Тёмный

Podcast In Malawi - Jetu Chakwaza (Reactions)  

AM TV MALAWI
Подписаться 35 тыс.
Просмотров 37 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 95   
@JohnOmar-mf2pu
@JohnOmar-mf2pu 4 месяца назад
Pitirizani mama asiyeni iwo anatha 🎉🎉🎉
@AlinafeSolomoni
@AlinafeSolomoni 3 месяца назад
Keep it up Jetu enawo amafuna nkhalamba zizivutika adziwanena kuti ndiafiti ngati momwe amawanenera azigogo awo.
@WonderDan1997
@WonderDan1997 5 месяцев назад
❤❤❤akuzitayisa thaw galu otupa khope uja ndikanakonda ndikanakumananaye ndipase zibongonya💪💪💪💪👊👊👊👊
@Ghama-k4i
@Ghama-k4i 5 месяцев назад
Team jetu from Somalia banadir
@ChikondiSaidi
@ChikondiSaidi 5 месяцев назад
We love her .....Adha okuda moopsa aja azivere chisoni
@DamusonJames
@DamusonJames 5 месяцев назад
Team jetu mufune musafune jetu is never give up 💪🔥🔥
@HalordChisonge
@HalordChisonge 4 месяца назад
Fire fire jetu amatha 🔥🔥🔥 4:40
@KondwaniNyambiBandah
@KondwaniNyambiBandah 5 месяцев назад
Jetu my favorite forever 💯💯💯💯
@MbebaNtchawakaJere
@MbebaNtchawakaJere 5 месяцев назад
Jetu🎉🎉🎉🎉
@AliceNgoma-u8v
@AliceNgoma-u8v 5 месяцев назад
We love jetu ada awo akuda anada ndi mtima womwe
@jacquelinecunningham363
@jacquelinecunningham363 5 месяцев назад
She is an inspiration to the all old people big up Jetu ❤❤💥💯🔥🔥🙏
@amtvmw
@amtvmw 5 месяцев назад
Zoona Zake
@unarinematshomo2841
@unarinematshomo2841 4 месяца назад
Jetu fire fire🎉🎉🎉❤❤❤
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 5 месяцев назад
jetu🔥🔥🔥🔥❤❤❤🙏
@deborahmakunganya2020
@deborahmakunganya2020 5 месяцев назад
Anthu ansanjewo amafuna nkhalamba zizivutika asaah
@DaveYusuf
@DaveYusuf 5 месяцев назад
We love jetu 3 stop 🔥🔥
@francisfabiano7545
@francisfabiano7545 5 месяцев назад
Jetu on fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@DysonBwanausi
@DysonBwanausi 5 месяцев назад
Mbuyo mwa jetu nganganga bas❤❤❤❤
@mercynyati8551
@mercynyati8551 5 месяцев назад
We love jetu🔥
@GraceMuvela
@GraceMuvela 5 месяцев назад
Our jetu on 🔥 fire
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw 5 месяцев назад
WE LOVE JETU
@ShuritaJansen
@ShuritaJansen 5 месяцев назад
🎉🎉
@AndrewSokela
@AndrewSokela 5 месяцев назад
Ilove jetu
@JosephWeruzani-o9h
@JosephWeruzani-o9h 5 месяцев назад
So far we love her
@PeterChinoko
@PeterChinoko 5 месяцев назад
🔥🔥🔥💯💯
@AliAli.aliheassim
@AliAli.aliheassim 5 месяцев назад
❤❤❤ Jetu
@charleshenry4042
@charleshenry4042 5 месяцев назад
🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼💯💯💯
@maviekuwili378
@maviekuwili378 5 месяцев назад
Jetu ndi dolo❤❤
@EsnartNkhoma-c1v
@EsnartNkhoma-c1v 5 месяцев назад
Jetu ❤️
@Jordannahuwo622
@Jordannahuwo622 5 месяцев назад
🔥🔥🔥 team jetu
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy 5 месяцев назад
Joy nathu nde ndaniso iyeyo apite uko wasamba liti agogo alakwa chani
@Esnart-s7h
@Esnart-s7h 5 месяцев назад
We like jetu more and more
@DalitsoKaunda
@DalitsoKaunda 5 месяцев назад
Akufuna adzikawakweza padenga lanyumba adzikati ndi Mfiti jetu siyani majerasi iyaaa
@NellieLPetulo
@NellieLPetulo 4 месяца назад
Koma nkhani ndiyoti Mai jetu ndizoonadi dziko lakulandirani koma yanganani msinkhu wanu mukupita kuti mulungu pokusungani ndi moyo anali naunu cholinga ndi moyo wanu bwerelani tembenukirani kwa yesu chifukwa nthawi yanu ndiyochepa kutsogoloku
@NellieLPetulo
@NellieLPetulo 4 месяца назад
Dziko Mai jetu lisakupusitseni mukulowako ndi kotumikira satana taonani gulo lomwe likukusapotaniniyo Pali msinkhu wanu answer ayi why? Kodi munthawi yomwe munabwadwa mumkavina myimbo zoterozo answer ayi nanga PANO chakukomerani ndi chani kutero dziwani kuti satana akudzera kwa inu kufuna kikoma azimai ofanana ndi msinkhu wanu
@NoelBMwale
@NoelBMwale 5 месяцев назад
Fact bro ❤
@prisicaedow
@prisicaedow 5 месяцев назад
Love you jetu
@lontouja1532
@lontouja1532 5 месяцев назад
Fire fire fada🔥🔥🔥
@BornfaceChiutura
@BornfaceChiutura 5 месяцев назад
❤❤❤
@mikegausi8552
@mikegausi8552 5 месяцев назад
Jetu goes international💥
@DoreemSemu-ho3lt
@DoreemSemu-ho3lt 5 месяцев назад
More fire jetu 🔥🔥🔥🔥🍿
@MaliPhiri
@MaliPhiri 5 месяцев назад
From cape town jetu yemweo
@YamikaniMkwamba
@YamikaniMkwamba 5 месяцев назад
🔥🔥
@winaranamalopa-hg8hj
@winaranamalopa-hg8hj 5 месяцев назад
Getu ali hot like fire❤❤❤❤❤❤❤❤
@bmbboymstyles5894
@bmbboymstyles5894 5 месяцев назад
Ine nd JETU🔥🔥🍒
@kelvwalk
@kelvwalk 5 месяцев назад
Fact❤🎉
@TsuzenThomas
@TsuzenThomas 5 месяцев назад
Malawi podcast & Joy Nathu is feeling headache with Chakwaza Wakwiya mfiti Akhalitse Jetu 💪🔥🔥🔥
@amtvmw
@amtvmw 5 месяцев назад
Amen
@MabelChisangwi
@MabelChisangwi 5 месяцев назад
Jatu my vote ❤
@JohnMasauko
@JohnMasauko 5 месяцев назад
The old woman is making money, more fire Jetu teach other old people that they can manage.
@patriciaKalombola
@patriciaKalombola 5 месяцев назад
She gat talent jetu ndi mooo
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 5 месяцев назад
Jetu❤ is good
@nditumenichagunda4192
@nditumenichagunda4192 5 месяцев назад
Jetu more fire
@ChikuMatemba
@ChikuMatemba 5 месяцев назад
Jetu fire burn
@PromiseKhenzo
@PromiseKhenzo 5 месяцев назад
I like JETU
@EstherDebwe
@EstherDebwe 5 месяцев назад
Me too I really like her💖
@Esnart-s7h
@Esnart-s7h 5 месяцев назад
Tikawona Jetu akuyimba timasangalala,nafenso tikamacheza ndi azigogo athu timati nawo Akhale ngati Jetu timaseka mitima yathu imasangalala
@endmwambene2766
@endmwambene2766 5 месяцев назад
Wawa zoona wansanje afe basi kkkk
@HaveLike-fs6nh
@HaveLike-fs6nh 5 месяцев назад
Jetu ndi one
@NerstyIbrahim
@NerstyIbrahim 5 месяцев назад
Pitiliza jet kuimba kkkkkm
@FrankKalanda-pz8qf
@FrankKalanda-pz8qf 5 месяцев назад
They don't nthawi ndi azigogo ndi makolo awo kumanamizira ulemu
@KelvMwanga601
@KelvMwanga601 5 месяцев назад
Adani okuda , vinyilu za athu , Jetu is making Money now
@ChifundoMajomeka
@ChifundoMajomeka 5 месяцев назад
Jetu ndiwotchuka kumalawi kuno kuposa Podcast Malawi ndi Joy Nathu
@YOUNGBOY-s9v
@YOUNGBOY-s9v 5 месяцев назад
❤️‍🔥❤️‍🔥❤️‍🔥❤️‍🔥❤️‍🔥🫶
@JoãoChirwa-n3l
@JoãoChirwa-n3l 5 месяцев назад
Adani okuda ase tsanje kuda mandeche😂😂
@CharlesMgemezulu
@CharlesMgemezulu 5 месяцев назад
Jetu ndi one 2gheto 22
@NellieMsamala
@NellieMsamala 5 месяцев назад
Team jetu nsanje sikusungani ayi please
@MaryoomAli-h1m
@MaryoomAli-h1m 5 месяцев назад
Adani akuda
@EstherDebwe
@EstherDebwe 5 месяцев назад
Onunkha kukhwapanso adan ake😅
@PeterMajid
@PeterMajid 5 месяцев назад
Jetu wabwera basi
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 5 месяцев назад
Malawi tili ndi jelasi ndiposo moyo wao udzikhala wa phavu
@Jasonnyatwa
@Jasonnyatwa 5 месяцев назад
Chilungamo cha oyimba safunika kuanyoza olo ata imba sonyatsa okondedwe basi
@amtvmw
@amtvmw 5 месяцев назад
Zoona zake
@mcphersonmkoma3829
@mcphersonmkoma3829 5 месяцев назад
Apepese amenei bushit human being
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 5 месяцев назад
Kkkkkkkk kkkkk inu tiyeni mukondeni jetu ndipo jetu wachukamumalawi muno ndipo akuyimba bwino arininyimbo zabwino wakaramba wafuna komaso anyamataakewo akuvina bwino kwambiri moto kuti.boooooo komaso oyimbaenao akumalawi muno sakuziwika chifukwa chamayimbibwe awo osakharabwino.komaso zovina zawo.zosagwirizana ninyimbo.zao inepambuyo pa jetu basi.wakaramba wafuna
@amtvmw
@amtvmw 5 месяцев назад
@IigIgf
@IigIgf 5 месяцев назад
Odana ndi jetu ndi mfiti
@EstherDebwe
@EstherDebwe 5 месяцев назад
Iwe ndy wandilankhulira bwino iwe
@elessjia9306
@elessjia9306 5 месяцев назад
Ndipo tikumufilla heavy awona kuti atani ndipo akagwele uko asamatinyaseso .mtima ofuna zabwino zonse zikhale zawo
@LukaThawe
@LukaThawe 5 месяцев назад
Jetu aaaaaaa
@isaacbandah3617
@isaacbandah3617 5 месяцев назад
Omuda jetuyo panyapako 😮
@priscakunjirima
@priscakunjirima 5 месяцев назад
Oipa
@Johnkasema-he1fl
@Johnkasema-he1fl 5 месяцев назад
Mbambande
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 5 месяцев назад
Jetu ali bho osabwelela kumbuyo
@amtvmw
@amtvmw 5 месяцев назад
Ndipo asafoolenso ayi
@christinamatemba4859
@christinamatemba4859 5 месяцев назад
Ali ndi ufiti.... Mtima wachikolopa
@IwalaniJeke
@IwalaniJeke 5 месяцев назад
Km joy nathu kudakumeneko km wailes imalemekeza chibwana ndithu asiye kuyimba axikadya kwanu mazilu mimba et
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 5 месяцев назад
2:42 2:45 2:45
@BlessingsBen
@BlessingsBen 5 месяцев назад
Ndioona amene asakonda jetu akolupe munyana ife tikukonda Ine BM1 13 Baby Rasta
@champianchampian2148
@champianchampian2148 5 месяцев назад
Iwe nde munthu iweyo
@RodrickNairuwa
@RodrickNairuwa 5 месяцев назад
Agog amatha ndipo ali more akwnila
@EllenMkweza
@EllenMkweza 5 месяцев назад
Vuto ndi kuda kuja kumaazunguza mutu
@LesterHussein-ky1go
@LesterHussein-ky1go 5 месяцев назад
Ndipo adan a black
@tenexchikumba
@tenexchikumba 5 месяцев назад
Kodi MMalawi sanazindikirebe tiziti, or chani anthu ena, I know is one foolish guy koma ambirife tili happy
@DismasKamenya
@DismasKamenya 5 месяцев назад
Jetu ❤
Далее
CRUISE 5 WITH JETU
34:03
Просмотров 366 тыс.
The Story of Chrissy Luhanga (41)
31:56
Просмотров 79 тыс.
Jetu-ndine_Produced by Edoh-Kay & E.K.C RECORDS
4:04
Jetu - Chakwaza  (Tswana reaction )
6:25
Просмотров 37 тыс.
KHASU-Malawian movie_PART 1[Akila films official 2024.]
1:06:28