Тёмный

NKHANGA ZAONA ZOBISIKA ZOMWE MR CHIKANGAWA AKUCHITA NDI MWANA WAO KU LIKOMA 

Malawi Trends TV
Подписаться 49 тыс.
Просмотров 38 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 147   
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 27 дней назад
Ntanyiwa machine bambo 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 Chakwera anyera manyi sanati uyu akuyenera kuzamangidwa
@BrownMatonyola-xi3lb
@BrownMatonyola-xi3lb 27 дней назад
God bless you mtanyiwa protection be with you and be with good life
@MillyKachepa
@MillyKachepa 24 дня назад
Amen
@EgressSamson
@EgressSamson 22 дня назад
OK 3|target try rgrgrggrrgggrg-gt4rggvgfttgt-😅tee loop da? Z
@BlessingsNowero
@BlessingsNowero 13 дней назад
😂😅
@smashonhaindi147
@smashonhaindi147 6 дней назад
Mtanyiwa Moto kut buuuu!!!!
@MoreenSelengu
@MoreenSelengu 27 дней назад
God Almighty will vindicate you ❤ you are so special in fact you're man of God mtanyiwa
@JamesBlack-t6o
@JamesBlack-t6o 27 дней назад
Big man mtanyiwa I love you for opening malawians there eyes
@MatthewsJohn-kv8fj
@MatthewsJohn-kv8fj 24 дня назад
Please your number Mtanyiwa
@BlessingsGama-j3r
@BlessingsGama-j3r 24 дня назад
May the Mighty God continue to work always for you .... Mthanyiwa
@EsnatKandeu
@EsnatKandeu 3 дня назад
Inu anakusakhani ndi Mulungu anakupattsani nzelu ngat mfumu Solomo amen
@PatriciaThipa
@PatriciaThipa 27 дней назад
More fire Ntanyiwa, Ambuye adzera mwainu kuti mutipulumutse a Malawi
@YotamPhiri-t8k
@YotamPhiri-t8k 16 дней назад
I wish you all the best mtanyiwa you are one in a million
@MacdonardMapala
@MacdonardMapala 27 дней назад
Ngat sindina vesere comrade ntanyiwa ndimawona ngat phone yanga sikurimenero ndekut siyinagwire tnchito more fire 🎉🎉🎉🎉 42:32
@DavidJabesi-r1h
@DavidJabesi-r1h 22 дня назад
Ntanyiwa mulungu akhale nanu bwana chifukwa cha kulimba mtima kwanu pofuna kulimbikisa mitima ya amalawi pa nkhanza zomwe boma likuchita , we love you comrede ntanyiwa may our mighty Lord continue protect you
@AliAbdul-s6u
@AliAbdul-s6u 23 дня назад
Umakwana iweyo ❤❤❤❤❤
@hastingskayange
@hastingskayange 27 дней назад
Amene agule Likoma adzaluza ndalama chifukwa anthu aku Malawi sadaike Likoma for sale so mind you that you shall waste your money..becareful...Likoma it's owned by malawians..dont try it
@cwsteve8233
@cwsteve8233 27 дней назад
well said
@ChisomoMalenga
@ChisomoMalenga 24 дня назад
May God protect you wherever you go whatever you wherever you stay God bless you mtanyiwa
@Moses51
@Moses51 24 дня назад
You're freedom mr tanyiwa keep we are together with you nose munzamangidwa amene mudapha chilima
@PhiriChiyambi
@PhiriChiyambi 27 дней назад
Eee koma atsogoleri athu ndiomvetsa chisoni mpaka kugulitsa dziko kwa zungu pa dziko la pansi izi sizinachitikeko ngati zili ndalama angobweza osalora zogulitsa likomazi tiyeni tidzuke tisalore
@lonnexjeke6840
@lonnexjeke6840 26 дней назад
God be with You Comrade Mtanyuwa always
@YotamPhiri-t8k
@YotamPhiri-t8k 16 дней назад
Mawa muyenda bwino madala God is wti us all the time
@Enifa-pj6kc
@Enifa-pj6kc 27 дней назад
Osatumiza chinthuz cha galimoto yanu kwa anthu plz Mr mtanyiwa
@SamManda-f4s
@SamManda-f4s 27 дней назад
God bless comrade mtanyiwa we love you so much
@gregchisuse830
@gregchisuse830 27 дней назад
May God protect you
@DiannaJanga-y4k
@DiannaJanga-y4k 24 дня назад
God bless you big brother waife aMalawi
@Costance-nf7ue
@Costance-nf7ue 24 дня назад
God bless you and protect you
@charlesjimu6054
@charlesjimu6054 27 дней назад
May God bless you and protect you with His long hand.
@MandalaChaona
@MandalaChaona 27 дней назад
MTANYIWA is a Chosen one whatever he gets is a blessed thing from the living God. Kuwadekhera Bas Brother Mtanyiwa, Satanic ya MCP yafika ponunkha. Brother Mtanyiwa keep it up God will never allow any evil to fall on you,the living God wants you to accomplish his Mission The true living God never fails. Stay blessed 🙏 Irmao MTANYIWA Stay safe a minha Irmao ✊✊ You are protected and covered in the blood of Jesus Christ.
@GiftMathewe-fr3kn
@GiftMathewe-fr3kn 27 дней назад
Mumandimvesa kukoma God bless you Mr Mtanyiwa
@MilesMakhamba-cp3vv
@MilesMakhamba-cp3vv 12 дней назад
Iiiiiii go deeper Comrade tikudziwa dzambiri
@LuckiaMatemba
@LuckiaMatemba 6 дней назад
Mulungu akutetezeni big muyenda boo
@blessingsmofat
@blessingsmofat 12 дней назад
god bless u mr
@kasimmussa-c5v
@kasimmussa-c5v 27 дней назад
Timakunyadlan Mr Tanyiwa Mulungu Azikudalisan each and every day ❤🙏🙏
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 27 дней назад
May Allah bless you Comrade Ntanyiwa
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 27 дней назад
Awuzeni chilungamo, anthu akupha awa, zikomo mulungu wathu, potipasa inuyo a comrade antanyiwa zikomo mulungu wathu, Ambuye apitlize kubisa moyo wanu, mumatiyimilira inu, kopanda inu, sibwenzi tikuziwa izi, chilungamo ichi.
@DicksonDavie-p6b
@DicksonDavie-p6b 27 дней назад
Nice ntanyiwa bundle yathu ikupindula 🎉
@LovemoreChimera
@LovemoreChimera 27 дней назад
Am surely God protect you wherever you go
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 27 дней назад
More fire mr comrade ntanyiwa timve basi mumakwana ntanyiwa more fire Allah azikuyang'anirani mpaka muyende bwino mr comrade ntanyiwa
@Agnessnkhambure
@Agnessnkhambure 24 дня назад
God protect you mtanyiwa
@DavidKantukule
@DavidKantukule 24 дня назад
Bwana Mtanyiwa musamupatse mpata Chikangawa tiyeni naye
@HarryMakwale
@HarryMakwale 27 дней назад
You are number one mr ❤❤❤❤
@hastingskayange
@hastingskayange 27 дней назад
Ndipo onse amene anankhuziddwa ndi kungwetsa Kwa ndege onsewo adzamangindwe ndipo onse adzaphedweso..osanyengelera ayi anthu anewa ndiwoipa
@MichaelHastingsGodfreyMvula
@MichaelHastingsGodfreyMvula 24 дня назад
Southern Region is blessed with three former presidents. There is no way people can lack food when they are there. That can't be the fault of a leader but out of selfishness. Unfortunately, any game that is played out of anger, is always lost.
@AlexanderBilliat
@AlexanderBilliat 27 дней назад
Our own comrade mtanyiwa
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 27 дней назад
God bless you comrade Ntanyiwa
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 26 дней назад
Tipulumuseni chonde Mr Ntanyiwa
@KondwaniHara-i2v
@KondwaniHara-i2v 9 дней назад
Mfana wogaza bho yachilima video mlibe😊
@yamikaniraphael4975
@yamikaniraphael4975 10 дней назад
Umakawana Mrntanyiwa
@JosephLuwembe-w8k
@JosephLuwembe-w8k 26 дней назад
God bless you people
@Iponga
@Iponga 27 дней назад
Antanyiwa mulungu azikudalisani tilimbali yanu osatopa ayi mulunguso akutetezerani mm ukugwira tchito yopambana
@PhiripChinkango-k5p
@PhiripChinkango-k5p 26 дней назад
Big up comrade ntanyiwa
@jeanbotomani9081
@jeanbotomani9081 27 дней назад
Uyu apweteka anthu
@EvasonThupilifana
@EvasonThupilifana 27 дней назад
Tiyenazo Mr DC Ana azadelela ❤
@TressLuka
@TressLuka 27 дней назад
Game on Mtanyi...... ayaluke basi. Machine MEC ablokedwe basi 😅
@MARAWIANMEDIAFM97
@MARAWIANMEDIAFM97 27 дней назад
Ahhhaye NKHANGA ZINAONADI NTANYIWA ON LIMPOPO FM RADIO STATION 📻❤️❤️💯 more 🔥🔥🔥
@MichaelHastingsGodfreyMvula
@MichaelHastingsGodfreyMvula 24 дня назад
None can accept to have Likoma to be given to an individual as was the case with giving Chikangawa plantains and bus depots of Malawi.
@HarrisonJimu
@HarrisonJimu 27 дней назад
Keep it up boss but you have to protect yourself from this ng'ona government
@MISHECKBANDAH-m3h
@MISHECKBANDAH-m3h 27 дней назад
Kkkkk km mtanyiwa anva naye madzi ndipo anthu awawa azathawa mmalawi muno
@KetrinaMpachika-c1p
@KetrinaMpachika-c1p 20 дней назад
Ndipo mtanyiwa umakwana ndipo akha madzi chifukwa chauchitsilu wawa coz uzingalula kumene mpaka aone polekera kkkkkk
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 27 дней назад
Lipopo FM number one ❤
@MillyKachepa
@MillyKachepa 24 дня назад
Uyu anatigulitsa kale aaaa sindkuona bwino😢😢😢😢
@MandaAlick
@MandaAlick 17 дней назад
Umandivetsa kukoma pa chilungamo chanu antanyuwa
@phillipchampoxychapola4165
@phillipchampoxychapola4165 27 дней назад
Keep on updating us
@LuckiaMatemba
@LuckiaMatemba 6 дней назад
Ambuye atuma David kutipulumusa
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 27 дней назад
Mulungu anasankha inu comrade ntanyiwa kuti mutiyimilire pa Kati pathu, ndipo Mulungu yemweyo ndamene atakutetezereni kwina kuli konse mutadzapiteko koma nde a pule agundika tu ndi mwana wawoyotu eishhhhhh China chilichonse mukufuna chikhale chanu nde mukatsamutsa anthuwo apita kuti? Ndakayika ngat anthu akulikoma ngati atadzakubvotereni
@ROBERTMUKHAYA
@ROBERTMUKHAYA 27 дней назад
Pita ku dzalanyama kulive a police ulowa mozambiki uyoooooo
@YonaPearson
@YonaPearson 27 дней назад
Ngani iyi ndiyowona security ili pa mwadza bodar mmm
@BrightKabvinah-j3f
@BrightKabvinah-j3f 24 дня назад
Fire dem mtanyiwa 💥
@KennedyMangani
@KennedyMangani 24 дня назад
Ulemu wanu Thyolo yonse imakunyadiran Nyanyowa woyeee
@ChiefJustin-cl8jl
@ChiefJustin-cl8jl 27 дней назад
Ntanyiwa mulungu asipitiliza kukudaliza tilinawe mmapemphelo
@WisdomJeremiah-s3y
@WisdomJeremiah-s3y 27 дней назад
Kodi Malawiyi ali mumanja a anthu otani zinayamba zachitika nkale kugulitsa mbali ina ya dziko?? Tiziti achakwera, zikhale, kunkuyu, chimwendo, Hala ndi anyapapi enawo onse achita misala ndi mwazi waku chikangawa???
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 27 дней назад
More fire palibe wina ali yense angapange Allah azikuteteza thawi zonse
@WellingtneblackisonWaidon
@WellingtneblackisonWaidon 27 дней назад
AComored Mntanyiwa musalekelele Malawi Kuti apite ki dzenje ayı monga pa nkhani ya ifa ya saulos chilima ife tonse imatiwawa kwambiri
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 27 дней назад
Comrade ntanyiwa osaopa osatopa osafooka Allah atimenyera khondo kuti chipani chamagazichi chituluke m'boma
@LeversonMondela
@LeversonMondela 26 дней назад
Bale wanga mulungu akupase moyo wautali ife tikudalira iwe kut utiombola from chikangawa party
@PaulKalima-i1j
@PaulKalima-i1j 24 дня назад
Go ahead Manyiwa
@DarlingtonChaura
@DarlingtonChaura 27 дней назад
Allah akbar
@WellingtneblackisonWaidon
@WellingtneblackisonWaidon 27 дней назад
Mr Mntanyiwa mulungu akupatseni Moto wautali chifukwa dziko lidali mtulo koma inu mwali tsegula maso
@BenjaminDickie-k6e
@BenjaminDickie-k6e 24 дня назад
Likoma ife amalawi sitinaike pa for sale iwo zimenezi akuzitenga kuti
@AuphieBannet
@AuphieBannet 27 дней назад
MULUNGU ADZIKUTETEZELANI ndikukusungani moyo wautaaaaaali Emeen Tili naanu ndiithu
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 27 дней назад
Powerful 🙏
@grinesskuyere
@grinesskuyere 23 дня назад
Under cover bambo
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 27 дней назад
Koma Chikangawa ulimba 😅😅😅😅😅😂😂😂😂yomweyo galu iwe Chikangawa
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 27 дней назад
Koma Mtanyiwa muli mwano wa nyooo 😅😅😅😅😂😂😂,koma ana achikangawa mulimba???mwachepa kwambiri achina Chikangawa 😅😅😅😅😅😂😂😂😂
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 24 дня назад
Machine!
@fahadmilanzi
@fahadmilanzi 27 дней назад
More fire Ntanyiwa
@cynthiandekhakatundu6890
@cynthiandekhakatundu6890 27 дней назад
Brother ku UNGA komweko amukwizinga nawo mafunso ukhuku onse balala kukanika kuyankha mafunso .... Amudzudzula kuti wanyamula mbumba yake kkkk ayanba chibwibwi ...
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 27 дней назад
Akabwila 😂😂😂 atilidwe battery basi ali pafupi
@SaidAbian
@SaidAbian 22 дня назад
Apanga misala ngati sakugona yoooo
@mollymasangano473
@mollymasangano473 27 дней назад
Amalawi tisalole kuti Likoma ILAND ligulitside chimenechi ndi Chibwanatu.😢😅 Anthu Adyera MCP(CHIKANGAWA CHAKWERA)
@DavidKauzu
@DavidKauzu 24 дня назад
Likoma kuyambila kale kale asamunda kamuzu pamkana pano ndi malawi nde zayambila pati
@WillmotChiuimia-vr6ou
@WillmotChiuimia-vr6ou 25 дней назад
Zowona zake anthuwa kumpha basi achoke
@mikesangano6624
@mikesangano6624 27 дней назад
Mumatiimilira Comrade Mtanyiwa, Onse anatengapo gawo pa ndege inagwa Mchikangawa, akanthidwe, azunzike, ma families awo asapeze mtendere, apenge misala ndipo mizimu ya anthu Onse adafera mundege muja, iwadzunze Onse anatenga gawo powapha monga adazunzikira adaphedwawa. Mkwiyo wa Mulungu ukukantheni ndi moto woopsaa ndipo mupenge misala nonse komanso muthawa mmodzimmodzi mu dziko lino.
@ChipiliroLungu
@ChipiliroLungu 24 дня назад
Antanyiwa inu ndale zanu mwaxiyamba molakwika , ndale sitimadzibisa kumbuyo kwa azanu ayi
@DanielMbendera-e3p
@DanielMbendera-e3p 14 дней назад
Trueth shall prevail
@veronicagullo9373
@veronicagullo9373 24 дня назад
Ngati muli dolo Man dzionetseni osati zonisalazo iyaaaaa
@DanielMbendera-e3p
@DanielMbendera-e3p 14 дней назад
Menemenetekelosiufarasi
@johnw.posomanchanel4023
@johnw.posomanchanel4023 24 дня назад
Ntanyiwa sangamuthe. mcp iyi ikutenga ma cyber security ku israel
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 27 дней назад
Palibe amene angakugwireni comrade ntanyiwa Allah ali nanu limozi mcp onse ndi mbuzi zawathu ndi manganya nayeso ndi mbuzi onse a mcp ndi mbuzi ndi dan lu
@philipoga2401
@philipoga2401 27 дней назад
bushiri mboli yake apumilansoo nmwamba chifukwa nama nchende ameneyuu afunika azatumizidwe ku south africa
@AbdulsartalSartal
@AbdulsartalSartal 14 дней назад
Auzeni aziwe chowona
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz 27 дней назад
Amva nyekhwee onse anapha chilima
@Edithmchinza
@Edithmchinza 27 дней назад
Aliyese amene anatenga gawo pa lmfa lmeneyi akufa
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 27 дней назад
Mudziti wina akuba misonkho ya anthu omwe akudya chitedzeo ndi mwana wake mkumaba ndalama ku immigration Inu zanu zanthumba mwanu mukuthandiza anthu ndi akubeledwao,Koma chakwera he is cursed ndi family yake yomwe but they will pay for what they are doing
@BadmanbBeesca
@BadmanbBeesca 27 дней назад
Umakwana ntanyiwa ndipo ine ndi makukonda avulazeni agaluwa
@DennisTobias-b4r
@DennisTobias-b4r 24 дня назад
Malawi wasanduka dziko la family sizinaoke mkale lonse dziko president kuyendesa ndi family his sons and his daughters, cousins and his friends
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj 27 дней назад
Mr mtanyiwwa ulemu wanuw bwanji osangokalla president of Malawi shifunkwa umankwana nkwambilli 🇲🇼🇿🇦
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 27 дней назад
Tell dem Ntanyiwa
Далее
Kangaude Kucheza ndi Mr god know Part 2
59:17
Просмотров 23 тыс.
Shadreck  Wame - Unyamata
41:41
Просмотров 39 тыс.
What’s your height?🩷🙀💚
00:59
Просмотров 4,3 млн
CHILIBE MANTHA ICHI!
15:35
Просмотров 1,8 тыс.
Rev Alexander Kambiri  Odala Akufa Mwambuye
19:05
Просмотров 219 тыс.
KHASU-Malawian movie_PART 1[Akila films official 2024.]
1:06:28
T.Y. Nyirenda - Tsiku lalikulu padziko lapansi.
47:35