Тёмный

TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 93 

Nkhalango Multimedia
Подписаться 20 тыс.
Просмотров 18 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 119   
@justinenambazo6855
@justinenambazo6855 7 месяцев назад
Achimwene anga a Chibiliti ndinu omvetsa chisoni
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 7 месяцев назад
Tonde samafuna kumpasa nzake mpata olankhula eeeh ali ngat zimveka
@MphatsoYusuf
@MphatsoYusuf 7 месяцев назад
Mr chibilitu adyesedya nkhuzumure, chifukwa sakugwilika❤❤❤❤❤
@jessienkhoma2492
@jessienkhoma2492 7 месяцев назад
Cecilia ndi muthinda tsopano😂😂
@ErickZgambo
@ErickZgambo 7 месяцев назад
Kkk koma a chibiliti ndinu number 1
@isaiahmajawa4534
@isaiahmajawa4534 7 месяцев назад
Big-up guys now ur back ... This is what we had been waiting for .. kuponya pafupipafupi
@violetnkhoma8535
@violetnkhoma8535 7 месяцев назад
Koma mimba ili ndi chisomo siya Tonde? 😂
@InnocentKanseu-u4j
@InnocentKanseu-u4j 7 месяцев назад
Muthinda akukayi ng'alura🔥🔥
@MphatsoYusuf
@MphatsoYusuf 7 месяцев назад
Komano chisomo walakwisa kwambili, atenga bwanji mimba kwina pamene farao alipankhomo pompo😂😂😂chidodo farao😂😂😂❤❤❤
@limbanigivinala3210
@limbanigivinala3210 7 месяцев назад
Farao ,palibe akukumvetsera ukudutsa muzowawa
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 7 месяцев назад
Bola panopa makware Ali ndi kharidwe amawayankhula bwino amalume ake
@evanceivaniemzama
@evanceivaniemzama 7 месяцев назад
Gaga alibe kopita akusungidwa Koma makani,mwano ndi ulesi😂😂 achoke koma
@MphatsoYusuf
@MphatsoYusuf 7 месяцев назад
Mkadzi kusegula chiseko atanva kut cheke chatuluka😂😂😂😂Gaga ndidolo🎉🎉🎉🎉
@VillanMakwacha
@VillanMakwacha 7 месяцев назад
Sisiliya aponda munthu uku kkkkk
@WilliamKapena
@WilliamKapena 7 месяцев назад
Tonde osakutheretu ntchito ndi phekeserazo zivelazo
@madalomachira7766
@madalomachira7766 7 месяцев назад
Mwendo wa Cecilia, muthinda wausiliranso kachikena.Anthuwa akufunananso 😂😂😂😂😂
@estherkamwendo7971
@estherkamwendo7971 7 месяцев назад
Anthu amenewa sasiyanatu kkk
@STEVEKaphuka
@STEVEKaphuka 7 месяцев назад
gaga wakakamila ngalawa we follow u guys in CAPETOWN big up
@robertrichman9376
@robertrichman9376 7 месяцев назад
Achibilit ngovuta kuwavetsa, muthinda naye nsanje yamubwelera 🤣🤣🤣
@MadaWilly
@MadaWilly 6 месяцев назад
Cicilia ndi amunanu mukufunana aaaaaa😂😂😂😂😂😂
@AfickDaud
@AfickDaud 6 месяцев назад
Cecelia asiya bwanj mwendo panja kumudzi mmalo movala chitenje kkk
@Matabwah5
@Matabwah5 6 месяцев назад
Chibiliti is resisting.... Tonde naye kudya mutu mix relationship yake is coming to light .... Muthinda...😢😢
@AgriwhatMW
@AgriwhatMW 7 месяцев назад
Gaga ndi number 1😂😂😂😂
@daviechibwana3137
@daviechibwana3137 7 месяцев назад
Km ma gyz awawa ndisaname amandivesa Sugar ❤'❤❤
@EndreckBen
@EndreckBen 7 месяцев назад
Mwendo wasiyidwa poyelawo uti nawe muthitha😂😂
@cliphtonulembanda
@cliphtonulembanda 7 месяцев назад
Mole ndatha kuwona Pano kuti akuziwapo kanth
@PatsonChima
@PatsonChima 7 месяцев назад
Fantastic
@YusufMaganga-rn3ju
@YusufMaganga-rn3ju 7 месяцев назад
Gaga sazatheka 🤣🤣🤣🤣 bodza la cheke 😂😂😂mpaka kupeza akisesi yolowela nyumba😂😂
@estherkamwendo7971
@estherkamwendo7971 7 месяцев назад
A tonde kulongolola musiyeni munthu afotokoze.
@KareemYahaya-ey6tf
@KareemYahaya-ey6tf 7 месяцев назад
Wosati kumatenga ndawi paka kukuyiwalanitu
@CharlesZimbiri
@CharlesZimbiri 7 месяцев назад
Kkkkkkk gaga iwey ndiwe dolo tabwali weni weni
@tadalapatrick5914
@tadalapatrick5914 7 месяцев назад
Muthinda Cecilia mwendo mpaka kuusiya chocho🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@FlavianoThomo
@FlavianoThomo 7 месяцев назад
❤😂 sanje che Muthinda
@FaithNgwalidi-hn8di
@FaithNgwalidi-hn8di 7 месяцев назад
A papa bolanitu muziika mkati mwa week chocnhi 🎉🎉🎉🎉🎉
@FrancisMulonga-ei1rb
@FrancisMulonga-ei1rb 7 месяцев назад
Mole ndikape ndaona sidolo kukana kupita ku court zoona amangidwa
@dicksonhangiwa7847
@dicksonhangiwa7847 7 месяцев назад
Che muthinda mukunama, mwendo wauveka bwino bwino
@justinenambazo6855
@justinenambazo6855 7 месяцев назад
Farao Mimba yaa zanu mutchuka nayotu kkkkk
@HaggetBanda
@HaggetBanda 7 месяцев назад
mwendo wakongolo che mthinda mwakomedwa kkķkkkkk
@patriciatembo3095
@patriciatembo3095 7 месяцев назад
Makwale wayamba kupita Ku church anasiya zomenya ankolo ake😂😂😂😂😂😂
@dicksonhangiwa7847
@dicksonhangiwa7847 7 месяцев назад
Kkkkkk, komatu Gaga sadzatheka ndithu, ndalama anakonza
@MariumBaluku
@MariumBaluku 7 месяцев назад
First to watch ❤❤
@JamesVicktor-yl4bj
@JamesVicktor-yl4bj 6 месяцев назад
Gaga more 🔥
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 7 месяцев назад
Muthinda akunedizowona
@TadalaByson-ew9qe
@TadalaByson-ew9qe 23 часа назад
Mwendo 😂😂
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 7 месяцев назад
Kkkkk muthinda sopano ndi mwendo wa cecilia
@YusufJamesYusuf
@YusufJamesYusuf 7 месяцев назад
Tonde ndi katundu watching from makkah
@FrancisMulonga-ei1rb
@FrancisMulonga-ei1rb 7 месяцев назад
More 🔥
@georgekchimwaza6838
@georgekchimwaza6838 7 месяцев назад
Ndikumva kukama kuno ku cape town ndi tonde wadura
@KassimRasheed
@KassimRasheed 7 месяцев назад
Koma achibiliti mukundinvesa chison😢
@MacksonTchovaNkwinika
@MacksonTchovaNkwinika 7 месяцев назад
Mnthindwa akuti Cecilia mwendo kuwusiya chonchi
@HarodKaliati
@HarodKaliati 7 месяцев назад
Give it fire
@dicksonhangiwa7847
@dicksonhangiwa7847 7 месяцев назад
Chibiliti sadzatheka ndithu, komanso muthinda ndi mole , mmmmm
@KareemYahaya-ey6tf
@KareemYahaya-ey6tf 7 месяцев назад
Eya apapa ndipamene mukubela
@FatimaYuda
@FatimaYuda 7 месяцев назад
Gaga yomweyo
@benniemontfort1228
@benniemontfort1228 7 месяцев назад
Kkkkkk aliyense alibho
@MercyMaloya
@MercyMaloya 7 месяцев назад
guys mumakwana keep it up
@BridgetGunde-w9c
@BridgetGunde-w9c 7 месяцев назад
Makwale wasiya kuwamenya ankolo ake😂
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy 7 месяцев назад
Coz of alipantchito akumawagulila ndio anambewe
@ShadreckMwija
@ShadreckMwija 7 месяцев назад
Achibiliti adya kenakake kkkkkkkkkk makhala kapena kusatha kufusira akazi ena kkkkkkk
@JamesMalango
@JamesMalango 7 месяцев назад
Koma Muthinda kkkkk nsanjenso
@ZexValera
@ZexValera 7 месяцев назад
Nagumbo yamuvuta game 😂😂
@anniewhite3497
@anniewhite3497 7 месяцев назад
Gaga bodza lake lopanda malo manyazi😂😂😂😂
@ThomasiSalijeni
@ThomasiSalijeni 7 месяцев назад
More fire guys keep it up ❤❤❤❤
@storytambala6088
@storytambala6088 7 месяцев назад
Makwale mutu wako sukugwira, lero malume ako akhala munthu wabwino chifukwa choti akugwira ntchito?
@EsawJonji
@EsawJonji 7 месяцев назад
Aziveka ndakazawo sakumapezeka bwanj
@vatineseduwin
@vatineseduwin 7 месяцев назад
cicilia ndi muthinda kkkkkk
@EbrahimPious
@EbrahimPious 7 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂😂 mo fire 🔥🔥🔥🔥🔥
@EmmanuelKatadzukacomedy
@EmmanuelKatadzukacomedy 7 месяцев назад
Gaga ndiwe galu kwabasi😂😂😂
@FredChilomo-g1p
@FredChilomo-g1p 7 месяцев назад
Mukhala ndimwana a falawo
@HaggetBanda
@HaggetBanda 7 месяцев назад
yaponda yamwa kkkkkk
@HusseinMachemba
@HusseinMachemba 7 месяцев назад
😂😂😂😂😂 koma farao
@justinenambazo6855
@justinenambazo6855 7 месяцев назад
Kkkkkk Cicilia mpaka mwendo pamtunda? Kkkkkkk
@KenedyJolamu-rs9xx
@KenedyJolamu-rs9xx 7 месяцев назад
😀😀😀😀🤣🤣🤣🤣🤣🤸‍♀️🤸‍♀️🤸‍♀️🤸‍♀️🤸‍♀️🤸‍♀️❤️❤️❤️❤️❤️🇲🇼
@dicksonhangiwa7847
@dicksonhangiwa7847 7 месяцев назад
Kkkkkkk, komatu lero alikazinga sewero LA lero , mmmmm
@JoãoChirwa
@JoãoChirwa 7 месяцев назад
😂😂😂😂Kom nganga anakoza guys
@DroliiDongowa
@DroliiDongowa 7 месяцев назад
Muthinda sutha kuyankhula modekha bwanji?
@shaibuJames-c3w
@shaibuJames-c3w 7 месяцев назад
washing from Durban gaga umakwana
@KassimRasheed
@KassimRasheed 7 месяцев назад
Kulemera kwayambika agaga😂😂😂?
@DavsonWatsopano
@DavsonWatsopano 7 месяцев назад
Gaga umakwanitsa
@HassanKasimu-u7l
@HassanKasimu-u7l 7 месяцев назад
Mbambande Inu musazafe muzangosowa
@BlantnaMachilika
@BlantnaMachilika 7 месяцев назад
More yikumera
@NicksonSalimu
@NicksonSalimu 7 месяцев назад
😂😂😂😂 kma gaga
@MosesChaphuka
@MosesChaphuka 7 месяцев назад
Chibiliti ndkape Kwabas 😂😂😂😂
@EthelOsman
@EthelOsman 7 месяцев назад
Tonde ndi number 1
@RodgersKanyasko-dh3cy
@RodgersKanyasko-dh3cy 5 месяцев назад
Kkkkkkkk koma gaga
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 7 месяцев назад
😂😂😂😂 muthinda
@HusseinMofatt
@HusseinMofatt 7 месяцев назад
Amfumu a William mumaitha🤝
@SurprisedDriftwood-ef3lc
@SurprisedDriftwood-ef3lc 7 месяцев назад
19:28 muthinda kusilila mwendo wa X
@rabsonbanda1571
@rabsonbanda1571 7 месяцев назад
Banja la Cecelia ndi muthinda anapezana ose asanje
@marianjeleka900
@marianjeleka900 7 месяцев назад
Ndipo abwelerana 😂
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy 7 месяцев назад
Mumakwana guys inuyo ndi 1
@blandinabonaventure
@blandinabonaventure 7 месяцев назад
Best drama
@ThomasiSalijeni
@ThomasiSalijeni 7 месяцев назад
Gaga sazatheka😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 7 месяцев назад
Gaga😂😂😂😂
@freedommuyaka8597
@freedommuyaka8597 7 месяцев назад
Muthinda ndi Cecilia akufunana ndithu
@BridgetGunde-w9c
@BridgetGunde-w9c 7 месяцев назад
Cecilia ndi more😂
@RichardAmosi
@RichardAmosi 7 месяцев назад
Mupatsa chani chisomo
@AndrewChasweka
@AndrewChasweka 7 месяцев назад
Kodi nkadzi chiphwanya phone waitenga kuti?
@MadalitsoMbewe-f2v
@MadalitsoMbewe-f2v 7 месяцев назад
Yaponda yamwa😂😂😂
@PaulKhumbeni
@PaulKhumbeni 7 месяцев назад
Koma Gaga ndi katundu
@BentryKumwenda-ze2gn
@BentryKumwenda-ze2gn 7 месяцев назад
Gaga kkkkkkk
@MavutoJackson-j3v
@MavutoJackson-j3v 7 месяцев назад
More
@Maria-nv8ev
@Maria-nv8ev 7 месяцев назад
Achibilit pezani Ena madam
Далее
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 94
27:31
Просмотров 18 тыс.
iPhone Flip станет ХИТОМ!
00:40
Просмотров 84 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 125
27:37
Просмотров 14 тыс.
Mfumukazi - 10 April 2024
28:14
Просмотров 22 тыс.
MANGANYA in Munthu Ep23
14:16
Просмотров 96 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 124
27:20
Просмотров 22 тыс.
Mnangagwa's Girlfriend Replacing Chiwenga?
13:02
Просмотров 11 тыс.
TONDE WADULA EPISODE 75
27:41
Просмотров 15 тыс.
Kunte - Mr. Loverman
13:37
Просмотров 85 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 100
27:56
Просмотров 21 тыс.