Тёмный

TONDE WADULA EPISODE 51 

Nkhalango Multimedia
Подписаться 18 тыс.
Просмотров 25 тыс.
50% 1

TONDE WADULA EPISODE 51

Опубликовано:

 

15 ноя 2023

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 123   
@MalizinZinazizi-in4wk
@MalizinZinazizi-in4wk 8 месяцев назад
Kkkkkkkkkkkkkkkk muthinda ndi chifunilo atseka makutu
@kelvinkhudze6241
@kelvinkhudze6241 8 месяцев назад
Muthinda ndi Chifuniro amuphunzitsa Gaga to mind his business😂😂😂😂😂😂😂😂
@evansjailos504
@evansjailos504 8 месяцев назад
Chfunilo wafikapono 🤣🤣🤣🤣🤣🤣 umatha. ulemuso Kwa Ama Dora🤣🤣🤣🤣🤣, kudzangotembenuka poyerayeraTonde kukhara Abambo in public forum 👍👍👍🤣🤣🤣👀
@user-lh9ue5np8o
@user-lh9ue5np8o 8 месяцев назад
Koma zimveka ulimmadzi😂ine ndikufunako nambala ya yunesi basi😊
@johnkayisi4043
@johnkayisi4043 8 месяцев назад
Plz Wina andiwuzeko zachimangacho chikura bwanji pamene kwathu kumangochi tinadzala pa 12 November 2023?, any way. we love you all team
@patriciatembo3095
@patriciatembo3095 6 месяцев назад
Makware good actor koma chimandibowa chosalemekeza amalume ake
@atom3492
@atom3492 8 месяцев назад
Chifunilo #1😂😂Koma aawa apwetekana
@user-po4ml7xt1p
@user-po4ml7xt1p 8 месяцев назад
Mthindwa and Chifuniro Mwabwera Ma Guy
@dominicmphepo-jk8lk
@dominicmphepo-jk8lk 8 месяцев назад
Koma Gaga yamukwana kuyesela kutele sizikumuthekela kkkkkkkkkk
@estherkamwendo7971
@estherkamwendo7971 8 месяцев назад
Koma mimba ya chifuniro nde asonkhelanatu azibambo eish, amuthinda zingoasalila poti ndiotengeka😂
@chimwemwekapeya7355
@chimwemwekapeya7355 8 месяцев назад
Moto kuti buuu,, anchana Nawonso😂😂,, Chifunilo amuna achulukatu
@user-gd2ng7xp1d
@user-gd2ng7xp1d 8 месяцев назад
Gaga zamvuta😂😂
@yohanekanjana4925
@yohanekanjana4925 8 месяцев назад
Mumatimvetsa kukoma kwabasi keep it up guys, koma Zakhwima mumuchotsemo mu program yi, emwe amalakwitsa program yanuyi ndi Zakhwima . Nanga zoona anthu akuku akulu angamawapange kuti iwe.? Achokemo sitikumufuna. Ife tikaona munthu wamkulu timamulemekeza ndiye zimatibowa azinena anthu akuku akulu kuti iwe. Osaiwala kuti cholinga cha program ndi kudziwitsa , kusangalatsa komanso kuphunzitsa. Ndiye iye ndi phunzilo lanji lomwe tingapezemo mwa iye ngati akumane a akulu kuti Iwe? achokeeee , achoke sitikumufunamo .
@user-xd5qw5yp4y
@user-xd5qw5yp4y 8 месяцев назад
Zoona or ili drama km ulemu uzikhalapo akuonongadi simukunama zankhwima achoke guys😮😮
@yohanekanjana4925
@yohanekanjana4925 8 месяцев назад
Ndipo inu, eti munthu wamkulu mpaka adzimunena iwe,? Aaaah ife zimenezo ayi , sizimatimvekela bwino. If he doesn't know how to act, they better found someone else who can perform better as long as he's gonna respect our elders. We will be more than happy.
@smithchalemba995
@smithchalemba995 8 месяцев назад
ayiso akhalemo.... inuyo ndamene simupezapo phuziro...inu ana otere mulibe mmakwanumo😂
@user-bl3fm7ji6l
@user-bl3fm7ji6l 8 месяцев назад
Chifuniro ndi muthinda mwandisekesa kwambili lero 😂😂😂😂😂 anyway watching u guys from south Africa _Durban. ❤ U all
@johnfred2525
@johnfred2525 8 месяцев назад
Nkazi ameneyu amatha ndipo ndiwa serious
@johnfred2525
@johnfred2525 8 месяцев назад
Mukumativetsa kukoma serious ndipo Tonde even ma camera man ako Ali bwino kwambili pitilizani good work
@goodwinnyirenda9679
@goodwinnyirenda9679 8 месяцев назад
Kkkkkk,a Tambala awiri sagona nkhola limodzi
@chiccokamangen4750
@chiccokamangen4750 8 месяцев назад
Gaga kķkkkkk iwe ndi dolo
@user-cv3zw9ic6d
@user-cv3zw9ic6d 8 месяцев назад
Koma chifuniro 😂😂 3 in 1 umatha kuyala ma shift kusamala amuna kuposa mabungwe guys mumandimvetsa kukoma Doro mwana wa Tonde azimveka analemba ganyu munthu wachabe
@user-ed2bq8nk7p
@user-ed2bq8nk7p 8 месяцев назад
Ma aDora you are a best comedian, keep it up!
@user-gu8rx9gq9d
@user-gu8rx9gq9d 8 месяцев назад
Tonde more fire whay to whay 😂😂😂😂😂😂mutaye nazombe akuchosesa tchito
@user-hp8gs8yz6z
@user-hp8gs8yz6z 8 месяцев назад
Go ahead gayz am enjoying your performance and always. Tonde 🔥
@CharlesSaid-cl8pw
@CharlesSaid-cl8pw 8 месяцев назад
😂😂😂😂😂 unagwa mupapaya iwe😊
@EniyaBanda
@EniyaBanda 8 месяцев назад
Chifunilo sudzatheka 😂😂😂😂😂
@mustafahaji2599
@mustafahaji2599 8 месяцев назад
Komananuso amore achifuniro kumawagwira koma orochochita ndiye mwafikapotu
@user-ec7du2yf9d
@user-ec7du2yf9d 8 месяцев назад
More fire Chifuniro,,,, l like the way u acting😂😂😂😂
@limbanigivinala3210
@limbanigivinala3210 8 месяцев назад
Inuyo ndi ma dolo...big up team # tonde
@user-hh7pi9ee7n
@user-hh7pi9ee7n 8 месяцев назад
Chifunilo aphetsa amuna😂😂😂😂
@kenstonszulu4100
@kenstonszulu4100 8 месяцев назад
Chifuniro , Kwini maza kkkk 3 in 1
@BlessingsBanda-qn7xr
@BlessingsBanda-qn7xr 8 месяцев назад
Taunde(tonde)u r the best
@gracegonani4360
@gracegonani4360 8 месяцев назад
Makwana 🔥🔥🔥
@rosemarymponda274
@rosemarymponda274 8 месяцев назад
Anyamata awa akuphunzitsa chikhalidwe choipa ana mdziko muno , Makwale ndi Zakhwima. There is nothing fun in what they do
@user-ys8tz8gp3v
@user-ys8tz8gp3v 8 месяцев назад
Chifu ngt Ali matenda akupweteka amuna
@giftblack7690
@giftblack7690 8 месяцев назад
😂😂😂😂😂 Chifunilo apweteka amuna umatha ayise aphunzitse atsikana anzako naye nazombe akufuna azimayi ose cisria ndi ziyone koma anthu mupwetekana kkkkkkkk Mbambande guys inuyo
@GOEMENGONDWE
@GOEMENGONDWE 8 месяцев назад
Guys , zinthu zili boh. However, malo omwe anyamata kumakanganilana chifuniro akanakhala by coincidence osati wina kungotulukila uko Basi kubwera ngat anaziwakale kuti Moleni ndi nzakeyo Ali uku. This is just
@user-sk1wj9bw6l
@user-sk1wj9bw6l 8 месяцев назад
Kkkkkk kma chofunika ndika clinic ka boma sure kkkkkkkkk
@MalizinZinazizi-in4wk
@MalizinZinazizi-in4wk 8 месяцев назад
Chifunilo eshiiiiiiii wazunguza wanthu kuno🔥🔥🔥🔥
@user-hh7pi9ee7n
@user-hh7pi9ee7n 8 месяцев назад
Muthinda nd chifunilo eeeeh ayaka moto
@RodgersKanyasko-dh3cy
@RodgersKanyasko-dh3cy 8 месяцев назад
Gaga zamvuta Osayankhidwa kkkkkkkkkkk Love you all guys
@elizabethkasambala9628
@elizabethkasambala9628 8 месяцев назад
Watching from USA 🇺🇸
@MathewsCharles-mh8yg
@MathewsCharles-mh8yg 8 месяцев назад
😂😂😂😂 kma makwale kkkk
@user-ez1dt2zh1m
@user-ez1dt2zh1m 8 месяцев назад
Muziyambira pomwe mwasiila guyz mwatani kodi
@user-jw5dh6md1z
@user-jw5dh6md1z 8 месяцев назад
Gaga ati muthinda wapasidwa mangwala
@BentryKumwenda-ze2gn
@BentryKumwenda-ze2gn 8 месяцев назад
Muthinda ndi mole more fire😂😂😂😂😂😂
@franciscoduartie5762
@franciscoduartie5762 8 месяцев назад
Mwatipanikiza😂😂😂 Zili sharp
@rabsonjali7697
@rabsonjali7697 8 месяцев назад
Kkkkk chifuniro ..... pangolin
@RAZAQJAMES
@RAZAQJAMES 8 месяцев назад
Ayiiiiii 51 sanaikite bwino chifukwa ikanayambila ku milandu
@MisheckAselo
@MisheckAselo 8 месяцев назад
Komatu Tonde umakwana 💪
@KhimzyMike13
@KhimzyMike13 8 месяцев назад
Koma chifuniro amandiwaza heavy ❤
@mickarison7488
@mickarison7488 8 месяцев назад
Chifunilo more fire 🔥😂😂😂😊
@patricksinyala1345
@patricksinyala1345 8 месяцев назад
Kkkkkkkk Chifuniro woyeee!!!!!
@user-oz9mr6rc5d
@user-oz9mr6rc5d 8 месяцев назад
Muthinda 😂😂😂😂😂 kusisa mfundo 🤣🤣
@gracekwapata
@gracekwapata 8 месяцев назад
Mwati mwanayo akakhala wa mkazi azakhala Queen eti?ai zikomo. Chifuniro umatha aise
@ZyduUmar-yw9nb
@ZyduUmar-yw9nb 8 месяцев назад
🤣🤣🤣😏🤣🤣🤣 Koma chifu mwadya 1 amuna statu osewa ako
@ThandoHazel-zz7ru
@ThandoHazel-zz7ru 8 месяцев назад
chifuniro kuno yooh🔥
@user-nz8zr9rl6j
@user-nz8zr9rl6j 8 месяцев назад
Mole iyambe ukudikila chan kkkkkkkkkk❤❤
@user-pu9kk6lk7f
@user-pu9kk6lk7f 8 месяцев назад
Boyizi tiyeni nazo 😂😂😂😂😂
@siskanyirenda
@siskanyirenda 8 месяцев назад
Chifuniro chiphetsa amuna😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@user-uf1tz7bp5q
@user-uf1tz7bp5q 8 месяцев назад
😂😂😂😂km nganga Moto Kut buuuu
@matembanevermind-po3me
@matembanevermind-po3me 8 месяцев назад
Kkkk km apa February nde eeeee
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 8 месяцев назад
Kkkkkkkkk koma ndskomoka gaga
@user-oz9mr6rc5d
@user-oz9mr6rc5d 8 месяцев назад
Gaga kusokoneza 😂😂😂😂
@jaffargeorge3477
@jaffargeorge3477 8 месяцев назад
Here we go❤❤
@edgarlastone
@edgarlastone 8 месяцев назад
😂😂 chifuniro uphesa anthu 😂😂😂
@user-kv7ye6jn9y
@user-kv7ye6jn9y 8 месяцев назад
Chifunilo umaitha never change ❤❤❤❤
@shupikayintuwaluwa-5899
@shupikayintuwaluwa-5899 8 месяцев назад
More fire
@mwanawevhudangwe7772
@mwanawevhudangwe7772 8 месяцев назад
Dora i like yo smile
@Festonsaulo1
@Festonsaulo1 8 месяцев назад
Nice
@user-xx4oz8yw7x
@user-xx4oz8yw7x 8 месяцев назад
Chifunilo umakwana inayo changu kumeme😂😂😂
@mosewallace9717
@mosewallace9717 8 месяцев назад
more fire 🔥
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 8 месяцев назад
Kodi anazombe aja asinthanso dzina kkkkkkk davie ometa mmbali
@user-hx8zk4dt5d
@user-hx8zk4dt5d 8 месяцев назад
Kd ku bangwe munazala kale kale ndikudabwa chimangaci
@anniewhite3497
@anniewhite3497 8 месяцев назад
Gaga suzatheka😂
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en 8 месяцев назад
Gaga kusokoneza kkkkk
@JuniorHardward-dk5pe
@JuniorHardward-dk5pe 8 месяцев назад
Kkkkkkkkkkk chifuniro mofire moto unandi guys
@alfredbatumeyo9191
@alfredbatumeyo9191 8 месяцев назад
Tonde izanthera ma penalty 😂😂
@user-de8vx6bh9q
@user-de8vx6bh9q 8 месяцев назад
Koma ikanayambila Kwa mfumu kesa kkkk
@matembanevermind-po3me
@matembanevermind-po3me 8 месяцев назад
Kod zinthuz mumajambuliratu? nanga chimanga chomakhala nd ngayayechi?
@NkhwaziB
@NkhwaziB 8 месяцев назад
Thanks. Frank Likhomo, for the background sound, i really enjoy it.
@user-hz8hp7md6c
@user-hz8hp7md6c 8 месяцев назад
Jane yo kod zikukhala bwanji Guys
@franciscoalexandre4168
@franciscoalexandre4168 8 месяцев назад
Chifuniro😂😂
@SleepyBeach-akawp5uy
@SleepyBeach-akawp5uy 6 месяцев назад
Tonde wayaka
@georgeamosi9931
@georgeamosi9931 8 месяцев назад
Komatu Muthinda😂
@goodwinnyirenda9679
@goodwinnyirenda9679 8 месяцев назад
Kwavuta 😅
@ZyduUmar-yw9nb
@ZyduUmar-yw9nb 8 месяцев назад
tonde Mooo fayaaa 🤣🤣🤣ATI akati Hwee ineso Hwee kkkk dola tsopano kuwakana bamboo ako 🤣🤣🤣😏🤣😏 bamboo ako ndi bamboo ako basi Kaya ndi mphawi Kaya ndiwakuda Kaya ndiwamaonekedwe otani vomeleza Kuti ndiomwe anakubeleka nanga utani 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 agaga kkkkkkk mulongolola mutopa makwale ayiziwa
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f 8 месяцев назад
Zilibwino❤❤❤
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 8 месяцев назад
Chifuniro mimbayo ya mezi ingati koma jjjjjjjjjj
@user-bn4bh3mo5i
@user-bn4bh3mo5i 8 месяцев назад
Gaga ati muthinda chifunilo wamudyetsa mankhwala
@jameskazembe1123
@jameskazembe1123 8 месяцев назад
❤❤
@blandinabonaventure
@blandinabonaventure 8 месяцев назад
Gaga mmmmm osasiya
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 8 месяцев назад
Ncy😂
@KimChisola-gm7yw
@KimChisola-gm7yw 8 месяцев назад
Chifunilo uphesa amuna kkkkkk
@yesayabongwe4234
@yesayabongwe4234 8 месяцев назад
Chifuniro apweteka anthu uyu
@user-gb1po5ql2e
@user-gb1po5ql2e 8 месяцев назад
Zio umakwana
@user-jw5dh6md1z
@user-jw5dh6md1z 8 месяцев назад
Chifuniro 3 in 1
@user-zj3bu3lm9f
@user-zj3bu3lm9f 8 месяцев назад
eish chifuniro umatha
@jameskadete2196
@jameskadete2196 8 месяцев назад
Koma muthinda mwana wankazi mpaka king
@macksonchimalizeni44
@macksonchimalizeni44 8 месяцев назад
🔥🔥🔥🔥
@user-oz9mr6rc5d
@user-oz9mr6rc5d 8 месяцев назад
Makwale phuma 😂🤣😂🤣😂
@user-yd7ks8tv5y
@user-yd7ks8tv5y 8 месяцев назад
Mmm koma tonde ndi 1 palibenso
@KenedyJolamu-rs9xx
@KenedyJolamu-rs9xx 8 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🔥🔥💪
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en 8 месяцев назад
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@user-ty5ih9uo3r
@user-ty5ih9uo3r 8 месяцев назад
chifuniro ❤
Далее
TONDE WADULA EPISODE 52
26:25
Просмотров 18 тыс.
TONDE WADULA EPISODE 113
27:54
Просмотров 18 тыс.
Zamalove Episode 006
30:05
Просмотров 18 тыс.