Тёмный

MICHAEL USI KUDYA PA CHIYIMILIRE ONELANI | 

DZIWE TV
Подписаться 34 тыс.
Просмотров 10 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

27 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 119   
@HamiltonwaNamuwah
@HamiltonwaNamuwah 2 месяца назад
Uku akuchitaku ndiye kuwuseweretsa udindo wa u VP. Izizo anachitapo Bakili Muluzi ali pulezidenti komano anadzudzulidwa. Ndiye uyunso akuyenela kusiya izi chifukwa cha udindowu . Asazitengele mmasewero ayi .
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 2 месяца назад
Ndiye zofunikazo adziwabwanji muyezo wamavuto womwe anthu alinawo ngati sangapange choncho keep it up vp .
@HumphreyKachepa
@HumphreyKachepa 2 месяца назад
Guy we need to be serious us Malawians munthu ngati uyu akupanga zopusa BT ilibe madzi wina akukwera njinga uku dziko likuvutika guys kumalawi tikulephela kutukuka chifukwa we have time to waist
@RoseGondwe-x5c
@RoseGondwe-x5c 2 месяца назад
God hiding himself in simplicity that's what Jesus was doing he didn't behave like he is the son of God just simple ❤
@estherkambewa7791
@estherkambewa7791 2 месяца назад
Akutionetsera chikondi, amadziwa mabvuto komaso ndi momwe boma lingapezele njila zotukulira ma business ampamusika
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Nawonso a Chakwera ndia chisiru akungoonerera madrama wa zoti zikuchitisa manyazi ziko sakuona?
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Pepani anthu akuoneka atavala makaka a Utm wa angovazikidwa makakawa si a Utm ndi Chikangawa Utm original inatuluka ku Tonse alliance
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Kunali ma vice president dziko lino okwana 6 komano uchisiru uwu sanapangepo kuyalukatu uku
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 2 месяца назад
Komatu asilikaliwa zikuwanyasa zimenezi. Kodi akuthawa chani mu office yake?
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Ndalama zaboma zikungoonongeka moti akagule mankhwala muzipatalamu kapena ndalamazo zoti akasiye ku fertilizer kuti asike mtengo ayi komano kumangopangira madrama basi
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi 2 месяца назад
Kodi izi nanu mukutanthuzanji, kkk kusowa zochitatu uku. Kodi simukudziwa kuti m'malawi anachenjela pano?
@JosephFerix
@JosephFerix 2 месяца назад
Ndithandize amnzanga Kodi limeneli ndi sewero la Tikuferanji kapena chani?
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 2 месяца назад
Dramma iyi
@francislimbani-jd7ft
@francislimbani-jd7ft 2 месяца назад
This is what we call umunthu...I love every step you are taking keep it up
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 2 месяца назад
Pameneponso Nanu palintchito yoti mungati aslikali akuvutik? anzawo pano akulupha mizinga .
@CathrineKumwenda
@CathrineKumwenda 2 месяца назад
This is your time Mr VP focus
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 2 месяца назад
Koma pa vp akukwana adziyenda adzidziwa kusiyanitsa mariport womwe abweretsera sipalhalanso ma report wonama Kwa president
@GracePhiri-f2u
@GracePhiri-f2u 2 месяца назад
Kodi Iwo VP sayenda NDA mkazi wawo bwanji?
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 2 месяца назад
Mbuzi iyi
@AnthonyChilenje
@AnthonyChilenje 2 месяца назад
Kodi zoti mukuononga misonkho mukuzidziwa??????
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 2 месяца назад
Awatu ngati akutenga u vice president ngati sewero akulakwitsa
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Nawonso akulu akulu a MCP akungoonerera uchisiruwu basi
@OnexAliMwale
@OnexAliMwale 2 месяца назад
Zinthu Zina ndizabwino ndithu koma zikaonjeza zimaonongeka. Asakomedye kwambiri kupanga zimenezi coz amadziwika ndi Drama ndiye zina zikufunika ka control kuti pazikhala kusiyana
@DalitsoDjimo
@DalitsoDjimo 2 месяца назад
Zoona, iyeyu nimunthu wankulu tsopano izizo aueonjeza
@AgnessChapinga
@AgnessChapinga 2 месяца назад
Kod akazi ake samayenda nawo bwanji? Kut aziona kuzerezeka kwa dad awo kkkk kkkk ndakomoka ine😅😅
@happychimwemwe-1805
@happychimwemwe-1805 2 месяца назад
Pa Chilima sungafike
@Allan-bk1
@Allan-bk1 2 месяца назад
Alikutari kwambiri
@AllanJentala-g6h
@AllanJentala-g6h 2 месяца назад
Iwe ndi kape ase ngat usi ndi chilima onse ndi atsogoleri basi zili ngat kufunaniza kamuzu ndi Bakili anthu tonse sitingakhale ofanana
@ThokoLungu-tq6pw
@ThokoLungu-tq6pw 2 месяца назад
Olo kutalitali
@IbrahimUseni-p8f
@IbrahimUseni-p8f 2 месяца назад
What is the main purpose of doing these toors,had it been that that they ware not correcting allawances it was good,this is one way of wasting resources,,,, shame on you
@CharlesPhiri-ds1rk
@CharlesPhiri-ds1rk 2 месяца назад
Hummillity bro!!!!
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 2 месяца назад
Kkk vice president woyamba kudya Sima murestraunt ndi anthu wamba
@edenbelievemseteka5197
@edenbelievemseteka5197 2 месяца назад
Even ine sindikudziwa kuti tanthauzo lake ndichan? Kutukula dziko uku? Or drama?
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Musiyeni akuona ngati u vice president uwu ndiwamuyaya
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 месяца назад
Kodi mbunzi imeneyi akuti usi alindichipani panopa kaya komwe akulowera akukuziwa ameneyu kapena ndimisala basi angoyendayenda kusowa zochita ndalama zaboma zabowoka kwambiri zoti misongo ya anthu iye zimenezo akuziwa ichi ndichisiru basi
@Allan-bk1
@Allan-bk1 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂😂 ndiwopenga uyu
@ThokoLungu-tq6pw
@ThokoLungu-tq6pw 2 месяца назад
Ikhaletu misala kma 😂😂a
@Nickman-o4t
@Nickman-o4t 2 месяца назад
Kumalawi tachulusa ma drama 😂😂😂
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 2 месяца назад
Palibe sewero apa akupanga zantchito baba
@ChrissyMoyo
@ChrissyMoyo 2 месяца назад
Anthuni mwawonjeza, kutukwana a vp msiyeni mwamva,,akuzichepetsa nanga,
@SimbeyeSimbeye-z7l
@SimbeyeSimbeye-z7l 2 месяца назад
Mizimu yakwiyadi eti😂😂😂😂
@BLESSINGSSTOLO-lt9di
@BLESSINGSSTOLO-lt9di 2 месяца назад
Bambo asikono akupenga ndithu zoti azipase ulemu mmmmh awa ayaluka bas.
@AxonVanjr
@AxonVanjr 2 месяца назад
Kmatu asilikali akanawapanga kalibu akuvetsa chison
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 2 месяца назад
Ameneyo akungoziwonesa kuzibwezizakezo paja ndi wa akazitu ameneyo koma apenga misara
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 месяца назад
Kukhala makola na wanthu namutemwa Usi vp wakwamba kupanga vya nthena,
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 2 месяца назад
Chilima ankayemda ndi mkaziwake ? Bodza lanulo .
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 2 месяца назад
Suzafikapo ada pa chilima uja anali achalum
@JimmyMhone-b5p
@JimmyMhone-b5p 2 месяца назад
Asing'anga apeza ntchito chakra chino tiziona chaka chino
@ThokoLungu-tq6pw
@ThokoLungu-tq6pw 2 месяца назад
Kma bamboo asikono kkkkkk
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira 2 месяца назад
Koma zimu wa chilima wayamba kupengetsa Athu
@Littlefair7
@Littlefair7 2 месяца назад
😂😂😂😂
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 2 месяца назад
chitsiru ichi yudasi siwuzaupeza utendere iwe chigawenga chinzako chapita kukalapa machimo akupha koma yehova sikulola zoipazo
@omarlux3434
@omarlux3434 2 месяца назад
Athu chitukwanila inu ndichan muthu uksmatukwana athu amaziwa kuti uemu ndimuthu mulibemo
@AkimumusaMusaakimu
@AkimumusaMusaakimu 2 месяца назад
Kk Za ma Drama zija 😊
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 2 месяца назад
Koma ya! Dziko la mkaka ndi uchi. Chonnzuna chifuma ku mwini mphanvu. 😁😁😁
@kondwanivyalema9449
@kondwanivyalema9449 2 месяца назад
Kamunthu kofupika ndi nzeru zomwe kamunthu aka kabalalika mwazi wachilima ukuwazunguza anthu amenewa mzimu wa Chilima SKC WHERE EVER YOU ARE KOMA DANDAULO BWANA CHILIMA MUNATITENGELA NASONGOLE PAKATI PA TILIGU MANGANYA AKUSOKONEZA ZINTHU KOMA MAYI KALIYATI ACHIGWILA BWINO CHIPANI NDI FREDDO KISS K
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 2 месяца назад
Koma a police anuwa aja? Bwanji nawonso wosawagulira mbale zawo?
@ChrispinTaombe
@ChrispinTaombe 2 месяца назад
Koma udindowu wapita kolakwika zedi Moti iye akujambulisa sewero anthu sakuziwa?
@SifatiMoses
@SifatiMoses 2 месяца назад
Ifa ya anthu nine, siyamasewera ndi misala iyi,, tsiku lina azavura zovala inu muvekere boma ili. Dziko la malawi asogoleri ake ndi zisiru ngati awa.
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 2 месяца назад
Kkkkkkk
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 2 месяца назад
upenga misala iwe ndithu
@lazaruschitsamba8394
@lazaruschitsamba8394 2 месяца назад
uyu ndiye akupanga politics wosati zamaliro akupanga enawo
@giftpeterbanda6274
@giftpeterbanda6274 2 месяца назад
Life is simple
@Jibsan-t2f
@Jibsan-t2f 2 месяца назад
Kdi imfa ya 9.Amalawi mumaiganizira bwanji athuwatu ukuku ndi mizimu ikuwasusa nayamba kuzerezeka nazo iziii BIZIWIKI uyu mmmm uwuwu siumuthu mwene
@isaacmanjele6487
@isaacmanjele6487 2 месяца назад
Anthu akadana ndi munthu chilichonse angachite anthu amadana nacho ngankhale zopheka kunzimvesa anthu munthu akamukonda olo atapanga choipa anthu amaombera mmanja ngozi chabe umakhala kwa munthu amene Ali busy kufalitsa udani pakati pa anthu pamene Pali udani palibe chabwino or munthuyo atakhala wakutha bwanji
@BwanaGD
@BwanaGD 2 месяца назад
😂😂😂😂 tikuferanji anambembatu komatu awa kwatsala ndikupega bas
@CharlesPhiri-ds1rk
@CharlesPhiri-ds1rk 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂😂 km usi pachiimilre
@AdamAPhiri
@AdamAPhiri 2 месяца назад
Comedian of the year 2024
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 2 месяца назад
Kkkkkk
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Mizimu ya anthu 9 ija wina ikuwazunza anthu awa zedi
@AishaLeman
@AishaLeman 2 месяца назад
Sindikuonapo vuto apa ulemu wachani munthu Ali ndi njala
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 2 месяца назад
Kenako timva kuti apenga ndi mzakeyo ndithu siza normal izi sure Mwazi wa munthu uja osazauphwekesa guys
@WilliamMasula-cb1mg
@WilliamMasula-cb1mg 2 месяца назад
Kodi malemu Dr Chilima adakakhala oyimba and nkuchitika monga zidachitikieamu pano mukuti adaphedwa ndi ndani? ( not kuti am happy ndi ya anthu 9 aja , inenso ndiokhudzidwa kwambiri) Uzimu ukusowa apa ndichifukwa timangolankhulapo anthufe))
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Asilikali enawa zikuwanyasa komapopeza ndi ntchito ai zikomo
@mcdonaldchirwa3182
@mcdonaldchirwa3182 2 месяца назад
Achitetezo aVP ali pa ntchitoo ya nyooooo
@Paul-q2p
@Paul-q2p 2 месяца назад
Kkk koma izi wapenga munthu tsinamuonepo
@robertchimulomo4885
@robertchimulomo4885 2 месяца назад
Loyalty
@AmosRichieKumbanga
@AmosRichieKumbanga 2 месяца назад
Munthu wakumudzi apindula chani apa
@MabvutoSembo
@MabvutoSembo 2 месяца назад
Apolisi akuzunzika inu eshiii
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Dziko la Malawi lalowa madrama komano ziwani kuti next year tikuchosa zibwana izi
@lastonedwin9144
@lastonedwin9144 2 месяца назад
Komano usi azuza asilikali kwambiri omwe akuyenda nawowo
@edenbelievemseteka5197
@edenbelievemseteka5197 2 месяца назад
😂😂😂koma mzimu wa Chilima si mitsala iyi?
@OmegaMussa
@OmegaMussa 2 месяца назад
Dzilibwino kwambili
@bysongeorge3243
@bysongeorge3243 2 месяца назад
Awatu ndi masanje basi , mtsogoleri wa dziko kukacha adzikhalira kupanga zimenezi.. za drama basi..dziko kulilowetsa chibwana basi..I don't think this is the way to tackle issues affecting Malawi right now...
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 2 месяца назад
Komano zimenezi zikuthandiza chani ku dziko la Malawi???
@WilliamMasula-cb1mg
@WilliamMasula-cb1mg 2 месяца назад
Zibwana ✋
@ChrisjuZiyaya
@ChrisjuZiyaya 2 месяца назад
Chamba chikuwapweteka
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад
VP more fire
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef 2 месяца назад
Kodi asilikaliwo sakuvanjala! Tikuwona akudya yekha, Koma dziko la Malawi lalodzedwa
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 месяца назад
When you are desperate for a vote.
@Allan-bk1
@Allan-bk1 2 месяца назад
😂😂😂😂😂 on point
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 2 месяца назад
Zalowa uchitsiru muti nchani iiiii
@milliambandah1939
@milliambandah1939 2 месяца назад
Asilikaliwo alibe njala? Koma 2024 kalikose tikaona🙌🙌
@ThokoLungu-tq6pw
@ThokoLungu-tq6pw 2 месяца назад
Ahaaaaaaaa uli mkuchikamwa ndaseka
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 месяца назад
Pala ulije vakuyowoya leka waka ,vakutuka ku mpoto kulije ,nkhwachi kutuka?
@MabvutoSembo
@MabvutoSembo 2 месяца назад
Kkkkkkk dziko
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 2 месяца назад
Kumaganizo anga nfikuona kuti ngati iytu munthu olemekezeka samayenera kabgodya zokudya monga zimenezi osati kuti zakudyazo zaunve ai koma potengera mpando onwe iye ali
@MustapherLino
@MustapherLino 2 месяца назад
Koma manganya uchisirutu uwu
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 2 месяца назад
Kkk usi alibe zibwana amayiwonesa
@MosesLeckson
@MosesLeckson 2 месяца назад
Tikuoneleratu ndalama za boma zikuonongeka.Ma allowance a anthu onsewa ndi misonkho ya a Malawi osauka
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 месяца назад
Uthamanga misala agalu amcp mizimu 9 ikuonesana anthu akufa ndi chanja atsogoleni opusa
@frankbenjaminpakaineweedmo5395
@frankbenjaminpakaineweedmo5395 2 месяца назад
What is this guy trying to prove? We don't want poverty n eating at such a place is never nice. We ought to promote standard things not subsyandard restaurants after all you might get cholera. You're not pleasing anyone
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 2 месяца назад
Kudzichepetsa kodi? 😂
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 месяца назад
anthu akufuna amuwone momwe akudyera ngati fiti anthu sakwaziwa eti uyu ndi galu kwabasi
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 2 месяца назад
Apepera ndi apolice wo
@MarthaBlack-l4k
@MarthaBlack-l4k 2 месяца назад
Zayenjeza
@PatrickMacheso-r6z
@PatrickMacheso-r6z 2 месяца назад
Dziko lasanduka ground ya Tikuferanji
@thulambale2836
@thulambale2836 2 месяца назад
My vote
@SimonGulani
@SimonGulani 2 месяца назад
What is a meaning of althis?
@FrancoKaunga-rq2ki
@FrancoKaunga-rq2ki 2 месяца назад
Kodi manganya walezera ndi gondorosi? Amalawi sometimes tizikhala serious kumasekerera mavi ngeniawa stupid.
@FosterZulu-b3j
@FosterZulu-b3j 2 месяца назад
Apengadi ndithu uyu
@josephgabriel5941
@josephgabriel5941 2 месяца назад
Yomweyo manganya
@HafizahHarack-bn3bf
@HafizahHarack-bn3bf 2 месяца назад
This is complete manganya
@SydneyNyasuli
@SydneyNyasuli 2 месяца назад
Take life easy thanks
@CharlesPhiri-ds1rk
@CharlesPhiri-ds1rk 2 месяца назад
Iwe ndabambo askonodi iwe
@ElizaJoseph-q9w
@ElizaJoseph-q9w 2 месяца назад
Zikundipasa manyazithu ngati ndi akoro anga
@RuthMkangala
@RuthMkangala 2 месяца назад
Chilima anali katundu osati zachibwanazi olo half sangafike
@AubreyWiskes
@AubreyWiskes 2 месяца назад
Malawi anali kale,
@milliambandah1939
@milliambandah1939 2 месяца назад
Koma simisala iyi🤔
Далее
TIKUFERANJI 22 JULY 2107
28:55
Просмотров 189 тыс.
TIKUFERANJI 28 APRIL 2018
28:26
Просмотров 110 тыс.
TIKUFERANJI 10 AUGUST 2006
29:11
Просмотров 179 тыс.