Kuganiza mwakuya Maso anga adali kwa a Chitsi sindimadziwa kuti angapange Khomani!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! Kunena zoona nthawi yatha tisamachedwe ndi kukokana
Mu dziko lino lapansi tili ndi soka lalikulu! We will surely die in the way zamasiku otsiliza... Ndilibe kanthu ndi munthu , ndili ndi kanthu ndi moyo wanga ndi onse akumvera chenjezo la Mulungu ndi kuyenda m'menemo! How would you say inu ndi Mulungu! Just worried of asking this such question