Тёмный
No video :(

MZIBAMBO WAPHEDWA MWANKHANZA CHIFUKWA CHA CHIMANGA CHITATU 

Hanifa Mw
Подписаться 72 тыс.
Просмотров 36 тыс.
50% 1

WAPHEDWA CHIFUKWA CHA CHIMANGA CHITATU

Опубликовано:

 

26 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 143   
@user-dn5sf3md5t
@user-dn5sf3md5t 4 месяца назад
NGATI YESU CHRIST ANATEMBERERA NKUYU CHIFUKWA CHOSABEREKA , INEYO NGATI MTUMIKI WAKE NDIKUTEMBERERANSO JERE KUYAMBIRA LERO NYENGOZAKO SIZIDZAKHALA MONGA KALE UDZAKHALA UKUZUNZIKA MOYOWAKO.ONSE ANA AKO APABANJA PAKO MDZINA LA YESU CHRIST AMENE ANAPACHIKIDWA PAMTANDA CHIFUKWA CHA TCHIMO LAKO,MDIKULENGEZA NDI MWAZI WAKE WA YESU USOWE MTENDERE , USOWEMTENDERE ,USOWEMTENDERE .
@user-xi6sr7kd7p
@user-xi6sr7kd7p 4 месяца назад
Pa dziko lapasi Pano akhoza Kukhala wandalama Koma mulungu ndi amene angaweruze pakuti tonse ulendo wake ndiwomwewu nayenso jereyo ulendo wake ndiwomweyo.
@user-rl5zq1qr4d
@user-rl5zq1qr4d 4 месяца назад
Bukhu lopatilika lamulo lachimvekere usanamizire mzako lamulo Lina usaphe truck driver sangabe chimanga chiwiri nzosatheka nkhanza panali udani pakati pa driver ndi driver mzakeyu
@user-xi6sr7kd7p
@user-xi6sr7kd7p 4 месяца назад
Zoonadi
@DorothyKaimfa-ns8su
@DorothyKaimfa-ns8su 4 месяца назад
The pain still fresh Mr Jere muliko zikuwawa zikuvuta kuiwala ambuye achite nanu munatiphera munthu ofunika kwathu nkusauka kwathu sitimadzadya kwanu ifeee linali thandizo kubanja kwathu ambuye akhale nanu akuoneni misozi iyi one day idzatembenuka ndikukhala pamutu panu ndithu 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 My brow anapita osalakwa or kwathu chikhalire sanabepo anali ofatsa mbale wanga osayankhula koma inuyo a Jere
@charleslimbani8590
@charleslimbani8590 4 месяца назад
Mr jere ngati simulapaa chuma chanu chiyamba kupita pansii koma simufa nsanga kufikira mutaona maxunzo oophyaa kwambiri
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 4 месяца назад
Ndipo asafe asazafenso azizangovutika mpaka kale
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 4 месяца назад
Osadandaula Mulungu ali mbali yanu..Mulungu akutonthozeni..ndipo Mulungu akumenyeleni nkhondo chilungamo chiyende ngati madzi....mulungu ali mbali yanu..
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 4 месяца назад
Kukhala waphedwayo ndim'balewanga chilungamo chake ndingachipange ndekha because our police is useless
@user-mx1jv8qn4w
@user-mx1jv8qn4w 4 месяца назад
Ndipo
@patrickkalivea6879
@patrickkalivea6879 4 месяца назад
Koma zovesa chisoni kwambiri Abele Malawi wasanduka Ngati mukango Mau amanena Kuti tinkhale anthu onkhulukilala Wina ndi muzache chifuwa Ngati ifeyo sitinkhululuka anthu ena ndiziwe Kuti pasiku lomaliza ambuye yesu sakatinkhulukila
@HannaBanda-pj8vr
@HannaBanda-pj8vr 4 месяца назад
Aaaaa Malawi able akupita Kuti ? Ndikulila ine mbaleyo au Se muntendele ,anthu achita izi mulungu asawakhululukile ayi ,akayakhe mulanduu Amen
@estherkambewa7791
@estherkambewa7791 4 месяца назад
Chimanga chitatu mpaka moyo wamunthu? Zomvetsa chisoni
@user-zy1br2fy6v
@user-zy1br2fy6v 4 месяца назад
Thanks to you Hanifa Tv for bringing us this story Ndimakutsatani kwambiri nkhani zanu Koma mufunika kukonza pa editing zuoneka kt zimakuvutani kupanga edit zinthunzi zanu pena timakhala ngati tikuonera beyond the scene ija 😂😂😂😂😂
@WilfredMathews-yl6ij
@WilfredMathews-yl6ij 4 месяца назад
Komatu apa apolisinu chilungamo chioneke pliz pliz pliz 😭😭😭😭 musadye ndalama zatemberero pamoyo wamunthu ngt momwe adachitiramo ngt akupha nkhuku
@EstherBair
@EstherBair 18 дней назад
Mmmmm kulakwa ndipo ajele ambuye akuwoneni
@NumbDee
@NumbDee 4 месяца назад
Ajemu ndi Louis Mzimu wamunthu ameneyu ukuzuzani koopsyani
@user-tt1kv3oh7c
@user-tt1kv3oh7c 4 месяца назад
So touched story eeish!!
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 4 месяца назад
Malawi it's no democracy democracy of it's only for rich people not for the poor people nkhani yomvetsa chisoni
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 4 месяца назад
Pakudutsa chinyengo apa,, ine kanakonda khuluyu ndimudziwe , ine nditha kuthana naye ndekha
@tianarose9380
@tianarose9380 4 месяца назад
Zovetsa chisoni kwambili osauka alimbe mawu 😭😭😭
@peterlowole7841
@peterlowole7841 4 месяца назад
No Mr jere 😭😭😭😭 kulira Kwa munthu asalakwa mulindi zambi bwanji osapempha anthu akulipireni chitatu chimanga kupha munthu ayiii inuyo mumafuna zizimba timaziwa olemelanu ,koma ziwani mulindi mlandu kumwambako
@Madalitso-sj6gg
@Madalitso-sj6gg 4 месяца назад
Very bad, koma this boy wafotokoza moveka bwino momwe zinakhalira, Eeee koma this is bad msaname, may his soul rest in peace
@user-tj8tt3ns6l
@user-tj8tt3ns6l 4 месяца назад
Zonvuta kwambili allah amulandile muthu ameneyu ndichimwemwe
@user-im4bs7fk9o
@user-im4bs7fk9o 4 месяца назад
Pepani kwa mbiri.mzimu wake use muntendere chimanga sizinthu zophera munthu ayi.amene anapanga izibadzakolola pangatalike Patani .
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 4 месяца назад
Chuma cha magaza muyaluka nacho ..kulora kuchosa Moyo wa munthu chifukwa Cha 3 pic of maize muli NDI tsoka ..poti muli NDI Chuma chambili mugure Moyo mubwezere Kwa mwini wake iwoso akubwezeren chimanga chanu ..Koma osaiwa nthawi ili mkudza yomwe mudzayankhe
@LoydKameza
@LoydKameza 4 месяца назад
😭😭😭😭😭abale kulakwa kupha Munthu osalakwa
@SawaJaribu-op1jj
@SawaJaribu-op1jj 4 месяца назад
Kulakwa zed mzimu wao uuse mumtendere Mulungu yekha ndamene akaweruze dziko lapasi lili chabe😢😢
@MulemeeDaza
@MulemeeDaza 4 месяца назад
Osauka alibe mau 😭😭😭😭😭😭
@user-zy1br2fy6v
@user-zy1br2fy6v 4 месяца назад
Mukapanda kupeza chilungamo kuchokera ku polisi, pezani njira zanu ndi abale anu mpaka mupeze chilungamo pa nokha A police wa sakuthandizani
@HajaSande
@HajaSande 4 месяца назад
Ayi kuno ku south Africa tingoyika zonse manja mwa chauta
@MichaelChaso
@MichaelChaso 4 месяца назад
Koma Ajele munapha munthu osalakwa, ndipo pangatalike bwanji Ajele mudzaona masoka komaso mudzayankha mulandu.Mulungu sagona ndipo sangakondwele nanu chuma chanu mulungu achitembelele anthu oipa inu
@frankkassim1254
@frankkassim1254 4 месяца назад
Ajele naonso aphedwe osangowasiya ndimoyo
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 4 месяца назад
Kumbali yanga ndikuona kuti anthu Adela imeneyo pamafunika kuthandizana chifukwa chilungamo chiziwike chifukwa boma iripoyi ndilopondereza koma patokha titha kuthananazo
@user-zr6te9uq7w
@user-zr6te9uq7w 4 месяца назад
Jele Mulungu akukathe, mu dzina La yesu khristu
@user-dv6wy1sq8g
@user-dv6wy1sq8g 4 месяца назад
Anthu tikama otcha ma police ndemuzit Malawi osauka tikulakwa?
@AnnieBanda-rb2dk
@AnnieBanda-rb2dk 4 месяца назад
One day tizazika mpeni pakhosi police imozi ndikuusiya pakhosi popo kuti apolice onse azave okasolola mpeniwo pakhosi azakhale apolicewo ndi chipatala, kuti azaziwe kuti zimawawa bwanji, olo mwana wa police imozi azakumana nazo adilikire one day azaziwa kuti khobwe sinyemba anthu timasungira chipongwe kwambiri anthu amenewo amaona ngati ochenjera akamadya ndalama zowahonga munthu wakupha mzake but one azaona zimene zizapangike, wa mozi wake azakhala ineyo ndizausiya pakhosi popo mpeni kaya ndikamwana kawo apolice eya ndizausiya popono azapange bwino birthday
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 4 месяца назад
Zomvesa chisoni ndiwakwathu munthu anaphedwayo😢
@user-nb7dp6pr9n
@user-nb7dp6pr9n 4 месяца назад
Munthu ameneyi muti A jere ozinvaa chuma, kunalinso nzawonso ku Mozambique pa Vila ulongwe dzina lomwe ankatchuka nalo linali Anzeru ndinu anali ndi chuma choti Jere mukumunenayo alibe ndalama, koma anaphanso munthu wakubanja lovutikanso ngati lomweri la a Mayi athuwo aku Machinjiriwo. Nkhani yake inali chonchi, M'bambo waku Mozambique ameneyo amawoda golide kunkansosole mu Mozambique monmo ndiye tsikulina anawoda golide wochuluka ndiye atalingalila anaganiza zomugulitsa uja Anzeru ndinu, anakumana kunyuma kwake ndiye ntengo anamuuza uja Anzeru ndinu anati mmmm sindingakwanitse wadula koma ndikupezera nsika kwa azizanga ena ku Beira kapena ku Maputo mwini golide uja ananyamuka ulendo kunyumba kwawo koma nayenso amakhala pa Vila pompo koma mzathu osaukayi amayenda pa njinja ya moto ya DT. Iye phee uku akudikilira Business ya golide, koma ndalama zomwe anamuuzazo Anzeru ndinu akanapeleka tikuti chinali chikhomo, koma plan yake ankafuna kuti angolanda two weeks inapita kumapeto kwa week yachitatu lachisano, Anzeru ndinu anamuimbila phone nkulu uja pastnine PM undipeze ku Bottle store kuno munthu uja ozagula Golide uja wayandikila uja anatsazika madam giya pa DT yake, anafika paja onse ukuakudikila ankamwamowa. Mwini golide anafunsa this's past ereven titan bwana? Anzeru ndinu uja anangoti nthawi ilipo, kenako mwini Golide uja anatengelana pambali ndi bg uja kenakonso pambali paja panafikanso anthu ena koma kwaiyeyo amaoneka anthu osokoneza ndiye mwini golide uja anaitulikila kuti anthuwa alilimodzi iye mwachangu anatenga Golide uja ndikumeza onse aja akuona, kenako madolo aja amamuonekera osokonekera kwaiyeyo anamugwira kupita naye malo ena manmawa kutacha anapezeka atang'ambidwa pamimba ndichotsamo Golide uja, koma zitachitika izi akuchikazi anaimbila akuchimuna kuwadziwitsa zaimfayo koma akuchimuna anawauza akuchikazi kuti musalore a Police kuchotsa thupi ife tisanafike, thupilinachotsedwa akuchimuna atafika koma kwawo ndi ku Chimoyo kumalile a Zimbabwe ndi Mozambique koma iwo ali mu Mozambique. Koma mawu omwe analankhula panthawiyo anangoti nonse mwatenga gawo pa imfa ya m'bale wathuyi tiona. Ndikukamba pano (Anzeru ndinu) kulibe magalimoto oyendera amasintha ngati zovala adafela pa chiongolero anangoti mutuwanga omwewo koma galimoto siinagwenso ayi pomwe amakafikanaye pa Dedza Hospital atafakale koma chifukwa chandalama achibanja samakhutila anapitanso ku Lilongwe Central Hospital anawauzanso chimodzimodzi. Iyeyo asanzinve ndalama ayi.
@jennygardemalm7559
@jennygardemalm7559 4 месяца назад
Ooo😢😢,Anthufe😢,pepani mamma mulungu aweluza mulandu umeneu.
@enochnkhata9812
@enochnkhata9812 4 месяца назад
Chimanga chitatu bwanji sanapite pamalo pamene panathyoledwa Chimangacho asanayambe kumumenya, kuti akapeze umboni woona aaa. Panangolowa chidani apa. Boma likulekerera ang'ona nkumamanga abuluzi nzomvetsa chisoni amphawi tizifa chonchi nkumapita kumanda achuma nkumakodzera khoma mmmm.
@joyedward45
@joyedward45 4 месяца назад
So sad Ambuye dziko lathu lija lasanduka phanga la a chifwamba ndipo mizimu ya anthu osalakwa yatsikila ndi ikutsikila kuli chete Ambuye tathedwa nzeru .Inu oweruza olungama muyimilire ndipo mugwire nthungo mumenye nkhondozi patokha sititha
@patricksinyala1345
@patricksinyala1345 4 месяца назад
Mtolankhani anaiwala funso limodzi loti, Kodi anthuwo anakwanitsa Lupita kukafufuza mmundamo Kuti akachitile umboni oti chimangacho chinabedwadi mmundamo? Chimanga chitatu, mmundamo munayenela kuonekanso miphesi itatu yochotsedwa chimanga Mmhmmh chilungamo chioneke pankhaniyi.
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 4 месяца назад
Simunave kuti anakamucholela chimanga kuti aonjezele pa chitatucho kuti mulandu ukule ambuye azitikhululukila
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 4 месяца назад
Ndipo munthuyo komwe ankachokerako anali atanyamula chimanga kale mmm zinali zobvutatu mh
@musadinalaanusa9931
@musadinalaanusa9931 4 месяца назад
Sanachite bwino anduo
@davidkadyakapita8836
@davidkadyakapita8836 4 месяца назад
Koma zoona mkuchotsa moyo wa munthu chifukwa cha dowe mutatu? Ngati akudalira ndalama mulodzeni ameneyo. Wapha tsogoro la anthu ambiri.
@user-xg5pq5ku4l
@user-xg5pq5ku4l 4 месяца назад
Sazapeza mwayi mzibambo waphayu,ndipo a Malawi,,,ena,umunthu mulibe.Akanthidwe ndithu anthu aphawo
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 4 месяца назад
Ndimulongosole khuluyu ulele chonde chonde
@tiwongehojaney5873
@tiwongehojaney5873 Месяц назад
Tangomugululabi mpezi ameneyo
@MasharPablo
@MasharPablo 4 месяца назад
Tangotipasani ganyu ife muwone. No money just give us foto
@giftblack7690
@giftblack7690 4 месяца назад
Anthu ngati awa sipafunikaso police kungopita kunyumbako kukawotcha chilichose komaso ine nditha kuthana nawo why amupha munthu osamufufuza bwino bwino bwanji eish
@henryngandu2936
@henryngandu2936 4 месяца назад
Malawi has lost it this is sad development even if person steal from you have got no right to take way life
@MatumeMkhondo
@MatumeMkhondo Месяц назад
Mzimu wawo ukawuse mutendele
@paulmakaula4937
@paulmakaula4937 4 месяца назад
Sad koma akuba chimanga akusowetsa mtendere ndiye anthu akupanga mob justice
@MkaiFrancisBendera
@MkaiFrancisBendera 4 месяца назад
Ash zobvuta ndithu koma limbani mtima kunjaku kuli mlungu
@user-vt4xw5px5h
@user-vt4xw5px5h 4 месяца назад
Anthu ndioyipa kwambiri maka apolice sianthu
@MuhammadYusufu-ri7lr
@MuhammadYusufu-ri7lr 4 месяца назад
😭😭😭😭😭 koma abare dzikori rikurowera kuti maka maka
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b 4 месяца назад
Koma Inu mumazitcha andalama ndi ndalama zanuzo nkumasowesa anzanu ntendere chifukwa CHOTI ndiinu achuma mudziwe kuti mulibe nzeru zomposa mulungu kupha nzanu ndi nkhani yongopeka ? Minyama masoko zipite pathupi lanu
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 4 месяца назад
Amalawi khalani ndi mtima wachison bwanji mukayitanisa ndalama mmmm
@HenryGulani-fq5js
@HenryGulani-fq5js 3 месяца назад
dzovetsa chitsoni ine ndili Joz muno ndikufuna number
@user-dn5sf3md5t
@user-dn5sf3md5t 4 месяца назад
NKHANI IYIYO SIZIMASOWEKANSO A POLICE KUNALI KUGWIRIZANA KUMUGWIRA NAYENSO KUMUPHA CHIFUKWA KUYENDERA A POLICE KU MALAWI PANO KULIBE POLICE
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 4 месяца назад
A police anamuthawitsa msanga
@user-mk8cn2no3o
@user-mk8cn2no3o 4 месяца назад
That's why aoolice Ali osauka
@HAPPY-mf3gw
@HAPPY-mf3gw 4 месяца назад
Sad story mmmm
@NumbDee
@NumbDee 4 месяца назад
Mr jere komwe muliko muvumbuluke moyo wanu uzakhala ozuzika mpaka kale
@amoschilangiza
@amoschilangiza 4 месяца назад
Malawi akupita kuti? Mr Jere amangidwe
@user-zo4ok7md5v
@user-zo4ok7md5v 4 месяца назад
God will punish them
@augustMag
@augustMag 4 месяца назад
Kodi apolice aku Malawi akafika pa maso pa Mulungu? Ndikunena inuyo apolice mukugwira tchito yanji? Chifukwa chiani simukufuna kuonesa chilungamo nkhani ikachitika? Muli ndi soka anthu obisa chilungamo chifukwa cha ndalama mukungokonda ndalama kusiya chimene munalembedwera tchito yanu koma ziphupu zokhazokha Mulungu ali nanu tchito inu iwenso mwini wake munda chimanga chitatu mpaka kuchosa moyo wamuthu? Dziko uliva kuwawa ukhala onthawaw ngati abele bolanso abeleyo Chauta anamuyika chizindikiro kuti anthu asamuphe koma iweyo usafa ngati galu mtembo wako abale ako sazauna athu kuipa mtima ngati kumanda choncho akapolo aka amene amafuna kuti uwatameyo kuti akugwira tchito bwino mzimu wamunthu ameneyu alange koopsya aszaonekenso padziko pano
@user-yh3dw6qu7z
@user-yh3dw6qu7z 4 месяца назад
Ngati boma likumva ndikuonera video imeneyi lamulo ligwire ntchito.
@alexsumani6823
@alexsumani6823 4 месяца назад
Dziko ili likungoyenda malamula anasiya kutsatiridwa Palibe chilichonse chimene chikutsatidwa ,very sad
@GrecianWyson
@GrecianWyson 4 месяца назад
Mzimu wake uwuse mtendere.chimanga chitatu zoona mpaka kuchotsa Moyo wamuthu Inuyo amene munagwira tchito yakuphanu mukuva bwanji mutima mwanu.Chenjezo mulanduwu sunathe oweruza olungama akudikilaso kukaweluza chifukwa mzimu wake ukulila kwambili kwamulungu.mwina inu NDA muyaya
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 4 месяца назад
Izi kukanakhala Kwa Bvumbwe okuphayi akanaphedwanso ndipo a police amene amakateteza Munthu okuphayi kunyumba kwake nawonso onse akanaphedwa Ndipo police ikanaotchedwa. Izi kwathu kwa Bvumbwe sitimalorayi komanso antchito atchulidwa omwe anamenya nawo abambowa kwathu tikapheratu onse
@user-lg2ws2ki3d
@user-lg2ws2ki3d 4 месяца назад
Very bad :(
@HashimMustafa-yj1or
@HashimMustafa-yj1or 4 месяца назад
Ndalama ikamayankhula chilungamo chimakhala chete Ambuye akuthandizireni mpaka chilungamo chioneke
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg 4 месяца назад
Soka kwaiye amene agwesa kachisi wa mulungu pakuti azalandla chilang'o chosatha
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 4 месяца назад
Jere ameneyu amangidwe basi, ndi a ntchito womwe akalongosole ku police.
@patiencetebulo
@patiencetebulo 4 месяца назад
That is nonsense akuyenela kumangidwa koma zitukuko zomwe wasiya malemuyo amalizise komaso aseve jele zikakhala dollar ndizache
@PeterNkwita
@PeterNkwita 4 месяца назад
Koma anthu muli ndi sambi
@khatazachibambo8732
@khatazachibambo8732 4 месяца назад
Koma Volume yanu very poor
@NaduMbewe-zz6iw
@NaduMbewe-zz6iw 4 месяца назад
Luwis anali paudani ndi nzakeyo
@user-lq4bc2dr2n
@user-lq4bc2dr2n 4 месяца назад
Nsambi kulakwa zandikhuza kwambiri 😢😢😢😢
@user-mo4tv5eu5y
@user-mo4tv5eu5y 4 месяца назад
Pachiyambi munaka nyanyala malilowo ku police then you could have get justice
@user-rh4hf3yo9t
@user-rh4hf3yo9t 4 месяца назад
Amwene nzanu akufotokoza pamene inu muyang'ana zina. Ntchito ikuvutanitu inu.
@EllamariaKaliya-tc2es
@EllamariaKaliya-tc2es 4 месяца назад
Ndipoo mtolankhani uyuuu abale
@mchipengule
@mchipengule 4 месяца назад
A Malawi Chikondi cha chibadwidwe chinatha zowona kupha munthu chifukwa cha chimanga chitatu? Ameneyu akaseweze ndende basi. A Police samalani ntchito yanu.
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 4 месяца назад
Ine mmene ndinabadwira pano ndili ndi zaka 36 koma ntchito ya a police sindikuiona mmalawi muno
@user-sb2bg3dd3k
@user-sb2bg3dd3k 4 месяца назад
Jemu ndi Louis tikukawatenga tipite nawo ku Police Akayankhe Mulandu.
@user-zy1br2fy6v
@user-zy1br2fy6v 4 месяца назад
Apolisi ndi ndalama za tsoka sungawalekanitse Anthu osamva chisoni ngati awa simnawaone mpake kuwasandutsa ma tumba amakala mxieeeeew
@user-od3vy2lg6p
@user-od3vy2lg6p 4 месяца назад
Ndamva chisoni kwambiri 😭😭😭😭
@rashidlamos3403
@rashidlamos3403 4 месяца назад
Pepani kwambili ofeledwa inu akulakwirani MULUNGU akuwona zonsezo
@user-dg3dn5zq7w
@user-dg3dn5zq7w 4 месяца назад
Koma kulakwa mmmmmmm athu amenewa anamuphwa angwidwe basi
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z 4 месяца назад
Truck driver ndimunthu oti amazioezera zake sangbe chimanga chitatu
@user-mx1jv8qn4w
@user-mx1jv8qn4w 4 месяца назад
Choncho kuti abwezeleno nde adzamanga iwowo
@AliajoeAliajoe-vv1wo
@AliajoeAliajoe-vv1wo 4 месяца назад
Eish so sad guys sorry
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i 4 месяца назад
Zimuwake akawuse muntendele koma ajele mulape kumanga chipatala kapena police chisakhale chifukwa choti muthele mizimu ya azanu apolece nanu mumuziwe yesu mupemphele zolimba kuti mulungu azele kwa chakwela akukwezeleni malipuloanu akhale okwanila musiye chinyengo zomwe mukupangazo zothela paziko mukayakha milandu
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 4 месяца назад
Pepani akubanja, Zokhudza kwambiri 💔💔mzibambo ameneyo akafere kundende koma poti dziko lanthu likukomera olemera.. Idont think you will get the justice 💔💔
@EllenBanda-gj4zb
@EllenBanda-gj4zb 4 месяца назад
Mulungu akumenyereni nkhondo akubanja!
@patricgama4788
@patricgama4788 4 месяца назад
Dziko lathuli muli tsatama dzinayambila kwabutsa athu onama ndiye aliyetse akupangadzofuna dzake koma Mulungu alinafe
@ritaoffen7912
@ritaoffen7912 4 месяца назад
So sad
@marynkhata9707
@marynkhata9707 4 месяца назад
Zomvetsa chisoni kwambiri munthu kuluza moyo chifukwa chachimanga chitatu pepani nonse kubanja la ofedwa
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 4 месяца назад
Anthu akulimba mtima et eishiiii
@mariamwandwanga3035
@mariamwandwanga3035 4 месяца назад
Ambuye wakanthe a jere
@user-mk8cn2no3o
@user-mk8cn2no3o 4 месяца назад
Apolisi amangothandiza a ndalama nde kumalawi kumeneko
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 4 месяца назад
Sanamangidwe apolice anamuthawitsa
@user-nb7dp6pr9n
@user-nb7dp6pr9n 4 месяца назад
Very sad😡
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r 4 месяца назад
Km zonvesa chisoni kwambiri moyo wamunthu sungafanane ntchimanga ayi ambuye awakanthe km
@AaAa-qy9id
@AaAa-qy9id 4 месяца назад
Apolsi athu ndi zitsiru za anthu chinyen go basi Anthuni mungomupha nanunso pitani pa sing'anga aphe wachumayo ndi apolosi onse achinyengowo analandira ndarama
@ziyamikanmakowa5981
@ziyamikanmakowa5981 4 месяца назад
Munthuyo wandalama Ka kukapha munthu chifukwa cha chimanga chawisi ,fear God
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 4 месяца назад
Under namabatile chakwera wa Amonika leadership
@InoquebosiCanhosa
@InoquebosiCanhosa 4 месяца назад
XWt😅😅😅😅
@Fridaus-kg2eq
@Fridaus-kg2eq 4 месяца назад
Malawi sali bwino 😭😭😭
@Fridaus-kg2eq
@Fridaus-kg2eq 4 месяца назад
Malawi sali bwino 😭😭😭😭😭
Далее
Only I get to bully my sister 😤
00:27
Просмотров 21 млн
Wife habit 😂 #shorts
00:16
Просмотров 58 млн
CHIBANGILI CHIKUPANGA ZODABWITSA KU BLANTYRE PART 1
13:53
GOtv Malawi Izeki ndi Jakobo Kukhala Awiri Simantha
19:56
Onesimus Controller  Remix Ft JoeBoy
3:10
Просмотров 303
WAPULUMUKA KOGULITSIDWA A KULONGOSOLA
14:25
Просмотров 21 тыс.
Zinakhala Bwanji Kuti Mwana Wa Miyezi 8 Abedwe
16:46
Просмотров 33 тыс.
ZODABWITSA MTSIKANA WAVUNDUKULA MVULA YA  A INI AKE
12:43
Only I get to bully my sister 😤
00:27
Просмотров 21 млн