Тёмный

Saulos Klaus Chilima zomwe ananena asanamwalire 

Malawi Top Talent
Подписаться 11 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

Saulos Klaus Chilima zomwe ananena asanamwalire
Make sure to like, share, and subscribe so you don't miss any of the exciting new content coming soon! Comment below on what you think about the changes.
Subscribe / @malawitoptalent
Follow me on Instagram: www.instagram....
Follow me on Facebook: / malawitoptalent
Chris II 👇
Subscribehttps:
/ @officialchrisii
Follow me on Instagram: www.instagram....
Follow me on Facebook: / officialchrisii
#SKC #Chris #UTM #MalawiTopTalent #SaulosChilima

Опубликовано:

 

11 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 38   
@EdwinThawani
@EdwinThawani 13 часов назад
Ng'oma yolira kwambiri. Sichedwa kung'ambika. Rip 😭
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 7 часов назад
Mumkaona kutali osadziwa kuti okupha ali pafupi pompo ndi izotukani chikangawa.
@RuthMkangala
@RuthMkangala 10 часов назад
Machine skc miss you badly my lovely vp
@MastonWatson-g7g
@MastonWatson-g7g 7 часов назад
Malawi ali pa moto chifukwa cha iwe chilima kupupuluma mapeto ake akutsitsilani ku dzenje la manda achakwela.
@tabithamkandawire2249
@tabithamkandawire2249 7 часов назад
🙄
@MaggieCement
@MaggieCement 7 часов назад
Lero anakumana ndi ozindikila akusogodza Pepa biyeni dziko ndilonyenga ili .
@nelsonmorris4352
@nelsonmorris4352 7 часов назад
Vuto la Chilima amalimbana ndi DPP pamene omupha anali Ena ....I love Peter Muntharika
@AsiyatuAkila
@AsiyatuAkila 9 часов назад
Ngat umaziwa zomwe zikuchitikilenit mawu akulu akoma akagonela
@JimmyLungu-h7m
@JimmyLungu-h7m 9 часов назад
Anamusiyila ndani
@SEEJSHJEFFREY
@SEEJSHJEFFREY 12 часов назад
😂😂😂😂😂😂😂Ada awa eeeeish
@GiftmwaleGreaSaidi
@GiftmwaleGreaSaidi 10 часов назад
Rip 😭😭😭😭
@IshmaelYasssin
@IshmaelYasssin 12 часов назад
Mmmmm
@HaroldMasanga
@HaroldMasanga 5 часов назад
Akuluwatu anazitemberera okha Amalawi ngati akuvutika akuvutika chifukwa cha akulu amenewa Munthu wachipongwe.
@ibraheemkala7581
@ibraheemkala7581 12 часов назад
Mphuno salota ukalozedwa sununkha chosaziwa anayimbila mfiti mmanja
@MagretBula
@MagretBula 6 часов назад
Reply to Mary tchapo😂
@MoosaSadi
@MoosaSadi 11 часов назад
Mwana akumaponyaizi, ndiwa against. Opandanzeru
@PeterKainga-e3h
@PeterKainga-e3h 12 часов назад
Kkkkkkk Koma amaugeya mwanoso paja, osamva saziwika
@chifundocharles2348
@chifundocharles2348 11 часов назад
Ati kutha akuyakhula,,plus phuma iiiiih 😂😂😂
@MchengaAssama
@MchengaAssama 12 часов назад
Zinakuvutani man kkkk
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh 11 часов назад
Waona komwe uli
@kingstonekalonga8435
@kingstonekalonga8435 10 часов назад
Lero waziitanira ifa kkkkkkk mavuto ndithu
@Malawian-q5f
@Malawian-q5f 13 часов назад
Lero alikuti
@WeaponChilungo-y4i
@WeaponChilungo-y4i 12 часов назад
No comment
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 10 часов назад
Ayi bola zili bwino pitilizani wamkulu
@festongreston
@festongreston 11 часов назад
Km umabebetsa eee
@jezalakaphuka7325
@jezalakaphuka7325 8 часов назад
Wanzeru ndinu Biyeni
@preciousmillion
@preciousmillion 13 часов назад
Anali dolo
@GrecianWyson
@GrecianWyson 13 часов назад
@@preciousmillionayiso doloso Kutiso zazi simesa waika pa Moto aMalawi ndameneyu
@spargomw
@spargomw 13 часов назад
Ankanyoza Peter, pano Peter uyo akudya mgaiwa wa Utaka ali pheeeee kamphepo kayaziyazi kakumudutsa.
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 12 часов назад
@@GrecianWyson ngati bodza mmmmmm anatiikadi pamoto ndipo gahena weniweni 🥲🥲🥲🥲
@FastonBanda-b1z
@FastonBanda-b1z 12 часов назад
@@preciousmillion dolo safa chonchija man
@GrecianWyson
@GrecianWyson 11 часов назад
@@FastonBanda-b1z etieti Ngati khuku zoona zazi
@OdreckNdemanje
@OdreckNdemanje 12 часов назад
Mphuno salota,.
@EnerstManess
@EnerstManess 13 часов назад
Muman
Далее
Уезжаю в лагерь
17:57
Просмотров 205 тыс.
Bajjo atabukidde Kwezi 🤓🤓
10:05
Просмотров 2,9 тыс.
JB Zamuvuta uku mpaka dzulo sanalowe Live 🔴
5:53
Просмотров 4,6 тыс.