Mulungu wa David muchilitseni mwana wanu. Zimene mudachita pa ana a Israel pa 2mafumu 2 vs 19-23 muchitireniso mzimayi uyu ndikuti dziko lapansi likulemekezeni🙏🙏🙏
What God can not do does not exist 🙏 ambuye onetselani Kwa mayiwa kuti palibe chokulakani, palibe chomwe mumalephera,Yehova akhudzeni mwapadela dela 🙏🙏
very sad but glad that her husband is still around. God will heal her, the fact that she met Rodwell it"s proof that God is clearing her healing journey.
Yehova adzakupewetsani ku matenda aliwonse. Sadzakugwetserani matenda owopsa aja munawadziwa ku Igupto, koma adzawagwetsera pa odana nanu. Deuteronomo 7:15. Get well soon mama
Satana amabweresa zosakhara bwno pa moyo wathu kuti tizimufusa mulungu mafunso osakhara bwno, km inuyo mulungu chitanipo kanthu pa Mai awa yesu mwana wa David muchitilen chifundo mwana wanu amene akuvutika ndi matenda
😢😢😢 We should thank God for the simplest things in life because there are people going through worse in life, may God heal her Komaso ku Malawi munthu momwe akuonekelamo mpaka November abale kutalikilenji