Тёмный

Mavuto A Ku Immigration Akupangitsa Ndi A President Ndi Attorney General - Bon Kalindo 

Nyasa VoiceBox
Подписаться 25 тыс.
Просмотров 8 тыс.
50% 1

On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo says, all the problems and inefficiencies at Immigration and Citizenship services are man-made and the culprits are HIs Excellency the President and the Honorouble Attorney General.
Pa Nyasa VoiceBox, a Bon Kalindo akuti, mavuto onse ndi kusakwanira kwa ntchito za Immigration ndi Citizenship ndi zopanga mwadala ndipo olakwa ndi His Excellency President ndi Olemekezeka Attorney General.

Опубликовано:

 

6 июн 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 12   
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 2 месяца назад
Ndipo zoonad koopsa, Chakwera achokeeeee achokeeeee pls we're tired with him.
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 2 месяца назад
Thank you so much our president, president for the poor, slowly by slowly we are winning the battle, proud of you always 🔥🔥🔥🔥
@ChristopherMadulira
@ChristopherMadulira 2 месяца назад
Thanks for advice
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 2 месяца назад
Mwana opasa theng'eneng'e boma koma iweee dc aaaa
@Moses51
@Moses51 2 месяца назад
The DC bon kalindo pangolin 🎉
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 2 месяца назад
Tchaka tchaka che nyirenda kumadziona kuti zinthu zolakwika koma kumasapoter mbudzi ya munthu. Tiye nazo anzako anakathera nazo ku jail.
@MagretMvula
@MagretMvula 2 месяца назад
Zikomo kwambiri mwatichosa mumavuto
@user-rm2xv8ys1i
@user-rm2xv8ys1i 2 месяца назад
❤❤❤❤
@user-qv4yu2ir2k
@user-qv4yu2ir2k Месяц назад
Zoonadi achoke m'dala ameneyo
@George-zd5le
@George-zd5le 2 месяца назад
Bon kalindo wakhala ukuyankhula zoona pakanthawi, Koma Chochitsa manyazi ndichakutu mu Malawi muli anthu ophunzila zedi koma wonse akuoneka ngati mu Dzikomo muli mbuli zokkha zokha, kaya mwina chifukwa akumukonda kwambiri chakwerayo kaya onse kuli ziiii Dziko lochititda manyazi
@user-pn7cj9hb3t
@user-pn7cj9hb3t Месяц назад
Brother kuno kuli mbuli zophunzira chomwe amadziwa ndikugawa matenda kwa ana a sukulu muma college mu.
@user-hq6dq7zr1e
@user-hq6dq7zr1e 2 месяца назад
Kumangoika anthu maudindo coz he's a president that's bulshit mn
Далее
A Malawi Muganiza Bwanji? - Mr Matemba
16:52
Просмотров 1,1 тыс.
Китайка Шрек поймал Зайца😂😆
00:20
SPILLED CHOCKY MILK PRANK ON BROTHER 😂 #shorts
00:12
Why Saulos Why - Bon Kalindo
4:56
Просмотров 38 тыс.
Times Exclusive featuring Bon Kalindo - 6 January 2024
1:03:20