Farai too much mwano😂😂😂 we are missing Mr shoprate pls abwereko ku South Africa. More love from Johannesburg ❤ Mundiuze dera lomwe Mr shop rite afikira ndikumane nawo😅😅😅
Chidwi changa chiri pa kukanidwa banja achisime ndi kuchoka kwa anafuneya komanso kodi amfumu.zinatha bwanji kubwelera kwawo after kuuzidwa ndi farayi kuti giring'anthe kulibe abwalo sitikuchoka moto kuti buuuuuu ❤❤❤❤