Тёмный

NKHANI YA LAWYER ALEXIUS KAMANGILA IJA YAVUTA MA BUNGWE ENA ALOWELERA NDIPO LERO APANGISA CONFERENCE 

Makosana
Подписаться 107 тыс.
Просмотров 9 тыс.
0% 0

Опубликовано:

 

13 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 63   
@RhoxinahMalamba
@RhoxinahMalamba 3 часа назад
Bravo!! Mr. Kamangira Dzuka Malawi Dzuka. Ma youths this is the right way to fight for our country osati kutumidwa kuyambitsa zisokonezo. Nthawi yakwana kuti achinyamata atenge udindo to shape their future. This is very commendable. More fire bwana Kamangira.
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 5 часов назад
Me too , I will in front... Amalawi nthawi yakwana kuti Malawi yopulumuke ku muchitidwe wobela amalawi aumphawi
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 3 часа назад
Congratulations brother Kamangira Mulungu akhale nanu nthawi zonse angakhale khamu la wanthu limadana ndi chilungamo pambuyo panu ngangangaaaa timakunyadirani kopotsa zedi
@MariaGatoma
@MariaGatoma 3 часа назад
Mr kamangila pitilizani kukoza Malawi wathu,,,wakutumani ndi mulungu,,anthu akufa osalakwa,,,kumangidwa,,okuba ali khale chifukwa ali ndi ndalama,,mulungu wakutumani kuti mupulumuse anthu osauka
@terezazakeyo2285
@terezazakeyo2285 Час назад
Congratulations brother kamangila,, God protect you and your family
@PhiriChiyambi
@PhiriChiyambi 3 часа назад
Let all Malawi'an tigwilane manja timusspote mu njira ili yonse chinyengo chikuchuluka kundende angopezeka osauka okha mbava zikuluzikulu zolemela sazimanga Kaya ndalama let's lez fund to support this laywer
@FredKanyerere
@FredKanyerere 4 часа назад
Well done brother kamangila.
@williamsmhango4318
@williamsmhango4318 Час назад
Loud and clear, iwe nde munthu 🔥🔥
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 3 часа назад
More fire 👦 🔥 guys 🇲🇼 Malawi is badly now 😫 😢 😩 be strong 💪 👏 we trust you guys 👦 more fire 👦 🔥 again
@ChristinaSimwaka
@ChristinaSimwaka 2 часа назад
Anthu akanena za çhikangawa mcp kuli ziiiii akuwapo kanthu
@MillieMalakam
@MillieMalakam 2 часа назад
Kamangila bolani asagudwe ndi mcp chifukwa tut mcp yalusa kwambili ndi kugula. God ahead u my brother
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 Час назад
More fire CSOs pambuyo pa Kamangira
@MrMagombo
@MrMagombo 4 часа назад
Apa Justice wo alowe mu khoti ndi a kamangilawo. Ndipo ikhale pa radio. Mlandu omveledwe ndipo ma CSO ndi ma Judge atatu amvele mlandu wo. Guys dziko limene athu akukayikila ma Court limakhala Lawlessness.
@emmanuelchirwa3420
@emmanuelchirwa3420 4 часа назад
Well done ✅ guys good job thanks, again well done guys together we can make Malawi better place for all,,
@twaibupatrick-k1n
@twaibupatrick-k1n 3 часа назад
Komaso ukunena zooona kuyamikaso ndikwabwino kwayamika anthu amenewa
@ziwani3682
@ziwani3682 4 часа назад
Powerful message
@AlexBanda-i1e
@AlexBanda-i1e 2 часа назад
Keep it up kamangira
@maxwellmashon4897
@maxwellmashon4897 Час назад
Kamangila will be our Attorney General next year when DPP will be in power
@williamsmhango4318
@williamsmhango4318 Час назад
Ndipo uyu wapita uyu, end of his journey
@JosephIsaac-s1c
@JosephIsaac-s1c 4 часа назад
I see changes in Malawi 10-15 years come
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 4 часа назад
Ma judge akakhala kuti ndi achinyengo dziko so silimalongosoka, komanso ma judge akumalawi panopa ali mbali ndi boma
@KikaImran
@KikaImran 2 часа назад
Kamangira ❤❤
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh 4 часа назад
Dziko lidaipa ili it's better maiko anzathu adaonongeka koma ku zachuma adasunthako,koma sikwathu kuno umphawi wa thoo koma kumangopondeleza anthu osuka Iwo nkumalemera modabwitsa why Malawi??? For example njala ili muziko muno sibwino kumafinyana tokhatokha pofuna kusangalatsa anthu oononga dziko ndi odzikonda 😢😢😢
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 4 часа назад
Powerful massage
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 5 часов назад
Even the devil knows that justice is sold in the country 's courts .
@SymonKachala-b2y
@SymonKachala-b2y 4 часа назад
Nkhani ndiyayikulu iyi
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 4 часа назад
Osawanyengera a justice lenani Manda atumbukawo kuopitsa mtundu wao..ife a malawi tatopa ndi zachinyengo zimene atumbukawa amachita mma office a bomawo..kodi ndi umphawi kodi ? Nkuona Dr H kamuzu Banda anawathamingitsa atumbuka onse azipita kwao in 1987..cos they are all corrupt .them are thieves.. ndiye apa akapitiliza onse atumbuka adzipita kwao not live in the southernbregion or the central region.
@Felie-p7l
@Felie-p7l 4 часа назад
Asasowetu ameneyo
@alickkachepa3801
@alickkachepa3801 5 часов назад
Let's protect this property ❤
@SymonKachala-b2y
@SymonKachala-b2y 4 часа назад
😊😊😊😊 I totally support this statement
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k Час назад
Gud one
@lenardmakuya
@lenardmakuya Час назад
Kamangira woyeee!!!!!
@GodfreyKamphiripiri
@GodfreyKamphiripiri 3 часа назад
Powerful message ❤❤❤
@peterbakuwo1249
@peterbakuwo1249 2 часа назад
I can sense seriousness in these guys... Go,guys go and bite hard.
@Haka-tb8ih
@Haka-tb8ih Час назад
If Kamangira happens to be touched in any way, ndekuti the judiciary is accepting their wrongs.
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 4 часа назад
IT IS TIME TO RESTORE MALAWI BELOVED COUNTRY
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 2 часа назад
Ayitu uyu yekha simukhwasula akuimila amphawife ma judge ena ndiomwe agudwa ndi boma cholinga azathandizile kubela chisankho
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 4 часа назад
Well done
@promixphotography8056
@promixphotography8056 3 часа назад
Vuto lomwe tili nalo ife aMalawi ndi matha chifukwa zinthu zambiri zikukhala zovuta chonchi tiyeni tione maiko ena akupangira kutuluka sikukutengera kuti atipha ai, ndipo sangaphe tonse ai.lets open our 👂 ndikuonaso
@BeatriceSaulosi
@BeatriceSaulosi 2 часа назад
Ndipo Nkhaniyo ndiyoona a Malawi tili ndi matha anyooo
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c 2 часа назад
Nthawi yakwana
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 4 часа назад
Chilungamo chibwere poyera basi
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 4 часа назад
Aaa mamvuto TIKUKOMANA NAWO LELLO AMALAWI NDIWOMWE AMABWALO LAMILANDIKU KUGAMULA MWA DZIPHUPHU LELO MALAW ALI PAMOTO APA AGALU KWABASI
@SprianoJeke
@SprianoJeke 2 часа назад
Restoration
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 3 часа назад
Truth is a spirit from God. No one can attack the truth because it's a product of Holly spirit. No matter how much the corrupt judges would try to silence the truth, they cannot win. Kamangila is a God sent lawyer to save justice at it's extreme level
@MissoutNiceday
@MissoutNiceday 4 часа назад
These people the dont have ashame ,when the west money for poor people.
@FrankKambwani
@FrankKambwani Час назад
Itangobwera mcp mabungwe onse adapangidwa corrupted ndi Chakwera
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 4 часа назад
Judiciary is wrong, you think kamangila is mentally ill... judiciary is rotten
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI 4 часа назад
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
@RuthUnderson
@RuthUnderson 2 часа назад
Anthutu paja amafunsa mukuti mulandu wachilima mwauthesa zatheka bwanji amawona ngati anthu athela pompaja lelo ndizi zotupa zingophulika zokha mzimu wachilima uzusa zambiri mdziko muno mene kuchele aliyense akubwelesa simoko yake mulungu wakwiya mdiulamulilo womwe ulimalawi muno
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 2 часа назад
Palibe chomwe boma linkgachite ma jugde onse anagildwa kale ndi boma
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 4 часа назад
Kamangila anaconda dziko lake wachita bwino kuyalutsa a galu amenewa kamangila suli wekha tili pambuyo pako ndinthawi yoti chilungamo chiyende ngati madzi coz chikangawa akuononga malawi
@SprianoJeke
@SprianoJeke 2 часа назад
Kwatentha 😂 palibe kucheza
@JerieWytonTengani
@JerieWytonTengani 3 часа назад
Zikomo kwambiri pothandiza dziko lino kwa Malawi aliens kuti tiziziwa chilungamo kwa anthu akuba ndalama za misonkho Mexico la Malawi.Wabayo asathawe ndipo tiwadziwe ndithu poyera.
@JerieWytonTengani
@JerieWytonTengani 2 часа назад
DONT LET THEM,BUT WE NEED THE TRUTH TO FOCUS IN OUR NATION .INDEED IT IS HAPPENING IN OUR GORVERMENT OF MALAWI.START WITH CHAKWERA AND ALL MINISTERS,JUDICIAL ,AND ALL DEPARTEMENTS.
@ChifundoGalusa
@ChifundoGalusa 4 часа назад
Corruption Corruption
@Chiso2019
@Chiso2019 Час назад
Mumayamba choncho you just want to be relevant ....tikuonani komwe mutanthere anthu oyipa inu....
@ruthchikhoswe6028
@ruthchikhoswe6028 2 часа назад
Kwachema
@Yamikanilikolome
@Yamikanilikolome 2 часа назад
Following
@williamsmhango4318
@williamsmhango4318 Час назад
Loud and clear, iwe nde munthu 🔥🔥
@Johndimechikonda
@Johndimechikonda 2 часа назад
Powerful message
Далее
这到底是怎么做到的 #路飞#海贼王
00:10
Просмотров 4,2 млн