Тёмный
No video :(

Oswald Jumani Kukamba Za Uladi Mussa 

Nyasa VoiceBox
Подписаться 26 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

29 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 42   
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 6 месяцев назад
Basi mdani wathu Ndi Njala Ndi maluzi very good speaking and special word anthu awadi alibe uchi,oladi is like a hunting dog amango kumba pamene Pali fungo za kanyama kamene kaditsa njira kumene akupita sakukuziwa Munthu wadyera zonse mzake Dzina lake Likhale Zaine
@user-jr4zn8bn8b
@user-jr4zn8bn8b 6 месяцев назад
Mwayankhula zoona okha zokha. Namayenda wina ndi Brown Mpinganji.
@masterkachingwe7448
@masterkachingwe7448 6 месяцев назад
Well articulated
@KhonzoBlose-wq7zm
@KhonzoBlose-wq7zm 6 месяцев назад
Kulankhula kumeneko a bro ,keep it up.
@ChisomoChikafa-dd3sj
@ChisomoChikafa-dd3sj 6 месяцев назад
In politics every vote counts so let's undermine his influence. He has family members who will follow him and add more votes to mcp.
@user-jd9yz5hp7y
@user-jd9yz5hp7y 6 месяцев назад
Ubwino wakenso MCP simuwinanso ataa Mumuyamike Chilima anakupangitsani kuti muwine komano ulendo uno iwalani brother Jumani
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 6 месяцев назад
Andale ena ndi awa : Ken Msonda, Nicholas Dausi, Patricia Kaliati, Mai Chilenje, Saulosi Chilima ndi ena otelo ziwanthu ivivi sizikukufuninso mu ndale za Malawi iwowa ndi amodzi akusokonedza zinthu
@user-et3il7pi7t
@user-et3il7pi7t 5 месяцев назад
Za Bakiri wanama Nena zauladi musa basi ndipo munthu uyu ndi wolephe na iwe bwanji osayima kuti uthandi ze Malawi PANO ngati ufuna kuthandi Malawi koma tuma inmy in boxi ine since from 1994 am a UDF member who can we put as our president a part from Atupele
@user-uf4db7im7d
@user-uf4db7im7d 6 месяцев назад
I salute you man, those people who did not know about him, we now know. He a jealousy and greedy person. How can he contribute or give votes to MCP when he is just a mere person? MCP keep that empty tin and assure you, in all those villages that are mentioned in the audio where uladi mussa comes from, people will never give votes to MCP. A MCP mukuoneka kuti muli ndi ndalama zosowa nazo zochita, zidyetsani ameneyo alibe kalikonse msilamu ameneyo. Tsiku likudikira kummwamba akayankhe milandu.
@ivychithyoka1551
@ivychithyoka1551 6 месяцев назад
A Msonda ndi a Uladi amangozidyesa Mumba zawo osati a Malawi
@frezargamah3438
@frezargamah3438 6 месяцев назад
Uladii Musa ndi dausi ndimbuzi maganidzo
@user-ii4fw3id6e
@user-ii4fw3id6e 6 месяцев назад
Panga Zako iweee
@ivychithyoka1551
@ivychithyoka1551 6 месяцев назад
Uladi ndi Ken Msonda alibe self direction in politics.
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 6 месяцев назад
Powerful words big boss
@CyprianoSandalamu
@CyprianoSandalamu 6 месяцев назад
That's true big,mr uladi want to benefit from the government of mcp yet he was speaking nonsense during the time of ruring udf ,dpp ,he said mcp will not enter into government,now ge has come to the same mcp very sharm.
@superiormoses4802
@superiormoses4802 6 месяцев назад
Waswa iyi ase kugagada mosanyengerela Ai bg up
@user-ii4fw3id6e
@user-ii4fw3id6e 6 месяцев назад
Ukulankhula bodza ife tapeza kuti Ulad anamanga ma xool komaso amalipilira a nthu fees moti iweyo ndi munthu oipa
@user-qq3ip1od6i
@user-qq3ip1od6i 6 месяцев назад
Uladi madeya mussa, alibe chabwino angatipangile
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 6 месяцев назад
Mahule pa ndale opanda chitukuko ongofuna kuti azingolemelerabe mbava zimezo
@user-ii4fw3id6e
@user-ii4fw3id6e 6 месяцев назад
Panga Zako iweee uyang'ane ma comment udziwe kuti ndiwe wabodza
@peterphir2250
@peterphir2250 6 месяцев назад
Mukuti bwanji za Nankhumwa?
@greychizaka4088
@greychizaka4088 6 месяцев назад
Ang'aluleni makape bigman. Mukawakhutire kaye😂😂😂😂
@PaulDaka-dc3re
@PaulDaka-dc3re 6 месяцев назад
Sibwino kutenga munthu amene analimu chipani china azingozungulira .ndale zotani mukupanga ku Malawi?
@user-xv5pr3ji6w
@user-xv5pr3ji6w 6 месяцев назад
Ndipo ulad musayo sazimvera chisoni ndithu eeesh manyaka a munthu
@user-uf4db7im7d
@user-uf4db7im7d 6 месяцев назад
Msilamu ameneyu ndiwadyera, ulendo uno saputsitsa a mmalawi, wakuba, mbuzi yamunthu, mcp ndiye yolowa munthu msilamu weniweni chitsiru Cha munthu
@abdulrafiquekalembo469
@abdulrafiquekalembo469 6 месяцев назад
Uladi Musa, Dausi, Patricia kaliati and Ken Msonda are the most useless politicians Malawi has ever had.You cannot show to anyone what they did to Malawians except jumping from one party to the other for their financial gains
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 6 месяцев назад
Chakwera Ali busy kugwesa anthu ose oziwika chakwera amapanga ndale zodanisa
@KapepuzaFernandos-bd6nv
@KapepuzaFernandos-bd6nv 6 месяцев назад
MCP sikulamulila ikulamulila ndi tonse alliance Kofi a MCP mukuiwala zimenezi chifukwa choti mwamuimisa chilima kumudekhesa NDE mukuona ngati mukulamulila ndi inu a MCP mukunamatu
@HildatoweraMhango-et4mz
@HildatoweraMhango-et4mz 6 месяцев назад
Nkhalamba zonse pano osazivotelaso ngati iwowo akuti peter saima nawonso saimaso
@ConfusedAtv-bs4gc
@ConfusedAtv-bs4gc 6 месяцев назад
Munasowa munthu wankulu izi ndizowowa Kuno kudowa tikudandaula kwambiri pakuona zimene zikuvhitikazi enafe takhala tikudzola mpaka matope timati kuifela mwina Kuti nafenso tizagwileko ntchito Koma lelo tikuona abwana akutenga anthu oti anaola kale kale pankhani zandale nkumati uladi tikumudziwa Kodi ndichani chimene anachita mudziko lino chooneka manga ndizaka zingati wakhala akugwila ntchito ndiboma manga wakhala maboma angati pempho Kuno kudowa abwana tisafele malebo owola kale ifenso tikudikila ntchito tachokela patali Mene tinkapha gwapeyi uladi Musa kudalibeko asamakonde nyama yoti azake APHA kale ayi
@faithkamlongera5128
@faithkamlongera5128 6 месяцев назад
Big up brother, titsukeni mitu
@PatrickNamakhoma-zm6kq
@PatrickNamakhoma-zm6kq 6 месяцев назад
mwayankhula bwino. mfundo zothyakuka. koma ka chingereziko komzani. kakamavuta kasiyeni. si mlandu
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 6 месяцев назад
Uladi Mussa he's a betrayer 😂
@user-xh1ve5ym3l
@user-xh1ve5ym3l 6 месяцев назад
Ulemu wanu munthu wamkulu
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 6 месяцев назад
Zoonadi
@user-qd2uy9fp9v
@user-qd2uy9fp9v 6 месяцев назад
Ukunena zoona kwambiri
@user-gx5ht9gm3z
@user-gx5ht9gm3z 6 месяцев назад
Kuyakul koveka kwambil
@kondwanimunthali7401
@kondwanimunthali7401 6 месяцев назад
Uladi is an empty tin making alot of noise
@richardbanda9997
@richardbanda9997 6 месяцев назад
A Uladi, kumeneko kuthokoza chifukwa akutulutsani kundende? Shame. Remember what you were saying about MCP? MCP, samala nayeni uyu.
@alexsumani6823
@alexsumani6823 6 месяцев назад
Change golo yu useless pa ndale
Далее
Ndikuopsyezedwa Chifukwa Cha Ma VN - Pastor Shumba
16:55
sendera sisters-patali
2:00
Просмотров 4,5 тыс.
Chakwera V Mutharika: 2025 Kuli Gule - Redson Munlo
23:01