Тёмный

Munthu wakomoka ndi Njala yavuta Malawi muno. Please aboma thandizani 

Jay Kawere TV
Подписаться 21 тыс.
Просмотров 2,8 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 76   
@blessingssaiti
@blessingssaiti 3 часа назад
Zopusa izi MCP mkumapereka ndalama kwa anthu oyimba 500,000000.anthu akufa ndinjala
@JuniorchokaniKhanene-f8e
@JuniorchokaniKhanene-f8e 3 часа назад
Ambuye liwoneni ziko lathu la malawi 🇲🇼
@happychimwemwe-1805
@happychimwemwe-1805 4 часа назад
Zovetsa chisoni kwambiri pamene wina sakufuna kuchitapo kanthu koma kumayendayenda
@Mustapher-fb4qp
@Mustapher-fb4qp 4 часа назад
Amene akuti boma diromweri diwasatanic
@SamuelChikomo
@SamuelChikomo 3 часа назад
Yehova tetezani dziko la Malawi
@oswardzenizeni1458
@oswardzenizeni1458 Час назад
Zovuta kwambili pamene mtsogoreli angoyendayenda
@EmmanuelRichard-k9k
@EmmanuelRichard-k9k 4 часа назад
Wina kumati boma ndilomweli ufiti chani ziko lanthu ntendele wasowabasi
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 2 часа назад
Mkumati boma NDI lomweli chisoni
@HoseKatsekera
@HoseKatsekera 2 часа назад
fiti ina ati ili kuja ukapanga zopusa, koma yaaaa anthu ndifitid mmmm
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 3 часа назад
Chakwera vomeledza kuti dziko la kukanikani kuyendedza this is bad news 😢 😞 😕 😔 😳 💔 will don't need you go pls live Malawi alone APM come take care about your beautiful 💙 Malawi peoples 💙 😀 please mr president APM will need u mr president
@AggieMayor
@AggieMayor Час назад
Kumvesa chisoni dziko lathu la malawi 😭😭😭😭
@ReginaMulipa
@ReginaMulipa 3 часа назад
Komatu zikutheka ngati mwasewerotu chocho😂😂 koma zachisoni ndithu koma muzilakhula bwino mukutisekesaso
@PeterJohn-b5t
@PeterJohn-b5t 3 часа назад
Mmmm ambuye kuvesa chisoni ananu akuvutika ndithu
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 3 часа назад
Nde kumati boma ndi lomweli guys 👦 chikangawa Mulungu achiteneye nthitu pasi popano APM do something please 🙏 to your beautiful Malawi 🇲🇼 peoples
@MussaZakeyu
@MussaZakeyu 37 минут назад
Nangati mukufuna thandizo osangopempha bwanji si bwino km akomoka bwanji wakulu ndi njala ana osakomoka
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t 55 минут назад
Njala yopanga chakwela iyi ndeno wina aziti chakwela woyeeeeee
@MisheckAselo
@MisheckAselo 2 часа назад
Wina amvekere Boma ndilomweri ngozi 😭😭
@JeanfatsanJere
@JeanfatsanJere 2 часа назад
Mvani kulira kwathu ambuye 😢😢😢😢😢
@MayesoBikefa
@MayesoBikefa 2 часа назад
Tili nyengo yosausa mulungu atiyendere kom asogolere akungoononga ndlam ndizithu zopand pake.
@MusaMajudu
@MusaMajudu 4 часа назад
Ena mkumati boma lomweri anthu oyipa inu
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 2 часа назад
Mmmmm zachisoni 😢 Malawi
@LidiaYasin
@LidiaYasin 15 минут назад
Zonvesa chisoni Malawi 😭😭😭😭😭😭
@mosesnjobvu716
@mosesnjobvu716 2 часа назад
Basi mkumati boma ndilomweri dzivereni chison ndithu
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 2 часа назад
Si drama think anakuwa is Like ngozi 😢
@LuciaKalumo
@LuciaKalumo Час назад
Ambuye atithandize
@ZinenaniPhiri-x1i
@ZinenaniPhiri-x1i 3 часа назад
Ambuye atithandize kwambiri
@EsetaGerate
@EsetaGerate 4 часа назад
😭😭😭nde muzit boma ndilomweri panyapanu a MCP
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 Час назад
Oooo bola akhale ndi moyo abale
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 4 часа назад
Ndekumati boma ndilomweli zopusa
@IbrahimMatola-h4i
@IbrahimMatola-h4i 3 часа назад
Chonena ndilibe mulungu ekha
@VeronicaYohane
@VeronicaYohane Час назад
Vuto ND chikangawa akugawa ndalama koma anthu akufa ku malawi
@ErickSaidi-sc4mp
@ErickSaidi-sc4mp 3 часа назад
Zomvesa chison kwambili 😢
@samdiverson9733
@samdiverson9733 3 часа назад
Ndie mkumati boma ndilomweli zachisoni kwambiri
@FelixWiskesi-d7w
@FelixWiskesi-d7w Час назад
Busy kugula 500 million oyimba koma MCP?
@PatrickZinenanie
@PatrickZinenanie 2 часа назад
Chakwera the great
@LoyidKarebe
@LoyidKarebe 3 часа назад
Ndiye makapeenaaziti bomandilomweli
@MussaZakeyu
@MussaZakeyu 41 минуту назад
Mwazilowesa Business mwatengela chasi chifukwa chakumachinga
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 2 часа назад
Achakwera akabwera mukumasekelela osagenda
@RebeccaChikalenda
@RebeccaChikalenda Час назад
Kma chakwerayu nd president kma
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 2 часа назад
Dziko lathu chibadwireni sizinafike apa mcp why? Fertilizer anakakhala otsika mtengo zinakachitika izi
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli Час назад
Nsambi esh
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 2 часа назад
Nde mkumati ndale what is kind of ndale for this malawian people, mkumati boma ndilomweli what is this? Koma anthu ena mukumati boma ndilomweli, please anthu amene mukut boma ndilomwelo tapitan mukawauze a president kut ife tikukhuta koma anthu kumuz akuvuta ,because anthu kumuz akuti boma silomweli chifukwa akuona mazuzo ,sikuti ndindale kapena chiyan chifukwa ine ndilibe mbali ndili overseas ,but am just kuva chison ndi mmene anthu akuvutikila mdziko lathu this is very sad story, inuyo inde khutan ndizopasidwazo koma kunja kuno kuli ena amene sadalira dzopatsidwa amadzilimbikilira paokha ,komano zinthu zikuvuta because ndalama ya sowa ndiponso ilibe mphawi zonthu zakwela, alimi ochuluka mudziko la Malawi ndiosauka amapeza ndalama movutika ,kuwatsitsila feteleza l think something it can be ok chifukwa kumudz
@EDSONNAKULENGA
@EDSONNAKULENGA 3 часа назад
Zosayedatuapa koma mulunguatitadize
@AlbunoCement
@AlbunoCement 2 часа назад
Mupiteneye kwa chakwela
@thomasmakata8861
@thomasmakata8861 2 часа назад
Masiku otsiriza ndithu
@ComfortSabe
@ComfortSabe Час назад
Nde tawaonani anthu akumudziwo nde wina angoseweresa ndalama za boma malo mosamala anthu ziko
@ImraanSambani
@ImraanSambani 3 часа назад
Apule mkumapita konjoya kunja kukasayinila zopusa kut nkhondo yophana yizipitilira anthu ake akufa ndi njala chonchi izi ndizoona kodi?😢😢
@JosephKosamu-r2v
@JosephKosamu-r2v 9 минут назад
Zikundivekera ngat ka drama Pena pake
@JailosAbdullah
@JailosAbdullah Час назад
Chakwera mbudzi yamundu serious
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 4 часа назад
Zoopyatu izi ena agundika kugawa ndalama zulo eeeee koma mbuye
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 часа назад
Aaaa koma MCP mwapanga chibwana dzedi ndi amalawi
@AlfredMathiah
@AlfredMathiah 5 минут назад
ZaChamba ena akusakaza misokho yathu kunja
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 3 часа назад
Achoseni chakwera mawa alibe ntchito
@AnajoiceSozinho
@AnajoiceSozinho 2 часа назад
Zovuta kwambiri
@Hopenandola-zg6kz
@Hopenandola-zg6kz 2 часа назад
Koma chakwela chakwela nanyongo wameke kwabas
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 2 часа назад
Ndiye muziviteranso Afitiwa zizadutsa pamenepo Ndalama akuthera kugura anthu a satanic wa
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli Час назад
Esh zobvuta izi abale
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 2 часа назад
Zachisoni 😢😢izi
@robertkalima874
@robertkalima874 2 часа назад
Ndinu opusa. Drama ndi njala? Mudzaziona agalu inu
@VincentKadzinja-q3b
@VincentKadzinja-q3b Час назад
Chakwela angoyang,ana e this is is fack news chakwela chitapo ka2
@AmosScott-z9x
@AmosScott-z9x 4 часа назад
Komatu amalawi ena ndalama ali nazo osathandizako amzanu koma mipira nde kumathandiza ma team
@AbudRahamanDaud
@AbudRahamanDaud 4 часа назад
😢 koma
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 часа назад
Drama kapena zoona, ndafunsa chonchi chifukwa choti pali a Camera, anadziwa bwanji kuti tipite ndi camera munthu akomoka. Vutolo ndi zoona lilikodi koma ili ndi drama.
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 часа назад
Drama imeneyo akufunilapo chithandizo munthu ameneyu ndiameneso adapanga video ija yachiteze
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 Час назад
😭😭😭😭😭😭🇲🇼🇲🇼🤔
@IsmailBrighton-w6u
@IsmailBrighton-w6u 4 часа назад
😢😢
@Pangolinimw
@Pangolinimw 2 часа назад
😭😭😭😭😭😭
@jangiamsume7248
@jangiamsume7248 Час назад
😭😭😭😭😭😭😭
@ChrisLessie
@ChrisLessie 3 часа назад
Zoopsa😢
@BuanarJoao-mi5ke
@BuanarJoao-mi5ke 2 часа назад
Boma ndilomweli sitikusitha
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 часа назад
Zochitika kukoza zimenezo sizoona akungofunapo chithandizo chabe munthu ameneyu ndiameneso adapanga video ija ya anthu amafuna chitedze ndiye anthu akumangochi ndiochenjera muone enaso akuseka pamenepo munthu okomoka sapanga zimenezo
@SamsonKunthani
@SamsonKunthani 2 часа назад
Iwe ndi chitsiru zedi ukuti boma ndilomweli.
@fosternyirenda-wo4eb
@fosternyirenda-wo4eb 4 часа назад
So bad😢
@Mstarndembe
@Mstarndembe 4 часа назад
😭😭
@MemoryKamanga-jv4jh
@MemoryKamanga-jv4jh 4 часа назад
😭😭😭😭
Далее
Bethel Gospel Sifa Njooni Kwa Yesu Official Video
7:07
DPP ndi Comrade Timothy Mtambo agwirizana.
1:31
Просмотров 17 тыс.
A ENOCH CHIHANA KUYANKHA MAFUNSO
24:54
Просмотров 774