Komatu a Mdyangunmutionetsa. A Nepman mwalepheratu kuyankha funso. Akuti Kodi ku Phanzi lanulo kulibe Chala chachifupi? 😂😂😂😂😂😂😂 Keep it up Guys mukutiimilira
Mlelemba it's too much...he is good acting koma he makes it beyond and boring..he needs azipereka mpata kuti ena azilankhulako otherwise it brings interest down
Kkkkk koma Nepman ai ndthu 😂 aMdyangu nde ana akungobwera mututumukatu atadzadza bus 😂 Gani nde ya Junior Mdyangu yamukwana 😂 Mlelemba nd best actor off course koma kulongolora too much akumafika pobowesa coz akumatenga nthawi yaitali nde pls konzaponi ndthu pamenepa