Тёмный

TAMVANI MFUNDO ZOMWE AYANKHULA ZOKHUZA UTM 

HOT 265
Подписаться 76 тыс.
Просмотров 15 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

25 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 108   
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 Месяц назад
Inetu ndikudabwa kuti mumgwirizanomo mwatuluka zipani zingapo koma kunalibe zoyankhula za anthu zambiri mbiri lero kwangotuluka UTM koma zoyankhula mbwee apa ndipomwe ndatsikimizadi kuti UTM ija osamaiphweketsa
@MaritaAubrey
@MaritaAubrey Месяц назад
UTM is movement Umbuli wakowo ukauze amako
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j Месяц назад
I mene mwalankhuliramu ndiye kuti anthu sakulakwisatu kuti m malawi anthu akufuna piter muthalika
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 Месяц назад
A Malawi ake ati? Don't generalize. Say some Malawians osati aliyense
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn Месяц назад
What you're saying it's true and it'll be hard for other people to understand for example, a lot of people like DPP because of the founder Dr Bingu wa Mutharika, others like DPP as a new party and it's manifestos or agenda
@NorahMangasanja
@NorahMangasanja Месяц назад
kwambiri anamuli munthud wina mmmmm rest in peace Chilima your in our hearts
@johnkanyika9465
@johnkanyika9465 Месяц назад
Mumva mubebe. Musegula nazo mmimba. UTM more fire.
@paullimpu2548
@paullimpu2548 Месяц назад
I loved this person there he has spoken to me the truth that is to me
@user-rf4br1fv2z
@user-rf4br1fv2z Месяц назад
Abig inuyo ndikatundu koma wakuva wava anthu ena aphuzilapo mau akuti chakwera sanakakhala pa u President kodi chilima adakakhala President yekha timaona mbali imodzi koma ndingapezepo number you are humble man stand for truth anthu amatambitsa chipani koma chilima adali ndi mwai kuposa anthu onse new party kupeza ma voti more than 1 million adakayenela kuthokoza
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 Месяц назад
I agree with this 100%
@AndreMadalo
@AndreMadalo Месяц назад
Zoona ena anagwa nayo pauphungu kamba kolowa utm komanso UTM payokha ndi zero
@JaphetSakala-pq4fl
@JaphetSakala-pq4fl Месяц назад
Fundoyanu ndiyosagwilika chilima anazalambeu zinalake ndi UTM
@user-nc4vi1jt5g
@user-nc4vi1jt5g Месяц назад
Akuluinu mwasutachamba
@gersommalama
@gersommalama Месяц назад
Very interesting analysis. Pure scientific from a smart person.
@robertkalima874
@robertkalima874 Месяц назад
Zoona wamkulu UTM iwoneka panopa ngati chili chipani chachikoka. Anthu amakonda malemu Chilima osati UTM
@BillyMhone-jp3kn
@BillyMhone-jp3kn Месяц назад
Ife a UTM tikukonda UTM the love we have for UTM is not entitled to Chilima....
@sinoadedza6231
@sinoadedza6231 Месяц назад
Reminds me of Hon Jon Bande.....Anthu amakonda someone's capability more than people's favourite party
@VincentChirwa-bf8zr
@VincentChirwa-bf8zr Месяц назад
A Malawi vuto lanu lakuvetsera chithu chomwe akuyankhula munthu mumango yakha mwano osava fundoyachimene wanena kaya xakuwawani muthuyu alibe mbali
@ZondiSundwe
@ZondiSundwe Месяц назад
Mwanena zoona akulu utm ilibemphavu
@user-oz1ts3yi7d
@user-oz1ts3yi7d Месяц назад
Thats is true bro
@AshimayeGama
@AshimayeGama Месяц назад
Chilimatu amene uja ndamene anati wonongetsa malawi galu ameneuja mumanyodza chakwela ndichilima lelo chifukwa wafa ndiye mukuti anali muthu wanwino ubwino wake uti amachendanu nose amene mukuyamikila chilima watidzuzitsa kuno kumalawi ameneyo wabwino ndi unja bingu basi osati chilima ayi amafuna kufa ameuja paka kutipangitsa kuti tivote kawili galu chilima
@bornface4786
@bornface4786 Месяц назад
Which side are you
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di Месяц назад
Say NO to Kabambe ( UTM presidency)
@JosephyKambalu
@JosephyKambalu Месяц назад
Ineso Kuwona kwanga akuluwa akunena zoona
@CathrineBizza
@CathrineBizza Месяц назад
Mwakhuta eti utm moto kuti 🔥🔥🔥
@FrankFrancis-ch3xv
@FrankFrancis-ch3xv Месяц назад
Iwe ndi..........kwabasi😊
@wilsonchitenje
@wilsonchitenje Месяц назад
limenero nde bodza akanafufuza za ma mp akanapezanso zolalwika chifukwa zisankho zinabeledwa ku ma mp konso kunaberedwa koma sanadandaule koma kwa amene anakadandaula zinawayendera
@francistonysanena5349
@francistonysanena5349 Месяц назад
Ndiwe Mbuli,. UTM members are royal adha. Uzizimuka.
@macdonaldchaonekera834
@macdonaldchaonekera834 Месяц назад
Iwe ndiwe mbuzi ya munthu suziwa zmene ukuyankhula
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 Месяц назад
Ukuzitenga ngati dolo wozitsata koma ndiwe kape
@Chikumbuso-l5m
@Chikumbuso-l5m Месяц назад
Zaziiii umthu wina ngat I alibe zeru amayakhula zopandapake timamukonda chilima ndichipanichake
@Chikumbuso-l5m
@Chikumbuso-l5m Месяц назад
Mutumbu wamako pitauko wa mcp iwe ngati unachoka kunyini yamako usayakhuleso za UTM
@mussatambuli6077
@mussatambuli6077 Месяц назад
Iweyo umangopelekela ndizopanda pindu zomwe amakulipila zingati
@petertaulo8014
@petertaulo8014 Месяц назад
I think you talking trush
@douglaskamanga7679
@douglaskamanga7679 Месяц назад
U. T. M akuiopa U . T. M chimodzi modz zipani Zina. Zimenezija anaphunzitsa
@user-im7sc2my4w
@user-im7sc2my4w Месяц назад
Uuuuu , suukudziwa chimene kuyankhula
@MphatsoIshmaeladam
@MphatsoIshmaeladam Месяц назад
Wapasidwa mtere,sizingatheke munthu kusiyana pachimene ali,sunganye manyi popanda mkodzo kutuluka
@greycianmbewe4573
@greycianmbewe4573 Месяц назад
Zakuwawani kuti UTM yakusiyani, munya muona
@harrispheleni2205
@harrispheleni2205 Месяц назад
Tizidutswa ngati UDF
@MsondaBanda
@MsondaBanda Месяц назад
Utm it knows only how to sault
@user-jn9tz3li3v
@user-jn9tz3li3v Месяц назад
Very poor analysis, Uladi Mussa was an MP candidate while Chilima was presidential candidate so your example is baseless. Compare Bingu and Chilima so that you explain better. Bingu was voted while in UDF and also voted while in DPP, waona umbuli wako?
@mdakakachokammanja7510
@mdakakachokammanja7510 Месяц назад
Tsopano how many votes did DPP get munthawi yomwe Chilimayo anapeza 1 million votes? Nthawi zina hatred imampangitsa munthu kuzungulila mutu kkkkkk
@HaroldNjewa
@HaroldNjewa Месяц назад
Mulila simunati. UTM forever
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere Месяц назад
Koma akulu awa akudwala ndaona, anthu amakonda chipani Chifukwa cha mtsogoleri mesa?
@IsaacTsinde
@IsaacTsinde Месяц назад
Kape uyu watumidwa wadya ndalama galu
@AllanThom-e6v
@AllanThom-e6v Месяц назад
Inu mukamuda chilima chifukwa chiyani
@AugustineTheu-of6nv
@AugustineTheu-of6nv Месяц назад
Question yako ndiyabodza bro
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf Месяц назад
Kuyankhula kwanu kukumveka. Mwachitsanzo ine muzisankho zonse ndimangyang'anapo presidential candidate basi. Phungu ndimangomuvotera chifukwa cha president kuti adzikamuthandiza ku Parliament asamakavutike povotera ma bill. Mwa kuti Aphungu ndi ma khansala ndimawatenga ngati anthu ongoononga misonkho yathu potengera ndi mmene ena amachitira mmaderamu ngakhalenso ku Parliament komweko. Choncho ndikugwirizana nanu.
@user-hq6dq7zr1e
@user-hq6dq7zr1e Месяц назад
True br
@MPHATSOKALUWA-lm2uy
@MPHATSOKALUWA-lm2uy Месяц назад
Palibe chanzeru coz aliyense akamapanga vote amvotera president not chipani and ngt tinene choncho nde kut zipani zonse zmne zinawinapo2 and sizngatheke kut aliyense wachipani awine ayii nde palibe mfundo yomveka APA coz akawina president timat chipani chawina popeza kut president amneyo amayimira chipani
@ChifundoChiwanda-ru3pg
@ChifundoChiwanda-ru3pg Месяц назад
Hmmmh! Muli ndi vuto
@williamsjonazie5764
@williamsjonazie5764 Месяц назад
Zipita ku MCP we know kuti walandila ndalama akutuma. Leave UTM why are you stressing about it?
@MorisSumaili
@MorisSumaili Месяц назад
Ndinchifukwa munapa chilima ndiye lelo ukufhothokoza nchani zopusa
@clojistix_g
@clojistix_g Месяц назад
You're entitled to your opinion, opinions are not facts
@Chikumbuso-l5m
@Chikumbuso-l5m Месяц назад
UTM iwinaso iweyo ukulakhula ndiwe mumozi unampha chilima muster pusi
@user-ie5pc4ox8i
@user-ie5pc4ox8i Месяц назад
Palibe zikuveka apa
@chrisgremu740
@chrisgremu740 Месяц назад
Chilungamo kuwawa
@FelixBoss-yn9pe
@FelixBoss-yn9pe Месяц назад
Mmmmmm
@DafterKhungwa
@DafterKhungwa Месяц назад
Mbuli imeneyi yangotha bundle yanga
@RaphaelKweve
@RaphaelKweve Месяц назад
Nanga nkhani Yachakwera ndi Mcp sunanenepo Bwanji ,, Galu iwee kagwere uko
@giftsululu4274
@giftsululu4274 Месяц назад
Kodi miyez yovota ilpotu uambiri tikamafika mu December tikhara titaiwara phokosori
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Месяц назад
Big zachamba ife ayi zautsilu appa ife ayi
@JasonMailos
@JasonMailos Месяц назад
Uku ndikuopa UTM ndikuvetsa bwino bwino stop tok no sense
@LaxKampinga
@LaxKampinga Месяц назад
Chimodzimodzi Ife sitikufuna chipani cha mcp kmso sitikufuna chakwela zonse ndizoipa
@PociahMack
@PociahMack Месяц назад
Anthu amafunad chilima,zawoneka pano UTM yagawanika
@AugustineTheu-of6nv
@AugustineTheu-of6nv Месяц назад
Bwwreranso mukalasi
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona Месяц назад
Mukuyankhula za chamba
@EnerstWilson
@EnerstWilson Месяц назад
Iweyo ukudwara
@user-zt6yl3de2h
@user-zt6yl3de2h Месяц назад
Thats your opinion......not everyone opinions
@YNOTGEORGE8
@YNOTGEORGE8 Месяц назад
Mbuli iyi
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Месяц назад
Zoona zake
@chesterkumwenda
@chesterkumwenda Месяц назад
mbuzi iwe galu
@RaphaelKweve
@RaphaelKweve Месяц назад
Talking useless facts ,,,SKC anali president wachipani
@EmmanuelKhumalo-ge3fy
@EmmanuelKhumalo-ge3fy Месяц назад
Palibe chanzelu mukulakhula akulu
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 Месяц назад
Ukunena zonama iwe chokazako
@Malawitrendingnews-j1o
@Malawitrendingnews-j1o Месяц назад
Osamangovomereza zili zose a malawi zomwe akuyankhula zopanda mutu, chilima is the former president of utm that's y chipanicho chinkakondedwa ok.
@HannockMesiwni
@HannockMesiwni Месяц назад
Ndiwe wambwerela usatipusise fundo zako zopanda mutu
@user-mw3kj4qz7b
@user-mw3kj4qz7b Месяц назад
Sure dear
@gregomando
@gregomando Месяц назад
Poor analysis
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu Месяц назад
Tiyeni uko nanuso lnu wapenga misara mbuzi lwe ukulakhura chani
@Chrissyluwe
@Chrissyluwe Месяц назад
Poor
@lastonekaponya7675
@lastonekaponya7675 Месяц назад
Amwene muona chaka Chino muva Bebe man MCP tikuyitulutsa
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Месяц назад
😅😅😅😅😅 inu ndindaniso nanu
@RaphaelKweve
@RaphaelKweve Месяц назад
Za ziiiiii
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Месяц назад
Mbuzi iyi ya MCP. Popha Chilima ndiye kuti mumafuna kupha mavote a Chilima?
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Месяц назад
Mutu wanu osayendawo chilima anachita kuphedwa or anagwa pangozi? Elsh
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Месяц назад
@@user-nv3rf7bl7r Anachita chophedwa. Chakwera anapha Chilima tonse tikuona.
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Месяц назад
@@actuarialscience2283 tonse ndindani bwanji muyipitise ku Cort nkhani mukapelekele umboni inuyo kuganiza mwa umbuli basi
@shotsfired588
@shotsfired588 Месяц назад
It’s true, UTM is nothing without chilima, who else is left in the party that you can actually say it’s a party to follow, Chakwera couldn’t even choose a minister from the party because everyone else including akweni are just party zealots.
@Vwalavwata
@Vwalavwata Месяц назад
Koma anthuwa ma comment akuwerenga nawo
@user-td1nu6iy2y
@user-td1nu6iy2y Месяц назад
I don't understand your point
@user-no2mx4go8p
@user-no2mx4go8p Месяц назад
Me too
@amoschataika7440
@amoschataika7440 Месяц назад
Pangani zanu Man
@CharlesBwino
@CharlesBwino Месяц назад
Wadya zingat useless
@alfrededwinmadziataika5869
@alfrededwinmadziataika5869 Месяц назад
Akulu ndinu achitsilu ngati akutumani....muchita manyanyazi thawi ikakwana......your views are very stupid.... leave Chilima alone.....may his soul rest in peace...
@danielmsowoya9107
@danielmsowoya9107 Месяц назад
Ankolo musanalankhule izi munayamba mwapanga edit mfundo zanuzi 🙄🙄, otherwise mfundo zanu zikuzipanga contradict. Ai zikomo
@MPHATSOKALUWA-lm2uy
@MPHATSOKALUWA-lm2uy Месяц назад
Ndipo palibe chanzeru mfundo zake zikuzipanga zokha contradict mkhoti titha kumpatsa mafunso oti sangawine mlandu coz it's foolish points
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Месяц назад
Kagwereuko iweyo wabosa
@user-nv3rf7bl7r
@user-nv3rf7bl7r Месяц назад
Amati waboza osati bosa 😂😂😂
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp Месяц назад
Ok
@yusufjaile5317
@yusufjaile5317 Месяц назад
Anyway It's your own opinion but according to me it's a very poor analysis, it just shows that you're MCP supporter
@alickziba6756
@alickziba6756 Месяц назад
Very Poor Analysis. Sorry for the whole time you spend for this poor analysis.
@cosmaspempherobanda
@cosmaspempherobanda Месяц назад
Iwe ndi mbuzi kwambiri
@anifoiuene6301
@anifoiuene6301 Месяц назад
Achimwene ndikuona ngati simunafike popanga ailise nkhaniyi za ndale chifukwatu apa palibe chomwe anthu atolapo
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Месяц назад
Poor analysis
Далее
NDUNA ZAMASUKA KU PARLIAMENT
23:05
Просмотров 909
Only I get to bully my sister 😤
00:27
Просмотров 17 млн
politics pa Malawi wafika povuta
4:28
Просмотров 6 тыс.
ZOMWE AYANKHULA A CHAKWELA LERO
14:19
Просмотров 4,8 тыс.