Тёмный

TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 101 

Nkhalango Multimedia
Подписаться 18 тыс.
Просмотров 18 тыс.
50% 1

TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 101

Развлечения

Опубликовано:

 

21 апр 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 138   
@user-nl5nk2wx1q
@user-nl5nk2wx1q 3 месяца назад
PLEASE DO INTAVEW WITH ZIMVEKA PLEASE
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 3 месяца назад
Komatu Asiyatu ndi mtsikana okongola 😊
@OmarWK790
@OmarWK790 3 месяца назад
Komatu mfumu William ndi mfumu ya nzeru,amaganiza bwino
@atom3492
@atom3492 3 месяца назад
Masiku ano nde mukumachedwetsatu
@jimybashil5350
@jimybashil5350 3 месяца назад
Ndipo akuonjeza aaaa mmene tayambira kudikilira
@BlessingsBanda-ih4th
@BlessingsBanda-ih4th 3 месяца назад
My best comedy
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 3 месяца назад
Comedy iyi ndi number one for who Malawi moti likamatha mtima ukuwawa ngat likhale 6hours Zimveka ur the best one
@user-wm7vl4wp8v
@user-wm7vl4wp8v 3 месяца назад
From nchalo watching and like you guys... Always having time for every Tonde drama
@jameskazembe1123
@jameskazembe1123 3 месяца назад
Amfumu kuyang'ana kwambwanji uku😂😂😂
@YusufMaganga
@YusufMaganga 3 месяца назад
😂😂😂 koma banja lachi phwanya 😂😂 ati mpaka chimakhala chani . Koma chibwenzi wachiyamba chija chithe .akazangoziwa chiphwanya 😅😅 kuzavuta ma bloodfull zako😂😂
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 3 месяца назад
Nyc
@user-nl5nk2wx1q
@user-nl5nk2wx1q 3 месяца назад
KOMA DOLA IWE NDI NTHIRA KUWIRI 😂🎉😂🎉😂 KODI BAMBO AKO NDINDANI 😊
@user-lx8ow6ek6k
@user-lx8ow6ek6k 3 месяца назад
😂😂😂 nsalu igwa bwanji pali mzibambo😂
@MajaidCassim
@MajaidCassim 3 месяца назад
Gaga 😅😅😅
@limbanigivinala3210
@limbanigivinala3210 3 месяца назад
Zimveka, story telling style, imandisangalatsa
@Matabwah5
@Matabwah5 3 месяца назад
Chipwanya... 😂😂😂😂😂😂😂 Kwachema...misala ya Zakhwim
@user-nl5nk2wx1q
@user-nl5nk2wx1q 3 месяца назад
Koma iwe Zimveka 😂🎉😂🎉😂😅😊😮
@ChisomoKapanda-jg2uf
@ChisomoKapanda-jg2uf 3 месяца назад
Koma amfumuwa eeeeish amatha acting🔥🔥
@sultansaidisaid-ft6yv
@sultansaidisaid-ft6yv 2 месяца назад
koma gaga ndi drama yokha mwina is the way he is 😅😅
@FaithNgwalidi-hn8di
@FaithNgwalidi-hn8di 3 месяца назад
Dola asunga bwanji change azimveka pomwe muli ndalama zambili😂😂😂😂😂
@user-xy5cf2gp2s
@user-xy5cf2gp2s 3 месяца назад
Km asiyatu usamale chiphwanya akazaitulukira azakupondesa nkasipa😂
@JoeMatter
@JoeMatter 3 месяца назад
Zimveka anapeleka dala mwana kwaTonde lero ndizimenezo
@user-qs2tx7wt6g
@user-qs2tx7wt6g 3 месяца назад
Komaa dotaa wa zivekaaa
@user-xv9en6se4i
@user-xv9en6se4i 3 месяца назад
Kazi chiphwanya
@user-Mamie461
@user-Mamie461 3 месяца назад
Verse yandisangalatsa ndi ya army pano 😂😂😂😂,,, chiphwanya akufuna kuthawa army 😂😂😂
@user-bq2zb1pc8m
@user-bq2zb1pc8m 3 месяца назад
😂😂😂😂 asiyatu kuyiputa imkata wekha
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 3 месяца назад
Koma I wish Zimveka nzacheze naye live,nzaone kut azizandipasa mpata olankhula koma..😅😅😅
@lontiaband
@lontiaband 3 месяца назад
Chhiphwanya nsanje bwanji berekani ana basi mkazi azikhala buzy pakhomo kkkkkk
@Fredcchilomo
@Fredcchilomo 3 месяца назад
Aziveka mukuyankhulitsat paka pamenepo
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 месяца назад
Azimveka ndi chitsilu 😂😂😂😂😂
@SMARTSeven-gx1qg
@SMARTSeven-gx1qg 3 месяца назад
Asiyatu mbambande
@watipasomzungu9911
@watipasomzungu9911 3 месяца назад
Koma Dorah a Tonde amawakonda mwa toto moyo.
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en 3 месяца назад
Chiphwanya machine 😂😂😂
@ChisomoMsiska-oi2vg
@ChisomoMsiska-oi2vg 3 месяца назад
Amfumu ndi azimveka akhalisapo kwambiri chonchi sizimakoma ayi
@Charles-bg5ul
@Charles-bg5ul 3 месяца назад
kkkk chiphwanya nsanje kkkkkk azakamva kut akumudabula azazipha ndithu. Epsod inayo please
@user-mp7wi4nq2f
@user-mp7wi4nq2f 3 месяца назад
Mr zimveka is fighting for a losing battle ,Dolla likes her biological father lather than zimveka
@JOHNMARK-sl5ff
@JOHNMARK-sl5ff 3 месяца назад
Zimveka my man😅
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 3 месяца назад
Ma hope anga chifunilo Abwele kwakufa kkkkkk
@Shannie-uw4wm5fn8k
@Shannie-uw4wm5fn8k 3 месяца назад
Azimveka mukuwayamba mai adola
@blessingsnaluso5477
@blessingsnaluso5477 3 месяца назад
Koma chiphwanya tie 👔 😂😂
@EdythGloryNamponya
@EdythGloryNamponya 3 месяца назад
Koma zimveka😂😂😂😂😂😂😂😂😂eish
@user-fg5iw1qy1k
@user-fg5iw1qy1k 3 месяца назад
Koma chiphwanya 😂😂😂😂
@user-zb6ch1zc9g
@user-zb6ch1zc9g 3 месяца назад
zakhwima kukubwela army kkkkkkk mumatha guys
@DaudiRose
@DaudiRose 3 месяца назад
Dorah kodi bambo ako enieni ndiatiwo kodi
@user-Mamie461
@user-Mamie461 3 месяца назад
Zimveka akudyatu ndalama
@AfickDaud
@AfickDaud 3 месяца назад
Eeee km azimayi akumatidoda mmakomomu,Asiyatu kuibisa 4n chplaninso thiii akut muzinamizira ngat mukudutsa aaaa zikomo Ambuye ndthu
@rabsonkaunda4554
@rabsonkaunda4554 3 месяца назад
Zimveka amatha. Tonde wadula ndi one
@EdythGloryNamponya
@EdythGloryNamponya 3 месяца назад
Chiphwanya wavala nsapato😂😂😂
@FlavianoThomo
@FlavianoThomo 3 месяца назад
❤❤❤ koma inuo guys mumakwana aaaaaa😂😂😂😂😂😂
@user-js9vc7hi6u
@user-js9vc7hi6u 3 месяца назад
Km zimveka🎉🎉🎉🎉
@robertrichman9376
@robertrichman9376 3 месяца назад
Anatsala pang'ono mayi chiphwanya kugwetsa phone tu
@user-wm7vl4wp8v
@user-wm7vl4wp8v 3 месяца назад
That's mr zmveka tsopano.. like this guy...osaiwala wamabodzayu Gaga hahahaja
@etomansailes4932
@etomansailes4932 3 месяца назад
Km achimphwanya adakwatira hule
@danielsulani8689
@danielsulani8689 3 месяца назад
❤❤
@GaudySamu
@GaudySamu 3 месяца назад
Zinveka iih😅muli zizungutu🔥
@user-zw8ns7bk7s
@user-zw8ns7bk7s 3 месяца назад
Ma hope anga Dora ❤
@Maria-nv8ev
@Maria-nv8ev 3 месяца назад
Well done guys
@BrightMzaya
@BrightMzaya 3 месяца назад
Koma Zimveka😂
@johnkayisi4043
@johnkayisi4043 3 месяца назад
panjatu ine ndi tonde ndiri drama ndine 😅
@justinenambazo6855
@justinenambazo6855 3 месяца назад
A Zimveka muli ndi confidence yokwanira, Asiyatu nsalu igwa bwanji pali anyamata
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 3 месяца назад
Ndimaona kuchedwa,iyyi olo ikumatulula daily nzingongolabe bundle nkuonera bas ❤❤❤❤
@user-pj7hn2ky5j
@user-pj7hn2ky5j 3 месяца назад
Nice guys❤
@user-hh7pi9ee7n
@user-hh7pi9ee7n 3 месяца назад
Musamachedwe plz 😊
@DaveSitolo
@DaveSitolo 3 месяца назад
Army ikubwera kkkk
@Dorah-zl9uf
@Dorah-zl9uf 3 месяца назад
My favorite ❤
@user-oh5vs1gl4n
@user-oh5vs1gl4n 3 месяца назад
ma guys mumakwana
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f 3 месяца назад
My favorite movies ❤
@superiormoses4802
@superiormoses4802 3 месяца назад
Ilibho guys keep on pushing 🎉🎉
@asifbwanali
@asifbwanali 3 месяца назад
Inu mukuwona bwanji pamenepo watching from cape town
@user-sk1wj9bw6l
@user-sk1wj9bw6l 3 месяца назад
Tonde wadula anakoza
@santossamissonesantos9264
@santossamissonesantos9264 3 месяца назад
Koma guys kunena serious Dola ndimakonda ❤
@KimChisola-gm7yw
@KimChisola-gm7yw 3 месяца назад
Waiting for the next
@shupikayintuwaluwa-5899
@shupikayintuwaluwa-5899 3 месяца назад
Kkkkkk asya2 khalidwe lakwakachere
@erickkadoh777
@erickkadoh777 3 месяца назад
@marynjanji985
@marynjanji985 3 месяца назад
Koma ziveka unkhalike ndithu
@FaithNgwalidi-hn8di
@FaithNgwalidi-hn8di 3 месяца назад
Kodi akazawo achiphwanya akale aja anapita basi sitizawaonaso?
@user-ll7fy1gz9m
@user-ll7fy1gz9m 3 месяца назад
ZImveka adha😂
@user-bp9ot1zo6z
@user-bp9ot1zo6z 3 месяца назад
Ndinapeza galimoto pa khomo paja kkkkk koma azimveka
@user-ev3fi1wz3d
@user-ev3fi1wz3d 3 месяца назад
Zimveka anakonza
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 3 месяца назад
Ndi dolo amwene
@user-bz7hm9qf4u
@user-bz7hm9qf4u 3 месяца назад
Makwala umakwan
@user-qs2tx7wt6g
@user-qs2tx7wt6g 3 месяца назад
Aaamee
@etomansailes4932
@etomansailes4932 3 месяца назад
Km nde mukumachedwatu
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 3 месяца назад
Mayi chipwanya ndi bomba
@user-qo6dx2iu4c
@user-qo6dx2iu4c 3 месяца назад
Ma hope anga asiyatu mukagwidwa zikuvutani
@user-zd2ne1ic2v
@user-zd2ne1ic2v 3 месяца назад
Kkkkkkkkk zikomo ndithu koma mukuchedwesa bwanji
@MacErnest-se1xm
@MacErnest-se1xm 3 месяца назад
Km tonde wadula ndi one
@NditajiMaxwell-cz8ir
@NditajiMaxwell-cz8ir 3 месяца назад
I wish amfumu a william ndi mfumudi cz ndimunthuu wanzeru
@EdythGloryNamponya
@EdythGloryNamponya 3 месяца назад
Ndiamfumu ndithu....moti amfumu william ndiomwewo mukadzafika mudzi mwaawilliam mwini mudzi ndi yemweyo
@SaimoneAssima
@SaimoneAssima 3 месяца назад
Mr zimveka your best m
@user-bj3gd2yp4u
@user-bj3gd2yp4u 3 месяца назад
Komatu zimveka matama
@jaffargeorge3477
@jaffargeorge3477 3 месяца назад
❤Here we go
@kho7676
@kho7676 3 месяца назад
😂😂😂😂 zakhwima kkk
@sharrifgwape7169
@sharrifgwape7169 3 месяца назад
Koma chiphwanya azapha munthu uku
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 3 месяца назад
Koma aziveka mwana amamukonda koma kusabarako ndichifukwa zikuchitika ndizimenezo kkkkkk
@williamkapena8783
@williamkapena8783 3 месяца назад
Koma afumu wiliam ndi khani zina seriously tu
@duncankamthemba1100
@duncankamthemba1100 3 месяца назад
Bwana Zimveka kumeneko ndiye kushosha yolakwika
@user-wm7vl4wp8v
@user-wm7vl4wp8v 3 месяца назад
Thawani achipwanya aamee ikubwera uku😂😂😂😂😂😂😂
@user-kq6bv1rx2n
@user-kq6bv1rx2n 3 месяца назад
😂😂 zimveka muwuzeni mwana zenizeni
@user-ql1ig3cv5j
@user-ql1ig3cv5j 3 месяца назад
Koma dzinveka
@KassimuMkwanjire
@KassimuMkwanjire 3 месяца назад
Chiphwanya naya nsanje km katundu nde akudyedwabe ndi ena😂😂😂😂
@chifundokambakaera
@chifundokambakaera 3 месяца назад
Anthu okonda zinthu ifeyo
@mosewallace9717
@mosewallace9717 3 месяца назад
tafika kale ife!!
@simeonkhamwaha8529
@simeonkhamwaha8529 3 месяца назад
Eeee koma ndiye kulawililatu 😂😂
Далее
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 102
29:34
Просмотров 20 тыс.
Пиратские котики
00:50
Просмотров 190 тыс.
Mfumukazi Comedy
27:54
Просмотров 40 тыс.
CHITSAMBA - Episode 96
13:33
Просмотров 156 тыс.
okuba akumana kokuba
4:50
Просмотров 5 тыс.
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Просмотров 51 тыс.
UMBONI wa a Twaibu - ZA SATANA SI ZAULERE
1:06:55
Просмотров 13 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 111
28:52
Просмотров 19 тыс.
Tikuferanji 03 March 2024
14:55
Просмотров 56 тыс.
TONDE WADULA EPISODE 004
26:33
Просмотров 30 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 114
28:51
Просмотров 12 тыс.
И что с этим делать?😃
0:14
Просмотров 1,3 млн