Тёмный

REPORT LOCHOKERA KWA ASILIKALI ANKHONDO LIDAPEREKEDWA🙌🙌🙌 

HOT 265
Подписаться 82 тыс.
Просмотров 23 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 38   
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад
We need report atharwise mademo aliko and sitisiya kulankhula nkhaniyi chakwela wapha anthu ndiye ine umboni ndilinawo
@Chrisfadamw
@Chrisfadamw 2 месяца назад
We Need A report Otherwise............. Ooh R.I.P Mr SKC🕊️
@jomochirwa
@jomochirwa 2 месяца назад
Adanena kuti august sadutsa ndi august ndi uyu wafikayo Ukachedwa sikuchedwa kucha .tiwona.
@UseniMailosi
@UseniMailosi 2 месяца назад
Chakwela wagwesa ndege kwasala kutinamisa
@AdiniKhama
@AdiniKhama 2 месяца назад
Akuziwapo kanthu ameneyo
@emmanueljelemani4203
@emmanueljelemani4203 2 месяца назад
We need a report
@TressLuka
@TressLuka 2 месяца назад
Chakwerayooooo akudziwachomwe anapangaaa. Chikumbu mtima chimupheee 😢😢😢😢😢
@ShaibuMose
@ShaibuMose 2 месяца назад
Chakwera ndiwegulu kobasi 😢
@HanafiBadat-i8s
@HanafiBadat-i8s 2 месяца назад
Zabwinotu sabisa
@MercyKatongo-p9b
@MercyKatongo-p9b 2 месяца назад
Chakwela today your denying right
@daviechannel8603
@daviechannel8603 2 месяца назад
Mavuto
@DrolieDongowa
@DrolieDongowa 2 месяца назад
😢😢😢😢 chilima wathu udafela boma
@yesayamatengere5703
@yesayamatengere5703 2 месяца назад
Like
@UsenLashid
@UsenLashid 2 месяца назад
Ndikadakhala kuti ndine chakwela zonse zomwe akuzionazi ,, ine ndikana nena chilungamo kuti ndine amene ndinapangisa kuti ndege Igwe pachifukwa Ichi ndi ichi, komaso nkhani ya kuvota ndikanati ndasitha ma plan wovotela aliyese adzavote ndi chilichose chomwe chingamuyeneleze kuti ndi zika ya malawi kuti athu ayambe kundikonda koma chakwela mizimu ya anthu aja kuchikangawa Kuja ikumuzunguza mutu, atapanga izi kuti anthu adziwe chomwe chinachitika komaso kuti anthu adziwe kuti chakwela ndichigawenga
@Mervic-vm8eo
@Mervic-vm8eo 2 месяца назад
Anadya ndiyeyo
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 2 месяца назад
Kd Mr chikangawa akubisa chani Lazaro sataniki ndi manganya agulu akutiphera chilima osalakwa zoona analakwanji chilima
@FrankBaison
@FrankBaison 2 месяца назад
Anapha yekha nde asabitse kkkk
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 2 месяца назад
Aululeeee!!!!
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 месяца назад
Chakwela akukhudzidwa ndi imfa ya samoa mashel wakumozambiq😢😢😢😢
@MercyKatongo-p9b
@MercyKatongo-p9b 2 месяца назад
Chakwela after killing your friend serious are you sure
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 2 месяца назад
Sangatuluse lipotilo
@martinmoyo4211
@martinmoyo4211 2 месяца назад
Zimene analankhulapo a Nkuche ndi a Bamusi ine sindikugwirizana nazo. A purezidenti ndi munthu ngati ife tomwe , tikuwanena kuti ali involved mungoziyi ndiye tiyembekezera bwanji iwowo kuti aulutse report imeneyi? Nawonso zikuwawa m'mtima zowanena kuti ali involved. Akawulutsa iwo automatically mnenanso kuti ndi abodza. Ine ndikuganizira kuti ndibwino a MDF ndi amene awulure report limeneli kuti pasakhalenso chikayiko chinachilichonse pa a purezidenti.
@MagaLassi-tg7lj
@MagaLassi-tg7lj 2 месяца назад
RIP continue chilima
@NearBanda
@NearBanda 2 месяца назад
😢😢😢😢 chilima
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 2 месяца назад
Mesa amapupuluma kunena kut Chilima wamwalira...leronso atiuze report pompano...shupiti
@alexsumani6823
@alexsumani6823 2 месяца назад
Ndiye chosatulusila report yo ndi chani abale
@AlfredNazombe-me2ly
@AlfredNazombe-me2ly 2 месяца назад
Waphadiii bs mfiti yamunthu inetu ndinaona mulomo wakewo kusonyeza ufiti
@OsmanChisi
@OsmanChisi 2 месяца назад
, zoona abwana milomo ya imfiti
@DevisonHala
@DevisonHala 2 месяца назад
Muja adanenera kuti ose anali mundegemo aferatu afunikaso kunena kuti lipoti ndi ili mwachangu moyo sagula ngati ndiye adapha chilima iyeso aphedwe asachite chinkhope kule ngati chikumwa supu
@emmanuelbanda2952
@emmanuelbanda2952 2 месяца назад
Ku Malawi kuli agalu ambiri eti
@swinibanda5412
@swinibanda5412 2 месяца назад
Muankhula mutopa koma osati kupangitsa phuma President kodi mukumuona ngati opusa amakhala ndizambiri zochita motion simudziwa ndinu mbulidi
@almadinaislamic9091
@almadinaislamic9091 2 месяца назад
Iwenso patumbo pako
@ISHMAELCHITENJE-ri9rq
@ISHMAELCHITENJE-ri9rq 2 месяца назад
Inuso ndinu achitsiludi,mwanva nkhaniyo momwe anenela,ati akatswiri achani,ndendiwe ndaniso?musapembeze fano ngati zalakwika ikaniponi fundo not kunyoza ena,Chakwera ndi mcp tafika pochita manyazi naye tizivomeleza kuti akulakwisa simulungutu iyeyo,
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 2 месяца назад
Anapha yekha 😂😂
@chifundoKaluvi-ey5uw
@chifundoKaluvi-ey5uw 2 месяца назад
Y
@ImranHassan-r8o
@ImranHassan-r8o 2 месяца назад
😠😠😠😠
Далее
Fake Referee Whistle Moments 😅
00:38
Просмотров 6 млн
What’s your height?🩷🙀💚
00:59
Просмотров 3,8 млн
FREDOKISS KUYANKHULA MOSAOPA
12:33
Просмотров 9 тыс.
Jomo wamukana Bon Kalindo
4:20
Просмотров 70 тыс.