Тёмный

NTHAWI YA UMBULI KUIMBIRA MFITI MMANJA SH.ABOU SUFIAN KHATWEEB DAWOOD 

Qassim cedrick
Подписаться 103
Просмотров 1,8 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

2 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 15   
@MariamJaffali
@MariamJaffali 25 дней назад
Naam sheikh ma shaa Allah ndipo anthu amaopa kukhala kuqibula Allah awakhululukire zofooka zawo
@Musa-cz1nm
@Musa-cz1nm 26 дней назад
Ma shaallah ma shaallah ma shaallah
@UseniMailosi
@UseniMailosi 27 дней назад
Ameen inshaah Allah
@user-gk6bf7xe9g
@user-gk6bf7xe9g 27 дней назад
❤❤❤❤
@user-lf5qw7mk3h
@user-lf5qw7mk3h 17 дней назад
Km this kind of lecturing sometimes zumandikhuxa bwanj Mmalo moti muzapephelera amzanu chikhululuko bas muli busy achibekete Panopat kumalawik kuli zambil zoti kalel sizimachitikai inuo ophuziran muthawi yanu samasephan pakhan ya eid km lero ikangofik mumangotukwanizana apa Be humble muziwapephera amzanu chikhululuk jaman kozan zomwe zilipoz pano a a jaman
@MoneyTiririMgwagwa
@MoneyTiririMgwagwa 22 дня назад
Munakakamba zoonadi koma osatchula muthu ngat inu mwazindikila muchoonadi munakalalikila pazomwe inu mwazindikila ndi mene mwaphuzilila
@user-rl5zq1qr4d
@user-rl5zq1qr4d 22 дня назад
Ulaliki wabwino ndithu koma kuchula mbiri ya munthu omwalira kuti anali wa shirik its very unfortunate mukanangokhonza zimene inu munaziwona kuti ndizolakwika in directily not directily nkutheka ena analowa chisalam kuchokera kuzimene iye amapangazo inde tiwalemekeze ndi amene anasunga deen inu ozindikiranu musanabwere choncho tiyeni tiwapemphere chikhululuko osati kuwapepusa MAY ALLAH SHOWERS US ALL WITH BLESSINGS FOR BEING MUSLIMS
@MoneyTiririMgwagwa
@MoneyTiririMgwagwa 22 дня назад
Zoonadi kuzuzula kwa bwino
@AdamYas-ec9oc
@AdamYas-ec9oc 9 дней назад
Uyu sadayange mafuso amene ana fusidwa komaso tingopemba allah kuti abwelere kudarassa chifukwa hukum ya deen mutu mwawu mulibe
@IsmaelBilal-lh1pi
@IsmaelBilal-lh1pi 27 дней назад
Tiyeni tiwapangile ma duwah mwina kutheka amaizichita mu umbuli. Allah awakululukire chifukwa anatisungira Deen
@Qassimcedrick
@Qassimcedrick 25 дней назад
Amee
@JohnAsendi
@JohnAsendi 26 дней назад
Koma amwene ndi makusati mukulankhulana kwanu kwaonesa kuti wabwera kuzalimbana ndi anthu omwe anaphunzira kale kodi tizinena kuti muli PA chiwongoko ndiinu choti muziwe ndi chakuti dini ndi ntchito sizingagwilizane mupite Kwame e mukuwanyozawo samalandila ndalama kutha kwamwezi pomwe Ena inu mumalandila ndiye kumati uza zabwino zomwe akuchita ungokhala zonse ndizolakwika alibe zabwino zomwe akuchita
@Qassimcedrick
@Qassimcedrick 25 дней назад
Sheikh kodi mitiuza mu Quran pomwe aletsa kulandira ndalama ukagwira ntchito ya Deen pakati panu ndi ife pali Quran ndi MA hadith atumiki basi palibe zokangana
@JohnAsendi
@JohnAsendi 25 дней назад
@@Qassimcedrick mumalandila ndiinu ingo ndiuzani lembalo mu qraan
@JohnAsendi
@JohnAsendi 25 дней назад
@@Qassimcedrick mumalandila ndiinu ingo ndi uza lemba mu quraan
Далее
SURAT AL IMRAAN IN CHICHEWA
2:01:06
Просмотров 49 тыс.
Survive 100 Days In Nuclear Bunker, Win $500,000
32:21
EP 2 KODI SINAKWANE NTHAWI
14:20
Просмотров 1,7 тыс.
Kuganiza Mwangwiro - Kuvomereza Ukalamba
27:23
Просмотров 1,7 тыс.
MALANGIZO KWA AZIMAYI by sh. AHMAD MUSSAH
50:24
Просмотров 2,9 тыс.
Professor Said Hassan Zambia
3:17
Просмотров 962