Komatuu ndipo apereke report limeri, asatana amenewa kwabasi. Chilima's soul will fight for the truth to be vindicated. We are praying every day , God will answer these prayers
Zekariya 11 15 Pamenepo Yehova anayankhula nane kuti, “Tenganso zida za mʼbusa wopusa. 16 Pakuti ndidzawutsa mʼbusa mʼdzikomo amene sadzasamalira zotayika, kapena kufunafuna zazingʼono, kapena zovulala, kapena kudyetsa nkhosa zabwino, koma iye adzadya nyama ya nkhosa zonenepa, nʼkumakukuta ndi ziboda zomwe. 17 “Tsoka kwa mʼbusa wopandapake, amene amasiya nkhosa! Lupanga limukanthe pa mkono wake ndi pa diso lake lakumanja! Mkono wake ufote kotheratu, diso lake lamanja lisaonenso.” Apule
A hyena cant bear a lion(kamuzu banda >>>>DR. chikangawa forest) Commenting from inside thickest chikangwa ....Am not able to see you bcoz of chifunga....anyone here raise a hand please
Waona zomwe zachitika ku utm saulo's atamwalira?zomweso zingachitike ku dpp iye uja kut achoke panopa,,,dekhani utsogoleri siwamasewela ndi mphatso yochokera kwa mulungu ,even inuyo atakutengani kut mukaime ngat nyamata ku dpp ko simungakhale ndi chikoka ngat cha iye uja,dekhani kae mphuma limeneli lomwe mumatenga nazo zinthu kuziika pa mpando
Malawi inapepeletsedwa,kale kale.kulibe, Anthu olimba mitima,ngati ku Kenya, tiyeni amalawi tibvomeleze,kuti'mphabvu,zathu,tinazipeleka'mmanja,mwa andale.citizen,ya malawi ilibe mphabvu.olo, president atakhala kuti akufuna akhale,pa u president for life zitheka.olo,atakhazikitsa,lamulo loti,tidzimuseta,akalowa mu chimbuzi zingatheke.chifukwa,tili opepela mu African continent.