Тёмный

MFUMUKAZI COMEDY SERIES..24/07/24..Flora Suya's👉+265883106798 strictly for purposes only. 

MPUNGWE-PUNGWE MW
Подписаться 65 тыс.
Просмотров 45 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 187   
@raytavares2256
@raytavares2256 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂😂😂Hilarious 😂hilarious 😂😂😂😂😂Hilarious " delete the car and the". Namoyo was a star today, her acting with mfumukazi in the pang village is fantastic.
@danielantoniomsutu8736
@danielantoniomsutu8736 2 месяца назад
Let's wait and see how mr Padela acted on the mzungu 😂😂
@FynessMasache
@FynessMasache 2 месяца назад
😂😂😂🎉
@LYDIAPHIRIKUMALA
@LYDIAPHIRIKUMALA 2 месяца назад
Kkkkkk koma yalero inali bwino chani ulemu upite kwa namaoyo wapeleka malangizo abwino kwambiri gututu ndi jamasoni sazatheka ndithu
@jackbello2170
@jackbello2170 2 месяца назад
Zikomo kwambili ndaseka Jemasoni ndi Gututu my Namoyo plus vizungu 😂❤
@peterkanjoma2601
@peterkanjoma2601 2 месяца назад
Palibe ndaluma ine 😂😂 Proudly lomwe
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 2 месяца назад
Kkkkkkkkkkkkkk koma gututu ndi jamasoni mmmm mukumuonerera namoyo
@FletcherWysonJika
@FletcherWysonJika 2 месяца назад
Kkkkk akuti ndramazi tigawane zabwera ndi nzunguyu
@TsuzenThomas
@TsuzenThomas 2 месяца назад
Namoyo malangizo aulele kwa Mfumukazi sopano 😂 Giling'ande kuchipinda kujatu kunali chakudya chabwno msangala zimenezizi 😂 Jamason nd Gututu munabwera ngat coming 😂😂😂
@hafeezismailnsamala8812
@hafeezismailnsamala8812 2 месяца назад
Chakudya chili kuchipinda chakhodzedwa kale 😂😂😂😂😅😅😅😅😅😅😂😂😂🎉🎉🎉🎉🎉 Mfumu mkazi ❤❤❤❤❤
@TsuzenThomas
@TsuzenThomas 2 месяца назад
Noliyeka zikwama zithera mnjira ndthu 😂😂 padera at umazitama mmudzi ulimbane nd zizungu kumeneko 🤣🤣 koma Mfumumuna zipongwe😂
@Mamaza-tr6zi
@Mamaza-tr6zi 2 месяца назад
Mfuku kazi malangizo anamoyo mwagwilitsa kale ntchito 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@ChifundoSikelo
@ChifundoSikelo 2 месяца назад
Zoonadi
@TIYAMIKEEMMANUELPHIRI
@TIYAMIKEEMMANUELPHIRI 2 месяца назад
Eya as soon as possible 😂😂😂
@CollinsLingu
@CollinsLingu 2 месяца назад
😂😂😂😅 timafuna kupanga pass away koma gututu ndi Jameson
@iamcrakie
@iamcrakie 2 месяца назад
Ati eyaa khoti liime😂😂
@BerthaNoniwa
@BerthaNoniwa 2 месяца назад
Namoyo ndi one ❤❤ km joswa wasowatu
@ChifundoSikelo
@ChifundoSikelo 2 месяца назад
Namoyo yemweyoooo😂 Nankungwi wathu..
@SquareBoma-vl2rj
@SquareBoma-vl2rj 2 месяца назад
Koma Jamason ndi Gututu eeeee inuyo ndiye kayaaaa kkkkkkk
@DaveSitolo
@DaveSitolo Месяц назад
Eish zidakwaa 😂😂 ati rest peace
@Gorilla-k8e
@Gorilla-k8e 2 месяца назад
Mr padela ndi 1 ma guys 😂😂😂😂😂😂😂
@MlengaFrank
@MlengaFrank 2 месяца назад
Ati khumba zozipedza mwagundika nadzotu 😂😂😂😂😂😂
@shakajudahTV
@shakajudahTV 2 месяца назад
Wavuta kwa mfumu kazi 😂😂😂😂😂😊
@PreciousJecky
@PreciousJecky 2 месяца назад
Kkkkkk padera maso ndi maso ndi mzungu🤣🤣🤣 Nde kuli Jemason nd Gututu🤣🤣🤣 opanda iwowo Mfumukazi singakome
@baldwinnjilika5070
@baldwinnjilika5070 2 месяца назад
That was really nice 😊
@pybenmbewe8462
@pybenmbewe8462 2 месяца назад
Job well done 👍 excellent 👍 keep it up 👍
@FannieChadabwa
@FannieChadabwa 2 месяца назад
Komaso mfumukadzi ndinu ophuzila😂😂
@BensonLitta
@BensonLitta 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂 next please iyi inalibwino kwambili tikhulupilira inayoso ikhala yokoma❤❤❤❤❤
@JamesWandari
@JamesWandari 2 месяца назад
Kkkkk ayi guttural ndi jamson kk
@NelsonRight-zf8bz
@NelsonRight-zf8bz 2 месяца назад
😂😂😂kkkkk koma next padela yamukulila
@EsteryHassan
@EsteryHassan 2 месяца назад
Kkkkkkk giling'ande ati tsalani muzilamvula zizingu❤❤❤
@MathewsBanda-s4s
@MathewsBanda-s4s 2 месяца назад
Mfunukaz inandiwaza maka jemason ndi gututu ali bho❤❤❤❤
@giftbanda7690
@giftbanda7690 2 месяца назад
Padela akuti Iman kaye 😅😅😅😅 can't wait next week
@brendawhite6583
@brendawhite6583 2 месяца назад
Km Jamison ndi gututu 🤣🤣🤣🤣🤣
@christinaibbu4339
@christinaibbu4339 2 месяца назад
♥️♥️♥️♥️♥️♥️🥳🥳🤣🤣🤣🤣
@ThomasiSalijeni
@ThomasiSalijeni 2 месяца назад
Jamason ndi gututu mwayigwira big up guys
@StatesManP-zq4ic
@StatesManP-zq4ic 2 месяца назад
😂😂😂😂😂 Ya PA 31 tikudikila tidzamve Mr padera akuthimula MA verb MA noun MA pronoun MA adjective kkkk mzungu mnyumba mwa apadera I know ndi bwana wamai padera
@hudsonjmaonga5433
@hudsonjmaonga5433 2 месяца назад
Kkkkkk ngat akudya pano it's my me
@merviskhongonyowa5621
@merviskhongonyowa5621 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂thank you thank you I am passing away 😂😂😂😂😂😂
@puxyyachina
@puxyyachina 2 месяца назад
😂😂😂😂 Koma yaah
@FrankAlli-g6i
@FrankAlli-g6i 2 месяца назад
Jemason ndi gututu umakwana 😂😂😂😂😂😂
@eunicekapindula5128
@eunicekapindula5128 2 месяца назад
Koma tchuzi Kaye, nyumbamo mtengowo utanimo Mfumuchaje 😅😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@TriciaMakolija
@TriciaMakolija 2 месяца назад
Kom gututu ndi jemason sadzathek at lero lilime lipwetek ndi kuyankhul chizungu
@HopeMachokez
@HopeMachokez 2 месяца назад
Km padela ayakhula chizungu😂😂😂
@YankhoBaysome-fd3mx
@YankhoBaysome-fd3mx 2 месяца назад
😂😂😂 tikugule more beers 🍻 😂
@OwenPiasi
@OwenPiasi 2 месяца назад
😂😂😂😂 zilibwino kwabac
@grantmagombo6465
@grantmagombo6465 2 месяца назад
Pagolin amudyetsa mbazi mfumukazi kkkkk
@HopeKeyz-pr5pw
@HopeKeyz-pr5pw 2 месяца назад
Padela walandila alendo 😂😂😂 koma simmene kulili
@giftbanda7690
@giftbanda7690 2 месяца назад
Agili...tabwerani chakudya chili kuchipinda kuno kkkkk hahaha Banja ilili limandiwaza kkkkkk😅😅😅
@ephraimchakwiya6756
@ephraimchakwiya6756 2 месяца назад
Eyooo tiyeni tiyeni tiyeni 😅😅
@georgekchimwaza6838
@georgekchimwaza6838 2 месяца назад
Namoyo ❤,A mfumukazi mwayamba zabwino..mfumu izikhara ndi chisazo chabwino drama iya ❤❤
@ThenfordNgomwavespa
@ThenfordNgomwavespa 2 месяца назад
Km achiphwanya kumunyoza noliyega
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 2 месяца назад
Namoyo ulendo uno wokha ndiyankhule ndikumwese fanta hhhhh
@SquareBoma-vl2rj
@SquareBoma-vl2rj 2 месяца назад
Munthu aziphunzira komanso kuphunzitsika, Mfumukazi mumakwanira. Learning nkuzichita pompopompo eeeeeee mbambandeee
@titusmasala3560
@titusmasala3560 2 месяца назад
Ati kwabwera shatapu😂😂😂
@TrinityBonjesi
@TrinityBonjesi 2 месяца назад
Kkkk namoyo wandiwaza kkkk paka kuwaphuzitsa mfumukazi chikharidwe kkkk iwe Ndi 1
@PeterBendeka
@PeterBendeka 2 месяца назад
Wamisala anaeona nkhondo namoyo wamanga mabanja ulemuwanu madam suya featuring namoyo from Joburg
@MICKSONMSAMPHA
@MICKSONMSAMPHA 2 месяца назад
Zoona zimenezo
@AlinafeMangazi
@AlinafeMangazi 2 месяца назад
😂😂😂😂 uzapanga regrace🔥
@WilstonPesuzgo
@WilstonPesuzgo 2 месяца назад
😂😂😂😂😂 Koma jameson ndi gututu simuzatheka
@eunicekapindula5128
@eunicekapindula5128 2 месяца назад
Namoyo Namoyo Namoyo😅😅😅😅iwe nde unafikatu asaah😅
@EstherandElvisJames
@EstherandElvisJames 2 месяца назад
Komatu chiphwanya ndi sasoka😂😂😂😂ndlibe mau
@MbigwaniKhun
@MbigwaniKhun 2 месяца назад
Ndie mwati msanje ya Padera yo saona ngat mzunguyo kufuna mkazi yo??😂😂😂
@JayMilazi-fv6px
@JayMilazi-fv6px 2 месяца назад
Koma nyumba ya mfumukazi pakhomopo galimoto ikhoza kulowatu😂😂😂😂
@MinoriaMitulo
@MinoriaMitulo 2 месяца назад
😂😂😂 eeeh km padera
@EvelynMasamba
@EvelynMasamba 2 месяца назад
😂😂😂😂koma gututu ndi Jameson sazathekaso ❤❤
@BronwynFlink-m7v
@BronwynFlink-m7v 2 месяца назад
Mfumumuna ati padera tsala uzikutumula ma noun ndma verb kkkkk
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
@dhaoudhiabedinegomaseko2363 2 месяца назад
Koma ya akuti his wife is mfumukazi and he is mfumumuna😂😂😂😂😂😂😂😂
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en 2 месяца назад
Wina wasazika osafuna😂😂
@Imranasedi-zw7cg
@Imranasedi-zw7cg 2 месяца назад
Ndilibe mawu koma kuseka basi kkkkk
@PeterBendeka
@PeterBendeka 2 месяца назад
Namoyo#1 ndakunyadila wandilangila NSO wanga
@nicholasshema9016
@nicholasshema9016 2 месяца назад
Kkk mwabwera kudzakhara gyz padera ayakhure chizungu
@peternashyo9850
@peternashyo9850 2 месяца назад
Malangizo abwino kwambiri, Namoyo umatha
@preciousnjazi7277
@preciousnjazi7277 2 месяца назад
Ati mutu ngat Batile 😂
@PatriciaDafter
@PatriciaDafter 2 месяца назад
🤣🤣 km Padera 🔥
@chipiezabula4080
@chipiezabula4080 2 месяца назад
ATI lero ndipita lilime likundiwawa ndayankhula kwambiri chizungu 😂😂
@grantmagombo6465
@grantmagombo6465 2 месяца назад
Waiting for the next plz
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 2 месяца назад
Koma Jameson ndi gututu sazatheka ndi khani zina kkkkkk
@WysonChimtengo
@WysonChimtengo 2 месяца назад
Namoyo kkkkk chakachino wawina bas
@TrizaMakocha-un4pi
@TrizaMakocha-un4pi 2 месяца назад
Udzapanga rigrace 🤣🤣🤣🤣
@samnhobandaofficial7693
@samnhobandaofficial7693 2 месяца назад
😂😂😂😂 mumakwana guy's 🎉
@lysonchasowa6124
@lysonchasowa6124 2 месяца назад
Deadly combination gututu and Jameson
@RashidOsman-d8l
@RashidOsman-d8l 2 месяца назад
Good ❤❤❤❤❤
@DrolieDongowa
@DrolieDongowa 2 месяца назад
😂😂 koma namoyo kkkkkkkkkk
@petrosmunthali5562
@petrosmunthali5562 2 месяца назад
Namoyo ungokhala mfumukazi😂😂😂
@PociahMack
@PociahMack 2 месяца назад
Namoyo kulimba mtima mpaka nyumba mwa MG 1 kumulangiza
@catherinekavalo2365
@catherinekavalo2365 2 месяца назад
😂😂😂😂mpezeni yemweyo
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en 2 месяца назад
Apumbwa😂😂😂
@nicholasshema9016
@nicholasshema9016 2 месяца назад
m'fumukazi anenepa zao zili pabwino
@halodesilvestregervasio
@halodesilvestregervasio 2 месяца назад
Watching from Tete-Moçambique
@MphayaBen-oz3pz
@MphayaBen-oz3pz 2 месяца назад
Ati tapita uzikawadyesa achapwakowo 🤣🤣🤣🤣🤣 koma guys
@sobbschipoya4100
@sobbschipoya4100 2 месяца назад
somoday called mercy name in mfumukazi and mercy anaoneka akuzuma
@OliveaMapanga
@OliveaMapanga 2 месяца назад
Jamisoni ndi gututu ulemu wanu inuyo kkkk
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂😂 uthane nacho chizungu umazitama ma verb kkk😂😂
@MalaikaLulker
@MalaikaLulker 2 месяца назад
Koma namoyo😂😂😂😂 umakwana
@billymhoni9527
@billymhoni9527 2 месяца назад
Kod jamison ndi mzake ali nkwaoo mu sewelomu?
@JustinWodala-d6p
@JustinWodala-d6p 2 месяца назад
Kkkkkkkl km gututu ndi zakeyo amakwan 😅😅😅😂
@FrankHaruni
@FrankHaruni 2 месяца назад
ATI mfumu muna😂😂😂😂 kom gututu
@edgarmax-pi1bx
@edgarmax-pi1bx 2 месяца назад
Mfumukazi ndi 🔥
@pemphokatembe443
@pemphokatembe443 2 месяца назад
Aweeeee!!!!!😂😂
@MemoriOsman
@MemoriOsman 2 месяца назад
koma akt fumu muna 😅😅
@TshepoModise-xs4qu
@TshepoModise-xs4qu 2 месяца назад
YOh 😂nfumumuna 😂😂😂😂
@EmmanuelMpalagule
@EmmanuelMpalagule 2 месяца назад
Eeeh koma next week padela samukwapula mzungu uja koma
@chiletsobisweck5007
@chiletsobisweck5007 2 месяца назад
Anayikamodi mutu😢😢😢
@AbuduRajjabu
@AbuduRajjabu 2 месяца назад
Kkkkk.koma giling nde
@DJcliffBandakhudzanga
@DJcliffBandakhudzanga 2 месяца назад
Koma mfumukazi inabwela
Далее
ОН У ТЕБЯ ЗА ДВЕРЬЮ!
22:33
Просмотров 470 тыс.
Mfumukazi - 2 October 2024
29:00
Просмотров 50 тыс.
Mfumukazi comedy series 14 August 2024
22:06
Просмотров 19 тыс.
Ana Amasiye
26:33
Просмотров 16 тыс.
Mfumukazi - 19 June 2024
28:00
Просмотров 10 тыс.
Mfumukazi comedy series 21 August 2024
26:56
Просмотров 22 тыс.
ОН У ТЕБЯ ЗА ДВЕРЬЮ!
22:33
Просмотров 470 тыс.