDI UMUNTHU IWEYO KOMA?
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d Месяц назад
Munthu oipa kwambiri eishiiii
@BadmanshutterZinkana
@BadmanshutterZinkana Месяц назад
Salute mi comrade ✊🏻✊🏻
@franciscomalola92
@franciscomalola92 Месяц назад
more fire nthanyiwa
@LuskaMoses
@LuskaMoses Месяц назад
Tapangani group ra WhatsApp plz nyimbo iyi ngawireni la kayin ndabare plz mtima ukuwawa ine atiphera anyamata akwathu Ku magoni Ife anyaparawa akutipezerera kwambiri😢😢
@TenahJustinnalia
@TenahJustinnalia Месяц назад
Nyimboyo ndaikonda undiuza bwino zakuchikangawa km nthanyiwa umatimvesa kukoma
@ImanRashidi-so4oo
@ImanRashidi-so4oo Месяц назад
Powerful massage big up mtanyiwa ❤
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk Месяц назад
Fm nomber 1
@InoquebosiCanhosa
@InoquebosiCanhosa Месяц назад
Auzeni agalu a mcp mumakwana
@lindamwanza4958
@lindamwanza4958 Месяц назад
More fire Limpopo
@user-xz3nz7dy1f
@user-xz3nz7dy1f Месяц назад
Ndipo azaza kale ku chikolobay
@FrankHaruni
@FrankHaruni Месяц назад
Pajatu amalawi ati samachedwa kuiwala adzidzudxika ife nde tinawasiila malawi waoyo
@UchiziMwakilasa
@UchiziMwakilasa Месяц назад
Munthu wamkulu Ntanyiwa,,,,,,,timakukondani kunoku bwana
@petermasenti2084
@petermasenti2084 5 дней назад
Comrade mumakwana
@davidkayangemakala7957
@davidkayangemakala7957 Месяц назад
ETI akufuna kukweza msokho ndicholinga atorele ndalama zomwe akutaya pa conversation ma 70mter kkkkk amalawi tinalakwa chani misokho ckugwira karechito kkkkkk
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Месяц назад
Tipasen gulup yan prz tikufuna tizimwaza mauthenga awa palipoose ziko muno, ifeso tatopa.
@AnussaAlli
@AnussaAlli Месяц назад
More fire ❤❤❤ ❤❤ comrade mtanyiwa❤❤❤❤
@NoxyChinsembe
@NoxyChinsembe Месяц назад
Antanyiwa muzakaponye kanyimboko nafeso tikhale nako
@FunnyDimSum-hk1so
@FunnyDimSum-hk1so Месяц назад
Kkkkkkkk kom ntanyiwa umatokan ❤one love
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga Месяц назад
Tipasen nyimbo yomwe yaikidwa kumapetoko
@user-on2me8ek5w
@user-on2me8ek5w Месяц назад
Koma mtanyiwa ndi nyatwa😂😂😂😂
@TressLuka
@TressLuka Месяц назад
Zilikotuuu 😂😂😂
@GLADYSCHIDOTHI
@GLADYSCHIDOTHI Месяц назад
Akamuna Mr. Ntanyiwa. Real comrade.
@FatimaBakali-v7q
@FatimaBakali-v7q Месяц назад
Ati mkabulamo muli juu 🤣🤣🤣🤣
@SelemanIssahAhmad
@SelemanIssahAhmad Месяц назад
😂😂😂😂😂😂limpopo😊😅
@Yungjoe786
@Yungjoe786 Месяц назад
The best TV in malawi 🇲🇼
@Shelifibraheem
@Shelifibraheem Месяц назад
We do love you
@moosaWilson
@moosaWilson Месяц назад
mumakwana bro
@MercyMithie
@MercyMithie Месяц назад
Yomweyo
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Месяц назад
Nde akunjawo anawalipira mmakwacha anthu akunjao nde oufoipatu
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v Месяц назад
Yomweyo Mr tanyuwa ineyo ndendimakukondani mwinatso kuposa inuyo kkkkkk awoneseni kt imfetso timatha timayenda akumfa kale
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Месяц назад
Shame Malawi Government shame😭
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp Месяц назад
Ine Kumva bwino mtanyiwa
@MillicaBanda
@MillicaBanda Месяц назад
Mativetsa kukoma kuno LL makwana
@Shelifibraheem
@Shelifibraheem Месяц назад
Mumakwala madolo
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh Месяц назад
😂😂😂 nkabudula mwatentha
@tannexmsukwa1918
@tannexmsukwa1918 Месяц назад
Ndipo Agalu amenewa azangifela kutulo,Anthu woipa sinaonepo pa dziko lapansi.Mulungu siopusa
@clementdzakumwashowlove7814
@clementdzakumwashowlove7814 Месяц назад
Nyimboyi yakumapetoyo ndikufuna plz
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o Месяц назад
Yomweyo pumbwa iwee 😂😂😂😂❤
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Месяц назад
Inuso masiku ano simukunena kuswakuswa muli ndi Mantha mwasiyana ndi mluzi channel
@SydneySingini
@SydneySingini Месяц назад
Umandiwaza badly awuze chilungamo
@PreciousMmodzi
@PreciousMmodzi Месяц назад
Mtanyiwa umatha iweyo ndi one
@MalawianMediafm97
@MalawianMediafm97 Месяц назад
This is comred ntanyiwa on Lipompo FM kuzangoturikira ndi more 🔥🔥🔥🔥🔥
@user-dq9oe8sp8k
@user-dq9oe8sp8k Месяц назад
Mbambande comrade ❤
@zoeysfunandplay
@zoeysfunandplay Месяц назад
Nyimbo ya Kaini yo anayimba ndani ? Nduyifuna
@user-ul8fp1ov1k
@user-ul8fp1ov1k Месяц назад
tigaireni nyimboyo,ulosi
@user-gg9hw4oj2v
@user-gg9hw4oj2v Месяц назад
🔥💪💪💪
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI Месяц назад
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Месяц назад
Nyimbo ya ayezayayo tikufuna ya full please plus ya Kaini
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx Месяц назад
Palibe yemwe angachithawe chilungamo
@AlesaBiyala
@AlesaBiyala Месяц назад
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd Месяц назад
nyimbo iyi guys eeeee
@IgnatiousFote
@IgnatiousFote Месяц назад
Koma zilipo chaka chino
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o Месяц назад
🎉🎉🎉🎉
@abdulkareemsaeed
@abdulkareemsaeed Месяц назад
Iwe ambuye akudalitse
@KhalideNerve-mu1eq
@KhalideNerve-mu1eq Месяц назад
❤❤❤❤❤
@tracybennie7783
@tracybennie7783 Месяц назад
Koma. Chaka. Chale. Ndichinoncho
@ReginaNyilenda-ug1lf
@ReginaNyilenda-ug1lf Месяц назад
Atanyiwa 😂😂ine mukundimalinza tiyeni nazo
@LuskaMoses
@LuskaMoses Месяц назад
Ntanyiwa osaopa osaopa tiye nazo Ife tilipamboyo
@user-tf7yi9fp2u
@user-tf7yi9fp2u Месяц назад
Ntanyiwa ndi machine
@sandebakali
@sandebakali Месяц назад
tikhala maso tionela live
@user-gi1gh9ry6h
@user-gi1gh9ry6h Месяц назад
More ❤❤❤❤❤❤ mtanyiwa😅😅😅
@RachealPongolani
@RachealPongolani Месяц назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@KhonzoBlose-wq7zm
@KhonzoBlose-wq7zm Месяц назад
Ifenso timakukondani bro
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo Месяц назад
Mudye koma 2025 sadzawina
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo Месяц назад
Inuyotu mumakwana antanyiwa
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 Месяц назад
Comryde ifenso timakukondani
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Месяц назад
Ambuye atithandize
@iddikassim
@iddikassim Месяц назад
Umakhwana ntanyiwa
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Месяц назад
Mungoti phee muwonee
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Месяц назад
Zopusa basi zazii
@UseniMailosi
@UseniMailosi Месяц назад
🐕🐕🐕🐕
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 Месяц назад
Palibe amakutuma kuti uzimvera,
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi Месяц назад
Ndipo palibe amakugwila pa khosi kut umvere
@user-tk6wf2eg4z
@user-tk6wf2eg4z Месяц назад
Chilungamo kuwawa ine abale
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Месяц назад
Zopusa wapanga chakwela and his useless government zokupha vice President kuchepaa?
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg Месяц назад
Kkkkkkkkkk iiiiii koditu afa chiimire cause to be honest all Malawians ndife okwiya pazimene zinachitikazi Mizimu yakwiyaaaa mtendere saupezaaaaaa ndipo kulibeso kudzalamulira 2025 achokeeeee
@HajjiSufiyani
@HajjiSufiyani Месяц назад
Mumati imilila AtaNyiwa pitilizani kutikonda. Kapeyu achokepo
Далее
Joseph Nkasa - Chakwera
5:45
Просмотров 2,1 тыс.
娜美这是在浪费食物 #路飞#海贼王
00:20
журавли в пятницу
00:14
Просмотров 57 тыс.
Umboni Oti Namadingo Ndi Dolo
10:10
Просмотров 16 тыс.
Joseph Nkasa Tithawile kwa iye
7:10
Просмотров 35 тыс.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Просмотров 239 тыс.
娜美这是在浪费食物 #路飞#海贼王
00:20