Тёмный

ZODABWISA ZIMENE ZACHITIKA LERO A CHAKWERA ATANGOLOWA MU NSIKA WA LUNZU LERO KU BLANTYRE 

Makosana
Подписаться 107 тыс.
Просмотров 9 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

13 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 100   
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 3 часа назад
🤣🤣🤣Ati kupita komwe anamva kuti akunyadila kumva kuti wafa chakwela zopusa kumakhala busy nd social media zachisoni
@McsensioMbawo
@McsensioMbawo 2 часа назад
Campaign sindalama tamayendani kumuzi muone anthu mmene akuvutikira
@macrinenduna1024
@macrinenduna1024 2 часа назад
M'Malawi muno muli zitsiru. Chikwawa ndi boma lokhalo linawonetsa kufuna zosintha. Mbava zili maboma enawa mnzosadabwitsa anali amasikini awa.
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 Час назад
Chikangawa band mwathedwa nzeru basi kkkk😊
@YahayaIssah-c3r
@YahayaIssah-c3r 2 часа назад
Pasana Pako iwe ukayamikire sewu 😅 azanu akudya chitedze
@domminicchikalenda
@domminicchikalenda 2 часа назад
Bravo Mr President for visiting your people and have a feel of what your people are going through. Short message of wisdom and unity
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd Час назад
Za ziiii8 ndiyeeee zisitha chaniiii zimenezi....
@GraceMasiye
@GraceMasiye 2 часа назад
Ku msika wa lunzu ckomwe kuja amavina kusangalala kut apule amwalira kuja😂😂😂kangachepeko makosana idyani Koma No Vote,😂😂 yomweyo ija eti
@johnmsona8845
@johnmsona8845 2 часа назад
Koma kumalawi kuli zitsilu guys 😮😮😮
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 3 часа назад
Nde mwagula ufa kuti mukatani nawo, malo moapatsa anthu amene akufa ndi njalawa chakudya.
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 2 часа назад
Idyani ndalama koma no vote
@JosephIsaac-s1c
@JosephIsaac-s1c 2 часа назад
Akulu kumaenda inu musakweze kamba mumtengo mukuonekeratu kuti mukuvutuka nenani zopempha bs palibe zothokoza
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 3 часа назад
Zayimbika zomadya usipa misika zija andale akumalawi ndiopusa
@ThomasJohn-j8x
@ThomasJohn-j8x 2 часа назад
Akumkuyu amalankhula mogawanitsa anthu
@HilidaHilida-e6p
@HilidaHilida-e6p 2 часа назад
Mudyelen ameneyo vote ilimutima
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd Час назад
Koma ndiyeeee
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira 3 часа назад
Iwe ndiwe wabodza tango kambani zopephazo chitukuko chake chiti zaziii nde ukuona ngati akupatsa ndalamazo
@LawrenceBelson
@LawrenceBelson 2 часа назад
Usachule dzina la yehova pachabe chikangawa
@EvansKachulu
@EvansKachulu 3 часа назад
Uku ndie kupepela komweko anthuo amavina atamva kt watisia ukupitaso komweko ukuona ngat akukukonda uzinbele chison anthu akubwerera ma 2 pin not love of you Apm is our vote
@SaeedMaunde
@SaeedMaunde 15 минут назад
MBC ,shame a biased television
@AsiyatuMazembere
@AsiyatuMazembere 2 часа назад
Zikuthandiza chani izi kuntundu wa amalawi zomvetsa chisoni akawagula zithu anthu kapena 5 pakhala kusitha kulikose amalawi ndife zomvetsa chisoni kwambir
@ChikumbutsoChomali
@ChikumbutsoChomali 2 часа назад
Koma iwe ukuyamikila zichan apa? Iwe opusa bwanj osangopepha bwanj akupase ndalamazo
@CadTafa2
@CadTafa2 4 часа назад
Osamanga misika yabwinobwanji
@charlessulumba2521
@charlessulumba2521 2 часа назад
This is a sign of poverty in Malawi.
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 3 часа назад
Kkkkk msiska wake siomweuja umavinawu
@AmosJere-ir4zr
@AmosJere-ir4zr 3 часа назад
Kuwanamiza awo akufuna awakawe chabe
@ChristinahNkwanda
@ChristinahNkwanda 3 часа назад
​@@AmosJere-ir4zr !] *v
@Alomwe
@Alomwe 2 часа назад
Chakwera Wants to be told lies. The truth is what they did after kumva kuti wafa
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 54 минуты назад
Achimwene ndinu iganiza mopelewela
@MisheckKamwendo-w9n
@MisheckKamwendo-w9n 2 часа назад
Mkulu akuyakhulao akungoonekeratu kuti ndi mbuli
@ChrissySalimu
@ChrissySalimu 3 часа назад
Mmmmmm nseu wake wahaf wooooo
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Час назад
Ndi bwana bwana akakhala alipompo akangosuntha ali km galu ameneyi😅😅
@BarnetMwanyula
@BarnetMwanyula Час назад
Kkkk kuwanyengelera kumeneko anthu anakwiya bac . Kkk eeew gyz mavutotu awa eeee mbiri safuta anthu awawa amasangalal atanva kuti bwana afa ndeee Oro atagula mulu wamatemba 100, 000000. Zilibe tchito
@LobertSamuel
@LobertSamuel 23 минуты назад
Chilima uja osazaphweketsa
@LloydChiposa
@LloydChiposa Час назад
666million Malawi kwacha mangoleka kuthandizila anthu akufa ndi njala inu mukugulila magalimoto...shmmm nde Ma Lexus awiliwoso ndekuti ndi billion
@DavieKumbanga
@DavieKumbanga Час назад
Tigaileniko ngongoleyo plz
@ehinsupport3217
@ehinsupport3217 3 часа назад
Macadet munya ndithu, tangiwonani nokha mmene dzilili pa Lunzu . Nsanje mukufa nayo
@OsmanChisi
@OsmanChisi Час назад
Koma munthu mesa dzana mmakondera Kuti wachita bwino wamwalira siinu?kkkkkk
@NewtonGondwe
@NewtonGondwe Час назад
Munthu wosaphunzila ndichoncho
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 3 часа назад
Zaziii
@HamiltonwaNamuwah
@HamiltonwaNamuwah 3 часа назад
Izizo sizingatithaze ata pang'ono . Tikufuna Economic and achepetse corruption.
@kenchitenje
@kenchitenje Час назад
ndiwe galu uli galimoto iwe osangopepha bwanji
@isaaczuze
@isaaczuze 46 минут назад
Robert jumbe mbuzi yeniyeni
@ElizabethAlick-e6b
@ElizabethAlick-e6b Час назад
Ndinu nomwe amene nukanvina mutava kuti chakwela kuti wamwari mumkavina pano muti boma ndilimweri 🤭
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 3 часа назад
Pajatu nthawi ya campaign ndi imene amayenda misika kumagula masamba.
@NoraSabit
@NoraSabit 14 минут назад
😂😂😂sintu sake
@EmmanuelPhirip
@EmmanuelPhirip 2 часа назад
Like this gvt
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l 33 минуты назад
Munthuyu alibe ngakhale njinga,kukayamikira nsewu,osa atsitse zinthu,atsitse Kwacha kuti aliyense anvekukoma,aliyese azipanga momasuka,azipindura tsiku ndi tsiku,koma mbulizi zingofu zinthu zausilunasi,uchikape,chimudzi mudzi, sorry for that😒✋
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 3 часа назад
System yandale yomagula zinthu munsika 🤣🤣🤣
@JosephMalata-v6y
@JosephMalata-v6y 3 часа назад
Nsika uyuyu nd umene MCP sikugona nawo tulo
@ehinsupport3217
@ehinsupport3217 3 часа назад
Ngati Kuli anthu dzitsiru nde ndi ma cadet, anthu osayamika inu ,agalu achabechabe. Boma ndilomweli ,sitikusintha ,opposition yake ndiyomweyi basi
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 3 часа назад
Apa ndiye muona ngati asintha chiganizo sumufunika basi
@AmosJere-ir4zr
@AmosJere-ir4zr 3 часа назад
Nkhan ndi imeneyo
@Issahdavie-w7d
@Issahdavie-w7d 3 часа назад
Landilani zakudyazo voti ndi mumtima bs at kugula mavoti kumeneko
@BenjaminKapale-k1f
@BenjaminKapale-k1f 3 часа назад
m.mene alili venda ameneyu pali kusintha kwanji pamoyo wake mbuli
@EnerstManess
@EnerstManess 3 часа назад
Wayamba kunyengelela mavoti galu ameneyu
@abdullalajabu5871
@abdullalajabu5871 3 часа назад
koma chilima amantha kulawa ndikudyala pomwepo anali dolo kwambili
@CharityKaonga
@CharityKaonga 3 часа назад
Paja nthawi yokudya matemba awisi yakwana
@MarryMartin-z6u
@MarryMartin-z6u 2 часа назад
Za ziiiiiii
@masakaunga4099
@masakaunga4099 3 часа назад
Munkasangalala kuti wamwalila lero mukukandila ndalama kwa yemweyo zitsiru a Malawi
@JudithKatungwe
@JudithKatungwe 3 часа назад
Ndalama akane??? Alandire zinazo pambuyo,vote nso mumtima
@masakaunga4099
@masakaunga4099 3 часа назад
@@JudithKatungwe mwagwanayo akulamulilanibe
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 3 часа назад
Bolanso manganya amakhola fanzitu.
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 5 минут назад
Ugalu wako vendor iwe
@IsaacPaul-vo5hy
@IsaacPaul-vo5hy 3 часа назад
Mudyeleni wakupezani dala
@AnnieJumaNaitanda-qj1iz
@AnnieJumaNaitanda-qj1iz 3 часа назад
Mhhhh nyenwa chinyenga aphunzitsi
@annamazingashaibuh6276
@annamazingashaibuh6276 31 минуту назад
Nseu athu adzidyaaa nonsense mulibe fundoo
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 3 часа назад
Paja dzana kunalitu ma dance kkkkk
@LuciusMaison
@LuciusMaison 3 часа назад
😂😂😂😂😂 zamanyazi galu uyuwochititsa manyazi
@BenjaminKapale-k1f
@BenjaminKapale-k1f 3 часа назад
Koma kuchikangawa sayima galu ameneyu
@NewtonGondwe
@NewtonGondwe Час назад
Mpisi wako galu iwe
@ceciliasokoh3779
@ceciliasokoh3779 3 часа назад
Za ugalu ndiye ufawo akausiya kuti
@MwayeMakwale
@MwayeMakwale 3 часа назад
Koma sitimuvoterabe
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 3 часа назад
😂😂😂😂😂chipha maso😂😂
@ChrissySalimu
@ChrissySalimu 3 часа назад
Kkkkkkkk kukusekanikoooo km mukupusa a mcp
@chikublea8982
@chikublea8982 3 часа назад
Waboza waganyu ameneyo
@RosinaPatel
@RosinaPatel 3 часа назад
Campaign kkkkkkkk
@MajiduMakiyi
@MajiduMakiyi 3 часа назад
Kusavuka ndi ndalama zakuba
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko 3 часа назад
Tionana 2025 😢😢
@VincentManyenje
@VincentManyenje Час назад
Mcp ndiyowinawina basi.
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 3 часа назад
Zazii
@ThomasPatrick-n3n
@ThomasPatrick-n3n 3 часа назад
Km okuchokabe bs
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 3 часа назад
Zadziiii
@RasheedAmifu
@RasheedAmifu 3 часа назад
Kkkkkkk
@ChaibishuSwadck
@ChaibishuSwadck 3 часа назад
Aaaaaaaaaaaaa saziiiiiìiiiiiii
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 3 часа назад
Zaziiiiii
@planmalawi-sm2cw
@planmalawi-sm2cw 3 часа назад
Umbuli
@McLoudStandy
@McLoudStandy 3 часа назад
😂😂😂😂
@HildaSingin-vm2tr
@HildaSingin-vm2tr 3 часа назад
This is no sense
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 часа назад
I don't think mcp can lose, coz they know how to unite people, it's very nice if a leader visiting his people and seeing how his people are serving , very good
@Alomwe
@Alomwe 2 часа назад
Go deep and then verify
@VincentManyenje
@VincentManyenje 2 часа назад
Bomaaaaaa iloooooo
@McsensioMbawo
@McsensioMbawo 2 часа назад
Campaign sindalama tamayendani kumuzi muone anthu mmene akuvutikira
@marryphili5419
@marryphili5419 3 часа назад
Za ziiiii
@chikublea8982
@chikublea8982 3 часа назад
Zazii
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 3 часа назад
Zaziiii
Далее
다리찢기 고인물⁉️😱 Leg Splits Challenge
00:37
Will A Basketball Boat Hold My Weight?
00:30
Просмотров 32 млн
BON KALINDO - 14/10/24 KWACHANO TIONE NYEKHWE
17:04
Просмотров 8 тыс.
다리찢기 고인물⁉️😱 Leg Splits Challenge
00:37