Тёмный

MDYANGU COMEDY..19/05/23..Flora Suya +265883106798. 

LIKI-LIKI Ladies
Подписаться 53 тыс.
Просмотров 33 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

8 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 93   
@collinstrevor
@collinstrevor Год назад
Tifani mwana wakula akuri kachibesi ofuna wina kkkkkll koma sasoka
@jamilahkhau3398
@jamilahkhau3398 Год назад
Ashokoshoko zinaz nde nzoziyamba tsopano 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@andrewmasangwi4916
@andrewmasangwi4916 Год назад
Eti eti abale 😌🤪
@chifundomhango3324
@chifundomhango3324 Год назад
😂😂😂😂😂😂zina umangoona waziyamba 😂😂😂koma ashokoshoko
@chifundopaulbonda714
@chifundopaulbonda714 Год назад
Big man wanyamula katundu wake mujumbo ati Banja latha😂😂
@IbrahimAdilu-nq5hr
@IbrahimAdilu-nq5hr Год назад
Mumatichotsa nkhawa please pitirizan ndipo othandiza azipezeka mulungu akudalitsen zikomo
@chancymaulana6185
@chancymaulana6185 Год назад
Masamba ngat livaaa😆😆😆😆
@preciousbonongwe1464
@preciousbonongwe1464 Год назад
Kkkkkk munyanyuwa umakwana
@RukayyahFanes-wr1fh
@RukayyahFanes-wr1fh Год назад
Ashokoshoko nanu...Mumawona ngati akamanga Mapiko kut ana acheze nako.... Mwazionatu.. Kupupuluma ngati mkodzo wa mamawa.
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 Год назад
Ashokoshoko mkadzi zowona kukuuzani kuti chilichonse mukufuna adzikupangirani muzinena inu basi mukuti mukwatire mitala mkazi olo atakondwq bwanji sangalore 😂😂😂😂❤❤😂
@stevephaka9253
@stevephaka9253 Год назад
Just because she said she can do anything ndiye mpaka kufuna ukatenge mitala kkkkkk
@chimwemwenyirongo1755
@chimwemwenyirongo1755 Год назад
Mlelemba alindintopola,ati pali kahule kenakake amati ka Queen.😅😅🤣
@robertchikungwa105
@robertchikungwa105 Год назад
Alira mai mdyangu
@LucyMathiwa-qs1nb
@LucyMathiwa-qs1nb Год назад
Mdyangu akufuna kuusumana😅😅
@mastermindmanyozo5853
@mastermindmanyozo5853 Год назад
😂😂😂😂😂😂 Sasoka akuti iyi waiyambayi azakulemba statement abambo
@anniewhite3497
@anniewhite3497 Год назад
Kusithako nde paka mitala Achokochoko zinazi mumaziyamba dala😂
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 Год назад
Mai chokoshoko best actor mumakwana .
@fastbanda3630
@fastbanda3630 Год назад
Khani sakamba pakudya ndinadziwa kuti ithera pa njira
@kondwaninyangulu5563
@kondwaninyangulu5563 Год назад
Shokoshoko APA ndiye mwakwatiladitu
@user-xu7ex1to7w
@user-xu7ex1to7w Год назад
Mayi Shokoshoko pano ndye akhudzumukatu
@chancymaulana6185
@chancymaulana6185 Год назад
Ati mukulira base mukulatu kumeneko🤣🤣🤣🤣😂😂
@gabbymagwaya5836
@gabbymagwaya5836 Год назад
kkkk kuthilidwa madzi
@saifullahalick407
@saifullahalick407 Год назад
Kkkkkkk Koma a shokoshoko kutsinira ma fulufute ku dzenje. Akamati chilichonse amatanthauza iyeyo ndinu osati nso wachitatu ayi.
@definitemalenga6507
@definitemalenga6507 Год назад
Mandivetsa love saname❤
@lucysangano1891
@lucysangano1891 Год назад
A flora mwatitenga inuyo🥳🥳🥳🥳🥳
@RachelChimwala-ck9rj
@RachelChimwala-ck9rj Год назад
Adyangu chonde panopa metaniko ndevu kkkkk zili bwino kwambiri kmmm
@peterasibu8676
@peterasibu8676 Год назад
Mlelemba nd nkhan zina
@marthaperete6045
@marthaperete6045 Год назад
Ati afunika mwa thuuuu
@chancymaulana6185
@chancymaulana6185 Год назад
Ine sewero li silingathe opamda kukomenta aaa aaaaa🤣🤣🤣
@lazarousnamakhwa6549
@lazarousnamakhwa6549 Год назад
Flora kod chiphwanya Ali kutiko tamusowa zedi
@eustermsamu
@eustermsamu Год назад
Kkkkkkk mulemba mwala ukupita nawo kutiko akuti utenge chisong'otho😂😂
@DANIELMajomeka-eu7tz
@DANIELMajomeka-eu7tz Год назад
Mulelemba umakana
@user-sd3cl2dq7v
@user-sd3cl2dq7v Год назад
Ashoko Shoki mulibe pabwino. Mkazi wayamba kukuonetselani chikondi, mukufunaso mkazi wina😂😂😂
@user-ep2rl3fy4o
@user-ep2rl3fy4o Год назад
😂😂😂😂😂😂 ju akulila mwa besi wakula akufunika wa 2 kkkkķkk km sasoka ndi 1
@jacquelinewasili-eh3uv
@jacquelinewasili-eh3uv Год назад
Kkkkk koma a Mjangu, " awa azipitiriza kuuluka kwaoko fuel akazawathera ..." Kkkkkk
@anniemajiri1220
@anniemajiri1220 Год назад
Kkkkk ndiye mwalawo ndiwachiyani a Mulelemba? Koma ndaseka 🤣
@ibrahimjackson-cg6tc
@ibrahimjackson-cg6tc Год назад
😂😂😂😂 koma chokochoko atenga nkazi wina nkatikati mosinthamo
@Imranasedi-zw7cg
@Imranasedi-zw7cg Год назад
Shokoshoko kkkkk
@De86666
@De86666 Год назад
Ashokoshoko 🤣🤣🤣🤣 mitala ndi khwini et hahahaha 🤣 kwachema
@calvinthomson6234
@calvinthomson6234 Год назад
Ju wakula akufunika kumpangila wa 2 😂😂😂😂😂😂 much love ❤❤❤❤❤
@isaacmussa2942
@isaacmussa2942 Год назад
😂😂😂😂koma banja la shoko shoko ayi taa kkkkkkkk
@user-ws4ue7tf6j
@user-ws4ue7tf6j Год назад
Mumandi nvetsa kukoma guys yooo!!!!!
@user-by3gf4lh4x
@user-by3gf4lh4x Год назад
chiphwanya sakuonekatu
@Chipholeboyz
@Chipholeboyz Год назад
Koma mulelemba ai ndithu mpaka ndifuna kkkkk
@user-de2wm3vh7u
@user-de2wm3vh7u Год назад
😂😂😂😂😂Akuti mwamuiwala komatu sasoka😂😂😂😂😂😂
@jamesdivarson1429
@jamesdivarson1429 Год назад
Chiphwanya tamusowa, we lov u gyz
@user-by3gf4lh4x
@user-by3gf4lh4x Год назад
👍
@thomchinjoka177
@thomchinjoka177 Год назад
Keep it up guys love Flora
@tisungewitness3548
@tisungewitness3548 Год назад
Kkkkkkk ukulila besi juu😊
@princefarukhanhamick
@princefarukhanhamick Год назад
😅😅😅akut. Awa ndie. Minister of Homeland et😂
@andreabrighten301
@andreabrighten301 Год назад
Kkkkkk Ana asamasiyane
@gracephiri1203
@gracephiri1203 Год назад
Ashokoshoko pabwino mulibe, mkazi wasitha Inu munena zamitala zoona zimenezo? Inu ndi mpira olandilana zoti mkazi asekelele?🤣🤣😘🔥🔥🔥
@adilyseif2409
@adilyseif2409 Год назад
Misala singathe
@cliffordbictor7684
@cliffordbictor7684 Год назад
Mdyangu sakugwira ntchito kunja kwa banja kkkkkk
@user-de2wm3vh7u
@user-de2wm3vh7u Год назад
Akuti akausumane adyangu😂😂😂😂😂
@ismailfelera-vp8ck
@ismailfelera-vp8ck Год назад
Bwino ndi nyumbazo zingwa kumeneko kkkkkkkkkk
@lusayongosi6733
@lusayongosi6733 9 месяцев назад
Komatu shoko-shoko
@DorcusDhuka-th8vi
@DorcusDhuka-th8vi Год назад
Queen umandiwaza
@adilyseif2409
@adilyseif2409 Год назад
Mleremba kuimba matafare
@PostanNkhoma-ql4if
@PostanNkhoma-ql4if Год назад
Mumantha madolo keep it up
@giftmarko5239
@giftmarko5239 Год назад
mlelemba number 1umatha
@IsaacBenala-hv4uv
@IsaacBenala-hv4uv Год назад
Keep it up guys we love you and I support your comedys for ever
@user-wd1zq5pj6l
@user-wd1zq5pj6l Год назад
Mulelemba umakana 🔥🔥🔥🔥🔥
@davenchimadzi6529
@davenchimadzi6529 Год назад
Zomba Chingale 😂😂😂 ndkumva kukoma kuno gayz
@lekenstima6308
@lekenstima6308 Год назад
Wakumudz
@stainleyhope9848
@stainleyhope9848 Год назад
😂😂 eti kakota
@maliyadaitoni
@maliyadaitoni Год назад
Chipwanya alipo
@rashidampinjira3923
@rashidampinjira3923 Год назад
🤣🤣🤣🤣 shokoshoko koma
@user-mc7iq8uw2v
@user-mc7iq8uw2v Год назад
Fire guys 😂😂😂😂
@veromalawi8768
@veromalawi8768 Год назад
Koma ashokoshoko mumaziyamba dala😂
@user-dd5zu8zp1b
@user-dd5zu8zp1b Год назад
Shokoshoko ukuwayambiradala akadzako bcz ufuna uwatole mkwamwa choringa udzidya kwini .
@giftbeka3667
@giftbeka3667 Год назад
Imwe mutenga matenda
@RuthRuth-jb6ko
@RuthRuth-jb6ko Год назад
Adyangu akupita Kwa anambewe
@lucysangano1891
@lucysangano1891 Год назад
Aagenda ndi nsima🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 Год назад
Kumuputa zimayi kumuuza za mitala 😂😂😂😂
@SkeverChiweza-fc6fs
@SkeverChiweza-fc6fs Год назад
So interesting
@yassinrashid7012
@yassinrashid7012 Год назад
Ka hule ka khwini🤣
@user-de2wm3vh7u
@user-de2wm3vh7u Год назад
Komatu mulelemba😂😂😂😂
@ibrahimdyman4356
@ibrahimdyman4356 Год назад
😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊
@ephraimbanda9813
@ephraimbanda9813 Год назад
Mmatha guys
@petersomiwa8986
@petersomiwa8986 Год назад
Ashoko shoko ndi deal
@hassanmussa1356
@hassanmussa1356 Год назад
Koma Mlelemba ndiolakwisa,simunthu basi
@Abdul-azizTawakali-cq5xw
@Abdul-azizTawakali-cq5xw Год назад
Mdyangu wapita tizamuona after winter
@giftbeka3667
@giftbeka3667 Год назад
Wandundu
@dbrohoffical-lt4td
@dbrohoffical-lt4td Год назад
😂😂😂 keep on guy's mumakwana mumam'vetsa seke seke
@ibrahimjackson-cg6tc
@ibrahimjackson-cg6tc Год назад
Kkkkkkk😅😅😅😅
@marthastima3864
@marthastima3864 Год назад
❤❤
@JohnChibalo-wf8gr
@JohnChibalo-wf8gr Год назад
Eeeee akharupa mwakumanapo sewero ndilachikhalire ntchito iripo ndipo kusogoko kukufunikanso muone kumbali ya izi zikutchuka zasatanikizi mutiyikireso chiphuzinso chilimbikinso kopangira achinyamatawa asamalowelere .kumanso chilimbikiso podalira mwamulungu taunikiraninso mbali zimenezo.
@user-fj7kz4cr2b
@user-fj7kz4cr2b Год назад
Nkhani ija ashokoshoko uku
@eliasmtonga8900
@eliasmtonga8900 Год назад
😂😂😂kakote
@lasmomasalaza
@lasmomasalaza Год назад
Kodi a Shokoshoko? Munatenga Mkazi Ali ndi misala kale? Kapena tiziti kalelo analibe chikondi chotere?
@Martha1436
@Martha1436 Год назад
Koma banja la a Shokoshoko?
@brianmakeke7011
@brianmakeke7011 Год назад
Shokoshoko kuputa
Далее
MDYANGU COMEDY SERIES..26/05/2023..+265883106798
28:23
Malawian Short film..Atambwali.2024
7:28
Просмотров 10 тыс.
MFUMUKAZI COMEDY SERIES...30/11/2022
27:23
Просмотров 39 тыс.
BON KALINDO LERO PA 9 SEPTEMBER 2024 |
17:43
Просмотров 8 тыс.
MDYANGU COMEDY..12/05/2023..FLORA SUYA..+265883106798.
30:49