Doctor Kabambe is not just an ordinary person. Ndaseguka nzeru kwambiri at how the economy works. Tili ndi anthu anzeru kwambiri koma we are not making good use of them for selfish political reasons.
With people like Kabambe there is hope for Malawi. A true genius indeed, humble, intelligent and knows his story. This is the best interview on Times Exclusive l have ever watched.
It's been a great experience and fruitfulness, to hear DK sharing his experience and rich mind God bless him he spoke with his truthfulness and he was very enthusiastic in his articulating economic experience, God bless him once again and you Brian for your choice of intellectual interviewe
mkulu wanzeru kwambiri now i can testify that we got intelligent brothers and sisters in malawi......vote yanga ndikudziwa kopita nayo tsopano.Thanks brian for bringing this gentleman invite him again
Kulankhula kwabwino,koma are you saying all this chifukwa choti mukufuna vote ya a Malawi kapena kufuna kukonza zinthu? What about ma salary mumadzikwezera aja? Munali ku reserve konko chiavuta ndichani kupanga implement zeru izi? How sure are you kuti mukabwera pachimpando cha unattainable chi zidzatheka izi? Vuto anthu mumakhala abwino ndi azeru mukamafuna vote, May God help Malawians! Zafikapa andale azingotipatsa chiyembekezo chabodza