Times Exclusive’s Brian Banda engages Vice President of Enlightened Christian Gathering Prophet Dr. Justice Hara on his mergence with Shepherd Bushiri and rebranding to Jesus Nation Church
wakunama palibe chomwe mukulakhulapo akufuna ndalama onse ndi buchiri , onse alibe muzimu wa Mulungu ali ndi ziwanda za boza asakunamizeni inu anthu .mubado uno kulibe amene amalakhula ndi Mulungu ndi boza lenileni
Drama sidzatha padziko pano🤣🤣🤣 Prophet my foot. Prophet okhala ndi church? Nonsense. Kumuuza Brian kuti sadziwa Bible, pomwe Brian is a trained and qualified theologian, koma mbava iyi🤣🤣🤣
Koma zinazi 😂 m'malo mophatikaza anthu ndi Mulungu mukaphatikizana ndi munthu, i feel sorry to followers of these kind of prophets, 😂 love not the World God spoken through his son Jesus Christ.
wow the guy is trying but failing: your interview would be even better if could be objective and more optimistic and acknowledge the truth. Malawi is changing for the best and they will do the same as South Africans and reject the prophet.
this guy is too natural to understand the things of the spirit, the prophet is wasting his precious time explaining the story of Abraham to a person of the world - who entertains baseless stories of persecution from My country South Africa where there is no respect for prophets and the work of God