Тёмный

MFUMUKAZI COMEDY SERIES..09/08/23..FLORA SUYA +265883106798 

MPUNGWE-PUNGWE MW
Подписаться 65 тыс.
Просмотров 42 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 149   
@GOEMENGONDWE
@GOEMENGONDWE Год назад
😂😂😂mafuneya wabwera tiva zambiri kkkkk
@AvailChimeta
@AvailChimeta 5 месяцев назад
Nafuneya ndi wa mabonyo 🙌🏼🙌🏼
@maundegift4851
@maundegift4851 Год назад
Anafureya sangapeze banja chifukwa mabodza🎉🎉🎉🎉
@clesheinvestments
@clesheinvestments Год назад
Komatu Mfumukazi ulemu wavuta kwa Malume Giling'ande. Nanunso a Giling'ande kudedeluka lero mwazionatu. A Giring'ande muuzeni FARAI ndikubwera kudzamanga naye Banja basi Keep it up Guys mukutisangalatsa kwambiri
@AnnieJackson-m6d
@AnnieJackson-m6d 9 дней назад
Eshiii apadela mulimakani😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@lukebanda2578
@lukebanda2578 Год назад
Nafuneya alanditsa mwamuna
@cathychimombo6884
@cathychimombo6884 Год назад
Koma mfumu kazi anakoza ayayyaya
@giftblack7690
@giftblack7690 Год назад
😂😂😂😂😂 koma osanama umu munali bomba I can't wait nex guys mumatha inuyo kkkkkkk from capetown woodstorck love you guys keep it up
@bysonsongola4373
@bysonsongola4373 Год назад
Guys mwandisia opanda mau anafuneya yaalakwira Bwana kalankaka apana Basi after Fallai atayamba kuziona okongola kenaka kumuonetsa kuti nao ndi dolo akumuzdi keep it up More fire
@StewartWitika
@StewartWitika Год назад
Mfumukazi mumakwana , awuzeni amvesetse kuti kuli amuna ogwirika more 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@IssahChiponda
@IssahChiponda Год назад
I love you people so much continue this love all you comedy
@crytonbizweck5140
@crytonbizweck5140 Год назад
😂😂😂😂zikuonesa ngati mfumukazi yakwiya giling'ande paulendo,big up guys from kzn,durban
@JohnChibalo-wf8gr
@JohnChibalo-wf8gr Год назад
Asaaaaa lululuuuuuu mfumu nkadzi mfumu nkadzi mr shop rite lathapo anafuneya pepani zavutapo mwachedwa mutalawira .farayi walanda .😅next week kuli moto buuuuu😅
@kondwanimwamba6907
@kondwanimwamba6907 Год назад
Farai mukuonjedza, sizikubeba
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 месяца назад
I love you everyday I can watch ❤❤❤
@tobiousmtenje139
@tobiousmtenje139 Год назад
Muuze asayerekedwe man Tee,asazimve mutenge akhale Mrs Tobias kalanka
@johnsondamson6145
@johnsondamson6145 Год назад
Kalamka ndikumuona tatawina chigayo kkkk
@alinafesawasawa3905
@alinafesawasawa3905 Год назад
I love you my people ❤️. Keep the fire 🔥 burning 🔥 ♥️
@HalimaDaud-dd2un
@HalimaDaud-dd2un Год назад
Mamuna ogwilika 😂😂😂 ai zikomo
@isaacmussa2942
@isaacmussa2942 Год назад
😂😂😂koma mfumukaz mpaka matuvi awo azikakambirana uko kkkkkkkk ayi zikomo
@mrscharleswebster6192
@mrscharleswebster6192 Год назад
Wow...chitseko chapakhomo achikonza chakongora❤❤
@anniewhite3497
@anniewhite3497 Год назад
Mfumukadzi ndi nkhani zina Abale😂😂
@SarahChitsulo-w6x
@SarahChitsulo-w6x Год назад
Farai mpakana nduna😂😂😂😂😂
@SquareBoma-vl2rj
@SquareBoma-vl2rj Год назад
Big up guys, mumakwanira ndipo Madam Flora apa mwafikapo. May God see you progressing into big industry
@ChisolaKim
@ChisolaKim Год назад
Nice
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 месяца назад
Padera wapondedwa ndi mukazi😂😂😂😂
@JohnChibalo-wf8gr
@JohnChibalo-wf8gr Год назад
Kkkkk farayi ndi namoyo unakumanapo moto moto
@JohnChibalo-wf8gr
@JohnChibalo-wf8gr Год назад
Anafuneya mukumva bwanji zomwe zipanga farayi ndi garanka
@abdulkha7810
@abdulkha7810 Год назад
Koma gututu ndi javasoni tikusowani bwanj 😌😌😌😌😌😌😌😌😌😍😍
@lukebanda2578
@lukebanda2578 Год назад
Tobiiiii wapeza Farai
@SarahChitsulo-w6x
@SarahChitsulo-w6x Год назад
Farai mpakana nduna😂😂😂😂😂Ati maloza chani😅😅😅?
@patrickdzombe461
@patrickdzombe461 Год назад
Mfumukazi naye kubweza moto
@harrisonnavayah6480
@harrisonnavayah6480 Год назад
Faya we proud of you falai princess chisulo
@DoshenSulan
@DoshenSulan 5 месяцев назад
Kkkkk kalankaa eee menya bell bwino bwino kkkk
@RonaldGama-gz9ug
@RonaldGama-gz9ug Год назад
Nafuneya iweyo anakozatu chifukwa azimuna akuthawatu sitha khalidwe lakolo ulipeza banja😅😅😅😅
@AbigailMilanzi
@AbigailMilanzi 2 месяца назад
Falai 😂😂😂😂😂 mumakwana mumatha kulakhula
@FlausyMijoya
@FlausyMijoya Год назад
Falai 😂 ayi ndithu zikomo
@NevermindMatemba-bk4eo
@NevermindMatemba-bk4eo Год назад
kkkk iweo umaliona bwanji, ndeno osamapita bwanji? kkkk km banja la mfumukazi eee
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
Fumukazi akuti nanu matuvi anuwo pano ayi,Giling'ande akuti tayimani kaye amvekere ndakhala pansi apa ndakhala pansi akuti iwe ndi kakamila ndithu.Komatu ndadzutsa anthu kuno ndikuseka amuna ogwilika mmanja
@brendawhite6583
@brendawhite6583 Год назад
Kkkkkkkk anafuneya game gada
@ethelsawerengera2140
@ethelsawerengera2140 Год назад
Apa namoyo wakumana ndi nzake fire for fire 🤣🤣🤣🤣
@JohnChibalo-wf8gr
@JohnChibalo-wf8gr Год назад
Anafuneya ndi kadzitape mugululi
@HamidaDaudi-e9e
@HamidaDaudi-e9e Год назад
Waiting for the next week from south Africa
@pybenmbewe8462
@pybenmbewe8462 Год назад
You guys you're 😂😂😂the best keep it up 👍
@JawaadHassan-h3k
@JawaadHassan-h3k Год назад
Mumakwana inu Mrs mukutivetsa kukoma
@lukebanda2578
@lukebanda2578 Год назад
Wina akusamuka basi 😢😅😅😅😅😅😅
@patrickdzombe461
@patrickdzombe461 Год назад
Farai mpaka chibwibwi 😊
@calvinthomson6234
@calvinthomson6234 Год назад
Aaaaaa nafuneya anakonza 😅😅😅😅😅
@richiethomas5084
@richiethomas5084 Год назад
Essence of the warm heart of Africa
@ElizabethKBanda
@ElizabethKBanda Год назад
Koma anafuneya makwana😂 kuyenda monyada kumeneko
@ethelsawerengera2140
@ethelsawerengera2140 Год назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤣😃ati tobii iweyooooo
@gracephiri1203
@gracephiri1203 Год назад
Nafuneya mukazapeza banja muzandidule Chala, kunyanya Inu bodza 😂🤣🤣😂
@mphatsolupiabanda6910
@mphatsolupiabanda6910 Год назад
Kkk ati matuvi anuwo
@ishmaelimranimenk9502
@ishmaelimranimenk9502 Год назад
NafuneyA KKKK NAFUNEYA
@victorbanda9039
@victorbanda9039 Год назад
Mfumukaxi mpaka matuvi anuwo😂😂
@afonsoisaqueisaque8392
@afonsoisaqueisaque8392 Год назад
😂
@dorisbwanali1267
@dorisbwanali1267 Год назад
Chipwanya wantchenatu kkk
@lukebanda2578
@lukebanda2578 Год назад
Mwamuna ogwirika mmanja 😅😅😅😅😅😅😅
@MariumVincent-z4j
@MariumVincent-z4j Год назад
Mfumukadzi ati km iwe ndi mkakamira 😅😅😅😅,,
@yohannkhoma9958
@yohannkhoma9958 Год назад
Farai best actor,koma zabwibwizo sizikubeba
@MercyKondwani-ey7zb
@MercyKondwani-ey7zb Год назад
Kkkkkk watha iwe😂😂😂😂😂😂
@andexnjale1963
@andexnjale1963 Год назад
Hahaha koma falayi kkkk
@mosewallace9717
@mosewallace9717 Год назад
more fire 🔥 🔥
@brinokalemba4503
@brinokalemba4503 Год назад
Nice one Nafuneya
@moyoemmanuel-qi3ef
@moyoemmanuel-qi3ef Год назад
😂😂Mfumukazi more fire
@jhbstreet3846
@jhbstreet3846 Год назад
ndimakupilirani farayi😆😆😆😆
@justicechikuse1443
@justicechikuse1443 Год назад
Kalanka 😂😂 waswa mtima kuno😂😂
@JamesImran
@JamesImran Год назад
Big up my brother and my sister fire 🔥 amfumukazi akwayi gyz kmanso farayi am watching from free state marquard
@CardoJustin
@CardoJustin Год назад
Ine kroostad free state
@ChrissyScot
@ChrissyScot Год назад
True
@SarahChitsulo-w6x
@SarahChitsulo-w6x Год назад
😂😂😂❤❤Farayi 😂😂😂😂😂Farayi chonde 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅❤❤koma farayi ndiye ndiwamakani 😂😂😂😂😂Ati tiktok si tchito 😅😅😅???? Komatu Farayi
@HassanBandah-l4t
@HassanBandah-l4t Год назад
Giling'ande koma ayimva?komaso mfumukazi ali srs kusiya kudya zamu shoprite kkkkk koma yaaaa farayi anakumana nazotu
@abraomarizani-sr6su
@abraomarizani-sr6su Год назад
Yeye
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en Год назад
Mr ShopRite ulendo 😂😂😂😂 next week more 🔥🔥 Malawi
@mrscharleswebster6192
@mrscharleswebster6192 Год назад
Koma nafuneya ndi one😂😂😂😂
@SarahChitsulo-w6x
@SarahChitsulo-w6x Год назад
Farai😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😢😢😢😢😢😢😢😢🤣🤣🤣🤣🤣🤣ati uncle!!?1, uncle!!!!!!2?, uncle,3😂😂😂😂😂😂😂 eeeeee wakumana nazo mfumu kazi woooooyeeeee nonse mumatha
@zaharahassanhassan3214
@zaharahassanhassan3214 Год назад
Kkkkkkk
@AbelMchima-tc5wx
@AbelMchima-tc5wx Год назад
Nafuneya Ali ndi ma qualities ose amzimai odziwa kufalitsa nkhani pamudzi 😂😂😂😂
@FavourTebulo
@FavourTebulo Год назад
Kkkkkkkk koma farai wayaka moto kumudzi kkkk mumakwana guys keep it up,.. Can't wait for next, nagama ndi Mai padera kodi chizake chipitilira? 😂😂
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 Год назад
apadela athetsa bodza lanagama 😂😂😂😂😂
@osmandavie5528
@osmandavie5528 Год назад
Giling'ande anachita bwino kukalowa kuti ena atengele phuziro coz azimayi ukamaletsa zama friends ena samafuna kuvayi
@maundegift4851
@maundegift4851 Год назад
Akalanka apano wagwano nchikondi ndi farai😅😅😅😅
@austinvincent1264
@austinvincent1264 Год назад
Nafuneya nd fire kkk
@justicechikuse1443
@justicechikuse1443 Год назад
Zodiak ya mudzi 😂😂
@abraomarizani-sr6su
@abraomarizani-sr6su Год назад
Akaramka aveka
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 Год назад
😂😂😂😂 falayi wakwiya eish 😂😂😂😂
@VeristarJangasia-s2b
@VeristarJangasia-s2b Год назад
Nafuneya amatha
@marthastima3864
@marthastima3864 Год назад
Kkkk ziliko 😂😂😂
@MegrinaEdson-ub9ts
@MegrinaEdson-ub9ts Год назад
A nafuneya tsopano 🤣
@justicechikuse1443
@justicechikuse1443 Год назад
Eeeeh Farayi apa nde makweshoni chibwibwi 😂😂
@brendawhite6583
@brendawhite6583 Год назад
Kkkkkkkk km falayi
@QADA-D-MW
@QADA-D-MW Год назад
Kom shorpleti imeney ikanankhal ku limbe
@paulinamashilo4014
@paulinamashilo4014 Год назад
Ndaima kale ine !😂😂😂😂
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 Год назад
Koma anafuneya akufunika chibagela chakumaso 😂😂
@kho7676
@kho7676 Год назад
Mfumukazi mamuna mukumusewelesa 😂😂😂
@wezziemzumara5511
@wezziemzumara5511 Год назад
Falai wavuta mumudz mwa mfumukazi
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 Год назад
mamuna ogwilika ndimamuna wanji 😂😂😂😂😂
@marianjeleka900
@marianjeleka900 Год назад
Kwachema 😂😂😂
@FaziraKapande
@FaziraKapande Год назад
Mumakwana people ❤❤❤
@jacquelinekamba1322
@jacquelinekamba1322 Год назад
Kodi imaonetsedwa liti ndipo nthawi yanji?
@hastingsmdindo627
@hastingsmdindo627 Год назад
Koma timilandu pabwalo paja tibwererenso bwa
@ChimundaoAndrew-gh5nl
@ChimundaoAndrew-gh5nl Год назад
Mbambande
@SarahChiwalira-ox3zg
@SarahChiwalira-ox3zg Год назад
Falai anabwera kudzakhala
@miraclechibwana9498
@miraclechibwana9498 Год назад
Farai u the best..tik tok kkkkkk
@pempheroraynnoxmpesi8713
@pempheroraynnoxmpesi8713 Год назад
umumu mabanja sachedwa kutha nde bolanso amu mdyangu amalimba😀😀
@agnessjuttah7491
@agnessjuttah7491 Год назад
Kkkkkk
Далее
Handsoms😍💕
00:15
Просмотров 4,8 млн
MDYANGU COMEDY..19/05/23..Flora Suya +265883106798.
26:41
KADIATOU MISQUINET ÉPISODE 2
32:11
Просмотров 91
Tikuferanji 12 October 2024
26:10
Просмотров 18 тыс.