Welcome Mundelanji, a Chibiliti tamalimbani mtima ngati a Zimveka. Nagumbo wakutani kodi. Mai Phiri game mumaitha. Muthinda samala mwana wako aise I love you welfare ya mwana umadziwa. A Nagumbo musamutaitse nthawi Chibiliti mwayi waupeza koma nayenso kaya ndi kupanda manoko chidodo. Love you guys mmakwana