Nafuneya pano wasinthadi,Unasiyadi miseche ija. Ndiye mwati chi Love chikumveka English,Masamu akukana?. A Maliro pezani Njira yabwino yothetsera mavuto anu ndi Duncan. Maliro be responsible Father osati za manja LENDE zakozo. Learn from Mr Kalanka, nthawi zonse amakhala ndi zochita za phundu kwa Iwo eni komanso ku Society. Dziko likufunika Anthu ngati achina Kalanka osati Anthu ngati achina Maliro omadikilira kukaba Cha Bwalo kwa Mfumukazi. One of my best MFUMUKAZI ndi iyiyi keep it up Guys. We love you all.