Тёмный

MFUMUKAZI COMEDY SERIES ….25/01/2023 +265885694888 let's support them. 

LIKI-LIKI TELEVISION
Подписаться 48 тыс.
Просмотров 43 тыс.
50% 1

The only team in Malawi taking our stresses away please let's sponsor them as much as we can +265885694888 reach out directly to Flora Suya.

Опубликовано:

 

25 янв 2023

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 73   
@user-nj5vu8cd5l
@user-nj5vu8cd5l 4 месяца назад
Nice mfumukazi wafela ShopRite 😂😂😂
@richardmasina5454
@richardmasina5454 Год назад
Akuti ndikuthamangireni, Loma guys 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@harrytepeka8721
@harrytepeka8721 Год назад
Kusinsamfundo che Jemasoni at muzanyozat kolemerakkkkkk
@mdokaamisi7453
@mdokaamisi7453 Год назад
Kkkk taonani mmutumo ngati nyerere zikupita kunsonkhano🤣🤣🤣🤣🤣
@user-hn8pq9lc5i
@user-hn8pq9lc5i 6 месяцев назад
Very good guys 🎉🎉😂😂😂❤❤❤ cute very good guys love it keep it up for us we love your shows always little🎉🎉🎉
@user-hn8pq9lc5i
@user-hn8pq9lc5i 6 месяцев назад
Your right ❤❤❤🎉🎉🎉😂
@chimwemwechilangwe5010
@chimwemwechilangwe5010 Год назад
kanthu nkhama gilingánde anakwatira mfumukazi 😆
@lysonmvula9986
@lysonmvula9986 Год назад
Kkkkkkk Agututu anikumbusa nyimbo ya the legend Phungu Joseph Nkasa tizazindikila bwino pasogolo, keep up the good work mfumukazi comedy series, from Zambia 🇿🇲
@lamzymoyokunyenga4086
@lamzymoyokunyenga4086 Год назад
🤣🤣🇲🇼
@manuelmichael8767
@manuelmichael8767 Год назад
Mfumu kadzi please musawaputsisetu Mr Shoprite apa ndie adaliratu kwambili
@shepardwallani5401
@shepardwallani5401 Год назад
Giring'ande iwe chomwe ukufuna sukuchiziwa kkkk
@robertgbanda3825
@robertgbanda3825 Год назад
Mfumu kazi apandidwa zomwe ayamba kumabera anthu pa in the name of king 🤴
@chiccokaduxybandah2748
@chiccokaduxybandah2748 Год назад
Mukuitha madolo.....
@daviejulius2625
@daviejulius2625 Год назад
Amupoilisa giling'ande a mfumu kadzi 😂😂😂
@madalitsomakawa9708
@madalitsomakawa9708 Год назад
Power of being a lady, kufewetsa mtima wa mamuna.
@benjulius6070
@benjulius6070 Год назад
Komatu guys mulibhooo
@halidiuseni3502
@halidiuseni3502 Год назад
Mukutivetsa kukoma osafoka makosana
@chimwemwechilangwe5010
@chimwemwechilangwe5010 Год назад
hahahaha ati chonde dzikoli lizatha ndipo tizaimbidwa milandu tanenani chilungamo ......😆😆😆 best line ever kkkkkkkkkkk
@charlesphiri9014
@charlesphiri9014 Год назад
Apa ndiye yayamba kubeba keep it up guys charles ku S.A
@CharesNgoma-dk4zh
@CharesNgoma-dk4zh 8 месяцев назад
Tikunyadira kwa mbiri kuno kwathu ku Zambia ma comedy anu
@user-hn8pq9lc5i
@user-hn8pq9lc5i 6 месяцев назад
I love what you said and it's pretty great we love you videos we want you to come to our house and perform please I need a note to match okay I just want you to be from to people
@kelvinkhudze6241
@kelvinkhudze6241 Год назад
This is nice🤣🤣🤣🤣 Giling'ande🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@planbkhamisolo2734
@planbkhamisolo2734 Год назад
Mukuitha ndithu 🔥🔥😂😂😂😂😂
@filipeinocenciolucianoluci4877
zilibwino zedi
@marychilima1661
@marychilima1661 Год назад
I salute you my pipo and God bless you all 🙏
@antonychika15
@antonychika15 Год назад
Aja ndiuku kkkkkk (Mr. Shoprite)
@patrickgawani5449
@patrickgawani5449 Год назад
Komatu padera
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 Год назад
Motooo buuuuuu pitilizani mumatisangalatsa ndikuphuzitsa
@jameschibisa1433
@jameschibisa1433 Год назад
Mumakwana I like it
@mlezanyirenda2815
@mlezanyirenda2815 Год назад
Kurora nthawi yomweyo Demand😂
@rashiddeula5715
@rashiddeula5715 Год назад
Koma Giling'andeeeee ayayayaaya
@esteryndau8546
@esteryndau8546 Год назад
Koma mr shoprite ur number one
@thimzymastermind9421
@thimzymastermind9421 Год назад
Apadera nsanje yawo yoononga kkkkkk
@chitimbethegreat8560
@chitimbethegreat8560 Год назад
Giling'ande ukufunanonso chiyani kwa Namoyo remember mapanga awiri abvumbwisa
@evancechipeta1250
@evancechipeta1250 Год назад
Gilingande ndi wani
@winniendalama2926
@winniendalama2926 Год назад
Iii kuchita kuona kuchedwa kuti episode Ina ituluke😂😂😂 zilibwino magaye
@SteveCharles-bb1mr
@SteveCharles-bb1mr Год назад
Nice one
@chitimbethegreat8560
@chitimbethegreat8560 Год назад
Amfumukadzi akufunika makofi kudyera udindo sikumeneko
@sofiasofia8561
@sofiasofia8561 Год назад
Kkkkkkkk km agiling,ande
@benjulius6070
@benjulius6070 Год назад
Butterlion
@erastokawina4550
@erastokawina4550 Год назад
😂😂😂mai kalaka zawo zayan'ana ku ngolo
@gracephiri1203
@gracephiri1203 Год назад
Amfumukazi kuifela Kwa giling'ande
@beatricedickson404
@beatricedickson404 Год назад
Zokongola mwava
@jamilamalinga9704
@jamilamalinga9704 Год назад
Kkkkkkkk apedela ayambano msanje eish zovuta kwabas
@hamzahrabanah1902
@hamzahrabanah1902 Год назад
Kkkkkk koma mfumu kaz
@halidiuseni3502
@halidiuseni3502 Год назад
Giling'ande mbambande
@giftjamali8204
@giftjamali8204 Год назад
Hahahhaa koma madolo inuyo apa giling'a.nde aberedwa
@omegamtokoma3122
@omegamtokoma3122 Год назад
Hahahah wazishosha
@shaibojames4369
@shaibojames4369 Год назад
Ulemu wanu makosana
@edwinlerwill6978
@edwinlerwill6978 Год назад
Ogulisa mpunga saziwa masamu🤪
@mathiasnyilili3066
@mathiasnyilili3066 Год назад
Koma giling'ande ichi chakoma ichi chakoma pusi adagwa chagada gwilira chimodzi ndasangalala kuti ukhale mwamuna wafumukazi koma nawenso ukuyenera kudekha iyayi nanga kungolora basi tiyeni mnyumba 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 ndimakunyadirani ndimamva kukoma mmutimamu ndikamaonera ndithu
@mercygalatiya1879
@mercygalatiya1879 Год назад
Good Job guys 😂
@lastlevel1999
@lastlevel1999 Год назад
Mfumukaz uyu ndimavuto ati mesa ndine mfukaz
@romsa4590
@romsa4590 Год назад
Mlibho magaye
@edythnamponya7701
@edythnamponya7701 Год назад
Namoyo🤣🤣🤣
@marthastima3864
@marthastima3864 Год назад
👍👍👍👍
@mbirinyirenda7482
@mbirinyirenda7482 Год назад
Kkkkkkj
@evancechipeta1250
@evancechipeta1250 Год назад
1kg 1350 half 350 kkkkkkkkk
@arfredidamuson1864
@arfredidamuson1864 Год назад
Koma mfumu kazi mukudya dzauleretu kkkkkkkkkk
@shukranphiri3958
@shukranphiri3958 Год назад
Giling'ande Kkkkkkk
@user-kh2di7pj4x
@user-kh2di7pj4x 9 месяцев назад
😅
@wicklyroshet9827
@wicklyroshet9827 Год назад
Giling'ande wawina mfumukazi eishhh koma ndikutha kuona mfumukazi wamuyenda double kick Giling'ande ndicholinga choti atenge Njinga kkkkkk koma zithera ma penalty ndithu
@adrianzulu4053
@adrianzulu4053 Год назад
Kkkkkk
@georgemsangu
@georgemsangu Год назад
Ziribwino
@yassinwisck4178
@yassinwisck4178 Год назад
Hhhhhhhhhhhhhhhhhhhhh
@mlezanyirenda2815
@mlezanyirenda2815 Год назад
Kkķkkk giling'ande wawina mfumukazi 😂😂 bora kusakhale kutengerako njinga ya karanka😋😋
@goliatbanda2818
@goliatbanda2818 Год назад
Nice one
@doreenverias5650
@doreenverias5650 Год назад
Kkkk
Далее
MFUMUKAZI | 31 JULY 2024 pa Times TV
28:28
Просмотров 27 тыс.
кажется, началось
00:45
Просмотров 1,7 млн
Help Barry And Barry Woman Scan Prisoners
00:23
Просмотров 3 млн
MFUMUKAZI COMEDY SERIES...30/11/2022
27:23
Просмотров 38 тыс.
MFUMUKAZI COMEDY SERIES..11/01/2023.
28:08
Просмотров 33 тыс.
MFUMUKAZI COMEDY SERIES...03/05/2023..+265883106798
29:14
кажется, началось
00:45
Просмотров 1,7 млн