Тёмный

UMBONI WA IMFA YA JOSSUA MZEMBE 

Nkhalango Multimedia
Подписаться 20 тыс.
Просмотров 53 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 27   
@PeterLingtone
@PeterLingtone 10 месяцев назад
God bless you woman for your heart
@GraceMuthema
@GraceMuthema 10 месяцев назад
Agness akufunika chitetezo chokwanira mmmmh naeso atha kukhala pa chiopsezo ,,,,,ambuye akudalitse Agness ndpo akuteteze
@PeterKachala-fw6ng
@PeterKachala-fw6ng 8 месяцев назад
Kumakhala ndi Moyo Ngati wa dzanuyu please azimayi
@marianyirenda
@marianyirenda 11 месяцев назад
Chinali chinsinsi cha mulungu kuti malemuyo adziwane ndi Aggie chifukwa kupanda Aggie kumuona malemuwo ali ndi Mark sipakanakhala umboni weni weni
@NoahChaseta
@NoahChaseta 11 месяцев назад
Asatana osazindikila.. They will think malawi police is useless until they start following you..
@fredlemani
@fredlemani 10 месяцев назад
Kumanda amataniko mzimayiyu?
@RAJABUALLIE
@RAJABUALLIE 11 месяцев назад
Amayi inuyo Ambuye akudalisen🙏
@ChisomoMsiska-oi2vg
@ChisomoMsiska-oi2vg 11 месяцев назад
Nkhani yomvesa chisoni😢
@GenialaChalera
@GenialaChalera 11 месяцев назад
Ife tikudziwa zolinga za nkhani imeneyi mukuchita mantha ngakhale mutelo siphweka
@jonesmichongwe8632
@jonesmichongwe8632 10 месяцев назад
Mwazi wa munthu siwamasewera
@bwatanbanda94
@bwatanbanda94 11 месяцев назад
Zokhudza zed chopherana ndichan? Mmm
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 11 месяцев назад
mayinu Ambuye akudalitseni
@MussahMandebvu
@MussahMandebvu 11 месяцев назад
Koma dziko?😢
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 11 месяцев назад
eish abale 😢😢
@JohnMoles-e6h
@JohnMoles-e6h 11 месяцев назад
Ayi awuse mutendele bwana mzembe tilipano kudikila zosatila
@fredlemani
@fredlemani 10 месяцев назад
Mmaziwa akati " kuusa mu mtendere " kumatanthauza chiyani?
@SdreckLashid
@SdreckLashid 11 месяцев назад
Mkhaniyi sindikuyimvesa ine
@AleksaWilliams
@AleksaWilliams 11 месяцев назад
Chomuphera ndi chani abale😮
@fredlemani
@fredlemani 10 месяцев назад
Ali kumoto pano.
@Ruth-y5q9n
@Ruth-y5q9n 11 месяцев назад
Kusakhutisidwa ndizimene mulungu wakupasa dziwa kuti ngati ulibe chinyenga kapena kunama boza ngakhale osapita kwasinganga ukhoza kuwinabe basi munjila ina iliyonse chifukwa mulungu amakhala nawe podziwa kuti ntchito zakha ndizabwino lelo ndiizi kuziwilatu kuti nkuluyu anali wabodza nchifukwa analudzapo pachiyambipo komanso nkuluyi ndiwoyipa ntima mukuziwa kale nsinganga zizimba zake nanga kumeneko akadakhala kuti zinayenda kenako ndikumuuza kuti apa pakufunika mwazi wamuthu koma akhale mwana wanu muthu ameneyi mukundiuza kuti sakanakapha nkuthekatu mwina ndinjila yamulungu kuti zikhale choncho kusiyana ndikuti apitise ambili akuntundu wawo chifukwa chau mp basi anthu andale ndiafitidi wapanga bwino ena atengelepo phunzilo wakuphayo asamangidwe chifukwa sanamupitile kunyumba kwake kwa mp yo ngati mukudziwa pakati apo akhaka anthu akutumiza ma mesegi oti mwawina ndalama anthu amapasidwa malo oti akatenge koma akafika kumaloko amapangidwako chipongwe ndikuwabela koma boma linangoti tiyeni tikhale wochenjela anati tidamangotengeka ndizilizonse uyu osamudandaula wafela ntcthito zake zofuna njila zamundima ayende bwino amafuna azawinenso azizazunzisaso athu ndinjala makomomu
@blandinabonaventure
@blandinabonaventure 11 месяцев назад
Kma
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 9 месяцев назад
km abale 😫😫😫😫
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 11 месяцев назад
😭😭😭mavvto
@gkldbmsgksldm5584
@gkldbmsgksldm5584 11 месяцев назад
Zovuta eti
@YamikaniChakwemba
@YamikaniChakwemba 11 месяцев назад
Zovuta kumvesa
@yanjalaura3355
@yanjalaura3355 10 месяцев назад
🥲
@FebsonMoyo
@FebsonMoyo 11 месяцев назад
Very bad
Далее
TONDE WADULA EPISODE 51
27:39
Просмотров 26 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 125
27:37
Просмотров 14 тыс.
Kunte - Chuma
10:24
Просмотров 37 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 124
27:20
Просмотров 22 тыс.